NKHANI YONSE MWATSATANI TSATANI/ NKHANI ZOMWE ZACHITIKA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 56

  • @PETERSINKADZIWA
    @PETERSINKADZIWA 5 หลายเดือนก่อน +2

    I have No doubt Emusipi ndi Chipani Cha Nkhanza

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 5 หลายเดือนก่อน +1

    Ndikunenesa apa Kuti chakwera sangawine akazawina chakwera ndiye Kuti chakwera wabera mavoti chifukwa kunena zoona Malawi wawonongeka ndi chakwera zinthu sizilibwino mpang' ono pomwe

  • @MonicamakwembaKunika
    @MonicamakwembaKunika 5 หลายเดือนก่อน +3

    A police akumalawi palibe chimene angapange chifukwa ndiwoledzela ndi umphawi makamaka akalaya zoti kwatsala masiku 400 kuti ufumu uwu ugwe sakudziwa

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 5 หลายเดือนก่อน

    Chongofunika apa ndichoti, Kuykendall okhonzeka India bouncer a bhobho, ndikungokwanitsa kumugwira olo m'odzi, ndikumutikita mpakana aulule amene akuwatuma ndikumpanga record ngati umboni.

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh 5 หลายเดือนก่อน +1

    Moses kodi umayakhula bwanji?apolice omwe ukuwayakhulawo bwanji anthu omwe adakhapa anthu aku Lilongwe adagwidwa mpaka pano kuli ziii pena moses ukamayakhula uzidziwa kuti naweso udabadwa ndi munthu,komaso pampandopo padali nzako amayakhulaso ngati mene ukuyakhuliramo koma pano adachokapo nde iweyo ukamayakhula ngatitu suzachokapotu pompo.Nde ife tikupepha apolice agwire ntchito yawo yowafufuza anthu omwe apanga upandu akufufuza asayiwaleso kugwira anthu omwe adakhapa anthu aku Lilongwe,

  • @Edwardtolo
    @Edwardtolo 5 หลายเดือนก่อน

    Ameneyo Ali kubali ya MCP Chakwera ndi a police amene

  • @PatriciaMkwenda-xc4mh
    @PatriciaMkwenda-xc4mh 5 หลายเดือนก่อน

    Koma chakwera mtima wake ndioyipa kwa basi nthawi yonseyi m'mene tavutikira munthu opanda kuganiza bwino ndi amene azaponya vote kwa iwe koma munthu oganiza bwino adzavotera ena osati iwe chakwera watikwana ife .

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 5 หลายเดือนก่อน +1

    Achinyamata tizikhala mu umbuli mpaka liti? For how long shall we live such a barbaric life? Chonsecho mnyumba mwako umphawi uli tho!

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 5 หลายเดือนก่อน

      Ndipo zosayenda

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 5 หลายเดือนก่อน

    Koma MCP ndi zigawenga zoopsa ndithu Koma chakwera wulindi wumunthu chilowere mu boma wunawononga Malawi panopa wuli ndi sanje chifukwa wukuziwa Kuti iwe kuyendesa boma walemphera

  • @SinoyaChild
    @SinoyaChild 5 หลายเดือนก่อน

    Aaaaa utsogoleri wabwino umaoneka nizipatsozake apa tikuona mathandizo nizina zotelo zikuchitika komaso zikubwera mdziko lino tiwathokoze achakwera

  • @CharlesChamveka
    @CharlesChamveka 5 หลายเดือนก่อน +1

    Ndizithu zovesa chisoni coz aboma sakuonesa chidwi pa ziwembu zikuchitika.

  • @isaaczidana2914
    @isaaczidana2914 5 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu ndi galu kwabasi, a Chipani cha dpp ana khapidwaso ndi mcp bwanji sakumangidwa?

