ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
😂😂😂😂😂😂 koma Mandota ndiwe waumbombo,,,,ndizabodzaso zoti ufa ndiwonongeka😂😂😂
Kkkkkkk bwera muzandisilikire mkazi wanga kuno😂😂😂
Udyekete watatu😂😂😂😂😂😂
Ka 10mita kaja pakana kuthamangitsa ma maili 😂😂😂😂😂😂😂Wasokoneza wa chiyao uja kuno😂😂😂
Iwe ndizakushilikani Mbambande 😂 much love ase
Kkkkkkkkkkk nsima yataidwa 😂😂😂😂
Tulo tamasana satengera guchuchu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🔥🔥🔥🔥pure talent
Che Mandota mbambande.Proud of you Big Brother.Mumatisangalatsa kwambiri
Kkkkkkk mwana wa kuchibwezi wa tundu wanji😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 musapaange ma comedy bring nsimaaaaa
Ndataya ndataya basi😂😂 zipewa ngat nthumbwana 😅😅
Kkkkkkkk koma ndaseka nsima yataidwa basi apa wachiyao waluzatu apa
Manthota iweyo mutu ngati phwichesi 🤣🤣
Kumapetoko😂😂 "mwai kuti kumafuta ndikwinakuuuu... Nkanakusiyaniiiii" lol😂
@@emsoulrealest9914 kkkkkkkkk eti abale koma che mandota aaaa batchala wachabechabe uyu akungofuna potipwetekesera ndi pwete iiiiiiii mbali inayi ndi dilu eti🤣🤣🤣🤣🤣
"Mwina mufuna kumwa madzi" 😂😂
Pachichewa Pali mwambi😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂 koma azimai tikuzigwila mmanyumbamu iiii
Tulo lamasana satengera gututu kmso wataya CMA 😂😂😂😂😂
malawi akuzutsa achinyamata ena ku ma drama like che mandota kkkkkkkkk
Chitemwe wanguwooo achmisyene ndauno 😂😂
Koma mandotaaaa anaza ndthu 😢😂😂😂
Iweyo ndi dolo kwambili 🤣🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌
Ama maili muziyana nawo ivetu zimunatiziwize 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 Che mandota, 😂😂 banja lakulepherani asisi mwataya sima inalitu pulani iyo malawi wavuta njala, aàaaa komtu ma mayere zimangovuta mbali inayi koma pulani amayiziwa 😂😂
Une brother wachiyao nguti ili chenene 😂😂😂😂😂😂
Kungofika ndi njala bas 😂😂😂😂 Komatu mbazada
Kkkkkkkkkkkkm tulo LA masana satengetela gututu kkkkkkkkkkk mandota umakwana uzangosowa
Kkkk kodi ma mayeri mwati zinakhalq bwanji😂😂😂
Koma Ine atakhala amunanga sindingakwanitse mmmm😂😂😂🙌🙌🙌
Tufuna ma mayili😭
Okay atsogoleri mwana wakuchibwez 😅😅
You deserve awards mandota😂😂😂😂😂
Ngati munthu amene kundipasa kuti ndikhala ndi data nde Chemandota, Bakili muluzi inuyo one day mudzandigawire wezi 😂😂😂❤❤❤
😂😂😂😂 Aaaah koma umbombo wake
Bwanawe 🤣🤣😂😅😂😅😂😅😂😅 umakwana iweyo kumeneko timati kubwera ysopano😂😂😂😂😂😂😂😊
Che mandota jekete yathatu😂😂😂😂
Mr che mandota mamayili alikut? Akanakhala mamayuli nsima sakana taya ayi 😂😂😂😂😂😂
bambo wawu mbombo😂😂 eshii
Kkkkkkkkk koma mandota umbombo wabwanj uwu
Kkkkkkkkkk chema ndota azanu kuwamwesa mazi😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Hahahaha akuti tingomwa madzi wa Cappella 😢😅😅😅
Buladi fwakala 😂😂😂
Ndalamazo tizidya nawotu bwana ife iliyose timaonera kukupanga support kkkk
Kkkkkkkk km ndee kwavuta ku malawi
Bambo amaini🤣🤣🤣🤣😅
Lero nde walongololatu😂
Mandota Nd dolo safuna dzibwana
Hard yako mandota
Mandota iweyo umantha😂😂😂
Ndiye mwati ubwino wake mbali yinayo siwachidodo ❤❤❤❤
Km Mandota umakwana Palibe Munthu Angaonele Comedy ya Mandota osaseka kkkk
Kod ma mayili banja linatha😂😂😂
Koma yeah mwambi wavuta umeneu......umakwana chemandota 😂😂
😂😂😂 next time feature Ma Mayili asowa ....🔥🔥🔥
Che mandota miyambi thooooo Kkkkkkk KKK
koma tulo la masana satengera gututu ayi ndithu mwambi uwu ndimakhwala amandota😂😂😂😂❤❤❤❤
😅😅😅eeeesh mwana wakuchibwezi
This is really amazing big up guys 😅😅😅😂😂
Mwachaje satafunadi 😅😅😅
Chemandota anadza kudzakhala. Akataye nsima zowona😅😅😅
Kkkkkkk KMA mandota Uli Nd umbombo wa secretkkkkk
Boss wanga mumatha ,, akataye bas kkk
Nsima ngat kachigumu kkkkkk ayi zikoma mandota
Kkkkkk akt kungomwa madzi akapela kkk
Dr mandotha Inu palibezo ❤
😂😂😂 ichi buladi fwakala😂
Tapanga Za ka 10mita 😂😂😂 Ma topfan asangalale
Mesa ni ndawi yasokudya😂😂😂😂😂😂
Komatu mkazi o enaso amamufuna ngati simukudziwa 😂😂
😂😂😂😂😂😂 Ati Mulungu anene kuti panyumba apa pasakhale usuwa
Ine ndimaganiza kut mwambi umabwela ndimmene nkhaniyo yabwelela sachamba basi😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 che mandota adah❤
Njili chenene brother
Kkkkkkk yatayidwa nsima amadota
Mandota❤
Chemandota mumakwana koma mmm umbombo mwawonjeza
Mandota No1
Asiyeni asanu adye mwene😂😂
Kkkkkkkkkk koma mandota ubobo umenewo
Km2 anganga akt kungomwa madzi kugaza akapela 🤣🤣🤣🤣🤣
Koma mwambi uja wavuta 😆🤣😆🤣
Kkkkk kma bambo ake ovuta
Vuto munapilikisa ma maili Actor mzako kkkkkkkkk ameneyo samadziwa kt ndiwe waumbombo
Mandota ujekete watha,mugule wina..
