BON KALINDO PA 9 OCT - TIYIWALE ZA MBIRI YA CHILIMA CHIFUKWA AKU UTM AKUFUNA KUGULISA UTM KWA MCP

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 9 ต.ค. 2024
  • AKUTI BASI TIYIWALE ZA MBIRI YA SAULOS CHILIMA CHIFUKWA ANTHU AKU UTM AKUFUNA KUGULISA UTM KWA MCP
    Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

ความคิดเห็น • 76

  • @BatumeyoChikopa
    @BatumeyoChikopa 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +9

    UTM my party and will never end SKC is the winner 2025 mhsrip😢😢

  • @GelsonBandah
    @GelsonBandah 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Zama demonstration zili pati?

  • @Lydia-t4b
    @Lydia-t4b 4 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Now i understand why minister of labour resigned 😮

  • @ConfusedFlamingo-tu9gz
    @ConfusedFlamingo-tu9gz 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Munthu wabodza ameneyu.Tinasiya kalekale kumukhulupilira.Ali MP palibe chimene anapanga oipa uyu komanso wakuba.

  • @MarkBannda
    @MarkBannda 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Chaboza I chi,

  • @thomasmakata8861
    @thomasmakata8861 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Iweyo ukumati kaya ndizoona kaya ukufuna ife tikhulupirire ziti

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Mayi Chilima mudakamusiya pliz a kulira mamuna wake 😭😭Ana akudalira iye pliz midakamusiya

  • @GiftMatewele
    @GiftMatewele 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Akudya ndalama za mcp ameneyu

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    The DCCCCCCCC booooon kalindooooooo mwana owopsyaaa kwambiri

  • @MikeLodzi
    @MikeLodzi 6 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    KUSWA KUSWA NG'ALULAIZATION THE D C booooooon kalindoooo

  • @VivienMalemia
    @VivienMalemia 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Let's pray for our country,,president uyu sakulabada zaanthu ndiozikonda ,,God will punish him

  • @emmanueljelemani4203
    @emmanueljelemani4203 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +4

    Koma UTM party will never die whether Ena alandire ndalama or not, alipo Ena ochepa atachiolotse chipanichi mpaka legacy ya SKC sidzafa

    • @bs-malawi
      @bs-malawi  20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      Amen

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

      Agree with you ndipo sizingatheke ngat usi akuona ngat agulitsa utm ndi anthu enawo mmmmm akunama ndithu

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

      U hv apoint broh ena ndiolimba mtima pitilizan kuyankhul maganiz owalimbisa mtima broh zoona mwanenazi

    • @ChimwemweDemelo
      @ChimwemweDemelo 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      UTM singathe chifukwa Cha anthu adyela never

  • @GomahiyaArsenal
    @GomahiyaArsenal 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    UTM mukuganiza bwanji guys ndalama yokhayokhayo imeneyo mpakana kugulitsa chipani simuzapeza mtendereinu aai zikomo

  • @Jackisonbanda03
    @Jackisonbanda03 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zione Kalako

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    They will sell the name UTM but the followers will return to the mighty blue party DPP....
    NDIPO MCP palibe kuwina..

  • @AndersonDPaul
    @AndersonDPaul 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Following

  • @MisheckMwachipitsa
    @MisheckMwachipitsa 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bon Kalindo mmm

  • @MirriamRaja
    @MirriamRaja 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthu mukutsutsanu muzazindikila bwino patsogolo

  • @kasimujuma1511
    @kasimujuma1511 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zekomo Dc

  • @GiftMatewele
    @GiftMatewele 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nakha aifewa atibwelesele km bz kuba

  • @ConnexbraveMapondo
    @ConnexbraveMapondo 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Katundu madzi the DC

  • @GiftMatewele
    @GiftMatewele 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo afuna chani ky

  • @GeoffreyShariff
    @GeoffreyShariff 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Malawi 🔥

  • @GiftMatewele
    @GiftMatewele 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bon kalindo pano anabwelad

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akunyeraomwemo uwu akuyalutsatu panja ku UDF akutulukila

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Na zankhondo sukunama Kalindo Iran Hezbroh Lebanon ndi Palestine panop yakwiya ndpo apapa kutha kwa Israel

  • @JailosPhiri-sk5ji
    @JailosPhiri-sk5ji 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    mmm koma Malawi

  • @overtonekanyenda9400
    @overtonekanyenda9400 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zopanda phindu bodza lokhalokha anthu anakutulukani kalekale

  • @GiftMatewele
    @GiftMatewele 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    tikumana povotr achenjele pano

  • @JoelNaphulu-p4p
    @JoelNaphulu-p4p 11 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😮😮😮

  • @MonicatimanyeShaba
    @MonicatimanyeShaba 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Utm singa gulusidwe tizawona zenizeni pakutha Kwa zose 17 September bus mabizaso aku chuluka kwambili

  • @emmanuelmanda2537
    @emmanuelmanda2537 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    If this is true, I will be a disappointed member for life....and will affect negatively many lovers of the party.
    I just hope it's FAKE NEWS !!

