Momwe zikukhalira ulamuliro wa m c p mosogozedwa ndi chakwera ndizachiwikire kuti kwa munthu aliyense wa m'boma yemwe azilimbana ndi munthu aliyense ozuzula boma la chakwera kwamunthu amuneyo azingoyembekezera minyama masoka umphawi kusayenda kwazinthu zipite kwamunthu ameneyo ndiye iweyo chakwera chimwendo nkaka biry malata musiye kulimbana ndi kalindo muzaona zoopsya m'manyumba mwanu upresidernt wake uti osonkheranawo ?🎉🎉🎉🎉
Ndmafuna ndi part ya bon Kalindoyo ..zinazo zikagwere
Zoona tikufuna part ya bon kalindo
Bon kalindo yoweeeee❤
Viva Bon kalindo ❤
Bon azatiyimilila Bolan akhale wachilungamo ngati mmene analili pule wakale ngati bingu wamutalika God bless you bon
Mr Bon Kalindo agwetsa bomaaaaa❤❤❤❤ Vivaaaaaa
Kalindo oyeeeeeee💥💥💥
King kalindo❤❤❤❤
Booooooon kalindo moto kuti buuuuuuh ❤❤❤❤❤
Bon kalindooo woyeeee
Bon Elias Kalindo 🔥🔥🔥 Viva Malawi First 🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥
Bonr kalindo ❤❤❤❤
Waaaaaaa woooooo the DC
Viva bon viva bon
bon kalindo ❤💙💗
the dc wathu wathu
Chipani chantendele!! Koma iwe galu kwabasi 😮!!!!
Viva booooooon kalindooooooooo
Bon kalindo the dc ❤❤
Vava the DCccccc viva❤
Kodi Ntambo ndiye alibe mulandu pamene ankapangisa ma Demo?
Mtendere wa kongolesi ulipati????
Mkaka ndi wachamba
Bon ndinyatwa
Tili pa mbuyo pan mr Dc
Mwana wina oopsa alinso ndi dread kumbuyoko 😂😂😂😂😂
The DC mwana oapsa kwambiri
Tili pa mbuyo pan mr Drc
Chipani chantendele nde chiti? 😂😂😂
Bon azatiyimilila basi
Bon kalindo ur number ndipo mukawasumire amulipe kalindo
Howaaaaa mkaka😂😂😂😂😂
Mnyamata wake nayeso wayamba kupota tsitsi🤔🤔🤔
Kosowa zochita ma member a mcp
Moto bon kalido
Sugar ati wayamba kupezeka nanga mtengo udakali okwerabe
eti ATI chamtendele
Momwe zikukhalira ulamuliro wa m c p mosogozedwa ndi chakwera ndizachiwikire kuti kwa munthu aliyense wa m'boma yemwe azilimbana ndi munthu aliyense ozuzula boma la chakwera kwamunthu amuneyo azingoyembekezera minyama masoka umphawi kusayenda kwazinthu zipite kwamunthu ameneyo ndiye iweyo chakwera chimwendo nkaka biry malata musiye kulimbana ndi kalindo muzaona zoopsya m'manyumba mwanu upresidernt wake uti osonkheranawo ?🎉🎉🎉🎉
chipani chatendelele iwe ndi gulu kwabas
Chipani camtendere onenayo ali mbuu kutuwa ngati wadzola fulutsa
Koma plz can u tell me more about that boy behind this man
bodgurd wakalindo....Ndi mmalawi km wakhalitsa ku china..18 years ali ku china ku xool yadza hiya huwa.😂😂😂😂... ndimfana ot maguys amapatsa ulemo
The dc
Chipani cha m c p sichojoina
Mwana opusa iwe chipani cha mtendere kut ndwe galu kwabasi
Kodi galu iwe umangotenga nkhani ku times kumaoneka Dolo apa. maso tuzutuzu
Iweyo vuto lako ndi chani kweni kweni
Kodi muzingoti kalindo anaonga zinthu Kodi madermo omwe ankachitika ndi achinantambo munthawi ya DPP kunaphedwa anthu angati katundu waanthu anaonongeka ochuluka bwanji ? Kodi apeter alipo anamusegulira mlandu ? Sono chifukwa choti chakwera usogoleri wakowo ukusogoleredwa ndi satana ndiye ukufuna uzilimbana nri anthu okuzuzula ? Palibe chokhalisa kudziko kuno boma mwalephera achakwera mutu owumawo .