A Bakili Muluzi Agulitsa Chipani Chifukwa Cha Mtima Wadyera - Apostle Austin

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 8 ต.ค. 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Apostle Austin claims that the former President of the Republic of Malawi, His Excellency Bakili Muluzi, has sold the United Democratic Front (UDF) to the Malawi Congress Party out of greed. He makes this claim in addition to another assertion that the MCP is actively paying off opposition parties to prevent them from forming an alliance.
    “Pa Nyasa Voicebox, Apostle Austin akuti mtsogoleri wakale wa dziko la Malawi, Bakili Muluzi, adagulitsa United Democratic Front (UDF) ku Malawi Congress Party chifukwa cha dyera. Iwowanso akuti MCP ikulipira zipani zotsutsa kuti zisapange mgwirizano.
    #Malawi

ความคิดเห็น • 92

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Koma wina amalira ndi alomwe bwanji ndne waku Mangochi makukondan alomwe nonse all Lomwez live long love u from the moon to the back all alomwe

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Alunena zoona ife a MCP ndi UDF ndi PP tili limodzi moti Atupele azakhara vice president

  • @RaffickAllie
    @RaffickAllie 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Koma bwanji tisafurumire kuwerudza chifukwa nthawi idakalipo.and Atcheya ndale sanayambe lero and onse omwe akupanga ndale panowa aziziwa ndi Atcheya ..and nkuru uja ndalama alinaxo choncho palibe wandale angawanyengere kuti apange gwilidzano ndi MCP.koti mukuganidza kuti imfa ya Shanil ija Atcheya akuigonera turo .😊

    • @JohnJohn-og8rt
      @JohnJohn-og8rt 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@RaffickAllie Zikom komazo athu akudabwa ndichani apa tupere ananena kuti ali ndi mcp ananena woka kut ayenda woka ndiyeno pali mvutoso

    • @RaffickAllie
      @RaffickAllie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@JohnJohn-og8rt nkhani ndiyakuti .sakufuna kutapidwa kamwa mudakali mawa .akudziwa kuti .kungoyerekedxa kurankhura monyedza apasa Wallet arrest cholinga kumufoora .iye uja zorankhura alinaxo koma tidikire campaign...

    • @RaffickAllie
      @RaffickAllie 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      @@JohnJohn-og8rt kumasintha kuja bwanji anatisegura maso

    • @JumaKachala
      @JumaKachala ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndizoona

  • @Sofi-p1v
    @Sofi-p1v 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndaitsika udf
    Dpp my vote

  • @driano763
    @driano763 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Osanamapo apa. DPP loves using UDF to achieve their political goals. After Bakili muluzi spent his time, money and energy he was dumped like piece of s…..t. Apa DPP,MCP,UDF,UTM,PP,Aford aliyense ayime payekha then after failing to get 50+1 you can form concrete alliances. Ma alliances opanga nthawi zino ndi aja mukangowina mmayamba kuwaudza ena kuti mukanawinabe popanda iwowo. Komanso why should youthful leaders with energy and vision throw away their ambitions because of old failed leaders. Chakwera has failed and Muntharika analephera kale. We need to be moving forward and way from these failed politicians.

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 35 นาทีที่ผ่านมา

    Hear his toung Mlomwe weni weni. Apostle ogwilira anatu. Mneneli onyenga Mphatso ya utumiki ulibe galu

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zoona Apostle Austin vuto pa Malawi anthu saziwa

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +3

    Atupele muluzi Mai Ake ndiaku lilongwe musiyeni apite Ku MCP koma ife sitingavotere mcp

  • @McDonaldMuyombe
    @McDonaldMuyombe 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Komatu mwavutika. Kodi chisankho muwinira nkhani zolenga basi. Apostle for propaganda 😂😂😂

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komanso sikoyamba ,a Muluzi anapangapo m'gwilizano ndi MCP mu 2009

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Muluzi ndiwa MCP,,😂😂 u are right bro😂

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Atupele Muluzi alibe utsogoleli ,analuza u MP kusonyeza kuti ,alibe Chitukuko

  • @GoldenNamanguya-q9u
    @GoldenNamanguya-q9u 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Atupele sazalamulila malawi chifukwa ndimuthu opusa chisilu chomangomvela zilizose komaso iwe muluzi uzikula kod ndalama zonsezo uzanyamula kumanda

    • @mauricechembe
      @mauricechembe ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Sono nde mukunyozatu Ngati kuti zomwe akuyankhula gang'a wanuyi ziri ndi umboni 100%. Alomwe mukamanyoza Muluzi mmandimvesa chisoni komaso kusayamika kwanu kumawonekera poyera. Alomwe munali ndani Inu kupanda Muluzi? Si munali agalu akapolo achabechabe Inu? Ankakudziwani ndani anyapapi achabechabe Muluzi asanakufukuleni pamatope? Anthu munkachita manyazi even kutchula ntundu wanu. Osamangomuyamika Bakili bwanji

  • @MACDONADLITIA
    @MACDONADLITIA 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chifukwa choti Atupele wanena kuti ayima payekha wabwela opanda Usogolele kodi mukutiona ngati ndife ana?

