This program is best of the best programs mostly to those who like this country.Times can make someone to stay in power or out of power unfortunately politicians never know.I like you guys I wish nditazakuonani pamaso mpamaso including Brian Banda mukudziwa anthu osaukafe timamva kuwawa km timaonekabe olimba chfukwa mumatiyankhulira.Long live times,Long live Hot current and times exclusive,Long live Wonder,Jonar,Ochunga and Brian.
Guys you have worked very hard this year dare or truthful zonse mwazipanga well done guys pitilizani ndithu kuwasegura mitu amalawi mu 2025 happy new year 🎉🎉🎉🎉🎉
Koma tinakakhala ndi njila yoti tisamadalire zolandila. Why? Tili ndi lake Malawi from chitipa to mangochi and Shire river from mangochi to Nsanje Why chaka chilichonse kulira ndi njala, mkumadalira zolandila. This must end...
Malawi azatheka kukazabwela President okonda dziko lake and akazangoyika lamulo loti oba ndalama za Boma Life imprisonment no any Lawyer allowed to represent him. that alone will transform our Nation.
for the point of bishop nsusa as ochunga says; he was speacking as who to answer quastion, i would say that ask brian banda to call bishop nsusa on time exclusinve interiew and then you will be able to know the trueth about that. by the wy nothing wrong with what archbishop nsusa say and he was right thats the trueth
This program is best of the best programs mostly to those who like this country.Times can make someone to stay in power or out of power unfortunately politicians never know.I like you guys I wish nditazakuonani pamaso mpamaso including Brian Banda mukudziwa anthu osaukafe timamva kuwawa km timaonekabe olimba chfukwa mumatiyankhulira.Long live times,Long live Hot current and times exclusive,Long live Wonder,Jonar,Ochunga and Brian.
Ndipo live sukunama
Guys you have worked very hard this year dare or truthful zonse mwazipanga well done guys pitilizani ndithu kuwasegura mitu amalawi mu 2025 happy new year 🎉🎉🎉🎉🎉
Work well done indeed ma hot currents
Happy happy new year 🎉 APM my vote for next year
Zitsiru za zibusa kametedwe ngatii okuba😂
100% guys , no.1 program. Moti George Kasakula adziyamikila azibusa amene aja pa program yake pa MBC .😂😂😂😂.
Amen chirima akutiwawa ndisaname ndithu marawi tikurira kharidwe rake anari nditima wozichepetsa skc koma ambuye munaroreranji kuti ramuro ra anthu awa nkhumbo rawo richitike zowona achakwera mtima wanga ndikawawona akundipweteka kwambiri ndisaname khope yawo sindifuna kuyiwona achimwendo nkukuyu akundiwawa siku ndirimozi murungu ariko
Mulungu ndiwoopsa kwambiri ngakhale atagwiritsa anthu ambiri kubisa chilungamo koma mulungu amagwiritsa anthu ochepa choona chidzakhala poyera izizi ndiye azidziwe
Ku mcp waononga chipan ndi chimwendo banda,ndipo izi chakwera azandivomereza kusogolo
Thanks for running the full programme from the beginning
😂😂😂😂koma guys brother awa amandifikapobwanji more fire wonder
Chimwendo munthu oyipitsitsa ndipo master planner yonse ndiiyeyo .
