*MADA Remix Lyrics* Produced by Sameface Beats & Cuff-B *INTRO - Phyzix* Yeah/ It's Only Entertainment/ Cuff-B Production/ Sameface on the Beats Mumakwana a Mada/ mwabhebha mwabhebha Mwaipatsa moto a Mada/ mwatentha mwatentha *VERSE 1 - K Banton* Woozzah Akakhosomola ndekuti afuna pizza // Amadaliso nthumba mwawo sachedwa ku pisa // Issa mpaka namupangisila Viza // Nkazi oti nangokumana naye pa Insta Gram// Pano ndi mlamu // Mmhu am so dam // Ine nkangofuna kudya Buble gum hmmm// Murder Murder Murder Murder hmm satha kumvetaa // Pena Gena.. zomwe imapanga the other gender // Pakakhala Dollar imangobenda Yeah // Malo mopala moto undipalimulisa // Mabomba a rasha ndizindikila nda phulitsa // Katundu wanuyo ndikuziwa mumagulisa // Mdulidwe wazimayi kulibe nde osadulisa// Iiih aMada *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 2 - JEG Tellem* Zofuna za Mada ase / Zikangolowa ku madance eti / Kugula Gin Wawa Castel / Aphula sin akangotell Mhuu Uyu singagwire mwa easy Kundipasa chance singasinze Ngati chux ndi maplan ndili busy Kuti ukhale mula wa Jizzy Nkazi wachi body chonyadisa nde sinzakubisa anthu akudziwe Pa Facebook insta ndi Twitter ndikasintha picture pakakhala iwe Koma MADA doesn't care / Ena ATI ndika wash and wear / ndimamufuna kuposa mpweya / Mundilangiza ine, Osamvera aaah *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 3 - Mellz Kumpanje* Ukumachita kundigwedezera matako mada, ine si charisma pa Tuno//aaah FADA (alipo samafuna kudya) (mada) ine ndiofewa mchiuno//atandimanga sangamve zokuti umachita kundipeza wekha kwathu kuno//nde panopa,sukumavalamo mwado (mada) ukumangongoyenda buno buno//ndikati easy--- umati NO..umaipatsa moto (ipondeni fadah)//umaiwala zoti amanjata (Gwii).........ufuna ndikalowe ndi Mada//?? Why you gotta do me like this mada// Ukufuna kuti ndipange commit mada// Ukupanga chani madalitso ufuna khoba izawatenge fada// *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 4 - Jolasto* Mpaka ndiphula ma sin kamba ka iwe Mada Wina ndimuNYIKA ndimadana ndizaFANTA Ndakumvela kuwawa kuti ufike apapa Ndipo muwuzane wina ndimuchotsa mphafa Unaponya status ukumenya nip Sikuti ndikuku kumba ndangowona ma pic Kuyiwala kwanu unapanga mistake Ati Blantyre sinodi? Zawu wayilesi Madaaa kaya unafa kwambiri Nane ndi mfumu ndikudyesa ma tick Ukuwonjeza my queen Nane town ndiyanga ngati maskin Eti uli blues? Ukumwa manica? Ukuspendar dollar Ulindima niga? Eti zafika poti boys ikukugwila? Ati uli ready akufunayo aika? *VERSE 5 - Guntolah* Mada mbuyo monsemu sinakhale case Mwina ndili mwana kusewelesa zikhesi Koma anthu akwathu akati napangidwa curse Akazi ndinkagwila ngat Shammah no reverse Nkaz opanda mbuyo, kumandibwenza mmbuyo Sinaphake naye life ati Anali smoke, sinatchaye olo life Ati Samva Maloza, chifukwa chan anaonapo maloza Ati x wake sankapanga cholozeka Asing'anga agwila ntchito ine ndekha ndolozeka Koma inalipo nthawi, yosowa chochitika Ma Beat mangonyika Asilamu akudanda ati sindipanganika Kubwera mada, kuwelama Kuzasikana kenako kukwerana Ndichi red sign nkona tikufilana. MADA *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 6 - Beejay* Mwana kazi undipweteka Unditakasa Undipepeta Ndikagona Ndiku Mbrupahur hvd Ndiku bwebweta! Upange zomwe wanena Ndipo ndizione zikuthekeka Ngati wati cheke Cheke apa! Ndikuone ukuchekeka iiiyh MADAm mada .ukalola Ine Wadya!! MADA undimadalits