Limpopo imfa ya Chilima yawaledzeletsa ndipo akuyankhula zosiyana Mr Don’t Trust wawatengetsa

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 14 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 61

  • @TressLuka
    @TressLuka 2 หลายเดือนก่อน +7

    Anapha anthu osalakwa awa . Achoke ndipo adzamangidwe basi 😢😢😢😢

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 2 หลายเดือนก่อน

    Yomweyo chikangawaaaaaa

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 2 หลายเดือนก่อน

    Tangoponyani mma Soshomo bas amalawi aziwed kut MSP ndiyakupha anapha chilima ndi chikwanje

  • @OusmanBen-f4o
    @OusmanBen-f4o 2 หลายเดือนก่อน +1

    ALlimpopo mumakwana ndithu inuyo, mumayankhula chilungamo kwa a Malawi kut tidziwe zomwe zimachitika m' dziko muno,pitilizani ndithu kutero❤

  • @shanlaljith5389
    @shanlaljith5389 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kkķkkkķ mitu yayamba kusagwira sichool yake iti ife simbulitu day and night simaesa imapanga 24 hrs we need the truth

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 หลายเดือนก่อน +5

    It's almost 145 days/ two trips.

  • @HarrietMtenje
    @HarrietMtenje 2 หลายเดือนก่อน

    Akuyesa amalawi ndimasavage Kodi ndegeyo imakwawa

  • @ZaccheousPetrol
    @ZaccheousPetrol 2 หลายเดือนก่อน +1

    What we need its report and asamakamba ngati Palin ana

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 2 หลายเดือนก่อน

    Okhuta kachaso emweyooo😂😂😂😂

  • @ChikondiKammaluwa
    @ChikondiKammaluwa 2 หลายเดือนก่อน

    Tamvanawo ndithu here from ntchisi

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 2 หลายเดือนก่อน +1

    Wapadela yudasi ali mommo manganya

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 2 หลายเดือนก่อน +5

    Usi anamupeleka chilima

    • @petrokagona1708
      @petrokagona1708 2 หลายเดือนก่อน

      Do you have evidence?
      We loved skc more than you did. We are weeping for the this misfortune but we see no reason of blaming the innocents

  • @hendkachibowo9672
    @hendkachibowo9672 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kodi limpopo imanveka pa frequencies ati?

    • @yassinn5634
      @yassinn5634 2 หลายเดือนก่อน

      Kodi ndi radio?

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kodi ndiye zitha chonchi,,osawafunsa pazomenexi

  • @MartinsCamalo
    @MartinsCamalo 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zoonadi abwathasa mumakhwana

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 2 หลายเดือนก่อน

    Maumboni ndi omwewo Kulankhula kosemphana akudziwa chomwe anachita pa tsiku lomwe anapha anthu 9 ku Chikangawa.
    Azisavuka choncho.

  • @BlessMnyenyembe
    @BlessMnyenyembe 2 หลายเดือนก่อน +1

    AnawaKweza munasunga kodi

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 2 หลายเดือนก่อน +1

    I'm first one to comment ❤❤❤❤ big up brothers

  • @Eggyolk-d1i
    @Eggyolk-d1i 2 หลายเดือนก่อน

    Amawerengela za ana a Israel muchipululu, from Egypt to Canan😢

  • @DavidMtambo-zm8ne
    @DavidMtambo-zm8ne 2 หลายเดือนก่อน

    Wamisala comanda

  • @dumbokadaluka5759
    @dumbokadaluka5759 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ndege ponyamuka pilot amapanga log mileage just like truckers do koma mileage a ndege amakhara hours omwe ndege yauluka chipangidwire just like galimoto imaonetsa ma miles yayenda chipangidwire.

  • @ganizanimanyamba
    @ganizanimanyamba 2 หลายเดือนก่อน

    Mr, Don't trust mumakwana fukulan zobisikazo mundifusileko kuti ukwati ukuyendabwanji achakwela🔥🔥🔥🔥

  • @HarrietMtenje
    @HarrietMtenje 2 หลายเดือนก่อน

    Anthu oyipa awa mulungu achite nawo

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa5348 2 หลายเดือนก่อน +1

    Koditu chilima anali ofunika kwainu amene mumadyela ndalama zake, si amalawi amene tikulira nao infa imenei

    • @yowasschitsosa5348
      @yowasschitsosa5348 2 หลายเดือนก่อน

      Si amalawi onse tikulira nawo infa imenei

    • @JackAmoss-zg2zw
      @JackAmoss-zg2zw 2 หลายเดือนก่อน

      ​@@yowasschitsosa5348ndiwe mfiti yamunthu

  • @Hamidaimran-ob2it
    @Hamidaimran-ob2it 2 หลายเดือนก่อน

    Gwenembe chakwera, ndi yudasi manganya

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em 2 หลายเดือนก่อน

    Munapha anthu osalakwa , mizimu ya anthu 9 ibweredi pa mutu wanudi,mudikire 40 days yanu ikubwera

  • @NeverBeforeMnesa
    @NeverBeforeMnesa 2 หลายเดือนก่อน +1

    Apa nde aledzeladi

  • @YusufChipojola
    @YusufChipojola 2 หลายเดือนก่อน

    I wish ndili olemela ndikumathandiza limpopo FM

  • @shephardlonex3371
    @shephardlonex3371 2 หลายเดือนก่อน +1

    Kwavuta ndiku mvesesa nkhani..wachuluka ndi umbuli apa..ma hrs aja akuimila mmene ndege ina yambila kuwuluka

    • @lucianogeoffrey4275
      @lucianogeoffrey4275 2 หลายเดือนก่อน

      Muuze mwiniwakeyo azayankhule ekha iweso nde uti😂😂

  • @JesseKanjanga
    @JesseKanjanga 2 หลายเดือนก่อน +1

    Akungoyenera kuledzela mizimu yaculuka
    Ndipo mabanja ao akudandaula kuphatikiza ma follower aofe
    Tidzakusowani aSKC pamodzi ndiena onse.

