Chakwera akakamiza apingo kuseka Chilowelen boma sanapitepo kophembera.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 135

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh หลายเดือนก่อน +8

    Be careful people of God,something will be happen there take care

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du หลายเดือนก่อน +2

    Chakwera anapha president wa assembles of god musazapite ndi chigawenga ichi ndi kale anayamba kupha anthu

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh หลายเดือนก่อน +2

    Oipa athawa yekha,afuna agawe ndalama ameneyo komatu ndalama zimenezo tizitafunadi koma vote ndiye ndi ija munakakwilira ku nsipe ija,sitikusinthaso chiganizo,pitani akhristu mukamuonere pafupi wakuphayo.

  • @immaculatechitsakamile252
    @immaculatechitsakamile252 หลายเดือนก่อน +6

    Musadzapiteko nonse!

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 หลายเดือนก่อน

    Mapwala Ake ameneyo

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 หลายเดือนก่อน

    Zitsiru ndi azibusawo, povomeleza ma instructions akupelekwdwao. Kumeneko ndikupembeza munthu osati mulungu ayi. Ndiye kuti m' awa ku tchalichi kumeneko mulungu wao akhala Chakwera. Koma dziwani kuti nzimu wa mulungu ukangochoka mawa lino pa tchalichi chimenechi, basi subwelelanso chifukwa mulungu sangamapikisane ndi munthu. U can only serve one Master.

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w หลายเดือนก่อน +1

    Aaaaaaaah! Uchimo wamela mphondo Chakwera, bwanji osapemphera kunyumba kwake komweko ndi security yakeyo. Chitsilu cha President.

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v หลายเดือนก่อน +2

    Chimo limadzuza olo anapeleka yesu uja anazipha yekha uyu siyeni azaseke ziseko zotse inu musade khawa koma lizasala khomo limodzi la mulungu sazakwanisa kuseka khomo limenelo ndilimene lili loopsa kwambili azisamala popanga zithu

    • @user-xo8ms5wh2s
      @user-xo8ms5wh2s หลายเดือนก่อน

      Mizimu yalusa mpingo wa CCAP ndi wake osapita ku Assemblers of God kwawoko bwanji chitsiru cha president wayaluka basi galu ameneyu dzikoli lamalawi lamuchepera akubisala mbatata nsana ukuonekera mumva kuwawa bwana😂😂😂😂😂😂

    • @user-fi3pj9uo7u
      @user-fi3pj9uo7u หลายเดือนก่อน

      Azimagililatu ameneyi ndikilani muzandinkhululupilila

  • @StewartGoma
    @StewartGoma หลายเดือนก่อน

    Chakwela the life of Malawian matters alot

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo หลายเดือนก่อน

    Chakwera ndiwe galu kwabasi, tapitani ku mpingo wanu mwayamba kusokeratu, inu mumkaona ngati mwakhoza kupha chilima hahaha chilima uja sanafe alipo, olo munamupha koma anthu sitikukufunani🎉🎉🎉

    • @TendaiMerisha-eh3gn
      @TendaiMerisha-eh3gn หลายเดือนก่อน

      Iyai auzeni kut asabwele church si chao apite Ku church kwao

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk หลายเดือนก่อน +5

    Church ndichanu osawopa osatopa osafooka vuto asogoleliso aku church dyela

  • @user-no2mx4go8p
    @user-no2mx4go8p หลายเดือนก่อน +2

    Osapita ku assembles koo bwaa mesa ndikumene anachokera musamulore akuphani galu yoooo

  • @JowasiMasina-fy8ji
    @JowasiMasina-fy8ji หลายเดือนก่อน

    Muletseni ameneyo ndi nyumba ya mulungu siyoseweletsa mulendo sapelela lamulo pa nyumba yaweni

  • @PeterKaiya
    @PeterKaiya หลายเดือนก่อน +1

    Bas nonse mumapemphela kumeneko muzakhale osaptakonso akhaleko ndi zikhalenhoma wakeyo

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 หลายเดือนก่อน

    Akuona ngati nayenso azathilidwa poison? Kkkkk

  • @StellahMsodoka
    @StellahMsodoka หลายเดือนก่อน

    Koma Mahule enawa paja muli mtundu uliwonse wa tchimo eti bodza momwemo eeee

  • @user-qq1uj7ct6n
    @user-qq1uj7ct6n หลายเดือนก่อน

    mmene wanenera comrade mtanyiwa... kut musazapiteko. Azapemphere ndi azibusa awoo.. Ku Limpopo yafika kale kkkkkkkkkkkk