Chakwela ndi president ochitisa manyazi kwambili akukhawulisa athu kwambili why why anapha chilima iwe lazaro mulungu akusende iwe
MCP za Chilima nde musaganize anthu tizaleka kuzikamba ng'oooo. Inu mpaka mutuluke m'boma kenako muzamangidwe
😂😂😂😂kumakhala ndikanyadzi guys 😂😂😂😂
Your so critical guys keep it up
Nice program kuyakhula wosawopa 😂I love you guys 😊
Am attentively listening to the conversation a good wrap up of the year always respect you guys and love your program
Chakwela Asaoneke Ngati Dolo Popha Chilima Nayenso Akufunika Afe Amalawi Tisamapuse Kuonelela Anthu Akuphedwa Chonchi. Chakwela afeso Nayenso asakhale president 2025
Nde mwati chimwendo kkkkk kma boy's
Ndizitsilu zaanthu zimenezija azibusa akumadzi ameneaja
😂😂😂😂😂 mwanena mwanena basi ndipo ndi za chambadi zeni zeni n no need to withdraw sir😅
Zimbani zochuluka zikukana kupanga alliance ndi mcp chifukwa cha fungo lakanyimbi lomwe akununkha nalo mmm ziwavuta ndithu😂😂
Nkhani ya a Bishop mususa unali ulaliki ndipo muulaliki wawo anayikamo maganizo awo pa nkhani ya report ndipo izi zimachitika azibusa amapereka zitsanzo kapena maganizo.Ndipo mboni yomwe akunena kuti anajambula chilichonse ndi MULUNGU.mawu anga omaliza ulaliki sitimayankha kapena kufunsa.
Koma tinakakhala ndi njila yoti tisamadalire zolandila.
Why?
Tili ndi lake Malawi from chitipa to mangochi and Shire river from mangochi to Nsanje
Why chaka chilichonse kulira ndi njala, mkumadalira zolandila.
This must end...
Nkhani imakhala kuti do you have capital to do something better kuti usamadalire?
Adakakhala m'busa sadakavotera kut nkhondo ya ku Palestine ipitilire anthu akuphedwa uku pa maiko onse ku Africa kuno malawi yokha bas ikat ipitilire
Chilima adafa kuthupi koma muuzimu tidzakhala naye forevermore.
Akuti udzikhala nalo nyazi limodzi😂😂😂
Faka iwee auzeni 😂😂😂 akuti azitsogoleri
Nda akuba aja ,anakanika kutchula chipembezo chimene amayimira.
Amagwiritsa ntchito anthu kuti apedze umboni koma, koma zinthuuu zina mwa zimene amafufudzazo anazitsiya sanawulutseeeeee chifukwa cha ndalama
Fungo la kany'imbi
Chakwela sibusa uja. Busa wanji osangalala kt chimanga chakwela.
Yochititsa manyazi ndi khalambayanuyo kkkk
Malawi azatheka kukazabwela President okonda dziko lake and akazangoyika lamulo loti oba ndalama za Boma Life imprisonment no any Lawyer allowed to represent him. that alone will transform our Nation.
Komaaa Wandor. Kkkkkkk a big up
ubwino wake Times group ndi ya MCP😂😂😂😂 kuphiphilisa chabe uku
Ine nde sindngavote ndpo sindzavotapo m moyo wanga onse
Ulemu wanu akulu akulu inu mumatimilira amalawife.mulungu azikupasani nzeru
Kkkkkkkkkk Mr pankuku akuti tikhala ndiwa chinambala china
Mmmmm mwezi wa June 2024 unali owawisa.
Brian ndi muthu olimbikila kuposa nonse koma muliboh
Sanali m'busa inu anali just an employee chifukwa ngat anali maitanidwe awo sadakachokako Mulungu samapereka short term contract ya maitanidwe ai
Zachamba zenzen ndakakonda kameneko
Ndiye mukut kaya ndiwamkulu mwendo?? 😄 😄 🤣 Bwinotu mutchula anduna ena ake kkk
Chimwendo
Wado wado ameneyo
Ali kuzanja lamanjawa mmmm ali mbali ya chikangawa
Nafe tuna kuza nyamata wathu pangizi sanadwale Eish chaka chamisozi
Big up wander 😂😂😂😂
Times why for two successive weeks you have repeated exclusive. Is Brian on holiday?