  • @EdwardSteven-t6h
    @EdwardSteven-t6h 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nkhani yonvetsa chisoni, si paja ali pa mpando iye ankati MCP chipani chakupha? A Malawi akufyza CHITERZE, iye akuononha ndalama kugula anthu ndi kumakopera anthu anthuwo

  • @PatrickChirwa-cv5cd
    @PatrickChirwa-cv5cd 55 นาทีที่ผ่านมา

    Nanga mukufuna UDF ijoine chipani chopha ma albino cha DPP? Chosafunanso anthu akumpoto. UDF mdani wawo weni weni ndi DPP asaisekerere. It's payback time ife a UDF sitingalodzedwenso kuvotera ndi DPP

  • @HamzaAyame-ch3et
    @HamzaAyame-ch3et 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤🙏

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 8 นาทีที่ผ่านมา

    Izizi nzoona Bakili Muluzi ankayankhula yekha pa statement yake okumva anamva

  • @AdyanaAjidah
    @AdyanaAjidah 36 นาทีที่ผ่านมา

    Ndekutiso DPP yagula aford

  • @Adamuson
    @Adamuson 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Galu iwe paribe chomwe ungatiuze ife anthu akuluakulu,osalowelera udani wa anthu awiri bwanji iwe ukulowelela za udani wa anthu awiri??

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aliyese osapota DPP ndimulonwe Kodi?? This is nonsense aaaaa,,zamitunduzo tizisiye Kaye uko,coz mavuto tonse tikuvutikila limodzi,,enanu mungopanga pretend apa yet mwadya chitedze aaaaah tikhalire imeneyo ife😢

  • @NoohNowa
    @NoohNowa ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ATUPELE MULUZI Mutu wake sumayenda bwino 😂

  • @asahelmachila3026
    @asahelmachila3026 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Do not be bothered by Bakili Mluzi's actions. His speech at UDF convention revealed it. He was Kamuzu"s henchman. One could not just hold the post of SG in the MCP of Kamuzu. Bakili anali chief planner wakuponyera anthu kung'ona ndikupa anthu. During his time in MCP, he oversaw the death of Albert Muwalo, Gadama, Matenje, Focus Gwede, Sangala, Chisiza brothers and many others

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 11 นาทีที่ผ่านมา

      Ine wa udf koma ine sinikuifuna mcp ndikufuna dpp mupita nokha Atupele kumeneko ku mcp kma mcp inagwa mbiri yoipa😂😢

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ineyo pandekha ndugwirizananazo zimenezoo,ndipo ndi Zoona,

  • @WitnessCharles-s7p
    @WitnessCharles-s7p 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Atupele uganizebwino Kumachingako anthu akufa ndinjala,mulibe chisoni zoona kugulisa anthu mwakonda ndalama mwandinyasa kwambili

    • @Okalekale
      @Okalekale ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Oh,ndiye kuti chipanicho tikusiyileni ndi chani aku Machinganu eti?,iwowo ndiofunika aphatikizane ndi zipani za ku m'mwera kuti anthu aku Machinga adye?,aMalawi ena alibe ntchito or atafa ndi njala?.Khala nachoni chipani chanu cha a Yao.

  • @HenriqueFrancis-cv6zc
    @HenriqueFrancis-cv6zc 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nanga chair pano ndi Bakili?

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ameneo amcp Agula bakili muluzi ndi mwana wa abakili basi osati anthu oza vota ayi ozavota azasakha kuvotela dpp

    • @MahometAli-e8w
      @MahometAli-e8w 4 นาทีที่ผ่านมา

      Wagula muluzi okha osati ife a udf tipita ku dpp my vote

  • @Adamuson
    @Adamuson 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Satan iwe wabodza ukufaritsa bodza kamba kofuna kuti UDF isankhe kufuna kwako??

