Ndichifukwa chake anapanga chiwembu chomupha Chilima ankafuna chipani chithe chonchi Ndalama a kukupatsani zo sikuti mudzalandira mpaka kale kale zotsala za dziko lapansi
Mr president waanthu osauka y don't tell Malawian kuti anyone ali okuzidwa tipange Mademo Malawi Shotdown chifukwa mau anu akumamveka patali anyone he understood you.
Kd Dan Lu ku DPP anal ndi mpando wanji? Ndye kuchoka kwake mpk munthu amwe panado aaaaaa Bon Kalindo ndwe wekha or akutukwane km more fire til naw nawe
Panyapako bon kalindo kod iweo ungaendese Boma iwe uli ndi chani machende ako ukuchitapo chani ngat ndiwe president wa anthu osauka ukalankhula-lankhula zako ndalama zimakhala kut zalowa nde ukumabwela pano ndikumatipusisa kunali mzako mtambo pano ali kut
Long live big man,you always feed us with facts koma mmakutu mwa anthu ambiri ndimogontha, wishing you nothing but the best
Wel spoken our comrade DC Allah guide you all the time
Makutu mudalira mfuti malo momveka mawu ,mpaka makutu adafa samamva mudabooka , koma ndaseka guys Mr karindo eeeeeeh ai ndi machine opangila machines azake uyu MCP akuwaning,ina iiiiii ndasekat
Mr bk umakwana athotoleni
Amenewo akuwonjeza
😮Amene akususana ndi boni kalindo ndi chitsilu kwambili ndipo alibe mzelu chifukwa boni kalindo amanena zinthu zimene zikuchitika kwambili
Onse omwe akuchoka ku DPP 2025 osazawalola kubwelela azawone kolowela, DPP woyeeee
Ubwelera Ku opposition ndiye misalatu DPP konzani matishet olemba opposition for life
Zoona zake osalola kuti azabweleleso
T/A Mabuka must be happy with his child
Ndizisiru zimenezo,,osadanda boss ayaluse amenewo May be atha kuchta manyazi
Kodi bon kalindo amthuwa sungangowalodzai kt asazabere zisankhozoyi 😂😂 aa inu
Kkkkkk koma inuyo bro kkkk mumakwana
Ndichifukwa chake anapanga chiwembu chomupha Chilima ankafuna chipani chithe chonchi
Ndalama a kukupatsani zo sikuti mudzalandira mpaka kale kale zotsala za dziko lapansi
Born kalindo chitsulo chanjanji.pangoline .ndiye kuti zitati Born kalindo,timothy mtambo.kamlepo kaluwa,kaliyate ,enock chihana ,achisale kuti ayime pamozi kuthana ndi chikangawa
❤❤❤❤ ndipo i can love that team ingakhale yabwino kwambiri
Katundu olemela Dr boooooooon kalindo ❤❤❤
Zitsiru za anthu ndi zomwe zikumalowa chikangawa party,game ndi DPP ndi APM
DC be strong 💪 mr president bon kalindo
Mr president waanthu osauka y don't tell Malawian kuti anyone ali okuzidwa tipange Mademo Malawi Shotdown chifukwa mau anu akumamveka patali anyone he understood you.
ineso ndikuziwa anthu ambili akufuna ndalama basi kuti ife amalawi tizivutika basi osati kuti tizisangalala anthu oyipa a mcp
More fire Mr kalindo
THE DC PRESIDENT ❤
Umakwana DC
The last man standing! The DC iiiiiiiiiiiiii munaneditu Mr president
Opposition ikugona heve wina ndi Matola
Koma chakwera akuchinda azimai moipa
Kkkkkkkk live??????
Kaswiri kwambili DC ❤❤
😂😂Achitsilu akalindo inu ingoyambani ndale 😅😅😅
Iwe chikangawa
The Dc mwana oopsa kwambiri
Bushiri usamale uzingodya ndalamazo wava
Pangolin wathu wathu uyu kkkk
Chakwera ndi MCP akugula a Ntaba othaitha pa ndale pamene opuma ntchito mboma mpaka zaka ziwiri ena zitatu osalandila ndalama zao what a shame
Koma chipani ndi chipani mkumagula Mr Mtaba?Anathatu kalekale ndipo padakali pano ndi nkhalamba
Ze DC kkkkkkkkk popanda inuyo Malawi sangapulumuke ipaseni moto Bondo yonse ili pa mbuyo panu MCP must go!
Mwandiphuzisa kulimba tima pachilungamo
Akalindo munakangoimila inuyo ife titha kukuvotelani kaaa zikutiwawatu ife zimene akupanga achina chikangawawo
Wokondedwa,Aplezidenti athu awumphawi,mutifunsileko,Alonda amuchikangawa,akutipo bwanji pa nkhani yandege,ija inagwa kuchikangawa, chifukwa tu mutchile lija la chikangawa,mulitu alonda,mumene muja,ndiye akutiponji?
Go deeper Mr Winiko
Born ndiwe mpulumutsi
kulowa chipani ndi ufulu wawina aliyese sizoti poti kalindo wadana ndi mcp basi onse adane nayo,kulibe zimenezo ndipo Anthu alowa2 Chaka chake chino.
Mufera zipani zomwezo ndalama yanu iposedwa ndi ya Zimbabwe anthu opepera!
