Ngongole za Malawi zachulukitsa. Abwana anapita kunja kopempha ndalama.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 169

  • @mussamapira801
    @mussamapira801 ปีที่แล้ว +3

    Achakwela angogwidwa kwachotsa pa u president 90 minutes eterber wakuba

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 ปีที่แล้ว +8

    Usogoleli olilisa kwambiri wa chakwera😢😢😢 Malawi will never forget you

  • @khalidwetchaua24
    @khalidwetchaua24 ปีที่แล้ว +3

    I like you Bro , you know how to analysis things . keep it up !

  • @wisikitiyesi1224
    @wisikitiyesi1224 ปีที่แล้ว +1

    I like you brother thanks you so much

  • @johnman4619
    @johnman4619 ปีที่แล้ว +2

    Zikumveka ndithu munthu wankhuru kumeneko ulemuwamu bwana ...ndizoona ndithu kutikodi awa analindani .big guestion sir

  • @GastonElias-rn2so
    @GastonElias-rn2so ปีที่แล้ว

    Bro i see you a very good analyst, kunena zoona tikifunikadi ma investor enieni kut tiseve zambiri

  • @KingsleyWakusa
    @KingsleyWakusa ปีที่แล้ว +2

    My man,,,,,,,,,,you deserve,,, much respect,,,,achakwela atipha awaa

  • @nelsonmacken7662
    @nelsonmacken7662 ปีที่แล้ว

    Well conclusion bro, that is the fact and reality let's bring people who have something better not mulimi all the way from asamunda no man please Mr president

  • @josephgabriel1016
    @josephgabriel1016 ปีที่แล้ว +2

    Chitini chopanda kanthu chimatsokosa kwambiri ndiye mwazioneratu nokha. Ndimayesa amanama that an empty tin makes noise.
    Thanks bwana pakusakatula maganizidwe aa anthu

  • @chrissygama8678
    @chrissygama8678 ปีที่แล้ว +4

    You are king 🤴 of history in our country 'kma chilungamo China kupweteka ndithu

  • @isaacfesani2357
    @isaacfesani2357 ปีที่แล้ว +3

    Perfect

  • @salomaoernestoernesto4573
    @salomaoernestoernesto4573 ปีที่แล้ว +2

    Ambuye siyani Dr chakwera agwire nchito mukuoneka kut za mboma simuziziwa mbwerera basi za ziii

  • @edwinrobert5346
    @edwinrobert5346 ปีที่แล้ว +1

    Well done brother koma tafufuzaniko za ma passport please malawi wawonongeka wuyu pakufunika ma demo anyone chakwera ndi mphawi wa chabe amene sangatukule ziko

  • @Shaabann
    @Shaabann ปีที่แล้ว

    Thanks God bless you

  • @anafieintuka8090
    @anafieintuka8090 ปีที่แล้ว +4

    🙏🙏🙏 timakusangalalilani achikulire

  • @PromiseBarton-em1ll
    @PromiseBarton-em1ll ปีที่แล้ว +5

    Boma ili nde zero pa zero.😢😢😢

  • @andersonmaster8055
    @andersonmaster8055 ปีที่แล้ว +1

    The king of history

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 ปีที่แล้ว

    Kkkkkkkkkk Eeee!!!!!! Koma ndie kwapephedwatu...kungozolowela Chachikhumi.mpaka kukapepha Company yopanga juice.

  • @BladesBullets-pu5uw
    @BladesBullets-pu5uw ปีที่แล้ว +1

    Zomwe zimandimvetsa Chisoni ndizoti mtsogoleri wadziko akamalephera kugwira bwino ntchito yake pali anthu ena osaukisitsa omwe akuponderezedwa ndi mtsogoleriyo, muwaona akuimbira mmanja ndikumamuchemerera mtsogoleriyo. Ndife olilitsa zedi.

