ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Omwe timafila sangie bwelani tikhale malo amodzi
akt ine millitary sindingapepese
Ndipo ndichi vibe
Koma Hyphen can act with confidence and serious 😂😂😂😂😂😂😂😂 I love it
The part I liked
It's Emmie and her Ben 10 for me 😂😂😂 crew yonse ndinu madolo ❤
Sangie is good at acting
True
I always say the same nane. She's great
She's Dope Indeed
I was about to type the same.
very exceptionalindered
Gani ndi sister wake tsiku lina adzaphulitsa bomba mnyumba mwa ngozomu
Izi akupanga Sangie ndi Ganizani kudana ndi m’bale wa Piksy zinandichitikirapo ndikukhala ndi mkozi yanga, a very bad experience I don’t wish anyone to go through 😢😢😢
Sangie apite ku mushroom shade she's too good
Neighbour wa mtebe nd doloso hvy🔥🔥💯
Ndipo zowona
Usampepese inenso sindngampepese koma Patricia nd Gani mmakwana 😂 neba wamasuka koma abusa nthandizeni 😂 anthu amaendadi awiriawiri kkkk Gani wada bwa . Keep the fire burning guys 💪🔥
Friends of Ganizani let's gather hear ❤
❤
😅😅😅Kodi ndi mabatchala okha okha 😅
Wow ine khawa chipere🤗Keep it up guys❤️Mpali yachimalawi
Who's watching because of Ngozo and Patricia?😂
Tonde, neba wa abusa; voice yake really fits for that one batchala in most yards.
Amatha
On point nice observation kkkk
@@NelsonMumbulu-mq5ob m'bale wanga iwe
Koma i admire relationship ya gani ndi sister wakeyu ndi fire eeh😂😂😂🙌
Ngati eni eni et?
Kungolowelera nkhani yosaidziwa.....😂😂😂😂
Koma Gani ndi sister wake eee 😂😂😂😂 smoko. Ndinu mtundu wanji was anthu 😅
Tizi fusana mchizungu uwu nde mwano of the year 😮😮😮😅 a Gun pwiiiii
Koma sangie ndi obheba💞
EEEE MAMA G ALEROYU
Uyu anabwera
Ndipo kwambiri,being black and beautiful❤
NDIPO NGATI AKUFUNA BANJA NDILIPO
😂😂😂gani ati ndiwe maskin-tu😂😂usauver is my favourite 😍 ❤❤
FROM ZAMBIA this is really Good PIKSAY continue acting movies we love your movies here in Zambia
Patricia pa chiwongolelo one body one soul amandiuza kuti ndipange verify 😂😂😂😂😂😂😂😂
Munthu ngati sangakangane ndi ine mu "English " Waluza🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Watching from mwineriwa vg mulanje Sangie kumulalatira munthu oswalakwa eee😂😂😂😂😢😢
koma sangie eeeeeeeeeee, nde kuli hyphen kuyankhula with khoffffffffffffi
Kam'busa kachinyengo in Patricia's voice😂
sangie is one of the reasons why I watch usauver😂😂
Patricial and Ganizani muzioneka kwambili u guys makes it gud recieve ur 🌹
Patricia nd moto keep up guys good work
Sangie is too good...
Kom sangie umatha kom ndimafuna nyimboyo guys please
I have liked the song at the end of the episode. Anybody who knows the title and where I can get it?
Bestie too continue kuipatsa fire😂😂😂😂
Sangie🎉 😅😅😅 Ati zinthu zambiri zitha kupezeka zachitika
Nice one Koma dry head mutu ouma😂😂😂
Koma Patricia. Kkkkkkk akuti inensotu ndi army.. Sindingamupepese
Sangie you will kill us with laughter one day
Koma Mtebe mmmm ayi,,mapemphero anji olipiritsa😅😅
where is part 2? this comedy is very very impressive.
Usauver is my favorite ❤
Sangie shiiii kkkk. Ndeno mwat makampanie oika ma shandiyiliyao ndachna genie wo 😮 kkkk. Here we goo!!