Iii taonani undibalalitsa! Azimayi Nthungululu pamenepa! Amanena kuti love Is blind Ine kuno khungu Nde yandipweteka Sindikuona komaso sindikubona undivetse *VERSE 7 - Ace Jizzy* Dzina ndani? Madalitso Ndiwe okongola ngati ku paradizo Tabwera kuno....mdzataniso? Tiime pachulu ngati bwana Mbizzo Ana okuposa palibetu Or nkhalamba paliJETU Gaire ndalama....pa Easy'tu Dollar yaine sungamalizetu Ine ndi mponda matik Ndimamenya ...mponda ma kick Nkonda ma gig nkonda ma chick Mada usanditole tola ma pic Umulore MADA gangster Honey moon ndiku MADA gascar Ndamva zoti wakana chi namtindi Iwe ndiine love Mwantinti *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 8 - Che Kalonda* Mfana ophulitsa life ngati Makombola Kuthamanga kwambiri kuposa Corolla Kumuuza Kuti tiye amangolola Chilichonse atha kupanga nabola Dolla Nde Ali Ndi chi figure Ngati Masamu Dzimatatoo Mbwee Mmatakomu.. Wapengetsa Ma Bwana Ntaunimu Koma Chonde Usadye Ndi Halamu Nde Mwati iyeyu ndi Ndani (KAYA) Wabwera Ndi Ndani, Akumwa Chani (KAYA) Mwina Kapena Ndimupatse Plan.. Mmmmh Dadda Uyu Akuchedwetsani *VERSE 9 - Waxy Kay* Akazi akalowa mu boy zone//olimbana nao amwa poison//Bambo anga paza kuden zima weapon//Wina azakushoshe azalira Ring tone.. Iwe Uzangomva ngiri ngiri//Wina azanditenge kuchigwiri gwiri//amuna anga alusiratu kuno dada//amuna anga atha kupalamula mada *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Ace jeezy, iyeyu kaya bwanj... Bax titola ma pic... Guntolah nanu mwakhazika bata enao...🎉🎉🎉 Young king lero simunatitengetu tinakonzekera inuyo komabe👍
*MADA Remix Lyrics*
Produced by Sameface Beats & Cuff-B
*INTRO - Phyzix*
Yeah/ It's Only Entertainment/ Cuff-B Production/ Sameface on the Beats
Mumakwana a Mada/ mwabhebha mwabhebha Mwaipatsa moto a Mada/ mwatentha mwatentha
*VERSE 1 - K Banton*
Woozzah
Akakhosomola ndekuti afuna pizza //
Amadaliso nthumba mwawo sachedwa ku pisa //
Issa mpaka namupangisila Viza //
Nkazi oti nangokumana naye pa Insta Gram//
Pano ndi mlamu //
Mmhu am so dam //
Ine nkangofuna kudya Buble gum hmmm//
Murder Murder Murder Murder hmm satha kumvetaa //
Pena Gena.. zomwe imapanga the other gender //
Pakakhala Dollar imangobenda Yeah //
Malo mopala moto undipalimulisa //
Mabomba a rasha ndizindikila nda phulitsa //
Katundu wanuyo ndikuziwa mumagulisa //
Mdulidwe wazimayi kulibe nde osadulisa//
Iiih aMada
*CHORUS - Phyzix*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*VERSE 2 - JEG Tellem*
Zofuna za Mada ase /
Zikangolowa ku madance eti /
Kugula Gin Wawa Castel /
Aphula sin akangotell
Mhuu
Uyu singagwire mwa easy
Kundipasa chance singasinze
Ngati chux ndi maplan ndili busy
Kuti ukhale mula wa Jizzy
Nkazi wachi body chonyadisa nde sinzakubisa anthu akudziwe
Pa Facebook insta ndi Twitter ndikasintha picture pakakhala iwe
Koma MADA doesn't care /
Ena ATI ndika wash and wear /
ndimamufuna kuposa mpweya /
Mundilangiza ine, Osamvera aaah
*CHORUS - Phyzix*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*VERSE 3 - Mellz Kumpanje*
Ukumachita kundigwedezera matako mada, ine si charisma pa Tuno//aaah FADA (alipo samafuna kudya) (mada) ine ndiofewa mchiuno//atandimanga sangamve zokuti umachita kundipeza wekha kwathu kuno//nde panopa,sukumavalamo mwado (mada) ukumangongoyenda buno buno//ndikati easy--- umati NO..umaipatsa moto (ipondeni fadah)//umaiwala zoti amanjata (Gwii).........ufuna ndikalowe ndi Mada//??
