ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Zomatchula aleluya andale musiye!! Zikumatinyasa mulungu sapanga ndale.
Ambuye mulungu amphavu zonse tipaseni mfumu yotikonda mutisankhire ndiinu poti mfumu yomwe iripoyi zikuchukuluka nkhadza kuba kupha kuononga amen
Fantastic speech guys ❤
Achewa kuyerekedwa wakubvutani chakwerawanu
More fireeeeeee sister mwayankhula bwino kwabasi Mulungu akudalitseni❤
zoona wazuru sakwatira mkhonde yomweyo kkk
Sure
Sindimayembekezela, awo ndiye mau zabwino zonse more fire!!!
Amayakhula ngati sanapiteko kusukulu kmnso akhangati sakudziwa zomwe zikuchitika muno Malawi zimvereni chisoni
Uku ndye kuwawanyaaaa kwekweniiii....🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Maloto achumba.Aford will never be the ruling party in Malawi.Mark my words
Mcp sidawinepo chisankho, boma iliri ndilatonse . Eee koma kuwaulatu
We are now fighting for democracy in a Democratic state kkkk embarrassing indeed
Aaaaaaaaa !!!! Zonama izi ngat chakwera mukuona kt akuononga dziko ndie kt inuso mukuon muli mgulu lowonga coz inuo muli momo mu TONSE ALLIANCE
Moto ngati umenewo ndi umene tikufuna kuchokera Ku zipani zosusa fire!!!!!!!!!
Eee apa Moto walavulidwa hvy kugagada 🔥🔥🔥🔥
Apm my vote ✊
Mpaka kunena kuti "ndi inu ndani akanyimbi inu?"
Koma ine ndawusa manja anthu chilungamo akuchisata🙌🙌🙌🙌
Chilima my vote 2025
Ndagwira mau amodzi akuti athu mu katopa simuyang'anaso za munthu kuti anali ndani zimenezi ndi zomwe zichitika 2025 DPP MY VOTE 💙
Powerful!!!! 💪💪💪
Big up Afford kuswa kuswa basi.
AFORD you deserve 2 points👍
Simbiyamoto number one ❤
Anthu a afodi iiiii amatha mbalume eishiii
Koma chakwera Ufa ndi mtimaAthu atopa nawe payakhulidwatu apa
Ndipo kwambiri
2025 tiona zinthu
From Capetown chakwera must go
Mai chilungamo muyakhuladi ulemu wanu. Zowona Ndithu
EKC my vote
Ndikanakhala olemera bomali ndikalanda mwaupandu, Anthufe tanzuzika kokwana palibe chikusintha
DPP + AFORD more fireeee!!!❤
Malawi is the best in Africa, Aford mwayankhula, i think chakwera he must resine he failed, all the way from johannesburg cbd
Anthu amayakhura eeeeee wandare usazamudelere
Nthawi yakwana Afford Moto !!!
Mwayankhura mwamphamvu mayi
🔥 📛
Tikufuna anthu olankhila chochi osati kumaopa agalu mbava za mcp
😂😂😂 Koma Mdala uyu waswa Mr Chihana ndi a Ntambo yendani limodzi ndi Mdala ameneyu akudziwa kuyankhula.
Zowona M'dala ameneyu amapalula mbalume, No mantha or Manyadzi iai ayende naye M'dala ameneyu pa Campaign imeneyi.
Don't trust in politicians you will get disappointed.
Utm my vote
Chakwera mbuzi ya munthu sazalowanso komanso afford ili kutali ndi Boma
More fire
Anthu anawawata tu ku Mponela!!! Eish!!!
Bola achewa mazindikila 😂😂😂😂😂
Dpp is only my last hope not Aford
🤣 🤣 🤣 Koma afford nde yayaka moto DPP my vote APM
Kkkķkk Zoona ❤
Koma sister wake wa Ntambo zikomo
Aford is not our hope. The first president comes from my home area but nothing cannot be shown they did even after being given 2nd vice presidency
Tamvanan nd Dpp ma guy muyatsa moto
Very true brPlease
Zoona zake
Sitikuso mawu achionvwe ayi tikuna fudo zabwino achimwene ndale zonyozana zinatha kale kale
Chihana yomweyo 😂😂😂❤
Ndipo ndizoonadi akulimbana ndi kukhapa athu m,malo mokoza zithu zitsilu za wathu achoke atikwana
Madam menya menya chilungamo chioneke.
