ZISAKUPHONYENI IZI ~ LERO CHAKWERA WALANDILA REPORT LA NDEGE LIJA WALIVOMELEZA NDE WATOKOTA IZI
ฝัง
- เผยแพร่เมื่อ 23 ธ.ค. 2024
- ZISAKUPHONYENI IZI ~ LERO CHAKWERA WALANDILA REPORT LA NDEGE LIJA WAVOMELEZA NDE WATOKOTA IZI
Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
#MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika
This is not 1990 This 2024 we know everything what happened to chilima with other 9 people don't take us full allah knows everything allah is greatest and best 😢😢😢😢😢
@@joyahmedjoma4615 u just mention the name of Allah, but u don't know what Allah said in the Quran about death.
Thanks for the job well-done.May God safeguard your lives
Achakwela mukanangolapa ndthu
Mulungu yekha amaziwa zose amen
Day's are numbered,.chowuluka,chimadzatela, tsiku lina,kulibe wamuyaya.
Next time muzizayanlhuravchochewa timavota ndife 😢
We are not fools please we will know the truth after agalu inuyo kuchoka mboma.
A political theatre indeed based on a true story.
Ndimapembedza Mulungu ine yemwe alibwana pasiku lachiweruzo sndipembedxa mafano ine imfa ikuthamanga iyi tikaonana kumwamba
MAN Chakwera ndi inu mudalamura kuti anthu asiye searching….?.
ZAWUCHITSILU CHAKWERA IWE UNAPHA CHILIMA UFANA TIKUWUZE MOTANI UZINGO DIKILA KUMANGIDWA PANYAPAKO
Tenga committee yakwanu ukapangenso kafukufuku wina. Kodi a Malawi munatani, chirichonse kuchirowetsa ndale? Yooooooh
Kkkkkkk MCP yitiwonetsa zinthu.
pafoni ndipabadza,,km,pawayilesi,,chifukwa,wayilesi,,imaulutsa,,zoona,,zokhazokha,,ngati,,sitiva,,pawailesi,,ndie,,kt,,ndizabodza,,zoti,,anaphedwa,ndi,chakwela,
MUNANGOSIYA MUNGO VUTIKA INU NOSE MUDZAYANKHA AMENE MUKUYIKILA KUMBUYO CHAKWERA NOSE TASUNGA MAINA ANU MULI MGULU LAKUPHA CHILIMA
You're wasting time with your hatred to the leadership. Suzikupindulira zimenezi.
14:03
Group photo for what?? Esh koma dziko lapansi kulibedi chilungamo😊
Nditukwanapo apa
HOW MANY LIKES FOR comrade NTANYIWA WAPA LIMPOPO FM AND BAKILI TV😂😂😂
And brother sallo of yao FM😂😂😂😂
Kusamva amalawi, mumati tikufuna report, ndiye mwaiwona report, panopa mwayambanso kutukwana, aaaaaaaa za ziiiiiiiiiiiii, wafa basi wafa sangaphulenso kathu, m'malo mogulira chimanga anthu akuvutika ndi njala, za ziiiiiiiii mukulimbana nazo.Sithani kaganizidwe amalawi.
Anthu onse akuoneka kuti akuzimva ku chimwa khope zawozo mukapysa kulola kuchita chosaluma chifukwa chandara
A president, chilungamo chimamasula, iyitu sinali Ngozo ai koma inali imfa yokonza kudzera mungozi. Mangani Ngoma, yolamu, Valentino, chimwendo komaso mkaka. Mukatero Bwana you are clean! Apo bii Bwana kutsogoloku zinthu sizizakukomerano or pangono. Ndanena Kaya simuzigwiritsa Ntchito izo ndi zanu
Tsiku lomalidza kudzakhala kulira ndi kukuta mano mu HADE
Zabodza basi Lero zachoka Kuti silence ya chilima Malawi siogona .kunja zinthuzi Kuno zinthuzi basi Za zii
Boma likangositha mzimai akutsogolera wa ku mbc yu kwake kwatha
Manja ena atakhala wonganiza bwino sakuyenera kulandila report . Wosamayesana ayi
Mmmmmm bwana vomelezani khani yakuvutani basi mukapanda kulapa Lelo kumwamba ngozi bale wanga
Mkungonenepera nenepera ndima gazi a chilima mwakonda ndalama amalawi kusiya Mulungu wanu wa choonadi kuphimba chilungamo chifukwa cha ndalama one day is one day pansi palibe chitsitsi, olo lipot lanu likungolakhura zot munapha inuyo chilima, achakwera ngat zakukanikani Siyani pansi udindo mmaliza tonse mmalawi muno chifukwa chalipot lanulo laboza
amalawi, munkafuna, lipoti lanji, kapena, chilungamo, munkachidzw, kale, nanga, bwanji,, osangobwela, poyela, ndikunena, zomwe, mukuzidziwazo, kusiyana, nkumango, tsutsa, chilungamo, mukuchidziwa,
Koma kenako nditukwana
It was a plan don't waste time you will reap what you sow Mr chakwera why Banda chimwendo you said you said the plan was full while we're 9
,zomangoti,, achakwela,,munapha,,chilima,,pa,,4n,,,olo, pa,,,makomed,nzosaveka,,,ndipo,,sakadasankha,,ofufuza,kt,,afufuze,pamene,ena,akuzidziwa,,fikani,pawayilesi,,iliyose,,mipeleke, umboni,,osati,,pa,,4n,,ayi,
Anthu awa aliserious koma ehhhh
Munthu ukakhala ozolowera chiwembu umangopanga palipose ndi azako omwe adakuchitila chifundo kukuchosa matope chifukwa umakhala wazungulilidwa ndi azakoso ena amene ndiokonda zachiwembuzo kma zonse ndi nthawi Mulungu amalola kut chinthu China chichitike pofuna kuvumbulutsa China ndipo Ambuye Mulungu adalola chilima kupita kut zikaoneke ntchito zake zenizeni za chakwera kt ndiye munthu ozala ndi nyengo,kuba ,kupha kmaso kuononga ufulu ndi chuma Cha A malawife.