  • @RichardChitenje
    @RichardChitenje ชั่วโมงที่ผ่านมา

    ndiinu muthu waboza kwambili

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Atupere yo akamufunse Chilima, ngat MCP imasunga pangano

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi UDF idakalipobe?Munthu kuvotera UDF kumati ingawine?bola kutaya voteyo

  • @MustafaAjalu
    @MustafaAjalu 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chisakho aliyese ndichake ,
    Inu nde mwalandila kwandani ndalama kuti
    Muwauze athu kuti asaza votele udf
    Anyozeni azanu akudya ndalama
    Amalawi kulubwa lubwa bas

  • @AbdullnoorCassim
    @AbdullnoorCassim 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Atupele walakwa UDF idzabvata chipani china

  • @WitnesAkimu
    @WitnesAkimu 9 นาทีที่ผ่านมา

    5b ndiyochepe

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bakili muluzi atupele ndi anthu adyera ndi mbuzi za anthu akufuna iwowo azilemela amalawi azivutika agalu a udf wosavotela ndipo atupele sazalamula dziko la malawi chifukwa ndi wadyera machende ake

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 38 นาทีที่ผ่านมา

    Pamtumbo oako iwe wa Ku Tysolo iwe. Ahlomwe muli pa tchito galu iwe, without UDG mukanakhala ndani ? Kulira uku pamtumbo pako chaka chonse. Okupha Albino pamtumbo pako

  • @stainbanda2424
    @stainbanda2424 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mlomwe ndiwe uli ndi mvuto. Bwanji mungomulola peter ndi dpp ingothandiza Atupeleyo ngati zukuwawani.

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi bwanji alomwe aliense amene sakuchita za DPP ndi mdani wao? Inu a DPP democracy mumaidziwa. Nthawi imene anthu amamenyera kuti kubwere democracy DPP ILIPO? Simudziwa democracy ndi chifukwa chake mungofuna kuti dziko lonse la Malawi likhale la DPP. SHAME ON YOU

  • @StevenFombe
    @StevenFombe 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Muluzi is Mcp guy shadow

  • @MicahNjeleka
    @MicahNjeleka 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kupusa uneneli onama😮😊😅😅😅

  • @PeterMaulana-f4g
    @PeterMaulana-f4g 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Eya ndizoonad wakunva wanva osanva sazanvanso

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Bali Muluzi si bambo wathu kuti angatitsogolele zochita ayi

  • @mikesandali8425
    @mikesandali8425 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe khala buzy ndi maitanidwe Ako osati za ndalezi

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pano akuterera anyani okhaokha basi mabwana anasiya

  • @ThembaShandu-m9m
    @ThembaShandu-m9m ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Or ku votera udf or not sazasaukaso panyopako

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi Austin nthawi imene UDF inapanga mgwirizano ndi DPP inu munali musanabadwe? Ndafunsa chochifukwa UDF inapanga mgwirizano ndi DPP ili mboma bwanji siunadzuke kuti DPP yagula UDF? Iwe ingonena kuti zikundipweteka kuti mwina UDF ikhoza kupanga mgwirizano ndi MCP. Palibe zanzeru ukukamba apa. Iwe isiye UDF payokha iwenso uzipanga za DPP yakoyo

    • @MCAnthonyNdau
      @MCAnthonyNdau 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Austin ndiwe chitsilu Cha munthu kwambili

  • @AbdulazizWyson-dq3ce
    @AbdulazizWyson-dq3ce 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Iwe tupere nde mbuli zoona m,paka ku mcp eee bassi suzalamulanso kumalawi kuno ndiwe kape
    ndipo sindikusapotanso

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    OLO ATAPITA KU CHIKANGAWA BOYS KO SANGAWINE ADZAWAVOTERA NDANI WAPITAKO NDI ATUPERE NDI BAMBO AKE ANTHU OWATSATIRA SANGAPANGE MANYAKA AMENEO

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    UDF sitilola kukhala munkhwapa mwa MCP or DPP sitikuifuna tipita tokha kumasakho win or lose

  • @KapoloWachitsanzo
    @KapoloWachitsanzo ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ukunama m'bale

  • @Adamuson
    @Adamuson ชั่วโมงที่ผ่านมา

    UDF tidalowa iwe usanabadwe galu wa munthu iwe ndiwe ndani iwe

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Inuyo a dpp ndinu ana pandale…MCP inakuphumitsani Boma APM atalumbiritsidwa kale nde what makes u think mungawine pano muli kunja kwa boma?
    Alomwe inu joke too much 😅

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma mukamati simukulola kukhala munkhwapa ndizipani zina mukafika ulendo wanu chifukwa or kutsutsanso simaysutsa nao

  • @ChimwemweMathyola
    @ChimwemweMathyola 5 นาทีที่ผ่านมา

    Munthu amadananacho chilungamo

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ufulu wa Atupele ndi umenewo. VN yake yopanda mfundoyi.

