History ya Ku Malawi ndiyosokonekera imaphatikizidwa ndi bodza kamba ka kaduka ndi tsankho, ofunsidwayo akakhala mngoni amakokera Ku chingoni,akakhala msena,amakokera Ku chisena,mu Yao,kuchi Yao, Mulomwe Ku chilomwe Akakhala mchewa ndiye anawonongeratu History yonse kotero amkati zonse mMalawi muno ndi za Kamuzu Banda,moti ine kale ndimkayesa kuti Kamuzu ndi Mulungu ndi pachibale ndipo adali ngati mng'ono wake
Big Up brother ❤❤❤
Andale mudzivetsetsa apa palibe corruption is true story in history
Thanks guys we need it kind of that story please u must bring it More
Zoti nthaka ya Malawi ndiya Queen ndi zoonadi ndithu
Kuluyi ndidoro
Mbulizina zimati misewu yakamuzu komaso coffee ndi Tea amati anayambitsa ndi Kamuzu,,,muzinva history 😂😂😂😂
Mm mm yatheramalele
Bakili muluzi tv inayamba chonchi
Eeee koma zandiwawa bwanji😭
History ya Ku Malawi ndiyosokonekera imaphatikizidwa ndi bodza kamba ka kaduka ndi tsankho, ofunsidwayo akakhala mngoni amakokera Ku chingoni,akakhala msena,amakokera Ku chisena,mu Yao,kuchi Yao,
Mulomwe Ku chilomwe
Akakhala mchewa ndiye anawonongeratu History yonse kotero amkati zonse mMalawi muno ndi za Kamuzu Banda,moti ine kale ndimkayesa kuti Kamuzu ndi Mulungu ndi pachibale ndipo adali ngati mng'ono wake
Dzikomo kwambili tamva nawo ndipo taphuzila history ya dziko lathu