Mneneri Wakale wa MCP Wazomeleza kuti A CHAKWERA AKANIKA KUKWANILITSA ZIMENE ANAWAUZA A MALAWI?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 22 ส.ค. 2024
  • We are reacting and commenting on what the former MCP publicity secretary is saying about Tonse Alliance Government failure to fulfill campaign promises.. Malawi is Worse off than it was 5 years ago...he admits!!

ความคิดเห็น • 17

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh หลายเดือนก่อน

    Ameneyo ndi neneli wakale nanga watsopano watipo chani

  • @petercaptain4462
    @petercaptain4462 หลายเดือนก่อน

    Very Sad Story 😔😔😔😔😔

  • @StandeyJanafordKandaya
    @StandeyJanafordKandaya 5 หลายเดือนก่อน

    Troo malawian no lidership

  • @richardbanda9997
    @richardbanda9997 5 หลายเดือนก่อน

    Enawo amaona ngati zisintha koma Chakwera ndiomwe amuzungulira ndiomva zao zokha. Kumuopa Chakwera kumuuza ngamo.

  • @richardbanda9997
    @richardbanda9997 5 หลายเดือนก่อน

    Saangavomereze koma akudziwa omwe ali ndi chakwera. Saangamuuze chakwera zoona kuopa kuwachotsa ntchito. Full of promises and lies. Munthali anachokako poona kuti zomwe anagwirizana sizikuoneka.

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 5 หลายเดือนก่อน

    Bro program ilibwino, komano chepetsani Kuyankhula Let Munthu emwe akupanga interview to do her job.

  • @KCS-vk3ce
    @KCS-vk3ce 5 หลายเดือนก่อน

    Iyi ndi commentary si interview.

  • @richardbanda9997
    @richardbanda9997 5 หลายเดือนก่อน

    He is sorry that chakwera has lost direction kkkkkkkk.

  • @mphatsojuliostandy4918
    @mphatsojuliostandy4918 5 หลายเดือนก่อน

    Program yabwino mwayiononga ndi MA comments afoira

  • @mikeaissa1872
    @mikeaissa1872 5 หลายเดือนก่อน

    Akulu musiyeni Leah afunse ma funso ake inu ngati mukufuna muitaneni Munthali mufunse ma funso anu

  • @h-one2656
    @h-one2656 5 หลายเดือนก่อน

    Bro stop this thing of commenting on top of another comment let Leah malekano do her work chonde

  • @KCS-vk3ce
    @KCS-vk3ce 5 หลายเดือนก่อน

    Tikaphunzira kusiyanitsa pakati pa interview ndi reaction timumvetsa munthuyi. Naye ndi style yake.

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 5 หลายเดือนก่อน

    Stop commenting my bro. ukusokoneza kwambiri

  • @AdamsBanda-st9fj
    @AdamsBanda-st9fj 5 หลายเดือนก่อน

    Unnecessary comments within the Leah conversation. Osangotisiya timvere than u commentator. Next time u can do better..introduce the topic then let it flow

  • @user-mq2or1lz8h
    @user-mq2or1lz8h 5 หลายเดือนก่อน

    Iwe ndiye ukuyankhulaso chani isiye kaye interview ithe asss

  • @RodrickMwikho-cj7yq
    @RodrickMwikho-cj7yq 5 หลายเดือนก่อน

    I wanted to say the same. This is a very poor interview. Leave the interviewer to do a good job