Am a graduate from mca, I did bachelor's in accounting and auditing - 2021. Mtamaliza xul mnapita ku blantyre kuchoka ku mzuzu, kut mwina ku town simkachedwa kupeza ganyu Koma guys there is real life after college eeh 😢😢 ndinayamba yoyitanila ma minbus mu limbe market pa 4ways, ndapanga izi kwa chaka ndi half anthu oti anali amzanga kumandinyoza plus ena kumandisala ena kumanditenga opusa komabe simnagive until pano pakatipa Mulungu anandidalitsa ndinapeza timaganyu ku sffrfm & mec pano mnapeza capital mnayamba business.. anthu amkandiseka aja pano akumandipempha ndalama... mmmm dziko ili kaya. Nice song and I can relate 🙏🙏💯😻
After graduating from MIJ I started looking 4 a job but no avail. And then I back in class to pursue another course ,I graduated agen with a degree in strategic management while searching 4 a greener pasture.tinayamba kuyendetsa lorry pa rank ,to make it worse my gelfrnd called me that ndilibe tsogolo and she left me. I cried while kneeling down to God asking for his favour. Guys mulungu sataya wake for sure. Am working now In government.

Ineso ndapanga program yimeneyo pa MCA abale inu 😢
Eeish bro this lyf😢😢
Moyo ndichocho
After graduating from MIJ I started looking 4 a job but no avail. And then I back in class to pursue another course ,I graduated agen with a degree in strategic management while searching 4 a greener pasture.tinayamba kuyendetsa lorry pa rank ,to make it worse my gelfrnd called me that ndilibe tsogolo and she left me. I cried while kneeling down to God asking for his favour. Guys mulungu sataya wake for sure. Am working now In government.
🙏🥳
Anakupatsa mwai ase
@winstonpchilonga6712 ndpo sukunama..anandiuza zimenezo mwenz ngat ,ine nxt month mkumapeza job eeeiah God really works and amalola zinthu zina zipite kt wina apeze mwai
eish it's getting hard everyday in this world,glad how you finally made it,it's all God's plan.
@preciousjonas5468 on a slow pace bro ..trust in the Lord bas
nyimbo za uthenga wa bhoo always stand out! nice concept ma guy
Ndinu madolo ma guy 🔥🔥 nyimbo mwapha
Mantha ndiye tilinawo ochuluka 😢😢😢😢😢, lovely song ❤❤❤❤❤
Eeeee anthu wa akupha kwambili 💥💥💥💥💥
Mantha fire mwapha ma guy
Mwapha azibambo👏🏽🔥
Those who failing in love with the hook let's gather here
Ada awawa hook aika🔥🔥
Nyimbo mwapha guyz,izizi nzomwe tikudutsa after Xul
Track gat all the struggles that graduands anticipate ku world but people just don't know✌🏽 nice one guys
Mwapha guys ✌️🍻 UNIMA ndi CHANCO
Tidikirebe komaso tipempherebe... Big up unima all will be well🎉
Big up ndakutenga basi ndizivela iwe basi
The songs hit in all angles 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Things that every college student like me fear....
The future
coz we ain't sure if this degree is our way out, at least we hope so. So help us God🤲🏾🙏🏾
Life is not fair
Nice tune ma Dollo🔥🔥🔥
Positive song bro.... I like it
😂 😂 😂 😂 😂 Ndipo zoonadi moyo ngobvuta lero tili Jonzi kumakhala ndimajigisi mushop pheee 🙌🙌🙌🙌
Local artist with reality yapa ground💯💔🔥
Fire my Gee
Reality 🤗 True definition of Life after college 😢
Peter amidu yi eeee NDIWACHABE kwambir chorus ngat akuyimba bass guitar mu blackmissionaries
Nyimbo yi ndi yokhudza 🥺 Enafe ikutikumbutsa tsogoro lathu lotayika🥺
Represent ma guy 🔥🔥
Unima well presented.. Song talks about reality of life😢😢😢
Ndasala ndi semester imodzi yokha , matha andizaza 💔
Nyimbo yanzeru ❤❤
Uku nde kuimba uku,ndinaphunzira koma pano ndili outside of my country,am working here my education is useless to me
Track mwapha boys 🔥🔥
Nice song young stars 🔥🔥
The concept....the lines...my guy flopa u delivered..Amidu as usual...am amazed boys🔥🔥🙌🙌
This song 🔥🔥🔥🔥
everything we live to almighty God 🙏
Talented 🎉🎉🎉🎉🎉
Akt this course is very marketable eee zazii🙌🙄
Ambuye ayankhe nyengo zathu 🤲😪🙏
Ma guys inu muli ndi luso. Keep pushing dudes
Mwapha nyimboyo madolo
This is great guys 🔥🔥
Nice some guys.mantha achulukadi🔥🔥
Nice gingii👌👌
Nice❤️🔥
Eee mantha 😢 mulungu akhare nafe.
Wow!🤝
Kupha sound🔥🔥
❤❤❤ Nice tune ma gee ikunveka pa 99.9% ku Durban Ladysmith kuno
Mwapha guys, so nice
Ife tamaliza pompo pa ntchinji koma pano ndikawona miracle ndi chinga, Simmene kulili Ku industry bro Flopa D
Mulungu samasiya yemwe anakhetsa thukuta lake kulimbikira. Tsikulina chimazapezeka chochita. It's just a matter of time. Nice tune Geez
Flopa D X Amidu = Hot hit song 🔥
Real life situation 😢 Matha. On repeat
Nice 🔥🔥
After kumvera 2018 degoss outgoing I knew Flopa ndi dolo
❤❤❤ epic
❤❤ mumakwana inu
😢😢😢ineso ndili ndimatha ndikamaliza school link tilibe shaaa...maguys mwaipha
Nyimbo mesa nde ndi izi
Nice😊😊😊
Reality Check.... Nice Tune
Hyphen style nice guys what a tune🔥
here at Luanar mantha😢😢
Nyimbo yaona u finali wanga, 😭😭😭
Hit🔥
🔥🔥✅
Ndinu madolo🔥🔥🔥
OSAOPA BRO FLOPA D❤ MULUNGU ALIKO🙏
Mantha basi bro keep it up
Mwapha iyi
This song Is missing on vidmate??
Ine chitengereni diploma ya Nutrition koma ya Distinction mpaka lero no work
Iyi ndi hit ma guys
pure talent
Last semester apa nkhawa yakeyo ine 😢😮😢😢
Zinthu zikungopanha relate ee
True meaning of life
Poguguda mtima kumakumbukira umakhala kumanzere
My artist
Nice one
Flopa D🔥🔥🔥
Chotsa mantha ndipo uziyendabe
Kkķkk koma school ya ku Malawi 🇲🇼 🤣
Osadanda mudzapita ku Jon
MATHA AFTER SCHOOL IYI😢
Finish school and face the world out here😔
That's true 😢😢😢😢
Matha that's hit me
Ndpo ndikuopa 😭💔 After all I don't have any connection mu industry
Four years now osayipeza ntchito azathu ama connection anayamba ambuye tioneni ana anufe
Drop a like if you remember Wisdom Chitedze .Through the hook ❤❤
Great song ma biggy
Nice one my geez
Ambuye aliko tikafika
💪💪💪💪
Touching
Mantha 🔥
Story of my life 😢
Osangopanga zotheka bwanji or ukhale ndimantha what's gon be yo benefit? hahaha
Nice time
🔥
Zoona zokhazokha men
Azibambo turne
Nice tune
This song😴😴