Wayana is number 1 bambo
Chunga ndi munthu wazeru kwabasi and saonesera mbali.koma ndevu zamwayi akutengera mbali kwabasi
Ndipo ine nde sindikumuona
Building malawi is not easy
Kkkk maganew enawa opusa nawotu
Ndikuonapo ine zisilu zokhazokha apa michila yao ndi omwe awatumao
Mmm bodza Chakwera siofatsa koma ndiopa Mtima kwambiri kapena kuti ndi mfiti
I dissagree with the point kuti zaubuusa zillimooo bodzaa
Kkkkk hijab amavala chocho ndazimayi oyenda yendadi mtaunimu😅😅😅😅😅
Kkkkk manyaka nvamkat mwa nkhumba a
Kabambe my vote next year
Watching live from Vitekete Banda village, Euthini, Mzimba, Malawi, Central Africa
for the point of bishop nsusa as ochunga says; he was speacking as who to answer quastion, i would say that ask brian banda to call bishop nsusa on time exclusinve interiew and then you will be able to know the trueth about that. by the wy nothing wrong with what archbishop nsusa say and he was right thats the trueth
Ambuye atithandize 🙏
Who was the master minder?
Wapakatiyo Sali serious akuwoneka kuti Alindimbali
ine ndisaname ndimanjoya ndikamaonera ma guys awawa
Chikangawa party umatha koma chilima munamuphadi galu zoona? Ai mulungu akuone
Kodi atamutenga Zikhale Ngoma tingati chiani. Kodi tatenga phunziro lanji kwa iye.
Camera yakoyi uziikonza wankhwa?
Andevu zamwayi pitilizani osaopa osafoka koma asukuluzi azikhala chakumbali komweku amasangalatsa amathila makometi ,amapha kombe azikhalebe pakati chonde timakunyadilani
To be honest DR CHAKWELA ANAFASA UDYO ANGALANDISE MUZI MMMM
Kodi maphang'ombeyo amapha ng'ombe?😂
Point of collection with latter f
Food
Fuel
Forex
Fertilizer
Female
Mcp inapanga mistake kusakha chimwendo banda ndipo chimwendo banda si wa mcp kuyambila kale ndipo sinkhaĺa kale mu mcp
Pa ma concerns pastor mwawaswatu ma guys 😂😂😂
Mavuto achuluka kwambiri
Mbuzi za pastor
Wadza iweyo!
Adzimayi asamachuluke nzeru mmanyumbambamu!!!!!?
Zanyanja yokhayo ikundiwawa kwambiri kugulitsa nyanja yamalawi
Osayiwalanso oyimba ambiri
Ngati usi
Maitanidwe salapika, that's true chaubusacho chilipo and chikuthandizira kuti dziko lipotoke kaamba kosangalatsa munthu
Sawangawachotse akuopa awaulula dzisisi
Were they trying to act? Kapena kuphunzira acting? Utsiru okha okha kumatuma anzawo opepera
Wakulu mwendo yemweyo
Even I don't trust all of them
Chakwela anatilakwila kumupha handsome chilima chimwendo Banda ndamene wamuononga chakwela
Anatumidwa ndi mcp
Anthu antchito awa akufuna kiwakweza udindo
Yaa koma anyamata inuyo mumakamba chilungamo simayikila kumbuyo chipani
Awa ayamba kukamba zofoira masiku ano.
MCP yanukha Magazi
Zachamba zenizeni tagwira kale malo
Mbuzi zeni zeni
Brain banda ali kuti kodi? Masiku ano sakuoneka bwanji tiuzeni
Mr msiska ndinu dolo kobasi
🔥🔥🔥🔥🔥
Akulu akulu inu tizakulilila niso kaya
Koma nde kung'alulatu umphawi wawapweteka stupid gorvement yongopha anthu nde at uchivoteleso manyi chani!!!
Koma anyamata inu mwayamba kukamba zosamveka kapena tinene kuti mwayamba kukamba zosamveka sopano
Inuso mukusuta fodya wanji Kodi zomwe zisakuveka ndi ziti and Ngati mwawona Kuti sizikuveka mukanangokhala chete coz mwa iweyo ukuoneka Kuti zeru mulibe
Okay
Ma big
Kkkkkkkk❤
Kkkkk eya dzachambadi