  • @HolickLemajomo
    @HolickLemajomo 15 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkk inu ndi big bas amangoona ngat zimangobwera ngat mana lerodi cyclone Freddy yasanduka bizines sopano 😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😅😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂

  • @georgemponda
    @georgemponda ปีที่แล้ว +3

    Koma iwe ndikatundu madzi😂😂😂😂😂😂😂😂🎉🎉

  • @irenechirwa9710
    @irenechirwa9710 ปีที่แล้ว +1

    Bwanji angotula pansi maudindo awowo tatopa nawo ife anthuwa

  • @johnkayisi4043
    @johnkayisi4043 ปีที่แล้ว +2

    😢 iiih koma ine chakwera 😢😢

  • @phillipstamaley7901
    @phillipstamaley7901 ปีที่แล้ว

    Always I disagree with you but now totally! totally agree with you accordingly

  • @LastoneBottomane
    @LastoneBottomane ปีที่แล้ว

    Kupempha like akupenpha chachikhumi ,he must go!!

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 ปีที่แล้ว

    Mr Atupele anayankhula kale kuti lenara samupasa bus or galimoto,
    Chimene tizawakumbukile agaluwa ndi kuba kowopsa basi ndikupempha pempha. Sindisintha Chichewa changa, kuti mwa Chakwera mulibemo ubwino, munthu wotumidwa ndi satana angapange zokhumba anthu? Mesa akupanga chimene tate wakeyo akufuna? Dont expect anything good from this heartles presdent.

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 ปีที่แล้ว

    Big man ndinu katundu omanga ndi mawaya afukuleni musasiye tiziudziwa usiru wawo akupangawu

  • @subederamado1977
    @subederamado1977 ปีที่แล้ว +1

    Dr chakwera and doog aaaa

  • @MaxBello-nc2gl
    @MaxBello-nc2gl ปีที่แล้ว

    Kodi awa adali ndani?

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 ปีที่แล้ว

    I used to LOVE Boma ili mbuyomo koma pano..
    Aaaaaaaa Zosayenda uyu or atangoyerekeza kuyenda wapasi nditha kusanduka DAVID . mwala utha kugwira ntcito

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessa ปีที่แล้ว

    Program iyi imandisegula maso, ndikunditsuka ubongo

  • @bubakalimustafa
    @bubakalimustafa ปีที่แล้ว

    Thanks u boss

  • @milajimussa4120
    @milajimussa4120 ปีที่แล้ว +1

    Kkk big man kutsitsa mfundo zabwino

  • @staceycossam5933
    @staceycossam5933 ปีที่แล้ว

    Salute bro

  • @Marialongwe-nzlib
    @Marialongwe-nzlib ปีที่แล้ว

    Tikusowa Mpapaya Mkumat Amakambilana Ndi Company zopanga Juice 😂😂

  • @richmondkilembe5449
    @richmondkilembe5449 ปีที่แล้ว

    Chakera awononga ku malawi bwanji mulungu tutandizen tuuu koma ndalama zimenez abweza ndan kod 😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @jimmyharris1330
    @jimmyharris1330 ปีที่แล้ว

    Respect to you my brother

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 ปีที่แล้ว

    Mupange video yoti ma donating a Cyclone freddy anabwera angati ?kikikiikiki Malawi 🇲🇼 😀 🇲🇼 wanthu akulowera ku ntchire. ♥️ Mapeto ake mitengo it itha, koma nawonso they are failing to empower Malawi 🇲🇼 😢 Shaaaaa.

  • @christopherbottoman9131
    @christopherbottoman9131 ปีที่แล้ว

    Big mumakwana koma ndaseka mpaka nthiti kuwawa🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 ndiye mwati chakwela amaganiza bwanji???? Eeeeeee

  • @RahimYusufu-u2b
    @RahimYusufu-u2b ปีที่แล้ว

    Koma nkhawa zanga ndi ndani yemwe angatipulutsr
    2:43 2:46

  • @rodwellmwenekitete8974
    @rodwellmwenekitete8974 ปีที่แล้ว

    Wa udindo aliyetse adziba,, akhulukidwa zili ku Malawi,,,pano palibe kuopa kuba chifukwa chikhululuko chilipo,,,koma tsoka ili kwamuthu ovota palibe chimene chikumukomela muthu otsauka.

