ACHAIR AKANAMULEKA BINGU KUTI AMTSOGORERE ZIKOLI NDI NZERU ZAKE OPANDA ACHAIR KUYIKAPO UPHUNGU WADYERA BWEZI TILI NDI UDF YOKHA BASI,,,, DPP ILI NDI TATHAUZO YA UDF
I wonder why till now udf is associated with dpp ,mpaka pano chipan Cha udf chinatha kamba ka munthu uyu ndi dpp yake ,udf ikuphuphaphupa kamba kamunthu uyu ,mene muluz anamenyela kampen bas pa mapeto pake kuwataya a udf zinali za chison
I was 20 years old when this happened. Am commenting on this today at 40. God is great!!! As you watching this in 2097..... know am your ancestor
Bingu our Malawian hero!!!sazapezekanso President wa vision ngat inu...May ur soul continues to rest in peace 🙏 🕊
Anthu akuba onsewa, dzisiru nkumango sekerela
Imagine pamenepo he could imagine Dpp woye...that was his heart 😂😂😂
This is sooooo beautiful. Button passed from Bakili to Bingu
Bingu timakusowani mpaka pano good guy
Zinalanga vadi ndimafuna ndifuse kuti mfumukazi amatuluka litindiliti
Bingu is only one who developed n loved Malawians
Bingu our father
Bingu anari munthu wa zachuma ndie anapanga Malawi kunkhala pa bwino koma lero kumalawi ndi Mavi onka onka
Bingu the greatest
ife akuno kumpoto tikufuna U D F ibwerele papando
Anavala shirt ya blue zomwe zinkatanthauza kuti sakukhalitsa koma Muluzi sanazione
Takusowani abingu kuchokwa kwa inuyo kukungobwera mphemvu zokha zokha
Kkkk 🎷
Sukunama zoona kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Repost this video BMTV please. Make it famous across the land
Akuti mosiliwa kaya nyene 😂
Ngati ukumusowa osamakagona kumanda konko bwanji?shupit
Bingu was ploting and had blue in his head 😅😅😅😅
Machine Bingu
ACHAIR AKANAMULEKA BINGU KUTI AMTSOGORERE ZIKOLI NDI NZERU ZAKE OPANDA ACHAIR KUYIKAPO UPHUNGU WADYERA BWEZI TILI NDI UDF YOKHA BASI,,,, DPP ILI NDI TATHAUZO YA UDF
Chisulo cha njanji
politics politics politics mmmmm yeahhh
Mumtima munali blue dpp😅
Sukulu is important. Bakili annagulitsa chipani cha UDF..Kuthiilidwa mchenga mmaso kkkk