Nyimbo yomalizayi siyimaipeza bwanji? Sounds good
😂😂😂😂😂 sangie ujayooooo ndi vibe
Sanjie ukuitha respect 😊
😂🤣 😂Sangie. Eshh kungofikila chorus.. Nkhani yosaidziwa "umbava "😂 🤣 Iwe ndi more bwanji😂
Gani upepesa bwanji! Ufuna uphweke😂😂😂
Sangie to the world.Mbambande 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥Best episode
Anthu amayendad awiriii awiriiii 😂😂 kma Gan , abusa kkkkkk winayo akut simungakangane muchingerez
Ati anthu andichenjelera zikhala ndekha😂😂😂😂😂 sangie
Albert yatenga lehu🤣🤣🤣
Ndaona chocho😂
Eee ganizani and sangie 😂😂😂😂😂 isowa bwanji power bank🤣🤣🤣
😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 e sugar mam
Ati azatchola nyumba😂😂 Patricia is dramatic ah
Big up guys ... Ma mic apa nde munakunga
Koma mnyumba mwa Ngauzo muzaphulika bomba day 1😂😂
Usauver ❤
Am watching it
Best usova
Keep on fire burning magaye YoooooooooYou rock guys 🔥🔥🔥🔥🔥
Emmie ati Ali ndi azilamu dziko lonse🤣🤣🤣🤣
Iyiyi yandikomera hvyy mmmm....u guys u just wow,,,,improvement ya boh hvyy.... this is professional
One body one soul 😂 mumatha
Sangie akuti iyeso Ndi army
agani nda matiyasi malo mokwatira muli busy kushishana pakhomo lamwana ngati sangie
Hyphen wasiya fulukutu fulukutu chifukwa chani😅😅😅😅banja ulilephera sure kmanso kumapetoku kwachuluka atambwali n ganizani emwe😅
Ati Gani akupemphelele zalowa masanje ndithu
I swear sangie is the best
Sangie eeeeeeeeee Ayi ndikawawa
Sangie is really good 😊
The last part though 😂
Sugar mamie wazemba I know amaziwana ndi Gan😂
Sangie ndidolo heavy ❤❤❤❤
Last week kungotigulisa ma bundle bwana???
😂😂koma ndaseka Emmie akuti kwathu sitimayikitsa ma Buble koma timayikitsa ma ShanDaria
😂😂😂😂 sangie ndi ganizani🔥🔥🔥🔥🔥
Sangie umandiwaza nsaname
Kmatuuu u always live me in suspense, owky mumath km ma gyz 🔥🔥🔥
Ma guy inuyo mumandiwaza heavy
Great job guys❤
😂😂😂😂😂😂😂koma ma guy ati nakumwesa wine kamozi😂😂
Ati poyamba umapanga fulukutufulukutu koma pano......? 😂😂
I love the confidence of hyphen ....
ask abusa for kupepheleledwa for kupeza mkazi while putting on a ring?.....anyway always on point
Koma sangie ada iwe nd dolo 🎉🎉
Sangie akuti nayenso ndi Army😂😂😂😂😂
ili bho❤
Kkkkkkk koma sangie basi kapangeni zandiwozo,zabala-zo zimandibwerera ukuku
Kkkk ati moyo wawumbanda kkkkk atii simunthyola nyumbayiii
Maguy inuyo mumatha ❤
Koma Gan adha akut amathu
Sangie ndi WA Army sapepesa adafa kwambiri lol 😂
Muzitulisa ma episode awiri bwanji 🔥🔥😂
Ati munakakwatilatu amkazi amathandiza 😂😂😂😂😂😅😅
Anthu amayenda awili awili kkk ndi emweyo kkkk
keep it up guys zilibwino
One body one soul😂 Patricia anakonza
At least you have extended the time guys, we appreciate ❤
Muli boh guys keep it up
This season magaye mwabwera❤
One body one soul😅😅😅😅 man munomo?😅😅😅😅😅 Patricia umandiwaza🎉🎉
😂😂😂😂
I need Theme Song please title yake ndichani
Sangie koma pepesani za usilikalizo ayi😂😂😂😂😂😂
Moyo wakubaaaaaaaaaaaa😂😂😂😂singapepeseee ine ameneyooo😂😂😂
Omwe timafila sangie bwelani tikhale malo amodzi
akt ine millitary sindingapepese
Ndipo ndichi vibe
Koma Hyphen can act with confidence and serious 😂😂😂😂😂😂😂😂 I love it
The part I liked
It's Emmie and her Ben 10 for me 😂😂😂 crew yonse ndinu madolo ❤
Sangie is good at acting
True
I always say the same nane. She's great
She's Dope Indeed
I was about to type the same.