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 5 หลายเดือนก่อน +1

    Tisadalile apolice chifukwa apolice akumalawi palibe tchito yomwe akugwila tiyeni titanile pa dzina lamulungu chifukwa ndiye yekhayo angatipilumutse ku zikhanila zimenezi

  • @AndersonBishop-i2t
    @AndersonBishop-i2t 5 หลายเดือนก่อน

    Mcp ndi yokupha timaziwa ifeyo kuti mcp ndi zigawenga fisi ndi fisi sangasinthe manga ndie mcp ndi makape okha okha kmaso apolice ndi mdf musamawapange trust kmaso ndi ma judge kod police ndi mcp anaigula panopa ili manja mwa chakwera ndie apolice

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 5 หลายเดือนก่อน +1

    Inuyo a Silvester Namiwa ndiinu munthu yekhayo yemwe akusonyedza kuimilira a Malawi komanso chitsanzo chabwino

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda หลายเดือนก่อน

    Towolananinge waka,

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali7401 5 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu time will come for a judgement day

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 5 หลายเดือนก่อน

    Apolice akumatan ziwembu zikachitika? Naye Nkukuyu mbuzi

  • @HopesonJailosi-vd6ou
    @HopesonJailosi-vd6ou 5 หลายเดือนก่อน

    Akukanika kugwira anthu amene akupangira chiwembu anthu azipani zina koma munthu amene watukwana iwowo, mulungu atithandize

  • @mrsmoseskita9180
    @mrsmoseskita9180 5 หลายเดือนก่อน

    Nduna yaku bagamoyo, RIP Allan wittka

  • @CharlesBanda-kv8bh
    @CharlesBanda-kv8bh 5 หลายเดือนก่อน

    Mai uyu ndiwabodza omenyedwa aja sadanenepo kuti Anthu anavala makaka achipani atawafunsa amangoti mabausa

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 5 หลายเดือนก่อน

    Police singagwile tchito moyenela ndi emusipi gromp imenei koma Malawi anakodza umbuli wausogoleli nde problem

  • @BashielSalade
    @BashielSalade 5 หลายเดือนก่อน

    Koma Mcp siizatheka ndi nkhaza

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 5 หลายเดือนก่อน

    boma lazitsiru ili kumkuyu ndi mbuzi ya munthu ndi apolice apolice ndi a mcp ndimakape

  • @YasinSabili-dj9xe
    @YasinSabili-dj9xe 5 หลายเดือนก่อน

    Kodi akukuyu ndiye ndani galu ya munthu

  • @Francismitengo-w6s
    @Francismitengo-w6s 5 หลายเดือนก่อน +1

    MOSES KUKUYU AND GOVERNMENT MUSAMALE KWAMBIRI

    • @KENETHMAJASA-ud5ee
      @KENETHMAJASA-ud5ee 5 หลายเดือนก่อน

      Ndipo kwambiri

    • @AndersonBishop-i2t
      @AndersonBishop-i2t 5 หลายเดือนก่อน

      Amenewotu azaphedwa akukuyo ndi achimundu banda kmaso ndi azizawo onse mpakana ndi chakwera yemweo ka

  • @Hendersonspoon
    @Hendersonspoon 5 หลายเดือนก่อน

    UDF mfundo yabwino kwambiri zipangisa Kuti atanbwari osiyasiya zipani Kuti asowe kolowera komanso zilimbikisa kukhazikika pa chipani

  • @CardoJustin
    @CardoJustin 5 หลายเดือนก่อน

    Apolicewonso mesa ndi a MCP nso ndiye azifufuza zichani? Za DPP zija si mpaka lero izinso sapanga kanthu

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 5 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu ndi chitsilu kobasi, ndipo adziwa kuti ndi achipani chawo MCP yikuchita zipolowe

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo4099 5 หลายเดือนก่อน

    A police amanganidi anthu awa? inu mukukhulupilira ine ndendakayika kobasi

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 5 หลายเดือนก่อน

    Nthawi yowopsezana inatha kale and tili mu nthawi ya Democracy not one party system, Chakwera ndi mbamva zinzake adziwiretu kuti nthawi yawo yatha.

