Nde mwapanga bwino reproduction 😄😄 I think you should be featuring Anganga Jabiru and Mologeni in most of your comedies, these guys are good...More lavuzi and respecting from Che Mathews Mandota Phiri from Lusaka Zambia 🇿🇲
U are bad boy , mandota 😂😂😂😂😂😂😂 Maso Award its urs again this year stand with u , free Palestine 🇵🇸 from River to the Sea Palestine will be free 😂😂😂😂 u never disappoint us at all long live Malawi 🇲🇼
www.maso-awards.live/category/best-comedian
Very nice
Kkkk umakwana 😬
Bro mulobwino
Yo map
@@GanizaniMasambukait
Mandota umandiwaza aise, watching today from Liwonde Township
This made me happy and free from stress
Nde mwapanga bwino reproduction 😄😄
I think you should be featuring Anganga Jabiru and Mologeni in most of your comedies, these guys are good...More lavuzi and respecting from Che Mathews Mandota Phiri from Lusaka Zambia 🇿🇲
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 this comedy was very nice from the beginning up to the end soil madothi
Che Mandota inuyo ndi One ndipo osadziwa za Inu ameneyo zokoma sanayambe wakumana nazo.
Ulemu wanu ndithu.
Koma Mologeni ndiwe oipa kwambiri 😂😂😂😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣koma this clip siyamasewera.... Maso awards abwana muwinaso kkkkkk
😮😮😮😮 Zonotu nsanga wanga mandota mwandipwetekesa mimba mkuseka apap kkkk....... Number 1
Odi ine ndiyambe ku commenter 😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣Sokosi zagulidwa ulere chemandota afa kuwiri
Inuyo ndi akita kwama akita kkkk😂😂😂😂kom ndaseka tu
Muli bhoo guys pomwe amr jokes amawafunsa kuti kumalawi comedian amene akukusangalasani sanatchule inu nde kuzikonda chabe
Kom khan yaiikulu ndiyakut soil madothi 😂😂😂😂 akutani kwnikweni
❤❤❤❤❤❤. Ndimakuvela mushe mandota ndi aZako
Mandota umaganiza bwanj koma ase 😂😂😂😂😂😂😂😂
Aaaaah mwayendana chapansitu apa....
Zomanganazo ndi chifukwa cha lack of communication tip siinayende bwino wayenera kupereka chindapusa mbasada.
Most of the times, i just watch and laugh without commenting on koma pa iyiyi mwanditha. More fire.😂😂😂
Chemandota iweyo udafika mu comedian..soil madothu😂😂😂😂
Yamologeni yadzuka mmalo moti inu mumuyamikire...mwamudaso haahahahha a mandota tiziyamikirana ikadzuka mesa
Mandota ndi dolo kkkkk Bola musapitilile ndi kukhala dolofekkkk
Ya Msako ikasuka ,,,kumayamikira_Nyumbatu, Koma CheMandotaa ,🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkk Mandota koma
Hahahaha ...iyi ndi mbambande adhaaaa😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Brother iweyo umatha heavy 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkk apa ma mayeri aiziwe basi, bolatu mologeni yawina kkk
This is Massive 😆😆😆🔥🔥 lemme vote for this guy mweeeee,,, 🤣😂
U are bad boy , mandota 😂😂😂😂😂😂😂 Maso Award its urs again this year stand with u , free Palestine 🇵🇸 from River to the Sea Palestine will be free 😂😂😂😂 u never disappoint us at all long live Malawi 🇲🇼
😂😂😂😂Koma mandota umata kkkkk kuzakha mkazi or odi 😂😂😂😂😂nice comedy
Iweyo pa dolo unadutsa pano ndiwe dololo😂
Ma khomedezi adatero prophet habbakukku😂😂😂😂😂🔥🔥
Chemandota suzapala pankhani zamacomedy tiyeni komweko komweko kumaso award
Mandota wadyerewa,akuti lnjini yako ndiyosakoka😂😂😂😂😂
Iiyi ndiye mwakunga guyz😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 inu munabwela kudzakhala eeee osapopa 😅😅😅
Kugwila umve wanu😁😁😁😁😁🔥
kkkk akulu awa zinthu amaziyamba bwino bwino ngati wanzeru ndithu, kaya vuto lilipati kaya? ndiye chipwilikiti wabutsa lerochi uthana nacho bwanjiii? chemandota iweee?
ndikupanga ma reprodution ndine 😆😆😆
Lafusiyu Mpasada
How to vote?
