ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

ma banja awiri aphedwa ndi anthu olusa powaganizira kuti ndinfiti ku tsangano ndi Angonia .

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 27 ก.ย. 2022

ความคิดเห็น • 23

  • @sergiopauloposse7610
    @sergiopauloposse7610 ปีที่แล้ว +1

    Tristeza. obrigado pela informação Balanço Semanal e toda equipe da Rádio e comunitária Angonia.

  • @AnnieBanda-ws5wu
    @AnnieBanda-ws5wu 6 หลายเดือนก่อน +1

    Mmm

  • @gudjaman5810
    @gudjaman5810 ปีที่แล้ว +1

    Sizili bwino zavutilatu a Thu akuzitenga ngati zili mufacho m,pamene sidelo ndine rosa kuno ku Maputo 🙏🙏🙏🙏🙏😭😭😭😭

  • @jfj-bu5wz
    @jfj-bu5wz หลายเดือนก่อน

    Mmmm Koma anthunii dzikoli. Ulemu Wanti nosse bs chanel

  • @christinaibbu4339
    @christinaibbu4339 ปีที่แล้ว +1

    Km kulakwa wallah asking,anga ndiofuna kudanutsa

  • @pililanibuliyani7684
    @pililanibuliyani7684 ปีที่แล้ว +2

    Nkhani iyi imafunika Agova

  • @frankdzombe8929
    @frankdzombe8929 ปีที่แล้ว +3

    Komatu Ku tsangano pakufunika boma litengepo mbali kukuchitika zinthu zosakhala bwino thank you guys mukugwila ntchito yaikulu

  • @iankenneth
    @iankenneth ปีที่แล้ว +1

    oky km achakwera akubzibziwa nanga atipo chiyani

  • @zainabchikakuda6297
    @zainabchikakuda6297 ปีที่แล้ว +1

    Abare dziko lupita kuti? Ambuye azikutetezani pamene mukujambula zoterezi Ameen,from Chiradzulu

  • @johnarushamasese108
    @johnarushamasese108 ปีที่แล้ว +1

    🔥

  • @lydiaamos4214
    @lydiaamos4214 ปีที่แล้ว +1

    Anthu angophana Ngati nkhuku, apolisi tenganipo gawo

  • @jvpondan4332
    @jvpondan4332 ปีที่แล้ว +1

    Koma mesa mumati chilungamo chimamasula?nde kuti chilungamo kupweteketsa eti anthuo ayankha bwino bwino bwanji chonchoo

  • @frankmaluwa5120
    @frankmaluwa5120 ปีที่แล้ว +1

    Zinthu zosakhala bwino, sakuyenera kutero onani myoyo itatu yatayika

  • @gifitygetho342
    @gifitygetho342 ปีที่แล้ว +1

    Triste

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu2599 ปีที่แล้ว +1

    Nkhani yosakhala bwino konse ayi

  • @pililanibuliyani7684
    @pililanibuliyani7684 ปีที่แล้ว +1

    Agova ali kuti Kodi

  • @mariamhalid9185
    @mariamhalid9185 ปีที่แล้ว +1

    Zovetsa chisoni

  • @carlosadelinoamor3189
    @carlosadelinoamor3189 ปีที่แล้ว +1

    nkhani yovetsa chissoni

  • @josuahkachali1489
    @josuahkachali1489 ปีที่แล้ว +1

    Very bad watching live from Kuwait