Kkkkkkkkkkkkkkkk Afford ikutenga boma boma lake litii azalamulira ku Rumphi konko ngati analephela Chakufwa chihana awa ndi andani
Mkazi walankhula mawu
Dpp boma limawakhara
Apm my vote
Aford atha kugwesa mcp anthu atopa ndi mcp
Following
Zoona achoke ameneyu kwakwana watizunza kwambili
Tell them the truth guys amarawi asukusura eya muzipanga choncho kuno kujoni anthu ndiwomwe amaramura boma osat boma kuramura anthu rimbani ntima amarawi chosani mantha timawopa murungu osat munthu nzako ayi
Km kumeneko kwachako bwino 😢😢😢😢
Kodi Aforld ndi chipani kapena club?? Fundo mukulankhuladi koma ku Malawi kuno sitikudziwani ndiye kaya mutani
Kuyankhula kwa phamvu.. 🔥🔥🔥
Malizan chuma chachihanacho
Dpp moto my vote is dpp
Ali nd maloto achumba awa, Afford ingawine? Hahahahaha akudzinyenga kwambiri
DPP woyeeeeeeeeeeeeeee❤❤
Mwan'galula kkkk
Maloto a chumba aford kulowa my boma
Malawi true meaning of dziko lapasi
Waitha ase ma speach enawa sitimaaziwa
Kuyesa madzitu kumeneko kkkkk mcp ikuwinaso or tisafune
andale awa musatitole n tinatopa nazo kagwelen
Zabvuta ndizo 😂😂😂😂
Zabodza tu izi moti afford mungagwetse mcp?mwakhuta gagatu inu😅😅😅😅😅😅😅😅
Sikut anthu alibe mantha ayi bro koma zonsezi ndi zoona coz sakuwanamizira zinthuzo zikuziyankhula zokha
Awa oro atakiwa chotani sangawine ndipo sizizatheka
Ponyelani kwa Kuya a Malawi akuphula njelwa zamoto
aford yomweyo. moto bhooo
Mbava izi zimene zakamba ndit za nzeru
Apm hope for Malawians
Wapenga
Achewa opusa awa atisawukisa amalawi sitdzakuvelani ayi
Koma chaka chamawa kuli zinthu tandipitisireni uthenga kwa mzimayi wavala dress 👗 ya AFD ayambe kutumikira mulungu muli utumiki mwayiye
Never Afford will not rule malawi unless otherwise, keep on dreaming
Iwe Mangochi, usatinyase ndi chizungu chako choola chothyokatyhokacho... Iwe tilibe nawe ntchito ndipo sungatithandize. Ife ndi The DC's followers...wadya chisikono galu iwe ungotithera data bundle wopanda phindu iwe.
Aford ilindimbalume koma vuto singawine payonga olo zitavuta ikuyenela kupanga mgwilizano
APM my vote
Kumakhala ndi chisoni ndi chikondi chenicheni pliz pension ikakwana osamakakamiza adzapuma liti kuti adyerere pension?
Maloto a chumba kkkkk
DPP bomaaaa
Afford muli kutali kwambiri
Mukuwona ngt ndi odzavota amenewo kkkkkkk nkhan mukufuna kuwononga chuma chamalemu chihana malizan tilimila limodzi fodya
Kkkkkkk kk auzechilungamo
Chokan akuba Inu lelo amalawi tinapenya muli ndimaloto owononga chuma chamunthu agalu inu
Ana inu
Ndieno muli Kwa lukwa!?
Kodi ichi ndi chipani
Kulangula muveka
vote spliting
Chipani cha rumphi
Mcp tikhadzula mwachipongwe
Koma wamva iyeyo kkkkl
Andale nose ine sindimawapasa ulemu
Zomatchula aleluya andale musiye!! Zikumatinyasa mulungu sapanga ndale.
Ambuye mulungu amphavu zonse tipaseni mfumu yotikonda mutisankhire ndiinu poti mfumu yomwe iripoyi zikuchukuluka nkhadza kuba kupha kuononga amen
Fantastic speech guys ❤
Achewa kuyerekedwa wakubvutani chakwerawanu
More fireeeeeee sister mwayankhula bwino kwabasi Mulungu akudalitseni❤
zoona wazuru sakwatira mkhonde yomweyo kkk
Sure
Sindimayembekezela, awo ndiye mau zabwino zonse more fire!!!
Amayakhula ngati sanapiteko kusukulu kmnso akhangati sakudziwa zomwe zikuchitika muno Malawi zimvereni chisoni
Uku ndye kuwawanyaaaa kwekweniiii....🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Maloto achumba.
Aford will never be the ruling party in Malawi.
Mark my words
Mcp sidawinepo chisankho, boma iliri ndilatonse . Eee koma kuwaulatu
We are now fighting for democracy in a Democratic state kkkk embarrassing indeed
Aaaaaaaaa !!!! Zonama izi ngat chakwera mukuona kt akuononga dziko ndie kt inuso mukuon muli mgulu lowonga coz inuo muli momo mu TONSE ALLIANCE
Moto ngati umenewo ndi umene tikufuna kuchokera Ku zipani zosusa fire!!!!!!!!!
Eee apa Moto walavulidwa hvy kugagada 🔥🔥🔥🔥
Apm my vote ✊
Mpaka kunena kuti "ndi inu ndani akanyimbi inu?"
Koma ine ndawusa manja anthu chilungamo akuchisata🙌🙌🙌🙌
Chilima my vote 2025
Ndagwira mau amodzi akuti athu mu katopa simuyang'anaso za munthu kuti anali ndani zimenezi ndi zomwe zichitika 2025 DPP MY VOTE 💙
Powerful!!!! 💪💪💪
Big up Afford kuswa kuswa basi.
AFORD you deserve 2 points👍
Simbiyamoto number one ❤
Anthu a afodi iiiii amatha mbalume eishiii
Koma chakwera Ufa ndi mtima
Athu atopa nawe payakhulidwatu apa
Ndipo kwambiri
2025 tiona zinthu
From Capetown chakwera must go
Mai chilungamo muyakhuladi ulemu wanu. Zowona Ndithu
EKC my vote
Ndikanakhala olemera bomali ndikalanda mwaupandu, Anthufe tanzuzika kokwana palibe chikusintha
DPP + AFORD
more fireeee!!!❤