Zikundisangalasa kut mukupanga zathu zachimalawi aliyese wapa school olo no school atha kuonela... keep it up guys..Kaya mkanapanda kubadwa Ku mw abusa mkanawadziwa Kaya 😂 ayayaya
three cameras on set, nice over the sholder, Wide Shots, Great camera quality, Tonde dont look at the camera, brother to tonde dont look at the camera, all in all your acting looks natural, like real life.
Best series on TH-cam Malawi, according to me of course
That's it
Fact🔥
You can say that again🎉🎉
Me too
True ❤
Proud to have nice episodes like this in our country. Love it, great quality, nice casting location. Nice dressing. All perfect
The best series in malawi so far enao ndi ana kkk komano Angozo ndi mai ngozo mumayenelana and munazolowelana kkkk lili banja mmm silingathe .
Adha a imvi wo ndi adha a daziwo acting ili mwala, zosachitaso kukakamiza mmm so natural and beautiful
Kom nde anaakakamil ma drink tu😂😂😂😂
Tufuna nyimboyonso ka soundtrack yakumapetoyo❤
Chiphaliwa. Ndalama zithela kudyesa Ganizani ndi azibale ake😂😂😂😂😂
Boys 3 ijayo ee🤣
Kaye dyela😂 ...kusakhuta
@@TiyamikeMituka 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@@FrankieBoe01 your comment made my day 🤣
Aduka😂😂😂
This is absolutely nice akuluakulu mwapha ndipo simasewera🔥🔥🔥🔥🙏
I love the ending 😂😂 ati zili kosiyana
Koma so this Edo guy is 🔥🔥
All in all this show is good guys. Keep it up
Eyaaaaaaaa zikomo nthawi ija mwakonza🔥🔥🔥 everything on point
Eeeeeeh Edoh ndi doloh ......Kmanso Ngozo ndi nzake hyphen mmmm.....Ganizan ma guy 👐🏻..patricia ..tingoti cast iyiyi ndiyachabe ...very talented
Abart ndi ngozo ndi one inuyo mumandiwaza heavy u gyz mumapanga modekha koma nice confidence nice on TH-cam comedy
this one got me laughing🤣😂😂the lines are just crazy
muli bho guys....Edo is professional...you Guys mumapangadi act ...like real life❤❤❤❤
Sangie❤❤ talking mwa pa easy but funny 😂
Ati yes yes am following😂😂😂😂😂 koma ashado abwera ndichizungu😂
This episode is so woooow❤ I have laughed my lungs out😂😂😂😂. You guys are the best ❤
Beautiful staff ⚕️❤️🔥🔥👍so good seeing this quality staff coming outta our soils
Kkkkkkk akuti ndikupangila iweyo zibayo😂😂😂😂😂 Koma ngozo
All I can say is that I love this series, you guys are investing in what's worth 🔥
Edo Aaaaa mwana wachikape, nane ndimakhala ndima lawyer awiri thawi zambiri😂😂😂nice episodes ma guy keep it up
Mtebe ndiye wati Belita ndi mlongo wako😅😅😅
Level up guys ❤, #usauver to the world.we want more eps........... please Ango...pat. AlbaGanizani bwino
You are the best guys. Keep on keeping on. Grow the movie industry in Malawi
Sangie kuzasiya usauver nanenso ndizasiya kuonera😂😂❤vibe killer amwene kkkk
Keep on fire burning magaye
I like hyphen's top
Watchena🔥
Mwabwera mwabwera inuyo maguy🎉 mutimvesa kukoma❤
Boyz eeeh... Perfect... Sindikuona chomwe mungakonze...
Koma ndikufuna sound track yo feat Sangie yo
Nafeso tiku isaka bwanj
Tilipo guru oyisaka😂
Big up guys mumatimvetsa kukoma, keep the fire burning 🔥
Hahaha ndiye mwati mowa wammusi 😂😂😂😂
Kudyera mchere kkkk koma guys
Ati ndupangira iweyo zibayo😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Gani is the best guys....komano Edo nkazi wanzako mpaka kumunena kuti nchamowa eish😂😂😂
Aaaaa km kamachep u live me in suspense bt i love u gyz and u teach me many kmas ndkamaoner inuyo kusek kokha kokh ❤❤❤❤
Gani is naturally an actor
Fakiti
Ndipo zoona
Straight up
😅
International level ma guys mumaitha kwambiri, keep it up😊
Edo mabonza 😂😂😂😂😂 at chamowa
Ati anabwera ndi chimkunda kkkkkkkk😅😅😅😅😅😅 Koma Albert ase
Mulatu nde ndi actor guys🐐🐐🐐
Chiphaliwa akudyera ndalama😂😂😂gani sanachenjere bwino
😂😂😂😂patricia at tea uyo mumwe mungayambe kukomoka nd mphepo🤣🤣🤣long live aunt pat
Sangie is the best for me especially okonda miseche ife kkkk
Edo knows everything about mkaz wa Albert😅😅
Komaso Ganiii eeeh sch yake it kundirande abale 😂😂
Kkkkkkkk akut akaphuzirako 2 months yokha kkkkkk
🤣🤣🤣 Muweta bwanj nkhumba ndi nkhuku malo amodzi,, A Eddoo adabwa nazo
Anthu inuyo nonse mumandiwaza eehhh😂🔥🔥 everyone is unique
Long enough to keep entertained for a while
I like these long episodes
Sangie ndi angozo munayamba mwachezapo za mtendere koma😹😹😹
Koma ngozo nkhukutembo, nkhuku ndi nkhumba 😂😂😂😂
Tonde wabwela kuzakhala! Just take your time when conversing.
