KODI MWATI IMENEYI NDE NDI PROGRAM YANJISO ABALE YOMAULURA KUTI NDI BODZA FOREX ILIPO AKUNAMA?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 11 ม.ค. 2025
  • Welcome to our channel, where we dive deep into the intricate and evolving world of Malawi’s politics. From the rise of powerful political parties like the Democratic Progressive Party (DPP) and Malawi Congress Party (MCP) to the powerful impact of the UTM Party and other parties like UDF, AFORD, PP, MMD, and PETRA, we bring you insightful analysis on the key players shaping the nation. Explore the journeys of leaders like Lazarus Chakwera, Saulos Chilima, and the influential activist Bon Kalindo as they navigate the challenges of governance, power struggles, and the quest for a better future.
    Our channel is dedicated to unraveling the complexities of Malawi’s political landscape, offering you detailed breakdowns of alliances, rivalries, and the significant events that continue to define the country’s destiny. Whether you're interested in historical perspectives or current political dynamics, we provide in-depth coverage and engaging content that keeps you informed and inspired.
    Subscribe to stay updated on the latest developments, and join us as we explore the fascinating stories that shape Malawi’s political narrative.
    NOTE : We try to be as neutral as possible when giving you news from all parties. Maybe sometimes we may seem to offer or insult a certain party, kindly forgive us and above all, tell us in the comment section.
    #MalawiPolitics #PoliticalAnalysis #DPP #MCP #UTM #LazarusChakwera #SaulosChilima #BonKalindo #AfricaPolitics #PoliticalActivism #petermutharika

ความคิดเห็น • 48

  • @SilvesterLGama-k6k
    @SilvesterLGama-k6k 14 วันที่ผ่านมา

    Perfect said!👍 Mr Maseko keep it up!!!

  • @FrancisChafudzika
    @FrancisChafudzika 18 วันที่ผ่านมา +3

    Maseko walankhula zogwira ntima thank you Maseko.
    Tisamvetu kuti mwamusowesa paja mumadana ndichilungamo.

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 18 วันที่ผ่านมา +1

    Eee km oyambayu waswa 😂😂😂 kmso ulemu upite kwa presenter akungoti mmmmm sakutsutsa bravo braz 😂😂😂❤❤

  • @SPEARJAMES-r7y
    @SPEARJAMES-r7y 18 วันที่ผ่านมา +3

    Inuyo simunawerenge mawu m'baibulo ziko likakhala ndi usogoleri wabwino Mulungu amalidalisa amateteza kimaso amalichiza

  • @HusseinAubrey
    @HusseinAubrey 18 วันที่ผ่านมา +2

    aaaaa watipha tonse ameneyo

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 18 วันที่ผ่านมา +3

    All it's about poor governance ,
    President akakhala mbuli kapena Kuti savage , zotsatila zake ziko limasauka ngati m'meme yafikila dziko la Malawi

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 18 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤maseko

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 18 วันที่ผ่านมา +2

    Kumalawi tilibe president koma tili ndi chisaini cha president

  • @KelvinGeorgeMatope
    @KelvinGeorgeMatope 18 วันที่ผ่านมา +1

    Forex ilipo yambiri koma ili mmakomo aanthu .opportunists are making all efforts to create panic. Okapita pa Black Market forex ipezeka

  • @MacxwellStuarts-h9r
    @MacxwellStuarts-h9r 16 วันที่ผ่านมา

    Zonama kuti akamapita kunja transport imachokera kunja kunangokhala kuziteteza mabvuto onsewa achakwera ndi nduna zawo akuwapanga dala

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 17 วันที่ผ่านมา

    Mulungu akudana ndi ulamulilo was chakwela ndipo musamakaike ng,amba yose mulungu akupangila dala tikusogoleledwa ndi chiwamda choti mulungu sadalilole

  • @MasikoAsiki
    @MasikoAsiki 18 วันที่ผ่านมา +1

    komandalamayokayo sanatinganisila😢😢 mwinasinasi koma aphande e

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 17 วันที่ผ่านมา

    Malawi watha, ndipo mistake yimene tidapanga posankha fisi Chakwera tisadzachitenso a Malawi.

  • @YovitaBanda-k4y
    @YovitaBanda-k4y 16 วันที่ผ่านมา

    Anangolanda dziko kuchoka kudpp alibe plan iliyose akangotula pansi udindo Ena apitilize mwina zinthu zingasinthe

  • @SsBakali
    @SsBakali 18 วันที่ผ่านมา +1

    Maseko machine omaganga ndimawaya

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 18 วันที่ผ่านมา +1

    This is true malawi government collapse

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 18 วันที่ผ่านมา +1

    We don't have forever guys

  • @TadalaBirsonkanjanga
    @TadalaBirsonkanjanga 18 วันที่ผ่านมา +3

    Bele lomwe anayamwa amcp lotembereledwa umunthu palibe

  • @bornface4786
    @bornface4786 18 วันที่ผ่านมา +1

    Komano chumacho chikuvuta ife anthu osauka komano anthu andalewa makamaka am,boma akulemelatu kwambiri.