😂😂😂😂ndataya ndataya basi 🤣🤣🤣
Ati bladi fwakali 😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 afa ndiimodzid
Eti nakusilikan kale Koma 😂😂😂
😂😂😂😂 Good mandota
Lindota iweyo ndi 😂😂😂😂😂😂
😊😊😊😊 koma che mandota umbombo wake 🤣🤣🤣🤣 ❤❤❤
Koma umbombo wake😅😂
Jeketelija anang,ambaso akuluaja
Mr mandota mumakwana inuyo ❤❤❤❤
Vuto munapilikisa ma maili Actor mzako kkkkkkkkk
Chemandota jacket ikuthatu amwene
Chemadota ni number 1
😂😂😂😂😂sashamba basi
Tili pambuyu pano chemandota❤
😆😆😆😆 MA MAILI ANAPITA KWAO?
Mandota king of umbombo
😂😂😂😂😂😂 koma Mandota ndiwe waumbombo,,,,ndizabodzaso zoti ufa ndiwonongeka😂😂😂
Kkkkkkk bwera muzandisilikire mkazi wanga kuno😂😂😂
Udyekete watatu😂😂😂😂😂😂
Ka 10mita kaja pakana kuthamangitsa ma maili 😂😂😂😂😂😂😂
Wasokoneza wa chiyao uja kuno😂😂😂
Iwe ndizakushilikani Mbambande 😂 much love ase
Kkkkkkkkkkk nsima yataidwa 😂😂😂😂
Tulo tamasana satengera guchuchu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🔥🔥🔥🔥pure talent
Che Mandota mbambande.
Proud of you Big Brother.
Mumatisangalatsa kwambiri
Kkkkkkk mwana wa kuchibwezi wa tundu wanji😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 musapaange ma comedy bring nsimaaaaa
Ndataya ndataya basi😂😂 zipewa ngat nthumbwana 😅😅
Kkkkkkkk koma ndaseka nsima yataidwa basi apa wachiyao waluzatu apa
Manthota iweyo mutu ngati phwichesi 🤣🤣
Kumapetoko😂😂 "mwai kuti kumafuta ndikwinakuuuu... Nkanakusiyaniiiii" lol😂
@@emsoulrealest9914 kkkkkkkkk eti abale koma che mandota aaaa batchala wachabechabe uyu akungofuna potipwetekesera ndi pwete iiiiiiii mbali inayi ndi dilu eti🤣🤣🤣🤣🤣
"Mwina mufuna kumwa madzi" 😂😂
Pachichewa Pali mwambi😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂😂 koma azimai tikuzigwila mmanyumbamu iiii
Tulo lamasana satengera gututu kmso wataya CMA 😂😂😂😂😂
malawi akuzutsa achinyamata ena ku ma drama like che mandota kkkkkkkkk
Chitemwe wanguwooo achmisyene ndauno 😂😂
Koma mandotaaaa anaza ndthu 😢😂😂😂
Iweyo ndi dolo kwambili 🤣🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌
Ama maili muziyana nawo ivetu zimunatiziwize 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂 Che mandota, 😂😂 banja lakulepherani asisi mwataya sima inalitu pulani iyo malawi wavuta njala, aàaaa komtu ma mayere zimangovuta mbali inayi koma pulani amayiziwa 😂😂
Une brother wachiyao nguti ili chenene 😂😂😂😂😂😂
Kungofika ndi njala bas 😂😂😂😂 Komatu mbazada
Kkkkkkkkkkkkm tulo LA masana satengetela gututu kkkkkkkkkkk mandota umakwana uzangosowa
Kkkk kodi ma mayeri mwati zinakhalq bwanji😂😂😂
Koma Ine atakhala amunanga sindingakwanitse mmmm😂😂😂🙌🙌🙌
Tufuna ma mayili😭
Okay atsogoleri mwana wakuchibwez 😅
😅