very exceptional
indered
Gani ndi sister wake tsiku lina adzaphulitsa bomba mnyumba mwa ngozomu
Izi akupanga Sangie ndi Ganizani kudana ndi m’bale wa Piksy zinandichitikirapo ndikukhala ndi mkozi yanga, a very bad experience I don’t wish anyone to go through 😢😢😢
Sangie apite ku mushroom shade she's too good
Neighbour wa mtebe nd doloso hvy🔥🔥💯
Ndipo zowona
Usampepese inenso sindngampepese koma Patricia nd Gani mmakwana 😂 neba wamasuka koma abusa nthandizeni 😂 anthu amaendadi awiriawiri kkkk Gani wada bwa . Keep the fire burning guys 💪🔥
Friends of Ganizani let's gather hear ❤
❤
😅😅😅Kodi ndi mabatchala okha okha 😅
Wow ine khawa chipere🤗Keep it up guys❤️Mpali yachimalawi
Who's watching because of Ngozo and Patricia?😂
Tonde, neba wa abusa; voice yake really fits for that one batchala in most yards.
Amatha
On point nice observation kkkk
@@NelsonMumbulu-mq5ob m'bale wanga iwe
Koma i admire relationship ya gani ndi sister wakeyu ndi fire eeh😂😂😂🙌
Ngati eni eni et?
Kungolowelera nkhani yosaidziwa.....😂😂😂😂
Koma Gani ndi sister wake eee 😂😂😂😂 smoko. Ndinu mtundu wanji was anthu 😅
Tizi fusana mchizungu uwu nde mwano of the year 😮😮😮😅 a Gun pwiiiii
Koma sangie ndi obheba💞
EEEE MAMA G ALEROYU
Uyu anabwera
Ndipo kwambiri,being black and beautiful❤
NDIPO NGATI AKUFUNA BANJA NDILIPO
😂😂😂gani ati ndiwe maskin-tu😂😂usauver is my favourite 😍 ❤❤
FROM ZAMBIA this is really Good PIKSAY continue acting movies we love your movies here in Zambia
Patricia pa chiwongolelo one body one soul amandiuza kuti ndipange verify 😂😂😂😂😂😂😂😂
Munthu ngati sangakangane ndi ine mu "English " Waluza🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Watching from mwineriwa vg mulanje Sangie kumulalatira munthu oswalakwa eee😂😂😂😂😢😢
koma sangie eeeeeeeeeee, nde kuli hyphen kuyankhula with khoffffffffffffi
Kam'busa kachinyengo in Patricia's voice😂
sangie is one of the reasons why I watch usauver😂😂
Patricial and Ganizani muzioneka kwambili u guys makes it gud recieve ur 🌹
Patricia nd moto keep up guys good work
Sangie is too good...
Kom sangie umatha kom ndimafuna nyimboyo guys please
I have liked the song at the end of the episode. Anybody who knows the title and where I can get it?
Bestie too continue kuipatsa fire😂😂😂😂
Sangie🎉 😅😅😅 Ati zinthu zambiri zitha kupezeka zachitika
Nice one Koma dry head mutu ouma😂😂😂
Koma Patricia. Kkkkkkk akuti inensotu ndi army.. Sindingamupepese
Sangie you will kill us with laughter one day
Koma Mtebe mmmm ayi,,mapemphero anji olipiritsa😅😅
where is part 2? this comedy is very very impressive.
Usauver is my favorite ❤
Sangie shiiii kkkk. Ndeno mwat makampanie oika ma shandiyiliyao ndachna genie wo 😮 kkkk. Here we goo!!
Nyimbo yomalizayi siyimaipeza bwanji? Sounds good
😂😂😂😂😂 sangie ujayooooo ndi vibe
Sanjie ukuitha respect 😊
😂🤣 😂Sangie. Eshh kungofikila chorus.. Nkhani yosaidziwa "umbava "😂 🤣 Iwe ndi more bwanji😂
Gani upepesa bwanji! Ufuna uphweke😂😂😂
Sangie to the world.
Mbambande 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Best episode
Anthu amayendad awiriii awiriiii 😂😂 kma Gan , abusa kkkkkk winayo akut simungakangane muchingerez
Ati anthu andichenjelera zikhala ndekha😂😂😂😂😂 sangie
Albert yatenga lehu🤣🤣🤣
Ndaona chocho😂
Eee ganizani and sangie 😂😂😂😂😂 isowa bwanji power bank🤣🤣🤣
😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 😹 e sugar mam
Ati azatchola nyumba😂😂 Patricia is dramatic ah
Big up guys ... Ma mic apa nde munakunga
Koma mnyumba mwa Ngauzo muzaphulika bomba day 1😂😂
Usauver ❤
Am watching it
Best usova
Keep on fire burning magaye
Yooooooooo
You rock guys 🔥🔥🔥🔥🔥