Report la bodza, munabisa brack box, mukuchoka basi 2025
U think is 1950 iwe chikangawa and chimwendo
ndale, zaamalawi, pamalilo, achilima, ,, mcp,,,dpp, ,,utm ,, singavoteledwe, kamba, kaifa, ya,achima, wa,,mcp,,,alipayekha,,wa,,,dpp,,alipayekha,,wa,, utm,,alipayekha, ,,olo,,,mutapanga, ndale, yotani, simungamusinthitse, ,,chipani, sizingatheke,
ndale,,pangani, pamisonkhano, osati, pamalilo, ,anthu, akufuna, fundo,,zanu,kt, anve, osat, zaanthu, omwe, anamwalila,,
Komansotu misonkho ikubwiliidwayo tayesani kupeza mafuta abwino odzoola. Eeee kumuwona secretary wa a bwannawo eeee ngati chojambula
Ayi zikomo
Chikhulupililo changa chikukulila kulila kuti anthu enawa si abusa
This is so closest to the end of you chakwera and mark my words truly am talking to you who are following mcp may God open your eyes and for sure this is end of mcp it will never return in government anymore and you will see
Lipoti achakwela ndi munthu amene anayamba kulandira zonamizana pano ayi
Achakwela munaphelanji chilima soka ndi thembelelo likhale pamutu panu
kwamene,,angatsutse, lipoti,,abwele,,poyela,,anene,,pazomwe,,akudziwa,,paifayo,,amalawi,adzakukhulupililuni,lipotilo, kusiyana,nkumango,,tsutsa,,mukudziwa,zomwe,zidachita,
Kungoonongapo ndalama zaboma on nonsense. Amalawi nkumavutika
MALAWI is now ruled by village headman , next year we will have president
komadi,nkhani,imenei,,pa,,4n,ayi,,mwatitopetsa,,bwelani,,pawayilesi,,,ndipo,,amalawi,,adzakhulupilila,,osamangotsutsa,,wayilesi,,singalole,,kuulutsa,,zinthu,,zabodza,,km,pa,,4n,,aaaaaaaaaaaaa
Mfiti iwe,,kwako kwatha bas,Ukapitilize kupha anthu
Pantumbo pako chakwela
titelo,kuti,,lipoti,,anena,,,kaya,,akunama,,sitidziwa,,km,,ngati,,pali,,otsutsa,,ndikunena,mu,nthu,amene,anaphayo,,amalawi,akhulupilila,,mupelekele,,pawailec,iliyose,,amalawi,adzakhulipilila,,,osatipafoni,ayi,,pa,,4n,,mulindiufulu,wakunama,kapene,,zoona,,,km,pawaeilesi,munthu,sangatsutse,,ngati,,simubwela,pawailesi,,,sitikuvelani,,zoti,,adapha,,ndichakwela
Chakwera panyero pako
KKKK JOHN 14 VS 1 TO END STATES THUS ;> WAKUPHA ADZAPHEDWANSO AT ALL.COST
God will judge you all
nose,,andale,,musayembekeza, kt,2025,,,mudzawina,,kamba,,kabodza,kapena,,kumukwenya,munthu,kaya, kutukwanana,,,mukunama, anthu, ,,tikufuna,,tive,,funda,,zanu,
otsutsa,,boma,,,anthu,,sikuti,,adzakukondani,,chifukwa,,mukukwenya,,anzanu,,zaifa,yachilima,ayi,,izondizanu,,komaso,,olamula,,anthu,,sazakukondani,,chifukwa, chalipoti,,paifa,,ya,,chilima,,zosezo,tilibe,,nazomtchito,,ife,,tikufuna,,fundo,,zogwilika,,basi,,osati,zamalilo
amalawi,,musamatipusitse,,ndikutsutsa,,mudayamba,,kalekale,,kutsutsa,,lipoti,,,landege,,,kusonyeza,kt,,mukudziwa,,m,mene,,zidalili,,km,,mukutsutsa,pa,,4n, ,amalawi,,kt,,akhulupilile,,kutsutsa,,kwanu,,bwelani,,pawailesi,,,,timayikhulupilila,,osati,,pa,,4n,,ife,takana,zotipusitsa,,
Asatipusitse ife sidzitsilutu chilungamo chioneka tsiku likubwela
Azibusa inu azibusa mukutani wetani khosa ndiyo Ntchito yanu
Akudya ndlam kae km adzaziwa kut zatha ali bokosi
Kkkkk koma lazaro amasekesa
Wakupha uyu mbuz
Commission yosappezekamo akubanja kapena akuchipani Cha UTM siya a malawi imeyo 😡😡 MCP commission of enquiry yowonetsetsa kuti zolinga zanu zinatheka. Days are counting down 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🔥🔥🔥🔥
Koza yako committee ikapangenso kafukufuku
@EvansEgra Chikangawa iwe ndilibe nawe phindu lililonse 🤮
Malawi akupita kuti?
Apa report palibe zovesa chisoni anthu ophuzira koma akupanga zinthu zoti even munthu oti sanaphuzire sanhazichite. Report ngat ili liri ngati nkhumba zakumana basi ndikulemba report mmmmm malawi wanga shame 5years ya chakwera
Anthu atsoka
Nonsense
Why wasting time speaking English?????
Muzilakhula chichewa ochakwela
Dog