Zikomo adad popereka ulemu kwa rate vice president ndi anthu ena 8 omwe anafa pa ngozi ya ndege God bless you protect you and give you long life♥️♥️♥️♥️🙏
Munthuyi amalikonda dzikoli kuphatikiza late Bingu and SKC. Komano Vuto ma Cadet munawononga maonekedwe a Chipani. Musadzapangenso. Next government is UTM 🔥🔥🔥
@@FranksonKatundulu in life kulimbana ndi mu2 umangotaya nthawi so nkwabwino ngt ukuona kti anakula kungosia kuwapanga suport bas bcz okula omweo anthu adakawapasabe molaro eeeeet.
@@BLESSINGSSTOLO-lt9di if u are a dpp fan just shut up your mouth coz they're a lot of comments there y tagging this message only. Learn to respect other people's views. Case closed 🔒🔒
May the GOD Almighty gives you a good leadership and long life ❤❤❤
Mawu akuchita kumveka kuti uyu ndi president osati mr chikangawa😂😂😂😂
Chipani cha nkhalamba
Koma chipani canzeru ico cokonda anthu ake osakhala cokupha anthu dpp woyeeee
Chikun chachikulu kusungadi moto APM my vote❤❤❤❤
I Love you dad so much Allah bress you dad❤❤❤❤❤
Mkuruyu ndiwa jokes😂😂, and am liking him more and more than ever ❤
WA M CP. Nayeso Ali busy kunvetsela zomwe Adad Akuyankhula 😂 my vote Adad ndi banja Langa 😂
Watching from Peru 🇵🇪. Makosi a Ana.
All the best my our president Dr Peter muthalika
It's professor not Dr🥱 APM woyeee🎉
Ambuye akudalitseni popeleka ulemu kwa malemu saulos Chilima ndi ena onse
Exactly....
Zikomo adad popereka ulemu kwa rate vice president ndi anthu ena 8 omwe anafa pa ngozi ya ndege God bless you protect you and give you long life♥️♥️♥️♥️🙏
The sound in the background is unnecessary please
What kind of journalism is this where you put a sound truck on a speech
Remove that stupid music from background
Please romeve the sound other wise we can stop following you
U can stop following this is democracy baba or mama
Ineso imandinyasa ndisaname
As he say inshaallah
Allah bless u sir allah give u long life
He deserve my vote ❤❤
Adad u loved here in Lilongwe
It is Allah who gives the leadership and takes it... and hope He will give it back to you in Shaa Allah.....❤@Apm...
Masha Allah
Aameen
Ameen Ameen
Maashallah ❤
❤❤❤ munthu koma uyu akuluakulua ndi dambo Mozilla moto ndizowana ndithu
Sure❤
Umunthu 🎉❤
Uwu ndye utsogoleri❤❤❤
APM mumatha ma jokes mpakana mtayanjinga kkkkkkkkk APM nd one
Ur great leader Peter mutharika, God protect u and give u long life
Watching live from Lilongwe. DPP woyeee. Tichose MCP basi
Uyuu ndi president osati chingawa wanthuyi❤❤
APM first priority yake ndi dziko lake❤❤❤❤ 🎉🎉 my vote bwana chongiiiiii
Adad always timakunyadilanndthu❤ anyway all the best to youMr President🇲🇼🔥🔥🔥🇲🇼
APM good idea of remembering the late VP chilima for one minute.
Adad he's a great man
Too old to rule.
😂😂😂 Better than Dr chikangawa @@Jele-mk9ip
Live from Capetown , my president my vote
All the best my president
❤❤❤❤❤❤❤
Apm my vote adada ndi one I love this guy 😂😂😂😂😂❤
💙💙 is my vote for ever 🇲🇼 💪🏽
🎉🎉🎉 boma ilooo
The good leadership APM 🔥🔥
I love you so much dad❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Much love Adadiiii! Dpp for life
Munthuyi amalikonda dzikoli kuphatikiza late Bingu and SKC. Komano Vuto ma Cadet munawononga maonekedwe a Chipani. Musadzapangenso. Next government is UTM 🔥🔥🔥
Za mphamvu 🎉🎉🎉🎉
Kupanda ma cadet bwenzi pano Chilima ali ndi adad asanasiyane koma vuto anthu adyera omwewa ndithu simukunama
Yes i can't wait our victory
Watching live from chikangawa😂... Paboma penipei
ALLAH is the greatest I wish you all the best ❤❤❤❤❤
Ine ndili kunja kuno ku 🇮🇱🇮🇱 koma ndiwonesesa kuti chaka cha mawa ndiyikwele ndenge ndizavote basi 🎉🎉
Vilombo vili busy kulemba against...vayamba kale kuwonda.......akangwingwi.
