GWEDE-GWEDE WA LERO KWAYAKA MOTO🔥🔥21 May 2024

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 20 ก.ย. 2024

ความคิดเห็น • 41

  • @KimChisola-gm7yw
    @KimChisola-gm7yw 4 หลายเดือนก่อน +8

    Ziko silikuyenda bwino nchifukwa mabanja akutha nanga ndalama zothandizila pa banjapo azikatenga kuti poti ntchito ndizochita zobweresa ndalama sizikupezeka

  • @Edwardtolo
    @Edwardtolo 3 หลายเดือนก่อน +2

    Ngati Dausi eee ndiwadyela kwambiri samadziwa chimene akuchita

  • @jameschibwana2751
    @jameschibwana2751 4 หลายเดือนก่อน +6

    Kkkkkkkk..."wa pa Carrier saimba belu, koma nanga bwanji wa pa Carrier sakudumphapo pa njinga po?" 😅😅😅😅

  • @somboka
    @somboka 4 หลายเดือนก่อน

    Kuchoka pa kaliyara kukuvuta,coz pasogolopo tizafunaso azathuwo kuti akhare pa kaliyara ife tizizayendesa njingayo

  • @StevenMbama
    @StevenMbama 4 หลายเดือนก่อน +1

    I love ur hot 265 from South Africa ❤❤

  • @fanuelbanda1228
    @fanuelbanda1228 4 หลายเดือนก่อน

    Akatulukanso mudziti ndi wa phuma, ndi wa dyera?
    Mulibe pabwino

  • @JanuaryGwere
    @JanuaryGwere 4 หลายเดือนก่อน

    Dausi

  • @GraceLakatika
    @GraceLakatika 4 หลายเดือนก่อน +2

    Mmmmm achedwa sitingamukhilupille talila mzaka 4 chomaliza ndi chàmawa❤

  • @edwinnyasulu2088
    @edwinnyasulu2088 4 หลายเดือนก่อน +1

    Program iyi ndaikonda kobasi

  • @Chiso2019
    @Chiso2019 4 หลายเดือนก่อน +2

    Kusayenda kwa zinthu mziko muno kwazetsa nkhanza mmitima mwa wanthu hence high rate of divorce

  • @MrMagombo
    @MrMagombo 4 หลายเดือนก่อน

    Kuli nyimbo ya Ndilibe Problem.
    Munthu wanzeru amadya ndikupukuta pakamwa

  • @WejesWailes-lk4cz
    @WejesWailes-lk4cz 4 หลายเดือนก่อน +1

    Pano nthawi yatha asatuluke amalize ndalama zasalazo bas

  • @DebruyneFavor
    @DebruyneFavor 4 หลายเดือนก่อน +1

    Amalizetse nthawi yawo yatsala pangno

  • @TrysonChimenya4-fm8nt
    @TrysonChimenya4-fm8nt 4 หลายเดือนก่อน

    Mukutambatsula bwino kwambili
    Bambo Steve Banda and Selina timakukondani

  • @GraceLakatika
    @GraceLakatika 4 หลายเดือนก่อน +2

    Tilibe nazo ntchito zawo zimenezo km sitikuwapasa voti

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly 4 หลายเดือนก่อน

    Guy's Chilima ndi mfana woganiza Bhooooo ndi mfana wapa NSIPE nu. Inuyo pheeee eeeee mlandu wawinatu Kokoliko ndi Dzilembwe zonse paulendo

  • @Laurent-h9u
    @Laurent-h9u 4 หลายเดือนก่อน

    Nice program

  • @RelaxCool-dp9jn
    @RelaxCool-dp9jn 4 หลายเดือนก่อน

    Munandiyankhulila bwino kwambiili fusolo chovutila kulumpha pakaliya ndichani kkkkkk

  • @yohanedaudi1740
    @yohanedaudi1740 4 หลายเดือนก่อน

    A UTM Ngati akulota asiyiletu zimenezi chifukwa Kodi a Chilima akhala nthawi yaitali bwanji mu mgwilizano adayankhulapo chiyani zokhudza a Malawi omwe akuvutika

  • @StevenMbama
    @StevenMbama 4 หลายเดือนก่อน

    Bamboo Steve kadona mumakafila mwapeleka bwanji ka example 😅😅😅😅😅

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 4 หลายเดือนก่อน

    Lero mwabwera zeni zeni zikomo chifukwa cha malangizo anu

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 หลายเดือนก่อน

    Wakudikilira victorious

  • @yusuphmangan5081
    @yusuphmangan5081 4 หลายเดือนก่อน

    Kuli tizilombo kutsogolo kwa camera ko plz get them off they are so annoying guys plz

  • @MariamJamalli
    @MariamJamalli 4 หลายเดือนก่อน

    Akuyenera kujowa pa keliyarapo

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 4 หลายเดือนก่อน

    😮there is too much complacency, ego and kudzimva, social media has been partners and spouses to most husbands and wives