  • @ConradccjSokoSoko
    @ConradccjSokoSoko 13 นาทีที่ผ่านมา

    Choka

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ife tidatuluka kale

  • @JenalaMsowoya
    @JenalaMsowoya ชั่วโมงที่ผ่านมา

    JESUS IS ON THE THRONE
    Mbewu zomwe timazala ndi zomwe timakolora... Mukudabwa chani? Mbewu zomwe timazala 2020 ndi zomwe tikukolora Panopa.
    Come 2025 mbewu zomwe tizazare ndizomwe tidzakolore zaka za kusogolo zikubwerazo.
    Ubwino wa Mulungu amavomereza chiganizo chomwe iwe mwini wapanga ndicholinga choti uzasowe ponamizira.
    Tiyeni nazoni.

  • @Adamuson
    @Adamuson 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Stupid Apostle bwanji osangonena kuti ndiwe wa DPP bwanji??

  • @MicahNjeleka
    @MicahNjeleka 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kupusa uneneli onama

  • @starneckkulemero7548
    @starneckkulemero7548 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Stupid wa DPP iwe ungolira lira Mesa iwe DPP ndimene inasokoneza UDF....alomwe oyipa inu wodzikonda.

    • @tasmania527
      @tasmania527 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Anthu amenewa ndi afiti, osayamika, asankho, ndi ozikonda osati masewera. Zikuwawawa za UDF kkkkk, amva bwino.

  • @johnkambala692
    @johnkambala692 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mabodza mwakalamba inu

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Uziti Aford ikuima ndi alomwe osati ikuimira aMalawi

    • @tasmania527
      @tasmania527 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Aford ilibe mojo(support)kumpoto. DPP is wasting its time

  • @ChiefJustin-l5p
    @ChiefJustin-l5p 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Muli ndi umboni wanji

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndiye ngati alibe utsogolleri nanga nanga Atupele ukulimbana naye chofukwa chiyani . Leave Atupele alone.

  • @ClementsKamanga
    @ClementsKamanga 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Aaaa munthu angavotele ppp

  • @WonganiKatchale
    @WonganiKatchale 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pepani kwambili

  • @GiftJulius-ro9ev
    @GiftJulius-ro9ev 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Agalu a Dpp anthu osowa khalidwe munatiphela chipani mbolizanu..

  • @RichardNsanama-m4q
    @RichardNsanama-m4q 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Ameneyu alibe fundo.
    Kuyankhula kwa muluzi kunali kubwelesa umodzi monga malawi.
    Komanso ameneyo wadya ndalama ku Dpp kut alimbane kunena za UDF.
    Mmene tazuzikila ife a udf ndi Dpp. Chopangila ngwilizano sindikuchiwonanso

    • @MchachaGoodson
      @MchachaGoodson 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Iwetu ndi modzi mwa abuli.amenene sukuziwa kathu
      Lather keep quiet.

    • @JohnJohn-og8rt
      @JohnJohn-og8rt 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      🎉zoona Zikom uyu chisilu

    • @Evelyn-q1o
      @Evelyn-q1o 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Abalalitsa anthu okonda udf cause iwo omwe a Bakili Muluzi anankhala akulalikira kwa nthawi yaitali za kuipa kwa mcp lero sangatiuzenso za ubwino wa mcp awa never

    • @mercerblair4841
      @mercerblair4841 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Mudzachiona chikadzakula even achina kalindo anena zimenezi

    • @GoldenNamanguya-q9u
      @GoldenNamanguya-q9u 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Man bakili muluzi ndiwadyela Muthu amene amangosamala zake ndichifuka chipanichi chinatha kukonda ndalama

  • @abdulhameed7808
    @abdulhameed7808 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Vuto lawo apostle austin ndichani mmesa chipanichi ndichawo anayambitsa wokha

  • @MicahNjeleka
    @MicahNjeleka 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zabodza😅😅😅

    • @MicahNjeleka
      @MicahNjeleka 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Zabodza akunenazi uneneli onama kufuna kinchuka

  • @Adamuson
    @Adamuson ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Don't bring your personal issues with Atupele and Bakili to all of us. Iwe ndi galu God will punish you for this lie mark my words

  • @EstherchavulankhomaNkhoma
    @EstherchavulankhomaNkhoma 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndiye udziunikile wekha Kodi DPP ndipaniso mwatisokonezakale inu

  • @JohnWame-u3l
    @JohnWame-u3l ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ineyo pandekha ndugwirizananazo zimenezoo,ndipo ndi Zoona,