Adad omwewo kuti whawha🎉❤
Koma amalawi Kaya timafuna chani kwenikweni
Adad 2025 bomaaa🎉🎉🎉 great thanks for the respect offered to the late Dr soulos chilima and other 8 ppls
Taonani ikungoiwala zoyankhula inu
He was just a jokes kkkk
Yawawa😂
Timayembekeza Inu adad tilinganganga pambuyo Pani ❤
Will support you A DAD
Full of confidence muntharika!!!!
May you live long with good health Malawians are ready to take you back to plot nr 1 2025
Tate wa fuko uyu ❤❤❤
Adad mzakhala president ❤ chaka chamawa mulungu anavomeleza kale zimenezi ❤ vote yanga ndizapeleka kwainu basi
Blue hearts and blue blood at the blue camp!!
APM my vote from Zambia❤❤❤❤
DPP 2025❤❤❤
Kudana ndi Dpp ndie eeee zako izo,love you dad❤
Pali zina zofuna achinyamata koma kuyendesa dziko ndi chinyamata very parallel
APM APM Bomaaaaaa ❤❤❤❤❤
More fire ❤❤❤❤❤❤ adad 2025 bomaaaaaaaaaaa
Uyu ndi msogoreli amwene 😅❤❤❤❤
Background sound itayeni inu muzitenga feedback positively and address zomwe anthu akupanga point out. It's to your own benefit mesa
Mawu adad dpp my vote
Kkkk is good nice adadi
Ipondeni dad❤❤❤
adad my vote
Dr raz my vote
Mulunngu pulumutsani Malawi inali nthawi yakusadziwa tikhululukileni
Ndukumvetselani ndithu kuchokela pompano pa nakonde border
Dpp 🎉🎉🎉
Adad my vote🎉🎉🎉🎉🎉
Komatu pali zina umangoona kuti apa ndisatukwane coz otukwana 5 osapota 1mitta umangoziwabe kuti mmmmm apa zatheka basi tiyeni timphunzile kuyamikila
Koma ndiedi osapota 1m kkkk
My vote 🗳
Dpp my vote
Adadi ❤❤
AII the best my president,,,Mulungu akusogoloren
ADad Mulungu akhale Nanu, palibenso mtsogoleri wachikondi ndi odekha ngat inu, DPP ✔️
My god bless you
My vote 🗳 💜
2025 my vote🔵
DPP my vote
Akalambadi awa eti Getrude anakhalapo president wa Malawi? Akapume basi
Chikangawa woooyeeeeee
My vote APM
Apm my vote from msundwe
My vote❤
God bless and protect you APM and almighty DPP
Tengani boma tilandire ndalama zathu za pension zaka zitatu ena angokhala chete
Background musamaike yubowa😊
President wachifundo uyuuu iye akamadya bwino ifenso amatiganizira ka Chipele ndi ka 2L ka mafuta kuti tifewetsr milomo my vote adad
DPP❤️❤️❤️❤️💯💯
We really need DPP back
APM 🔥🔥🔥🔥
Agogo mwakula perekani mpata kwa achinyamata
What do you mean????
@@BLESSINGSSTOLO-lt9di uwauze kt adakula asiye ndale
@@FranksonKatundulu in life kulimbana ndi mu2 umangotaya nthawi so nkwabwino ngt ukuona kti anakula kungosia kuwapanga suport bas bcz okula omweo anthu adakawapasabe molaro eeeeet.
@@BLESSINGSSTOLO-lt9di if u are a dpp fan just shut up your mouth coz they're a lot of comments there y tagging this message only. Learn to respect other people's views. Case closed 🔒🔒
@@FranksonKatundulu but it's nosense.
Ooooh yes❤
Great man of God
Real dad 💗💕
Apm my vote
DPP for life
We love n miss you dad ❤❤❤❤❤❤❤
Mulungu akusogolen Adad
Mumakwana ❤❤
A APM ASAKHALENSO PRESIDENT AYI ANGOKHALA MSANGALASU WA AMSANGALASI WANDIWAZA ZEDI "MWAYESA UFUMU WANU NDIPO MWALEPHELA UFUMU WANU UZAGAWIDWA KWA DPP, UDF, UTM KOMANSO AFORD.