Why you gotta do me like this mada//
Ukufuna kuti ndipange commit mada//
Ukupanga chani madalitso
ufuna khoba izawatenge fada//
*CHORUS - Phyzix*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*VERSE 4 - Jolasto*
Mpaka ndiphula ma sin kamba ka iwe Mada
Wina ndimuNYIKA ndimadana ndizaFANTA
Ndakumvela kuwawa kuti ufike apapa
Ndipo muwuzane wina ndimuchotsa mphafa
Unaponya status ukumenya nip
Sikuti ndikuku kumba ndangowona ma pic
Kuyiwala kwanu unapanga mistake
Ati Blantyre sinodi? Zawu wayilesi
Madaaa kaya unafa kwambiri
Nane ndi mfumu ndikudyesa ma tick
Ukuwonjeza my queen
Nane town ndiyanga ngati maskin
Eti uli blues? Ukumwa manica? Ukuspendar dollar Ulindima niga?
Eti zafika poti boys ikukugwila? Ati uli ready akufunayo aika?
*VERSE 5 - Guntolah*
Mada mbuyo monsemu sinakhale case
Mwina ndili mwana kusewelesa zikhesi
Koma anthu akwathu akati napangidwa curse
Akazi ndinkagwila ngat Shammah no reverse
Nkaz opanda mbuyo, kumandibwenza mmbuyo
Sinaphake naye life ati
Anali smoke, sinatchaye olo life
Ati Samva Maloza, chifukwa chan anaonapo maloza
Ati x wake sankapanga cholozeka
Asing'anga agwila ntchito ine ndekha ndolozeka
Koma inalipo nthawi, yosowa chochitika
Ma Beat mangonyika
Asilamu akudanda ati sindipanganika
Kubwera mada, kuwelama
Kuzasikana kenako kukwerana
Ndichi red sign nkona tikufilana. MADA
*CHORUS - Phyzix*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*VERSE 6 - Beejay*
Mwana kazi undipweteka
Unditakasa Undipepeta
Ndikagona Ndiku Mbrupahur hvd
Ndiku bwebweta!
Upange zomwe wanena
Ndipo ndizione zikuthekeka
Ngati wati cheke Cheke apa!
Ndikuone ukuchekeka iiiyh
MADAm mada .ukalola Ine Wadya!!
MADA undimadalits
Iii taonani undibalalitsa!
Azimayi Nthungululu pamenepa!
Amanena kuti love Is blind Ine kuno khungu
Nde yandipweteka
Sindikuona komaso sindikubona undivetse
*VERSE 7 - Ace Jizzy*
Dzina ndani? Madalitso
Ndiwe okongola ngati ku paradizo
Tabwera kuno....mdzataniso?
Tiime pachulu ngati bwana Mbizzo
Ana okuposa palibetu
Or nkhalamba paliJETU
Gaire ndalama....pa Easy'tu
Dollar yaine sungamalizetu
Ine ndi mponda matik
Ndimamenya ...mponda ma kick
Nkonda ma gig nkonda ma chick
Mada usanditole tola ma pic
Umulore MADA gangster
Honey moon ndiku MADA gascar
Ndamva zoti wakana chi namtindi
Iwe ndiine love Mwantinti
*CHORUS - Phyzix*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
*VERSE 8 - Che Kalonda*
Mfana ophulitsa life ngati Makombola
Kuthamanga kwambiri kuposa Corolla
Kumuuza Kuti tiye amangolola
Chilichonse atha kupanga nabola Dolla
Nde Ali Ndi chi figure Ngati Masamu
Dzimatatoo Mbwee Mmatakomu..