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl 4 หลายเดือนก่อน

    Musiyeni mafana oganiza bho mesa atamuganizira kuti walandira katangale mumkati asiye pansi udindo koma iyeyo chifukwa ndi oganiza bho heavy sanasiye mpakana milandu yopanda umboni ija aithetsako lero mukuti achoke ku Tonse iye aliphee akudziwa chomwe akupanga pajatu Pali ma date omwe anagwirizana osoyilana tsiku limeenero likadzafika osamusiyira ndizomwe muzamve po nkhani inu mungoti phee musiyeni mafana oganiza bho yu

  • @evansntokotha6626
    @evansntokotha6626 4 หลายเดือนก่อน

    Inuzifukwazake simukuziziwa zinthu sizikuyenda kuno kumalawi enaife tingonkhalila kuti nanga titani komapalibechomwechikuyenda kuno kwanthu

  • @TrysonChimenya4-fm8nt
    @TrysonChimenya4-fm8nt 4 หลายเดือนก่อน

    Mumpatse moni Abena Chdzanja Bekete
    Mumuuze Unpack program Ku MBC aipatse Moto mosayangana nkhope ngati mmene ankachitila pa gwedegwede!!

  • @wysonmaya
    @wysonmaya 4 หลายเดือนก่อน

    koma bwanji apolisi sapanga athendi pa dziwawa dzikuchitikasi kodi anduna apolisi akutani

  • @BenjaminKamanga-p8w
    @BenjaminKamanga-p8w 4 หลายเดือนก่อน

    Chilima sioganiza bo, saziwa chimene akufuna komanaokomanso
    ananama kwambiri nde bodza linatha loti atiuze

  • @moseskathekeni8848
    @moseskathekeni8848 4 หลายเดือนก่อน

    Mfana oganiza bho ndiopora. Ngati akuona kuti Mcp yalephera kuyendetsa dziko, osatulukamo mu alliance mo bwa.

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 4 หลายเดือนก่อน

    SKC azichoka ku Alliance mukufuna azipita kutiko??? MCP sinawine yokha, iyiyi ndi Alliance...or achite mithulo khalanibe konkoooo tinasonkha nawo over a million votes....Team UTM khalani nchathu nafe ngakhale kuli zokhoma ndiye ndalezo

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 4 หลายเดือนก่อน

    1.Mabanja ena akutha chifukwa, cha mavuto a zachuma omwe Ali mdziko muno.
    2.UDF yapanga bwino kwambir, akamberembere pa ndale asowe zochita. Mwachisanzo MCP ikut DPP inaononga dziko koma chonsecho Ali busy kulandira anthu omwe akuchoka Ku DPP , ndie anthu ngat amenewa angabwerese kusintha kwanji pa ndale???
    3. UTM isapepese nthawi yatha chiona chipande pomola, Langizo a UTM akhale ndi vision asamagwedezeke ndi mphepo ikaomba. Chikhala kut anasunga cholinga chomwe anatulukira Ku DPP mwenzi zonsezi kulibe, koma mtima wa dyera ndie zikhala zovuta kwambiri kut amalawi awakhulupirirenso.

  • @StevenMbama
    @StevenMbama 4 หลายเดือนก่อน

    Koma zamalamulo za 5 year muchipani ndizabwino kwambili athane ndi achina golo change ndi amusonda

  • @MaulidiAtibu
    @MaulidiAtibu 4 หลายเดือนก่อน

    Gwede gwede ndi yausilu ndi ya ku Israel

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 4 หลายเดือนก่อน

    Kutha kwa mabanja khan Nd uphawi zimene zimayambitsa kusamvesesa khan ya financial service
    Any way dziko silikuyenda bwino

  • @LamekiMawindo-kl2cw
    @LamekiMawindo-kl2cw 4 หลายเดือนก่อน

    Zoona

  • @AbuduRajjabu
    @AbuduRajjabu 4 หลายเดือนก่อน

    Kodi tikhululuka bwanji pomwe ife.mitima ikupweteka tikuxuzika chifukwa cha athu ake inuyo koma chosecho inu mukudya manyumba mwanu ma anja anu ife latchele lomwe kusowa nde muziti tikupepesa zichani DPP ibweleso bas

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 4 หลายเดือนก่อน

    Ai pepani pepani utm a gwedegwede onse alephera chilima ndipo amakhalaliranji pamozi ni MCP walephera basi ifeee amalawi tooonse ambiri sitifunanso utm nayenso ntambo ndilephera chifukwa adamuchosa uminisitala

  • @MariamJamalli
    @MariamJamalli 4 หลายเดือนก่อน

    Kungot athuwa akutiona kupusa

  • @WejesWailes-lk4cz
    @WejesWailes-lk4cz 4 หลายเดือนก่อน +2

    Pano nthawi yatha asatuluke amalize ndalama zosalazo bas