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 2 หลายเดือนก่อน +1

    24hrs=1day
    3485hrs=more
    3485hr*1day/24hr
    =145 days, then let them tell us the truth.

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw 2 หลายเดือนก่อน +1

    brother mumatha kurongosora ithin voice yanu ndiyachikoka

  • @marknkhata6207
    @marknkhata6207 2 หลายเดือนก่อน

    Ngati ndege imayenda 5hrs from cape Town to Malawi

  • @SurprisedBuoy-vq5pl
    @SurprisedBuoy-vq5pl 2 หลายเดือนก่อน +2

    Analakwa pochotsa Moyo wachilima

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 2 หลายเดือนก่อน

    Misaala anapita kuñja

  • @MikeKholomana
    @MikeKholomana 2 หลายเดือนก่อน

    Lipopo we love

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 2 หลายเดือนก่อน +2

    😂😂😂😂zopepelazen zen imapita kutiko galimoto imayenda 4hrs from bt to lilongwe ndiye ndengeo ma hrs oseo achan

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 2 หลายเดือนก่อน

      😅😅😅😅😂😂😂tawafunse bwino imapita kuti 😅😅😅😂😂😂😂😂😂

  • @RhodaBandah-sh1ir
    @RhodaBandah-sh1ir 2 หลายเดือนก่อน

    Analakwa chani chilima ,mai zimbiri, flora , chisomo ndi ena onse abale

  • @DavieKumbanga
    @DavieKumbanga 2 หลายเดือนก่อน +1

    Ng'aaaaaaluuuuuuu

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa 2 หลายเดือนก่อน

    Ndimakape MCP chipani chakupha agaru zisiru izi chakwela popano popano awona zowopsa khalani phe

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 2 หลายเดือนก่อน +2

    Evil people

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 2 หลายเดือนก่อน

    Chakwera is so evil

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw 2 หลายเดือนก่อน +2

    kkkkkkk Mwadxi wamunthu ndiovuta .

  • @HamzaMkwanda-bh8dc
    @HamzaMkwanda-bh8dc 2 หลายเดือนก่อน +2

    Chakwera evil man

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe 2 หลายเดือนก่อน

    Koma anthu mukudzukuta mmmmmmm iyiyi ikathela kuphedi sure

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน +1

    Dzinamiza mbuli zizako zomwezo ife tipange ndalama

    • @EmmanuelGasiten-fo5dr
      @EmmanuelGasiten-fo5dr 2 หลายเดือนก่อน

      Mbuli yaikulu ndi iweyo, coz Limpopo sikakamiza munthu kuimvera. Komanso ukati ukupanga ndalama, ulindichani kutuwa kumeneko. Andalama sitiyankhula kape iwe wamva?

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 2 หลายเดือนก่อน

    9:42 Kodi ku Malawiko kuli mtunda wawutali bwanji kuchoka ku Lilongwe kupita ku mzuzu kodi ndi mtunda wochoka ku Malawi ku pita ku America? Pakuti kuchoka ku Malawi kupita ku South Africa ndi 2hrs 45munits ?

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki 2 หลายเดือนก่อน

    Timakunyadilani alimpopo fm Nyimbo mwayamba nayo programyo tatibwelezeleni zinali please 🙏 I

  • @AllieFunaya
    @AllieFunaya 2 หลายเดือนก่อน +1

    Judas scaliot

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n 2 หลายเดือนก่อน

    kunena moona mtima anthuwa ndi asatana. cos anatitseka mmaso. or azitolankhan athu sanakhaleso ndimafuso pa nkhani imeneyi. nde or ma duration akuchokera tsiku lomwe inayamba kugwila ntchito.. ma hrs ake akuchepa kutengera Chaka chomwe inayamba kugwila ntchito ndegei.
    ma hrs apatsikuli ndi abodza. komaso ngat akut ndi ma hrs ot kuyambila tsiku lomwe linayamba kugwila ntchito akuchepa.
    foolish pipo

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 2 หลายเดือนก่อน

    zoona

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 หลายเดือนก่อน +1

    Zopusa kumangokalila kupeka mabodza dzianamizani anthu akwanu konko

    • @yassinn5634
      @yassinn5634 2 หลายเดือนก่อน

      Sibodzatu ili ayi koma UMBUTUMA

  • @petrokagona1708
    @petrokagona1708 2 หลายเดือนก่อน +1

    Why complicating straight forward issues? These hours are for the flying span of the jet. You are showing ignorance here.
    It might be heard wrongly here. The commander was not referring to your stupid insinuations.
    He is talking about duration the aeroplane had been flying since it was assembled.
    Ndikumumva bwino bwino ine mkulu wa asilikali uyu ngakhale ndili osaphunzira. How far did you go with your studies?
    The guys might have a hand on this accident but not the way you are putting it.
    Don't implicate the innocent with fake stories.