Wapengetsa Ma Bwana Ntaunimu
Koma Chonde Usadye Ndi Halamu
Nde Mwati iyeyu ndi Ndani (KAYA)
Wabwera Ndi Ndani, Akumwa Chani (KAYA)
Mwina Kapena Ndimupatse Plan..
Mmmmh Dadda Uyu Akuchedwetsani
*VERSE 9 - Waxy Kay*
Akazi akalowa mu boy zone//olimbana nao amwa poison//Bambo anga paza kuden zima weapon//Wina azakushoshe azalira Ring tone..
Iwe Uzangomva ngiri ngiri//Wina azanditenge kuchigwiri gwiri//amuna anga alusiratu kuno dada//amuna anga atha kupalamula mada
*CHORUS - Phyzix*
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
This is really nice
No🎉😅 2:00 😢😮🎉😅😮😅😢🎉😢l
No🎉😅 2:00 😢😮🎉😅😮😅😢🎉😢l
Ace Jizzy ndi Bee Jay ndi anthu owopsyatu 💥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Jolasto fans let's gather here 🎉
Dolo ndi jolasto 💪
Shasha uyu
Jizzy ndikatundu wambiri eee🙌
Remix iyiyi palibe number 1, nonse mwawina maguy👊💪💪
Mellz fans gather here aphwetekatu kuno gist ija..umatha breda
Fada awa🔥
BEE JAY top funny let's gather here😂😂😂
🔥😂
Team of Young King Waxy Kay lets come here verse wapha bwino kwambiri katundu Waxy Kay ukali wanu fadah 🔥🔥🔥🙌
Guntolah and kbanton
Mellz, Bee jay eeee mwaipweteka guyz ...... Big up
Guntola wabwela iweyo❤
Mada on repeat iyiyi ndie ndi Mada😊 all fans of mada lets gather here
❤ Guntolah 1, ace jizzy 2 for me 😊😊😊😊Mellz 3,Banton 4 content and styles kwinako mumaliza .... Collaboration of the year hip pop
K banton big imavuta uyuu listen ma headset abho bho u will see fact! , koma Mellaz wapweteka onse
Young King siwamaswera, koma mellz uja osadzamuphweketsa
Che Kalonda- usadye ndi halam🏃🏃
😂😂😂 wapha 🔥🔥🔥
Chilombo ichi
Ace Jizzy mofaya🔥💫
Ace jizzy waidya 🔥🔥🔥🔥
Tidulirile pa ace jazzy plz ndizimvera pokhapo😂
Bee jay and Ace jizy guys mumatha 🤘
I hated the song but this remix phyzix big up u jxt take it too far I love this ❤❤❤❤ remix
Nonse mwaipweteka....Banton...Gunto..waxy....Jizzy....Jolasto🔥
Well done guys iyi mwaika a phyzo ngati panokha simukwanisa kubebesa nyimbo kumaitana azanu moyo ndi lende
Ine sikalizima pa Tuno🤣🤣🤣 mellz
Mellaz waipha kwambiri without jealous!
❤❤❤ nice guys za srs pamalo
Ma verse awawa samayenera hook ndi beat ngat iyi, Phyzix aaah do chi hit kuposa legends
🔥🔥🙌eeeh boiz inasiya kucheza
Nyimbo yomvela pa repeat ija nde ndiimeneyi✊🏿big up
Ace jizzy no mistake, deliverance on point
Big up yanu mesa
Guntola, Jizzy, Bee Jay & Waxy Kay 🔥🔥🔥
Nyimboyi yangokhala ngat cypher 🔥🔥😂
Ace jizzy uja osazaphwekesa osaiwala k banton💥🔥🔥
Nyimbo Mwaipanga mada iyii ❤
Love mwantiti😂😂🔥🙌 Ace
Koma k banton uja eti🔥he’s underrated koma ndikatundu 🔥
Jolasto ❤waidya za ana amna izi
Guntolah congratulations ulemu wanu thanks🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Aace jizzy palibe size yake🔥🔥🔥
Ndipo aa😂😂 chimandidabwitsa
Bee jizzy eeeee mapazi awo amatha kubwebweta😂😂
Make space for ace jizzy🎉
Mayine melz waigwiradi❤
K bantu mabomba arasha
Che kalonda 🔥😌big up
Guntola fans lets Mark register here
Oro nkhalamba palinjetu pali jetu km jizzy
Ace Jizzy ndi dolo kwambiri😂
Guntola ma lyrics ngati angotola, mwana wachabe
Falling in love with the song ❤️
Nyimbo iti eeh😂😂 muma pub mu
Iyiyi iswani video bas 🔥🔥🔥😂😂
Its Ace jizzy and bee jay for me👍
🔥🔥🔥 collaboration of the year
Chikazati Madam mada 😂😂😂😂 palibe mbola umu
Koma number 1guntolah ace jizzy 2 k banton 3waxy kwinako njee!!