  • @luciomodestosimao6650
    @luciomodestosimao6650 ปีที่แล้ว

    Dziko lingatha zimayenda ngati Baibulo. Mwawonjezatu pamenepo

  • @brightbautbright8028
    @brightbautbright8028 ปีที่แล้ว

    Ine sindizabweraso ku malawi kulimose kulimanda ku malawi ndizataniko ndizafe. Ndi njala ine ayi Malawi 🇲🇼 anavunda kwambir chakwara zeru alibe wawononga malawi

  • @wilsonmsoke2060
    @wilsonmsoke2060 ปีที่แล้ว

    Mumatha man keep it upp

  • @symonyohane6989
    @symonyohane6989 ปีที่แล้ว +2

    nothing to say you man you deserve medo koma ndimafuna nditakuona uli ndimawu aboh

  • @patriciakenmuir
    @patriciakenmuir ปีที่แล้ว +1

    Muluzi anali makina mseu wathyolo mulanje its like built yesterday

    • @chrissygama8678
      @chrissygama8678 ปีที่แล้ว

      Kmans mumamunyoza kut sangapange kanthu koma mwamva lero zimene muluz anapanga ķwa anthu amene amazitsata

  • @rodwellmwenekitete8974
    @rodwellmwenekitete8974 ปีที่แล้ว

    Achakwela mukhululukiletso ma prison amene alibe mulandu wakupha,,ogwililila,,ndi opyanya nyumba please atuluseni

  • @jamesmadalitsomchenga5308
    @jamesmadalitsomchenga5308 ปีที่แล้ว

    Atsogoleri a mu africa lero ayamba kutseka zitseko za atsamunda ndipo ali pa mgwilizano wochotsa US dollar mma bank mwao. Pomwe President wa Malawi Ali busy kupempha kwa ma oppressors. A disgraced man. Experience alibe zoona.

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera ปีที่แล้ว

    Ngatikuli program yomwe imandinyasa ndimeneyi yokhuzana mcp ndachizawowa

  • @johnchilima6351
    @johnchilima6351 6 หลายเดือนก่อน

    Tenaon amenyo nchewa wasiru amneyo wanonga Malawi 🇲🇼 akuyesa kuvena gule

  • @hughmankalonga3769
    @hughmankalonga3769 ปีที่แล้ว +2

    Amakakumana ndi Sattar ameneyi

  • @BizweckMasamba-pe5bu
    @BizweckMasamba-pe5bu ปีที่แล้ว

    Munthu wankulu ulemu wanu 👏👏👏

  • @kelvingremphiri565
    @kelvingremphiri565 ปีที่แล้ว

    Komaso trip ya President ya ku Malawi anthu ambiri,there is no war on Malawi but security yambiri

  • @johnshaka3
    @johnshaka3 ปีที่แล้ว

    We need to vote again awa zikuoneka Kuti zawakanika basi

  • @issabwanali29
    @issabwanali29 ปีที่แล้ว

    Keep it up big

  • @Vava-up5dc
    @Vava-up5dc ปีที่แล้ว

    Kodi awa anali ndani?😂😂😂😂 Yankho mulipeza nokha😂😂😂😂

  • @abumussah9766
    @abumussah9766 ปีที่แล้ว

    Is true he think like mana like time of Moses

  • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
    @dhaoudhiabedinegomaseko2363 ปีที่แล้ว

    Chakwera ndi anthu ake nzeru alibe ndipo kaya ndinene bwanji?pena ndimalakalaka ntakhala ujeni ndikuthana nawo andale opusawa

