ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

DR NAMALOMBA KU LAKHULAPO ZA KUSAKHIDWA KWA DR MICHAEL BIZWICK USI.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 18 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 64

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 หลายเดือนก่อน +7

    Uku ndiye kulankhula kwachilungamo.

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e หลายเดือนก่อน +5

    Mwayakhula bwino mr namalomba ambuye akutetedzeni

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 หลายเดือนก่อน

    That’s exactly good speech!!!!

  • @robertkalima874
    @robertkalima874 หลายเดือนก่อน +2

    A DPP malamulo mumawadziwa koma? Komanso malemu akoma lero chifukwa atisiya? Suja mumati ndi njoka yosafunika kuweta. Use your heads please

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 หลายเดือนก่อน +2

    Very true 😢imfa iyi will stay in our hearts, MTSRIP 🌹,

  • @blessingkamanga1781
    @blessingkamanga1781 หลายเดือนก่อน +1

    After the Death of Bingu DPP was busy that night to abuse the law by trying to replace Bingu with APM.

  • @moirngwira4748
    @moirngwira4748 หลายเดือนก่อน +3

    Malawi has lost a true leader. A man of wisdom. RIP Dr Chilima. It's sad indeed.

  • @PatienceMphuche
    @PatienceMphuche หลายเดือนก่อน

    Kuyankhula kwa umunthu uku Mr Namalomba mulungu akudalitseni ndipo akulise malire anu

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba หลายเดือนก่อน +1

    Replacement ya Bingu before death announcement kuti Peter alowe.
    DPP afuna awoneke ngati Ma angele😂😂😂😂 .izi ndiye mbava za mbava

  • @RobertKingsleyMarevon
    @RobertKingsleyMarevon หลายเดือนก่อน

    Yes kuyankhula mr Namalomba big up

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h หลายเดือนก่อน

    Ku yowoya, unenesko dpp chipani cha mutendele Dpp my vote u munthu nde umenewo

  • @OliverChimsewu
    @OliverChimsewu หลายเดือนก่อน

    Mwayankhula zoona Mr Namalomba,tinataya munthu amene ifeyo timayan'ganapo maso athu kuti azatithandiza ndimaso mphenya amene adali nawo.

  • @user-bm5yg6zm3c
    @user-bm5yg6zm3c หลายเดือนก่อน

    😂😂Koma dziko ndi ndale eee anakonza lero DPP kulira kuli kufuna mavote a UTM 😂😂😂

  • @GeaorgeMussah
    @GeaorgeMussah หลายเดือนก่อน +1

    Ndizowona ife tikulira maliro sitingakhale tikuvina bale wantchu titaluza😢

  • @user-ro9qb2gg9h
    @user-ro9qb2gg9h หลายเดือนก่อน

    Palibe cha nzeru mwalankhula apa paja ukakhala otsutsa umafuna kukhala wa nzeru..

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 หลายเดือนก่อน +1

    Ndipo ndi zoona DPP ndiyoferedwa

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu หลายเดือนก่อน +1

    Osati boza lnu enafe president wanthu anamwalira osati lzi zamanganya yudasi uyo anamupereka chilima

  • @user-xs3pk1vp8i
    @user-xs3pk1vp8i หลายเดือนก่อน

    Namalomba usatitsokoneze mitu wamva pangani zanu ndi gogo wako wa DPP

  • @user-mf7hf7we2u
    @user-mf7hf7we2u หลายเดือนก่อน

    Namalomba mudzaziona mukadzatenga boma

  • @RobertChipatala-ow9vn
    @RobertChipatala-ow9vn หลายเดือนก่อน

    Namalomba wasowa chorankhura pamenepa, ndibwino akanangoti ndiribe mawu .

    • @user-un6qv6sj3h
      @user-un6qv6sj3h หลายเดือนก่อน

      😂😂😂bro choyankhula ndichimenecho

  • @isahMapemba
    @isahMapemba หลายเดือนก่อน +2

    Koma ndizoonad umuthu uzikhalapo nanga malikhwelu ameneaja zulo ayi sizoona

  • @williamsalexmbonga
    @williamsalexmbonga หลายเดือนก่อน

    Malamulo azikhala ndi umunthu mmmmmh inu ndachitsilu eti who made the constitution Dr Laz M Chakwela?

  • @SteveKachilala
    @SteveKachilala หลายเดือนก่อน

    Malawi and politics

  • @RABSONSIKELO
    @RABSONSIKELO หลายเดือนก่อน

    No one above the laws ....lamulo likuenera ligwire ntchito posaendera umunthu or chikhalidwe

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt หลายเดือนก่อน

    I mourning SKC RIP

  • @user-bc2mu2ns5n
    @user-bc2mu2ns5n หลายเดือนก่อน

    Koma Malawi umunthu udaticgokeladi eti inu A DPP Chilima akome lero poti watisiya? Si zija Peter Mtharika akhala kuti anakuchosani mu Boma mwakhala mukumunyoza lero mukati eni imfa kuti chani sopano? Ndipo mwachita bwino kubwela poyela taziwano kuti Maliro mwapezelapo campaign umboni ndi ma 1 billion timawona ngati kulila kuli kunyengelela kuti mloweso mu Boma.

