*MADA Lyrics by Phyzix* Produced by Sameface Beats & Cuff-B *INTRO* Yeah/ It's Only Entertainment/ Very Good Very Good/ Sameface on the Beats Mumakwana a Mada/ mwabhebha mwabhebha Mwaipatsa moto a Mada/ mwatentha mwatentha *CHORUS* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 1* Amati akanyamuka ndi ma baddie/ akupita ku mango talati/ akachoka pamenepo restaurant/ kenako ku zi ma photo kwa stunt/ popita ku dance savala panti/ kuti mphepo idutse bwino pati/ amakonda nyama mu chapati/ ngati kuli kobhebha ali mkati/ ali ndi chi latest iPhone/ akundivutitsanso ndimugulire Benz/ akumangojomba daily class akudziwa kuti lecturer adya beans/ why you gotta do me like this? Mada/ ukufuna kuti ndipange commit murder?/ ukupanga chani Madalitso/ funa khoba izawatenge Fada? *CHORUS* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 2* Kumupempha kuti abweze ko moto wakana/ ati palibe zopola/ ukamuonaa akubalalitsa panopo nde zinamuyanja zodzola/ wachita kumenyetsa nkhwangwa pa mwala kuti iyeyo ndi loan ndi wokongola/ ukaona pa watch ndi nthawi yake yamukwanira ndendende yonjoya/ akumandikanda pa bala/ kunyamuka kwawo kumakadukula ku Bala/ Nsanje zochita kuputa dala kuti ine ndizikangana ndi midala/ why you gotta do me like this? Mada/ ukufuna kuti ndipange commit murder?/ ukupanga chani Madalitso/ funa khoba izawatenge Fada? *CHORUS* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *OUTRO* Cuff-B Production.
Ndinanena kuti Ty grin music genre iyiyi anayitha. This is the real identity ya music yathu kudziwika ndi ng'oma basi we will be recognised on the international market
I think now it high time we take phyzo seriously kuyambira pa nyimbo anayimba ndi eli njuchi sanapaleposo en en my number one song is mwatinti seconded by mada I love this guy we have drank together penapake ....
Frankly speaking This guy has talent and logical presentation of information. This song based on real life situation wakutumula. I believe many youths undergo this kind of situation
*MADA Lyrics by Phyzix*
Produced by Sameface Beats & Cuff-B
*INTRO*
Yeah/ It's Only Entertainment/ Very Good Very Good/ Sameface on the Beats
Mumakwana a Mada/ mwabhebha mwabhebha Mwaipatsa moto a Mada/ mwatentha mwatentha
*CHORUS*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*VERSE 1*
Amati akanyamuka ndi ma baddie/ akupita ku mango talati/ akachoka pamenepo restaurant/ kenako ku zi ma photo kwa stunt/ popita ku dance savala panti/ kuti mphepo idutse bwino pati/ amakonda nyama mu chapati/ ngati kuli kobhebha ali mkati/ ali ndi chi latest iPhone/ akundivutitsanso ndimugulire Benz/ akumangojomba daily class akudziwa kuti lecturer adya beans/ why you gotta do me like this? Mada/ ukufuna kuti ndipange commit murder?/ ukupanga chani Madalitso/ funa khoba izawatenge Fada?
*CHORUS*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*VERSE 2*
Kumupempha kuti abweze ko moto wakana/ ati palibe zopola/ ukamuonaa akubalalitsa panopo nde zinamuyanja zodzola/ wachita kumenyetsa nkhwangwa pa mwala kuti iyeyo ndi loan ndi wokongola/ ukaona pa watch ndi nthawi yake yamukwanira ndendende yonjoya/ akumandikanda pa bala/ kunyamuka kwawo kumakadukula ku Bala/ Nsanje zochita kuputa dala kuti ine ndizikangana ndi midala/ why you gotta do me like this? Mada/ ukufuna kuti ndipange commit murder?/ ukupanga chani Madalitso/ funa khoba izawatenge Fada?
*CHORUS*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*OUTRO*
Cuff-B Production.
Yomweyooooo iweeeee
🐐
Iyiyi mwayesetsatu man Phyzo..
The only artist yemwe amatipatsa ma lyrics anyimbo yake ❤
UFUNA KHOBA IDZAWATENGE FADA
Ndinanena kuti Ty grin music genre iyiyi anayitha. This is the real identity ya music yathu kudziwika ndi ng'oma basi we will be recognised on the international market
Apa mwamuposa ty grin🎉 Muzik yizimveka choncho this is Sweet
I think now it high time we take phyzo seriously kuyambira pa nyimbo anayimba ndi eli njuchi sanapaleposo en en my number one song is mwatinti seconded by mada I love this guy we have drank together penapake ....
Is anyone going to talk about the BASE outfits? Damn... Christopher Ngalu is a genius
Thanks Gamba for involving our friends Burundi 🥁. One Africa 🔥
Mwabwera madhalla let's gather here guys and support our own Mountain GOAT 🔥🔥🔥🔥🔥
youtube.com/@NormalBenzin1?si=F9n4_hx07tmDQny-
Nyimbo koma iyi😊😊😊 mix amapiano vibes
Eeee man phyzo iyiyi ndi madam case 😅😅 nice track bro 🔥
Achina Mada amzanga let's gather here tiipatse moto
Veri gud veri gud...