man edoh za ulimi tisiyireni anyamata aku bunda mungawanamizepo a ngozo wo😀😀😀
🔥🔥🔥 ati nd nkondii kwambri 😂 maguy munaza
Amuna kunama eeeee😅😅😅😅 ati ndi ss wake
To say truth
Your episodes makes me feel happy
Thank you
Ndie kuti tingo funa kudya basi😂😂😂😂😂
tikaphunzire basi nkhani ndika sukulu 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Giya on fire Madala gani ndi munthu wa mmutu ngt choko
Ati chizindikiro chawo ndi dzungu😂
From RSA Cape Town South Africa Stellenbosch....Mr mp chimphaliwa azigawa ndalama Kwa mulamu wake wa piksy😂
Guys or mutama shorter ma episode daily ine mkumtimaku aaaaa kumva boboooo basi keep it up ❤❤❤❤❤
Ati akukula ndye ambuyakotu 😂😂😂 umakwana Gonzo
😂😂😂😂 nde mwat nkhan yama lawyer imayenda bwanj ukakhala sober kmso ukalezer
Where were you guys..I can't remember when last I watch this
Kip fire 🔥 buuuu
Ndimachita kuona kuchedwa kuti Friday lifike❤
Koma Hyphen iweyo!!!! Hmmmm.
Komanso Patricia 🤣🤣🤣.... Ati phone mukamaiimba muziiyankha... Eish
Hahaha kwachemelatu😂😂Ulendo uno Gani nde maluzi amuchapatu eeeh🙌😛
@ ndekuti Cash yatalikilaaa🤣
Komatu a Edoh osadanitsa anthu😂😂😂😂 ati mchamowa a Hyphen ali nchikondi cha nyoooo
Ati akukula nd ambuyako Piksy amwene😅😅😅
This vibe of usauver its something else ❤ big up ,we are enjoying and getting the lesson as well ❤️🩹
One of the best series ever 🥰
Maguyz inuyo mundipanga insipre msaname ngakhare msanakwatire😢😂
Mwatinyozatu aku ndirande ma guy😂😂😂🤝
Kom sangie 😂😂😂😂 can't stop laughing 😅
😄😄😄😄 kma man Eddo 😂 ndimkona ine sindimamwela kumeneko ulindikuchikamwa kkkk
Zikundisangalasa kut mukupanga zathu zachimalawi aliyese wapa school olo no school atha kuonela... keep it up guys..Kaya mkanapanda kubadwa Ku mw abusa mkanawadziwa Kaya 😂 ayayaya
ATI ukuweta nkhuku ndi nkhumba pamodzi chifukwa chani😂
Eeeehh Zoonad Busa Wachinyengo Eish !!! Ati Shop Ndiyanga 😂😂😂😂😂
Uhule😅😂
Gani akuzembela jetu😅😅😅
Akuti ndimkondi😂 😂 Edo ulemu wako
I always enjoy this, flowers🔥🔥🔥
koma sangie ndi mau a chinyeeeeeeengo kkkkk eshiii unawavetsa
Chiphaliwa samala ndalamazo zitha uwona😂😂😂
Akuti belita ndi mulongo wanga😂😂😂😂
three cameras on set, nice over the sholder, Wide Shots, Great camera quality, Tonde dont look at the camera, brother to tonde dont look at the camera, all in all your acting looks natural, like real life.
Eish camera anaying’ana kwambiri eeeh
Yes indeed tonde stop look on camera
No, he wasn't looking at the camera, amachita kuoneka but angle ya Camerayo ndiyomwe siinayende. I don't know if that's making sense
@@BlklilSis kkk
Kkkkkkk sorry chabwino hahahahaha
Watching from Polokwane 😂 i like the point kukula ndimu mtima
a Edo ndiamasokoneza kuyambira kale😂😂😂
The day ones of Usaver let's gather here💃💃💃
Day ones we here
Ati ndimphepoyi mungakomoke😂
Idzituluka daily bwa...so nkhukutembo nde uti ..nanga nkhumba iiiiii
Ndekuti cash yatalikila😂😂😂
Let me be your top fan 😂🎉. I love this Usauver serie❤
Patricia undipolere fire😂😂😂
Talented malawi gyz 📍🔥🔥🔥
Ati ndiwozichepesa sakufuna kung’animilatu 😅
Koma Sangie😂😂😂 One love Sis!
😅😅😅 barman uyu ngosokoneza zithu atha kukupangisa bp
😂😂gan ku jon kwamulephela apa akufuna kupita ku xul 😂😂 ayi zikom
Motivational speech from Albert 'munthu siumasiya zomwe umatha'😅
Komaso Belita anazivutila mavuto😭😭😂😂😂💔
Komatu a Eddo kukonda kunyanyala nangatu mkazi aaaaa. Koma zikubeba guys 🔥🔥🔥
Love you guys❤ keep pushing matimvetsa kukomaaa
Today's episode was very much ok... keep it up
Fire 🔥🔥🔥
I am enjoying this