Koma ma boys meakeapula za town.
Mellz, Bee Jay & Ace Jizzy murdered this eish 🙌🙌🙌🔥🔥🔥🔥😂😂😂😂😂😂😂
Phyzo ndi dolo kwambiri for pulling out this 🔥
Guntolah1, Ace Jeezy2, Mellz3,Waxy 4. Nice coraboration guys. Yabeba.
Apa pa repeat basi
Mwaphatu ngati simuzayimbanso 😂💔
Chekalonda ndi waxy big up
Ace jizzy 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Pali jetu
I'm just repeating this song again n again.....nyimbo iyi ndi Bomba lakurashadi guys
Eeee melz kuzitengera ngat zeni zeni 😂😂😂
Jolasto ndidolo osamutola💥💥
Mellz eeeeeh wadya ma guys
Ace jeezy, iyeyu kaya bwanj... Bax titola ma pic... Guntolah nanu mwakhazika bata enao...🎉🎉🎉 Young king lero simunatitengetu tinakonzekera inuyo komabe👍
@Ace jizzy 🔥dolo kwambiri
Phiyx sazatha uyu
K bantone woooo zaaa
Koma ace jizzy adah🔥🔥🔥
Song 🎵 mwapha iyi.....
Olo nkhalamba paliJetu😂😂😂
I was waiting for Malinga 😢😂
Nonse amene ndikupaseni ma % wofanana mix number one sakuwoneka
Nyimbo ili 🔥🔥💯
young king never disapoint
Jolqsto my guys ndakufilq
Bee Jay and Ace Jazzy ndi nkhani zina
Kuinyenkhemesaaa!!!!!
Yaphedwa bho
Anthu mwabulazanamo umu eeehhh...hip hop yobhebha chani.
Now I understand the meaning of ( anaibweza nyimbo)
They want to come up with something beautiful ❤
K Banton, Guntola And Ace ayipweteka hvy respect ❤️🫂
Ace jizzy amaganiza chan kweilnikweni guys ah
Ndikubwebweta😅 Representing 🇲🇼 to de fullest
Chi nyimbo on repeat 🥳🔥😩
To say the fact these guys made it I like the flow of their lyrics booooom kip the oneness very tight .u all spiced the song love it
Mellz🙌🙌🔥🔥
Ace Jizzy udyayo
Waxy n guntolah mwabwera
Osafera zinazo jolasto waika power
K banton ndi Waxy waipweteka💥💥💥💪💪💪💪
1 Ace Jeezy
2 Che
3 Waxy basi ❤
Mwapha❤
Eeh Boiz mwaphwetekana no lie 🔥🔥
Eeeeeeh mwaikidwa ma bars okungana umu🔥🔥🔥
Iyiyi yaphedwa guys🔥🔥🔥 mada on repeat
Yachina kumpanje inabwera mesaaa
Bee jay yo yo yo yo unamuyambila kukuwa kwa anebatu😂😂😂😂😂 umakwana fire ❤
Iyiyi ndiyama Dolo okhaokha 🔥🔥
Ace jizzy🔥🔥🔥🔥🔥
Ace jizzy Guy'z 😮🥴😂😂👊🏾🔥🔥
Ace Jizzy my gee 🔥🔥🔥🔥
Mellz mwaonatu zomwe mwapanga, anyway wayipweteka ndiwe dolo ukufuna kundigwiritsa mada 😂😂