  • @BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4gr
    @BeatriceMANDEVUGONDWE-iv4gr 5 หลายเดือนก่อน

    Palibeso anthu ena opanga anzawo zipongwe ndi amcp basi, iwe Moses kukuyimbiran usamale ndimbuzi inzakoyo chakwera mbuziyo kumpoto msazabwereko agalu inu

  • @LamiziIgshaan
    @LamiziIgshaan 5 หลายเดือนก่อน

    zopusa agalu inu tikumana 2025 mbuzi zanthu inuu

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 5 หลายเดือนก่อน

    Iya chakwera iwe watikwana ife kumupoto nafeso tikhare ni president wathu basi

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface4282 5 หลายเดือนก่อน

    Kumalawi mwatipanikiza abale kupuma kulibe tikapuma kumwamba

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 5 หลายเดือนก่อน

    Kod awasila bwanj apolic kumachit kt ngakhal apolisio amalamulidw ndi olamul ngakhala A dpp amachit chimodz modz
    Mwaiwal chilam adagendedwa kuthyol

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 5 หลายเดือนก่อน

    Moses kukuyu ndiwe Gulu ndi chakwela 2025 mukupita

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 5 หลายเดือนก่อน

    Chakwera sangatheke olo pang,ono muthu waji osava chison

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 5 หลายเดือนก่อน

    MCP ndi yakupha,

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 5 หลายเดือนก่อน

    chakwera ndi chitsiru

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 5 หลายเดือนก่อน

    A kukuyu ndinu mfiti otamba ndi kudya nyama yayiwisi

  • @MartinMajola
    @MartinMajola 5 หลายเดือนก่อน

    Chakwela mbuzi

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 5 หลายเดือนก่อน

    Namiwa uli bho kwambiri

  • @CharityChirwa-t1e
    @CharityChirwa-t1e 5 หลายเดือนก่อน

    Apolice sangapange chilichose kukhuzana ndichipani cha MCP why apolice athu alimukhwapa mwa chakwela chimozi mozi ngati mene anamuyikila mukhwapa matha chizuma koma pangatalike misonkho ya Malawi mukadya nayo khobwe opanda chele

  • @CardoJustin
    @CardoJustin 5 หลายเดือนก่อน

    Ine kunkuyu kungokumana naye azandipha

  • @DicksonLutere-p9k
    @DicksonLutere-p9k 5 หลายเดือนก่อน +1

    Andale muphana komaso mutukwanana. Akulu akulu aliphee inu umphawi ukuphetsani lekani kutsatila ndale ingodikilani tsiku lovota

  • @BashielSalade
    @BashielSalade 5 หลายเดือนก่อน

    Mcp sizatheka ndi nkhaza

  • @patrickdzombe461
    @patrickdzombe461 5 หลายเดือนก่อน

    Apatu ofunika aliyense kumayenda ndi zida apa diso kulipa diso

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 5 หลายเดือนก่อน

    Cakwera ndi wasatanic palibe comwr angathandidzepo pakhani chifukwa iye ndi yemwe akutuma anthu kt adzivuladza anzawo iyeyo adzitenga magazi adzipita nawo kusatanic cakwera mbusa wakumidima leka kudzudza anthu dziko silako

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 5 หลายเดือนก่อน

    A police akulowelela ndale koma awonatu zovuta

  • @sungananigondwe2807
    @sungananigondwe2807 5 หลายเดือนก่อน

    Kunkuyu machende ako

  • @MustaphaChimangeni
    @MustaphaChimangeni 5 หลายเดือนก่อน

    Panyini pa mayi ako kunkuyu iwe

  • @francischikaya3146
    @francischikaya3146 5 หลายเดือนก่อน +1

    Inu a Namiwa tikukuprmphani kuti kutsogoloko musazasithe mawanga chifukwa sitinayiwale kuti nthawi ya DPP inu munali ku State House. Tikudziwa kuti inu mukutumikira chipani chotsusa. DPP ili m'boma inasakaza ndalama za boma zankhani nkhani pogwiritsa ntchito mabungwe monga Escom, Water board ndi zina zambiri. Kunapezeka anthu ambiri a DPP kusanduka ma millionaire munthawi yochepa kwambiri. Palibe chomwe mungatiuze DPP inalepheranso kukwaniritsa zofuna zambiri za a Malawi. Ma blue night ife sitikuwafunanso.