  • @RahimYusufu-u2b
    @RahimYusufu-u2b ปีที่แล้ว

    Koma nkhawa zanga ndi ndani yemwe angatipulutdr

  • @AnordThomson-iw5ny
    @AnordThomson-iw5ny ปีที่แล้ว

    Ntundu umenewu sibwino kuwupatsa u president m'malawi muno chifukwa ndidzilombo, a malawi tinapanga mistake

  • @thegreens9075
    @thegreens9075 ปีที่แล้ว

    Kusowa kolima chifukwa choberekana ngati ntchentche ...palibe chomwe amalawi angapange pawokha .

  • @machonabanda5752
    @machonabanda5752 ปีที่แล้ว

    I think in future Malawi will be part of zambia because it's too much now

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 ปีที่แล้ว +2

    Kwathu kuja amene anatiloza akanatikhululukira 😢

  • @MosesLusale
    @MosesLusale ปีที่แล้ว

    Koma ndiye Malawi tifapo 2 chifukwa anthu amenewa akungoba ndalama basi
    anyway big timakunyadirani

  • @icelenzoaustin9513
    @icelenzoaustin9513 ปีที่แล้ว +1

    Chakwera why 😢😢😢

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 ปีที่แล้ว +1

    😂😂😂😂 ati kodi awa anari ndani ?? Yakho mulipeza nokha 😂

  • @giftgannet6871
    @giftgannet6871 ปีที่แล้ว +1

    Mumatha abwana awa anali ndani awa😂

  • @GiftHaward
    @GiftHaward 5 หลายเดือนก่อน

    Malawi tili ndi madzi ponsenponse koma boma limangoganiza zokuba ndalama zathu iwo kumalemela

  • @chitimbethegreat-pc1bp
    @chitimbethegreat-pc1bp ปีที่แล้ว

    Ndinanena kale kuti mmutu mwa mkulu ameneyo muli mamina okhaokha komanso okuba ndalama za a Malawi

  • @bayview4554
    @bayview4554 ปีที่แล้ว

    Bomali ndilasatanik coz ngongolezimenezo azabweza ndimagazi amalawi ndichifukwa akusowesa mankhwala zipatala ndi chakudya Kuti amalawi azimwalila azipeza ziwalo ndimagazi sure

  • @alicklongwe6375
    @alicklongwe6375 ปีที่แล้ว

    Tht true bro

  • @MaxwellMustafa-ec8fc
    @MaxwellMustafa-ec8fc ปีที่แล้ว

    Zikomo kwambiri abraz we vote MCP out

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 ปีที่แล้ว +1

    BIG 👍

  • @aggogokina8992
    @aggogokina8992 ปีที่แล้ว

    Kudzavuta kumuyiwala chakwera ndi team yake wagwiritsa a malawi mafuwa a moto kudzera mu bodza. Ndithu anthu awa palibe choti angapange choposa kupemphetsa nkumagawana ndalamazo mu team mwawo

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 7 หลายเดือนก่อน

    Anazolowera kusonkheledwa ndi mpigo kumati zabusa kuparsidwa chopeleka kudya zachinkhumi

  • @sammyjonnes
    @sammyjonnes ปีที่แล้ว

    I wish to have chakweras number so that I can send this to him, # this is the most corrupt government in Africa

  • @piliranimphepo1920
    @piliranimphepo1920 ปีที่แล้ว

    Uyu mumati chakwerayu ndi chitosi basi aah!

  • @lewisbonongwe8518
    @lewisbonongwe8518 ปีที่แล้ว

    Mbuzi ya President iyo
    Ananena kale APM
    Kuti ndi Bulutu Chakwera

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 7 หลายเดือนก่อน

    President cakwera tidzamukumbukira kuti anali wakuba wakupha oononga.