Kod fuso kumati mafuta amakarandira achakwerawo alikuti poti njaji kuchoka kusanje sinafike kuno ndiye kuno azifikamotani
Kd Dan Lu ku DPP anal ndi mpando wanji? Ndye kuchoka kwake mpk munthu amwe panado aaaaaa Bon Kalindo ndwe wekha or akutukwane km more fire til naw nawe
Bakili muluzi anati asiyeni aphatitikizani azathela limodzi akugula Athu opanda phindu osakhwima pa ndale.
Ngat munthu ndiwe mfiti ukhoza kulowa Ku MCP.
Our own DC
Mutchulen amene akugulisa UTM mutchulen mwamsanga kut anthu asakamuvotere Ku conversion
A prothet b adayaluka
DC umatimilira
Choipa Chima satadi mwini eeee
Dc🎉
A mtaba anali a mcp kale ndiye inu mukudabwa bwanji
Ineyo mkanakhala ngati inuyo biggy bwenzi ntayamba kulowetsa modzimodzi ayambe kupereka ulemu
Apa Dpp yatha tiyeni tivomeleze Vuto ndimtsogoreli wawo yemwe alibe kuwona patari , anthu womwe achoka achulukitsa tsono kuwona ndikuchulutsa anthu wosati kuchepetsa anthu apa Dpp wolo itatani yapita basi palibe kulankhula kwina , tinkanena kuti akapanda kusintha chipani chiphwasuka lero ndi izi .
Ndiye chipani chomwe chaphwasuka ndichiti?.....DPP forever
DPP 🔥 🔥 🔥 🔥 basi
Mi lavu kalindo
Panyapako bon kalindo kod iweo ungaendese Boma iwe uli ndi chani machende ako ukuchitapo chani ngat ndiwe president wa anthu osauka ukalankhula-lankhula zako ndalama zimakhala kut zalowa nde ukumabwela pano ndikumatipusisa kunali mzako mtambo pano ali kut
Yes our hero
Kalindo chilichonse amakhala osokoneza ngakhale Ku tikufelanji ndiamene amasokoneza.moti akalindo atsala pang,ono awapeza ndimavuto aziwalo chifukwa AAAA kuyankhula kwambili
when you stand for the truth,you always stand alone,amakonda chilungamo that's why amaoneka ngati osokoneza
Amako ndi amene ali osokonedza zomwe akuyakhula akunama mmene amalawi tikuvutikira iwe suuona
@@JoyceBanda-k8t ulemu umapita Ku ulemu uzake chimene ukutchulira makolo ndichani? Nanga ineyo nditakuuza Kuti kunyini kosatsukako komaso kunyini kwakoko uchoseko manowo .chinyemba chachikulucho
Mutu wake sumagwila
Anthu wakulowa MCP kamba ka umbuli
Oopsya ndi Mulungu
Ntaba mbolo yopindika ngati uta😂
More 🔥
Zoonadi izi
andale si athuu abwino poti osewwa atuluka anja dppkuwinna addzawalanddila markmy wrds
😂😂😂 Kalindo
Kkkkkk iwe ndiwe suzgo
Nkhuku yoweta sagula pa nsika alowa ndicholinga adye misonkho yathu bas koma voti umakavota wekha chakwera sazakhala naye ndipo azalira
Zaziii zopanda ntchito
Tatchulan dzina a Prophet wo a Booon😂😂😂
Kalindo kuvesa chisoni galu ya dpp
Koma inu
DC❤❤❤
Nkhani ndi chisankho osati adzinva maganizo ako .
Dpp wooye
Auzeni amanama amenewo otaopa tilindinu akalindo mulungu azikutetezerani
Nsanje iwe udzafa nd mtima zikuchitika uku chipani chikukulirakulira wamkulu sangagulidwe ngt nkhuku amadziwa chochita ukunama.
Kkkkkkkk kalindo ukutaya nthawi ndpo ukufa ndi umphawi, umaonetsa ngati ndwe m'malawi oyamba osowa zochita kumalawi kuno
😂😂😂😂
The DC
Koma DC
Matiyimilila musadzafe mudzasowa
Wamisala iwe tangoyambitsan chipan coz zot DPP izalowaso mu boma muiwale akalindo
Bushiri usamale
Koma mcp ilibe manyazi bon kalindo akuwauza mayeso mcp ikukwika ikudana nayo tiziti mcp mulibebo wa school kodi
Anthu oaamva ngati munthu okufa ndi omwe akumalowa mu Chikangawa party
Bon ur true activist, representing millions of malawians
Chamba Kalindo
Koma zikuchitika zomwe akuyakhulatu. Ndekut chamba chake ndi chabwino
Yaaaa auze
❤
Komanso athu Ake akulowa mchipani ndi athu omwe adatha kale kale
Ku MCP tikudya money
Mumatha bigy 😂😂
Go deeper
Katundu mwana oopya kwambili
A MTABA AKUNGOFUNALO BOKOSI LODULA AKAMWALIRA
I thought Mutharika is older than Ntaba? Kkkkkk
😅😅😅😅😅
Kkkkk
Kkkkkkkkk
Mmmmm mcp
DC
💪💪💪💪💪
❤❤❤❤
Utupa mutu born kalindo ndi mcp umaturusa ma oudio every day ndi mcp panga zako aseyi
Aaaaaaaaaaaaaaaaaa
Za ziii
😂😂😂😂😂
iwe dpp ikutha and siyizatengaso boma