Well done bro mumatitsegula maso ndipo keep it up ...... ma Africans tikadagonabe system yomweija yopatsidwa sugar nd msalu ndikumasithanitsa ndi zinthu za nthengo wapatali Ndikumvera from Capetown
Zikomo kwambiri madara. M'makhwana ndithu. These western countries used to do so. The problem is our presidents but also ife. Africans have to wake up and fight for their right.
Thanks we have been waiting for this one Thanks we need wagner, Russia to help into this one thats why America and the west is fearing but they caused the coup. Africans we are neo colonised there too much economic emplosion
so the system of attacking protesters with teargas is not only in Malawi... i think let youth rule the african nations... we are tired with crueless leaders
Your genius keep updating us updated m'matha mumazisata
Always well said boss. We appreciate
My brother ndimakunyadila every time God bless you thanks from Durban
Mumativesa kukoma bg keep up it good work bro 💪
Inu ndi number one channel in malawi!!
Timadikira ❤❤❤❤ from here south Africa 🇿🇦 Johannesburg
Panopa am trusting you , you are growing
Watching from Malawi 🇲🇼....Best TV ever!
Our best Chanel ❤️
Thanx
You are true man i spotting you man
may god keep u long and bless u
Following mwachidwi brother
Matiimilira bro
We proud of you my brother 🙏
Ndimadila inuyo big boss keep it up good work ❤❤❤from Johannesburg
Ndimadikilila
I was waiting for u my boss
Well done bro mumatitsegula maso ndipo keep it up ...... ma Africans tikadagonabe system yomweija yopatsidwa sugar nd msalu ndikumasithanitsa ndi zinthu za nthengo wapatali
Ndikumvera from Capetown
Thank you always we are supot you
Umaitha 🙏🙏🙏🙏 god bless you
BIG 👍
Thanks 🙏
Very interesting. Zimatha wawa.
America
England and France. Mayiko awa akusawukitsa africa chifukwa chakupusa kwama president ena opusa
Number one king of history
Bakili Muluzi TV you are the best
Ulemu wanu boss timakunyadilan
You are our heroes man
❤❤❤Thx
You're the best
We just need another John Chilembwe ujayu adali wa phuma
thanks brother
Zikomo kwambiri madara. M'makhwana ndithu. These western countries used to do so. The problem is our presidents but also ife. Africans have to wake up and fight for their right.
Zoona izi bg mn respect nthawi zonse
Zoona big agalu amenewo amathipyesa mitima
Vuto la Africa likutsogoleledwa ndi azitsogoleri a dyera akawapatsa ndalama samalankhula kalikonse
Loud and clear bro
Nthawi zonse amabwera m'dzina la Democacy, ndipo tonse tikudziwa zomwe akufuna. Ife pansi ndi iwo mmwamba.
Thanks we have been waiting for this one
Thanks we need wagner, Russia to help into this one thats why America and the west is fearing but they caused the coup. Africans we are neo colonised there too much economic emplosion
Alright
Iwe ndichikolomandiya
Big boss bwanjimunkusowa
❤💪👍
Izi ndy zoyambila kale Africa timadalila maiko aluya
First to watch and to comment😂
Yess
Big up bro
Munasowatu bro
What about porand an Russian now ?
❤ mmakwana Big
Salute❤❤❤❤❤
I think zinazi zikuonetseratu kut the end of the world is near
Any time timuona mwana wa munthu akubwera😢😢
Big up brother ❤😂
Inuyo simukhala ndi mantha bwanji?
Mumatha keep up bro
Koma ndimakunyadilani broh
Never give up ❤
God bless Africa please 🙏🙏🙏🥺🙏
❤❤❤
A malawi zoti afirika akhale ndi president modzi komanso gulu la khondo limodzi mukuziwona bwanji osayiwala ndalama imodzi
Mumativesa kukoma bro
Keep it up man
open the mind
We are African sleeping toomuch
would war3 🤔🤔🤔
iweyo sumapsatila pofuna kulankhula Mulungu adzikuteteza nthaw zose
Inuyo maganizo oyambaso ndale alipo ngat ndli nd vote yanu
so the system of attacking protesters with teargas is not only in Malawi... i think let youth rule the african nations... we are tired with crueless leaders
My brother from another mother umakwana
Mumativetsa kukoma ❤
munasowatu big
Eish zovuta
First to view
mwakwana faddah
Zikomo kwambiri abigy mumakwana
Eeeeeee Uku kuli mavuto zedi
Africa izazuka liti gays , ndichifukwa chiyani Africa ikupembezabe mafano azungu
Announcing every seoson
Palibe chosatha American idzatha
Mukugwila nchito yaikulu, kutitsegula maso, mulankula zooona
Umakwana big umanena nkhani mwaukadaulo
Ndikadakonda ku Malawi tikanakhala ndi anyamata a Army ozindikila,a mphamvu komanso olikonda dziko lawo alichose boma lolepherali
Channel chabwino
Munthu wankulu kwambr inu
Reader of Africa is botch t
Trump azawine kuti nkhondo izathe basi
Don't mislead people plz
Number one king of history
❤❤❤
❤❤❤❤