  • @GloryShera
    @GloryShera หลายเดือนก่อน

    Malamulo wakupanga mbanthu wene wawo wa wangasinthaso

  • @user-xd1cm7tm7t
    @user-xd1cm7tm7t หลายเดือนก่อน

    Namalomba nice tolk

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s หลายเดือนก่อน

    eeeee kuyankhula kopanda chigamba thank you namalomba

  • @shuraimuwamama2349
    @shuraimuwamama2349 หลายเดือนก่อน

    Pajatu chilungamo chimawawa anyapalawa mchaka sakumvetsa,point yawo akuti imfa ija yawawa kusonyeza kuti mphamvu alibe musakakamile,imfa yatameki ndiyodwanzika imakhala yosiyana kalilidwe khalani ndi umunthu point taken

  • @SamsonJenala
    @SamsonJenala หลายเดือนก่อน

    Chakwela samagwila Muthu Kodi tisiwisen zoona

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 หลายเดือนก่อน

    Chilimatu ndale anayambira ku DPP ndiye a MCP chilichonse akuyesa ochenjera adzaziona

  • @henryhenry6632
    @henryhenry6632 หลายเดือนก่อน

    Nambalomba tauzen zoona amalawi kuti a dpp mukanali buzy kusangalala kumwa wine 🍷 ndi imfa ya achilima

  • @user-rf4br1fv2z
    @user-rf4br1fv2z หลายเดือนก่อน

    Izi zikufunika mukakambilane ku nyumba ya malamulo anthu adayamba kukakhula kuti wadutsa thawi

  • @user-ft2bg6om7s
    @user-ft2bg6om7s หลายเดือนก่อน

    DPP maboza kulira kuposa eni ake maliro? Lamuro ndi umunthu ndizosiyana zikuwapweteka awa ndipo sazabwelanso muboma

  • @IssaKapalamula
    @IssaKapalamula หลายเดือนก่อน

    Mumafuna asankhe wa mcp, kuti mupezerepo zoyankhula kuwagawanitsa a utm ndi mcp😂😂😂

    • @RaymondKaumba
      @RaymondKaumba หลายเดือนก่อน

      Zoona .anthu awa ndi a chameleon

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r หลายเดือนก่อน

    Sichifukwa choti inu kaya mzalowa m boma kapena ayi koma ndinu chisilu adpp mulibe nzelu nkuona mathangisa anzanu mchipani nzelu mlibe

  • @user-jb5yb9wq3y
    @user-jb5yb9wq3y หลายเดือนก่อน

    It's too early, samayenera kusankha panopa mlowa mmalo ai

  • @thomaskalima7379
    @thomaskalima7379 หลายเดือนก่อน

    A Namalomba ndinu member of Parliament, bwanji osakasintha malamulo????

    • @user-rl5zq1qr4d
      @user-rl5zq1qr4d หลายเดือนก่อน

      Kusintha malamulo si kwa a Namalomba okha komanso lero ndi lero sizingatheke aphungu kapena phungu amangopereka maganizo oterwo kenako nyumba ikambirane komanso a dzamalamulo awunike ngati ndikoyenera kutero sasintha ngati Malaya monga mmene Inu mukuganiziramo 😂😂😂😂😂😂

  • @BenardMwale-g9x
    @BenardMwale-g9x หลายเดือนก่อน

    Pitala wakoyo adameza miyala sadzafa anthu oipa kwambiri ngakhale mumayankhilako mulibe nzeru mfiti pano malonino akhala mwamtendele kwambiri

  • @BenardMwale-g9x
    @BenardMwale-g9x หลายเดือนก่อน

    namalomba palibe chimene uzayamikila ngakhale adakasankha mkazi wako

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of หลายเดือนก่อน

    Koma ndale za anamalomba ndizoseketa kwa basi

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os หลายเดือนก่อน +1

    Mwayankhula bwino kwambiri a Namalomba

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq หลายเดือนก่อน

    Nalomba Usamati president wathu ayi chakwela ayi agalu yu chichakwela mbudzi yachakwela chi machendake jfe kumalawi tidzakhala ndi president 2025 Peter muthalika ndamene tikudikila

    • @YusufMillion
      @YusufMillion หลายเดือนก่อน

      Uziyambira kutchula machende a bambo ako aja usananene amunthu wina

    • @YusufMillion
      @YusufMillion หลายเดือนก่อน

      Uilondole ku nyanja konko nkhalamba yakoyo izikakutuma kokagula kachasu😊😊😂😂

    • @estherkambewa7791
      @estherkambewa7791 หลายเดือนก่อน

      Kutukwana ndikumene anthu ambiri sitikonda dpp, mukatukwana mumasonyeza kuchepa nzeru ndipo mukuchotsa ma voti

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน

    Awa ndi achisilu kwambiri chilichose chandale chomwe angalakhule Mesa chilima munamukana

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole หลายเดือนก่อน

      Kodi iweyotu ndi bwampini palibe chamzeru chimene umachiona kamtima ka ngona ku mcp kwakoko usamatinyase apa 😢

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj หลายเดือนก่อน

      @@SolomonNjolomole panyapako pa mako wava

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole หลายเดือนก่อน

      Udachokera kutiko swiswiri iwe paja adakuponya mchimbudzi chitsiru chamunthu iwe.

    • @williamsalexmbonga
      @williamsalexmbonga หลายเดือนก่อน

      Mmafuna asankhe vice ku DPP

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r หลายเดือนก่อน

    Boza inu adpp inuyo mwasangalala kuti achilima amwalila bingu anamwalira koma lamulo linagwila ntchito inu mwaziwona liti anamalomba ndinu ausilu msapange ndale pamaliro ayi

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

      Amene mwasangalala ndi inu a MCP sipaja mukufuna Chakwera apezeke pa ballot paper.

    • @JeanKambala-gm1zr
      @JeanKambala-gm1zr หลายเดือนก่อน

      Mulungu akunkhululukile iweyo wa MCp iwe anthu 9 anafa Anja iweyo Uli gulumo

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 หลายเดือนก่อน

    Za ziiii

    • @User_n6-8n
      @User_n6-8n หลายเดือนก่อน

      Zilikutiko