Frankly speaking This guy has talent and logical presentation of information. This song based on real life situation wakutumula. I believe many youths undergo this kind of situation
Don Dada is back always coming with fire 🔥🔥🔥 koma munakajambulako Mphawi ija next time
Ooo!! Yes mwabwera big
Mmmmmh❤😊 something is different maah phyzoh mwabwera 🎉🎉
Mahn phyzoooo!!!!!! Apapa mwabwelaaaa!!!!!
I see Bujumbura Boyz n girls BIG up 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Best hit
Chi graphic cha well
Zimadance za sharp
Ndi Mada case carry
Nice song dear
I don't mean that siumatha kuimba but this song is number panyimbo zako zonse fada salute and keep it up my G
More fire umatha iweyo phyzix🔥🔥🔥🔥
Eeeeh mwadza fadah
iwe umati ee mkanziameneyu akufunika kuti nthawi zonse umuyang'anile chifukwa nde ee mulifiga too💚💚kkkk👊👊
Oyimba wazi confi...inuyo mumakwama fadah 🔥🔥🔥
Gamba// access granted 👌. Mada akufuna Khoba idzawatenge fadda
My favorite phyzix❤
Banger 🎉🎉🎉mwapha boss ... You Keep delivering!!! IOE 😊
Fada, iyi eeeeh🔥🙌🏿Umaganiza bwanj. Ma bars oopsa
Nyau muzik to the word 🌎💯🧢🔥
Gamba🗣️🎉
Truly local amapiano 🔥🔥🔥 Physal u came
Phyzix ndi dolo kwqmbiri ❤️❤️❤️👀
this is lit...tizavina December🙂🙂🙂😊
Chi vibe chanyatwaa🔥🔥🔥 very good very good
Mwayipha ndithu😂❤🎉
Physix ❤❤❤ you are a true Gee. I love you and your music 👑🕊️
From Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
No lie iyiyi nde mwapha man Phyzo🔥🔥💪🏾💪🏾
Iyiyi mwadza fada 🔥🙌
For the 1st time phyzix drop a song that i can put on my playlist
Iyi sitidilita fada /apa nde mwayamba kuyimba😊😎
The fact that you would put this song on your playlist among all of Phyzix songs makes me question your taste in musik🤦. Cause this song is pure 🗑️
Yikuyenera award iyi this year❤
Captain doing is best 👌 ❤️🔥apa nde tadya 1
Eeh Gamba has come ‼️
Nuff respect fadha🔥🔥
Nyc song biggy
kip it up
0:55 🔥
Mwapha boss.
Versatility on point Gamba…u keep on perfecting ur craft…very good very good🔥🔥🔥
Iyi nde ndi hit eer🙌🔥
We love you here in usa
Nyimbo ili bhooo man phyzo
Big Up Fadah...
MADA on point!
Wow ❤ lit ngat mchigubu 💥
aaah boss 😆Nyimboyi mpaka zoyenda osavala pant nde zitiso izi
ati kuduse mphepo😅😅😅
nyimboyi nditengera etchaivi kma tikatenga pep patiiiiiii
Iyu ni mautan goat magaye❤🎮
Ulemu wanu eeee 🔥🔥🔥🔥🎶🎶🔥🔥
The beat itself is amazing and the way u coiled your words💥💥💥💥💥💥
Mwaphaaaa
Gamba Nd Gambadi🔥🔥🔥🔥🔥
This is too much bruh💥💥💥
Tilibe tym yopuma MaDa🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Queen sophie i see you❤
This is the genre to carry... Nyau music to the world 💥
Very good very good🎉🎉
Let's support this guy
On 🔥🔥🔥
🔥🔥🔥🔥. Remix muzakhale Tay Grin😁😁
Nyc
video ya sharp
😮mada hits
Iyiyi nde ndi mada kesi 😊👍🔥
Hit ❤
Nyau Prince now
Phyzix ujaa🔥🔥🔥😋
Wow that's great
What a masterpiece ❤🔥.. Noel koma ofunika uphunzirenso kuvinatu 😂😂😂
The video is lit
Wampha 🔥 🔥
❤❤❤❤❤❤❤❤ Inu ND boss
Yoh!!! Phyzix apa ndee murder case yeniyeni! Chifukwa mwaphaso nyimbotu apa🔥🔥🔥🔥🔥
More fire🔥
Popita kuma dance savala MPANTII🔥🔥🔥
Nice piece gamba
Nice❤
Umakwanila 🔥
Iyiyi nde mwayipweteka2....eh🎉🎉
Hard phyzix 🤟
Great video 🔥🔥
Smart video
🎉 we like you ase
Fire
Combination of Amapiano+Fikisa beats🎉
The Gamba vibe
🔥🔥🔥
Iyiyi ndy Mada case Mada case🔥🔥🔥🔥
Kuswaaa!🔥
Mwabwela akamuna phyzo
Nice visuals! I enjoyed it especially after I muted the music
I feel good when you say very good very good 💥🔥
fire🎉🎉🎉🎉
Madala 🎵🎶🔥🔥🔥🙌🙌
Iyiyi mwakupa😂😂🔥🙌