Ku MCP Kuli Nkhanza - Samuel Lwara

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ส.ค. 2024
  • Samuel Lwara, today discusses Intra- Party Politics in the Malawi Congress Party and his experiences dealing with State House.
    Samuel Lwara, lero akukambirana za ndale zamkati pa chipani mu Malawi Congress Party ndi zomwe adakumana nazo ndi State House.
    #malawi

ความคิดเห็น • 24

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i หลายเดือนก่อน +3

    Munayakhula bwino koma misiye kulimbana ndi APM alibenanu. Zifukwamumuwuzeso chakwela ndinduna zakezose azipanga zawo amusiye APM

  • @tamikathadzi
    @tamikathadzi หลายเดือนก่อน

    You are a legend Mr Lwara. I love your wisdom, I wish these leaders had this kind of wisdom. They are so consumed with greed and they can't even see the bigger picture

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน +1

    Good Messnge Mr Rwala

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 หลายเดือนก่อน +1

    May Tonse Alliance leaders accost the H E and redress the current national teasers.Learn to canvass amicably to bring solidarity where there is schism.

  • @user-uv5rf4zt5q
    @user-uv5rf4zt5q หลายเดือนก่อน

    Greedy and dictatorship is worsening in Malawi is the poorest country in the world.

  • @LumbaniNeba-d9n
    @LumbaniNeba-d9n หลายเดือนก่อน

    Mwayankhula bwino Mr Larwa

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl หลายเดือนก่อน +1

    Inu ndimakusatani koma pamene mwamunyoza peter takutulukani iweyo munthu wako sukugwira ndi wachabe

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 หลายเดือนก่อน +1

    Nkaka akulembanso MSCE 😅😅

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน +1

      Ndiopanda nzeru mfiti yopanga ndale usiku

    • @user-xt2ic5gg1g
      @user-xt2ic5gg1g หลายเดือนก่อน

      Akulembera kuti

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

      @@user-xt2ic5gg1g Akulembera ku nyumba kwake. Paja MCPigs ndi ya katangale.

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน

      😂😂😂Nde ngati ankhonze zikhala ndalama zomwe wa bazo alibe busy kuhonga kuti amuuzire mixeeeee

  • @christopherchikankhen
    @christopherchikankhen หลายเดือนก่อน

    Zaziii

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 หลายเดือนก่อน

    Ine ndimadabwa Kodi athu akusaka inu amenewo ana awo alibe kuti muwapheleso ana awo kuti AVE pain Mene imawawila?

  • @beakab2378
    @beakab2378 หลายเดือนก่อน

    Ati kuchipatala ndinakumanakp ndi atumbuka anzanga anandithandiza.....kkkkk okheeee😂

  • @user-lr5bz7qk2d
    @user-lr5bz7qk2d หลายเดือนก่อน

    Chakwela ndi wakuba ndi chifukwa nduna zake zakuba sazichosa chifukwa iyeso ndi mbava ku Kenya president wachosa mbava zonse koma Galu ayi chifukwa naye mbava

  • @MarkinaJohn
    @MarkinaJohn หลายเดือนก่อน

    Ndmakulava sumaopaso same as DC

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

    MCPigs ndi ufiti

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw หลายเดือนก่อน

    Zovuta kwabasi

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9d หลายเดือนก่อน

    Zikhale ng'oma ndi kapee

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p หลายเดือนก่อน

    Give people direction not just talk

  • @NedsonKavala
    @NedsonKavala หลายเดือนก่อน

    Mcp timayidziwa tikadwabwakuti mukati yasitha komatikadziwakutisinasithe mwanawasatna oroatasaduka gero sarrepherakuchitazakwao