  • @Jacksonmuhackeya
    @Jacksonmuhackeya 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Dc mukunena zoona anthu awa amalimbikila maboza akatero aziti boma ndilomweli

  • @IdahKadewere
    @IdahKadewere 10 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Netanyahu chimwene wake wachakwera kwasala kumalawi nkhondo uzabwera ma Isreal akufuna chakwera abwezele ndalama zawo akudya panozi😅😅😅

  • @HeerahJohn
    @HeerahJohn 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    My country 😢😢😢

  • @GiftMatewele
    @GiftMatewele 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Waboza ndiwe zanga zikuvutilam ungayamikr chakwel aaaaa ukupenga

  • @PhillipChisanu-k3r
    @PhillipChisanu-k3r 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Wamisala adaona nkhondo, akunena zoonadi ameneyu

  • @daviechibwana3137
    @daviechibwana3137 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Paja winiko amakomoka anatiuz yekha mbuz yamunthu uyu akatere afuna atikomokole popez mwez wakhal kumene

  • @P.Mdzinga
    @P.Mdzinga 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zisis za ehova zovumbuluka za ana anthu bs

  • @FatiwelloKatema
    @FatiwelloKatema 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Amalawindife ogonakwambiri

  • @charitykanyenda8831
    @charitykanyenda8831 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Zimvere mtolo, wamzeru wamva

  • @BensonChikopa
    @BensonChikopa 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndizoona kapena ndizaboza,,,,😂😂😂😂

  • @RitchardBandah
    @RitchardBandah 7 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Abon ngat mulib phamv yotenga boma mulibem ingokhalan mutu wanu suyenda bwin

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kalindo muuze Chakwera kuti dzulo lomweri Iran yanena kuti ali 100% kuphulisa Israel ndye muuze Chakwerayo kuti mzake Netanyahu nthawi yake yatha

  • @LeversonMondela
    @LeversonMondela 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndizoona sakunama ayiii

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 8 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkk nchifukwa chake kunkuyu amakana kuti atolankhani azifunsa mu chizungu mbava zokhazokha

  • @NemezioMaganga
    @NemezioMaganga 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    That can not happen to UTM

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma Bon Kalindo mutu umagwira??????

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Humm

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The DC mwana woyipa kwambiri ndimanyadira naye amaswa palipose

  • @charitykanyenda8831
    @charitykanyenda8831 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkk😂😂😂😂😂😂😂ndaseka, akuwapusitsa ma supporter awo.

  • @GodfreyNdhlovu-rm5uj
    @GodfreyNdhlovu-rm5uj 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwana wovuta kwambili the Dccccccccc

  • @stainbanda2424
    @stainbanda2424 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe kalindo ndiwe wabodza, stima ya mafuta itafika un lato simafuts chosecho masna ake stima inayamba kutsitsa. Nthawi zonse mabodza basi. Koma suphura kanthu. MCP ikupitilirabe

  • @AmosScott-z9x
    @AmosScott-z9x 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mulli anaonekako kumenekuja?

  • @EviChio
    @EviChio 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela uli nditsoka zedi chifukwa ukunamiza ndikunzunza mtundu wa amalawi

  • @JAMIELBILLIAT
    @JAMIELBILLIAT 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ine iww sindikukhulupilila zomwe umanena sizichitika..

  • @HenrySabudu
    @HenrySabudu 15 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ngati muliko ku Israel tatumizani ma Video, tikuoneneni ngati simunaphulitsidwe 😂😂😂

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kalindo anapenga

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwera ni galu basi

  • @JeanKabotolo
    @JeanKabotolo 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zovita

  • @EverylessBenika
    @EverylessBenika 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ku isreal kwavutaa eti😢😢😢

  • @FanuelMalanga
    @FanuelMalanga 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sakunama ndizoona

  • @JonaZimpita
    @JonaZimpita 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Galu uyu singayamike

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 19 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndpo zomvesa chson panopa nkhondo yavutira ku Israel ndye wina sakupanga kanthu za anthu ake aliku Israel zachison dziko la Israel panopa ngt layamba kusamusa zinthu zawo kuopa nkhondo ndye winawe anthu ako zikuti bwanji

    • @EverylessBenika
      @EverylessBenika 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @DonataGogwe
    @DonataGogwe 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    L
    P

  • @Danp-q4n
    @Danp-q4n 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    😂umakwana Mr DC put it up

  • @HenryKalimbira
    @HenryKalimbira 16 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Wa Chamba iwe

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 18 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    The Dcçccc

  • @Fanie-i7z
    @Fanie-i7z 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kalindo amanena zoona zokhazokha wopenga ndiwe

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 13 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akalido mulibodzazedi kodi inuyo ndabodza bas mwalemeranawo manodzawa chifukwa mukufuna kuthwilitsa tchito inuyo muzilemera.aaaaaaa wadziwika t