😂😂akupanga reproduction nkazi
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Machine opangila machine azawo akokedwa kuno 🤣🤣
Brother iweyo umatha heavy 🔥🔥🔥🔥🔥
Eya alakwisa kumumanga mbasada chifukwa apereka matha kwaathu Ena zomwe zingapangise kuti asamaulule poopa kumangidwa.
I have watched again 😀🤣😂 full of immorality in this video
nganga jabilu ndiosokoneza kkkk apeleka bwanj number 😅😅😅
Mandota ndinu ozokonesa mundu wamkulu 😂😂😂😂😂😂 Apa sakufutan noka
Mandota suzatheka aaaaaa
Yavuta ndi venue
Imeneyi so ndie iti ya soil madothi🤣🤣🤣🤣 mwamtolakuti ameneyuuu
Apa pokha ndie MA maili aidziwa basiii ugona panja uona kkkk ndie chimkazi chake so chodablitsa pompopompo asaaaakkkk komanso ndiiwe galu kwabasiii mandota mwambiumenewo ndiutiii oti chikadzuka chamzako kumayamikila kkkkk
Kkkkkkkk chemandota sazatheka😂
😂😂😂😂😂😂😂 km ndye kufa kuwiri
Ndee machine osakoka Ndi andani?? 😂🤣😂🤣😂 Nice Doc
Apa mologeni wakuyendani pasi😂😂
Hahahahahaha koma iweyo aise umakwana kkkkkkk mungodyesa akazi anu et kkkkk
Iyiyi nde mwakunga jentomeni
Akita wafadi.😃😃..koma award ndiyanu
Wakhaula nayo😅😅😅😅😅 tangotikongozan galimoto ife😅😅😅😅😅😅
Yazako ikadzuka kumatan😂
I like this vide chief
Mandota never disappoint us 😊😊
Mwangopezana basi😂
Watching from Durban RSA ❤
Kkkkk...! Mologeni ndi deal, Venue plus Stonkeni
Kkkkkkk chemandota umatha ndipo uwinaso
😂😂😂 Koma guys flim sindinamalize koma ndakomokela ayi zikomo
❤❤❤❤ mandota umatha usazabwelele mbiyo nice job
😂😂😂😂😂😂koma nditseka bwanji ineyo mandota?
My vote always for you
ati aVanessa mukudya nokha😂😂😂😂😂😂😂😂😂wapalamula Mandota
Kkkkk machine okoka omwewo
Ma maeli enieni aja mwasiya kuti....as a mataofu fakitole kkkk
Ampanga upongwe 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
iyiyi ndiye ili bhoo
You never disappoint sir keep the fire 🔥 burning 🔥
Che mandota mpuma mu chepese please 🙏 kugofikila kuulula aaaaa zizikhala chocho
Mumakwana che mandota ilofusi you
Yowinila guys,inuyo ndi wani mwampanga nsanu upongwe😂😂😂😂😂😂
Ndota sumakhumudwisayi🔥🔥🔥🔥🔥
Yansako ikasuka kumayamikila 😂😂😂😂😂 mbasada
Hahaha koma Chemandota ndi more fire!!
You are creative
Chipongwe 😂😂😂😂😂
Chemandota will kill me😅
My favourite comedy
Nice comedy
Nice comediy mandota
Mandota siwuzatheka bs😂😂😂😂
Kkkkkk koma yathela pa.njila mr
Iyiyi ikhale ndi part 2 😂😂😂
Matchini okoka
Yiweyo umakwana mandotaa
Mmakwana 🎉
Moto unandi 🔥🔥🔥
Apa panali luso zikomo kwambiri
Kkkkkkk aaaa mandota ndwe dollar kwabas
Kkkkk 🎉machine ako ndiokoka
Mandota 😅😅😅😅😅 machine ofoyila
U have my vote
🤣🤣🤣🤣🤣wafa kuwiri akita
😂😂😂,uyu amatha
Koma iweyo aise😂😂😂
Great job mumatha
Koma che mandota iyi wapha ayise kkkk
Mbambande mandota komano ipitiliza
Keep up the good work sir