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 ปีที่แล้ว

    Usaiwaletu Paja dpp yakoyo imanama kupereka ma figures ndipo ndalamaso paja amkangogawana pachilomwe pawo kumangopatsa muli ndalama azigulila gondolosi

    • @BladesBullets-pu5uw
      @BladesBullets-pu5uw ปีที่แล้ว

      Zoona m'bale siukunama koma ubwino wake tili nacho choloza chomwe pitalayo anachita, kusiyana ndi achakwera osabawa tikungoloza ngongole zokha basi.

  • @MacmillanMakombe-sz4iy
    @MacmillanMakombe-sz4iy ปีที่แล้ว +1

    Kkkkkkk koma ndasekaa kkkkkkkk

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 ปีที่แล้ว

    Please president chakwela leave presidency and go

  • @elidajuma5207
    @elidajuma5207 ปีที่แล้ว

    kutipweteketsa basi olo misewu ya mamidzimu osapalanso yakumbikakumbika nde ndalamazo akungodya kwawoko ayiwala kuti adzafunaso anthu

  • @totaln12potchefstroom98
    @totaln12potchefstroom98 ปีที่แล้ว

    Chakwela ndi mbudzi😅

  • @frankcholimbirapo262
    @frankcholimbirapo262 ปีที่แล้ว

    Kkkkkk km man mwayakhula masikini aulesi kkkk ndie mwat chakwela al mgula lamasikini kkkkkkk

  • @giftmapilaherbalist6803
    @giftmapilaherbalist6803 ปีที่แล้ว +1

    Tcheya mani wa anthu ovutikaa kkkkkk

  • @dilmayankam4052
    @dilmayankam4052 ปีที่แล้ว

    Sibola atsamundawo asatenge malo anga 😢ndikuopa

  • @rowanziya1561
    @rowanziya1561 ปีที่แล้ว

    Mmmm inupenapake paja
    Ndinu audf

  • @pastonmoda6588
    @pastonmoda6588 ปีที่แล้ว

    Akhululuke ndithu Chonde mulungu dalitsani Malawi

  • @ibratime
    @ibratime ปีที่แล้ว

    Iyeyo anali mbusatu basi kenako president

  • @eliaskachali-xn2ve
    @eliaskachali-xn2ve ปีที่แล้ว

    Boma likulamulidwa ndi zigewenga chakwea ndiwakuba

  • @nyararaishumba9288
    @nyararaishumba9288 ปีที่แล้ว

    😂😂😂😂😂 wabaya zed president uyu watitola mudziko Muno kwabas dziko lonse walitenga ngat mudzi wakwao kulamulira dziko ameyesa zibwana eti

  • @joicemartin-ji5zu
    @joicemartin-ji5zu ปีที่แล้ว

    Kkkkk k zoopsa abuse opanda nzeru okuba cisiru mbava yachabe chabe mbuya wakumidima okumwA MAGAZI

  • @ThomSaidi
    @ThomSaidi ปีที่แล้ว

    Anali mkulu wampingo uyu apite akatumikile nkhosa zake

  • @Alex-j4m5k
    @Alex-j4m5k ปีที่แล้ว

    Ichi ndie ayi chichoked 😢😢

  • @popisiphiri-gf5rm
    @popisiphiri-gf5rm ปีที่แล้ว

    Mbatata yamuthu muthu yu kuba anayambira ku assembly

  • @mafukenimasangwi5487
    @mafukenimasangwi5487 ปีที่แล้ว

    Mwayi okwela ndege alibe kkkk

  • @MacmillanMakombe-sz4iy
    @MacmillanMakombe-sz4iy ปีที่แล้ว +1

    Tanditukwanireni ameneyu bwana,

  • @imransamson5308
    @imransamson5308 ปีที่แล้ว

    Mkulu uyu ndi wa BaBulo basi 😂😂😂😂😂🤣

  • @humairamalombe295
    @humairamalombe295 ปีที่แล้ว

    Tell them bro don't get tired