  • @YounusWabullah
    @YounusWabullah 18 วันที่ผ่านมา +1

    Bambo maseko apweteka gulu ndithu 😂😂😂😂😂

  • @JulioChiwalo-t4f
    @JulioChiwalo-t4f 18 วันที่ผ่านมา +1

    Kunena zoona a Malawi akuvutika kwambiri kamba Ka kugwa kwacha kumene kwachitisa kukwera kwa Katundu

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 18 วันที่ผ่านมา

    Mpakana R1 ikugulidwa kumalawi 167 kwacha hamayooo
    Dzulo ndatumiza R6,000
    Kumalawi yafika 10145,600
    Mpaka million mmmm
    Komatu malawi watha ngati makatani😮😮😮

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 16 วันที่ผ่านมา

    Ubwino wake tikubvutika tonse,chisankho chili pama vote asatinamidze anyani amenewa

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 17 วันที่ผ่านมา

    Iweyo ukamalankhula ndi anthu wusamakhale ngati ndiwe munthu wakuti siwukukhala M'malawi momuno kuti zinthu suwukuziwona m'mene zili liri ndipo makutu ako

  • @JamesMaduka-wk8xi
    @JamesMaduka-wk8xi 18 วันที่ผ่านมา +1

    Vuto ndi readership silibwino chomweakuchita sakuchidziwa

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 18 วันที่ผ่านมา

    Inu dziko muno mulibe presdent tisadabwe ndimmene zinthu zilili palibe ciliconse cikuenda dziko muno.Mabvuto onsewa atha 2025 cifukwa tikhala ndi presdent.

  • @BlestoneJonas
    @BlestoneJonas 18 วันที่ผ่านมา +1

    Forex ndiyambiri koma BOMA ili njakuba
    Zigawenga zimazapha abale wathu kusaka anthu kiti awaphe amawalipila ma kwacha
    Nanga zimene amagawa mmisonkhano kugulila ziphatso za unzika ndalama zake amazitenga kuti

  • @HenrySikumbili
    @HenrySikumbili 18 วันที่ผ่านมา +1

    Kuvomeradza ndi bwino😂😂

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 18 วันที่ผ่านมา +1

    Chakwera kunyini kwa make nkazi wake kunyini kwake

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 18 วันที่ผ่านมา +1

    Aloma ee aloma

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 18 วันที่ผ่านมา

    Malawians are not solving problems. Lack of foreign currency is not a problem but the Root Cause that has brought this lack or dearth of foreign curreny which our economists can jointly and easily redress.

  • @AlbertMatola-u9r
    @AlbertMatola-u9r 17 วันที่ผ่านมา

    Koma yokwela njinga yokhayo 😂😂😂😂😂

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 18 วันที่ผ่านมา +4

    Ndalama zilipo zina zomwe amakakwelela njinga 😂😂. Dzina anakadyela rice biliyana otila ziboda zangamila😂😂😂.

  • @ObvinessKBanda
    @ObvinessKBanda 18 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂 ku malawi kulibe president

  • @JafarAnusa
    @JafarAnusa 18 วันที่ผ่านมา +1

    Ndilikuno ku SA inde zinthu kunoso zikukwera koma fuel alipo palipose ndalama yayo ilinganganga osagwa

  • @RaphaelLikhomo
    @RaphaelLikhomo 18 วันที่ผ่านมา

    Bwanji inuosaidzutsa ndalama yagwayo mukutani . Inu

    • @symoldicky
      @symoldicky 18 วันที่ผ่านมา

      ndi achitsilu akulu uMunthu muziulekeza , anakuwuzan ndani kut aliyese Ali ndi mphanvu yolamula kut ndalama igwe or ikwere zopusa basi . timasankha mtsogoleli nkumpatsa mphanvu zoti asogolere moyenera osati zankutu zomwe MCP ikuchita just bcz akudya misonkho yathu

  • @BusaGaniza
    @BusaGaniza 18 วันที่ผ่านมา

    Satana ndi padela Chakwela womposa

  • @HERMANMALIWA
    @HERMANMALIWA 18 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkk yah ndaonadi ine ma pulezident ambuyomu akuuza anthu tiyeni tipemphere mvula yavuta koma achakwera mpomwe akudzazitsa mtouni yonse ndi nyau kkkkkkkkkk😂😂😂😂 Mr president😅😅😅

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 18 วันที่ผ่านมา

    Koma kunena zoonadi achakwela apitirira satana kuipa mtima kwake

    • @AlumakioChingalu
      @AlumakioChingalu 18 วันที่ผ่านมา

      A chakwera enawa dzimangani....kodi Bongu uja ankamuseweretsa chonchi..ndi Akapunthabuye omwe kunyoza president

    • @IbrahimMatola-k9p
      @IbrahimMatola-k9p 18 วันที่ผ่านมา

      Mesa president tili nayeyu ndichisilu chamunthu ndipo Muthu mwake mulibe dzeru dza ulamuliro akudziwa iye ndikuba basi

    • @MarthaMalopa-kw9xw
      @MarthaMalopa-kw9xw 17 วันที่ผ่านมา

      Vuto ndikusavomereza kuti zinthu zikumuvuta​@@AlumakioChingalu

    • @BrightZionga
      @BrightZionga 16 วันที่ผ่านมา

      ​@@AlumakioChingaluinunso ndakape amange ambuyanu ndithu back to the sender to you amangidwe ndimmbale wako

  • @ChrissieNyasulu
    @ChrissieNyasulu 18 วันที่ผ่านมา

    Phungu ofuntha