  • @duncainjimmy
    @duncainjimmy หลายเดือนก่อน +1

    Mingo suikilidwa malire

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba หลายเดือนก่อน

    Pita Kaye ukamine usatipangitse nseru

  • @user-ey6in8is5h
    @user-ey6in8is5h หลายเดือนก่อน

    Malamuro awusatana basi kkkkk

  • @usherjamson174
    @usherjamson174 หลายเดือนก่อน

    Koma ichi nditsilu kobasi amazitenga ngati ndani 😢

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t หลายเดือนก่อน

    Kkkkk kodi chimenechi chikufuna chani kweni kweni

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm หลายเดือนก่อน

    Osapitako kumeneko something will happen there osalola zimenezo

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp หลายเดือนก่อน

    Vuto ndiazibusawo Adya zambili

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 หลายเดือนก่อน +1

    Komatu galu iwe president wamanyi usatizolowere ndikupha kwakoko

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 หลายเดือนก่อน

    all the best mr president God help you

  • @JohnAsendi
    @JohnAsendi หลายเดือนก่อน

    Zikomo kwambiri madam taziwa n busa ameneyo ndi street wasatanic azingopita kumeneko kuli nzake akubisalawo koma muvumbuluka tikuziwani ponpano Nzimu wachilima ukumuzuza uona sizinati akanakhala kuti alibe ndalama bwezi tikuti wayamba misala poti wandalama akuti Ali pamwamba palamulo keep it up sister 🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏🙏

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym หลายเดือนก่อน

    Ndpu wasiyilanji kupita ku church kwake kt akamuchose ma demons amene Ali naye..walowa chiwewe sanati, kupha mnzake ngati garu anthu angamukonde chitsiru Cha munthu

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 หลายเดือนก่อน

    Osapitako akhristu akapemphere ndi abusa,mayi oyendela komanso akazawo aabusa kkkk abwere kuno ku MAKATA CCAP izamuimbile chitsitsimutso mutu wanyimbo CHIFUNGA

  • @user-xm3zl5cg6x
    @user-xm3zl5cg6x หลายเดือนก่อน

    Osapita kumeneko amalawi chikumbutima chimupha oyo

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 หลายเดือนก่อน

    Nde mapephero ake abwanji amenewo

  • @MatiasChimsakasa
    @MatiasChimsakasa หลายเดือนก่อน

    Mulendo kubwera ndikalumo kakutwa

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef หลายเดือนก่อน

    Chakwera ndi satana kwabasi

  • @KaiffaSkefa
    @KaiffaSkefa หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkkkkkkk azakupa inu eeeeeeeeeeeee mavuto😅😅😅😅😅

  • @user-nb8wg3fh4u
    @user-nb8wg3fh4u หลายเดือนก่อน

    Mukapemphelele pakhomo osapitako

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j หลายเดือนก่อน +1

    Chikangawa chakwera sunakhuthe nyama za anthu.
    Khalani tchelu mamembala nonse olo kakhaleni kunyumba nose akapemphere yekha galuyo

  • @TruthChilungamo
    @TruthChilungamo หลายเดือนก่อน

    Mukanamukanira Galu wachiwewe uyu

  • @Fatima-f5c
    @Fatima-f5c หลายเดือนก่อน

    Mama musapiteko kuntchalichiko tiponyako bombaa kumeneko😂😂😂😂

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂 wa satanic wasowa mtendele mzimu wa chilima ukumusausa wanya uona machende ako

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 หลายเดือนก่อน

    Chilipo chachikulu kukapanga kumeneko, pajatu muthu akalowedwa ziwanda amavuta mmm

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw หลายเดือนก่อน +1

    Abusa akazapora manyii .asazatyrukeso mmmmm

  • @CharlesBENE-tv9wn
    @CharlesBENE-tv9wn หลายเดือนก่อน

    Musapiteko akakhaleko ndi ndunazakezo bass

  • @FisherAction
    @FisherAction หลายเดือนก่อน

    Chimo kuzunza kupha anzako ukuyesa suzafa , anthu ayeza usogoleri wako chakwera walephera

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 หลายเดือนก่อน

    Wafa wafa imeneyo

  • @user-kt5bq2wg6v
    @user-kt5bq2wg6v หลายเดือนก่อน

    Palibe chimene mwalakhula chazeru mayi, zingowonetsa kuti inuso mulibe zimu wachidziwitso kapena kuti inuso ndale zidakuwonongani.

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 หลายเดือนก่อน

    Kma chakwera akuzioona ndithu 😂😂

  • @giftnyirongo-ey3qy
    @giftnyirongo-ey3qy หลายเดือนก่อน

    Nde mwati ndan ameneyui 😂

  • @PetroMatias
    @PetroMatias หลายเดือนก่อน

    Musapiteko apiteko ekha

  • @Blessings-td4cr
    @Blessings-td4cr หลายเดือนก่อน

    Apenga mkuluyitu ndikuti ndikaona,,mizimu yakwiya ya a Malawi.

  • @FisherAction
    @FisherAction หลายเดือนก่อน

    Galu ameneyu alesedwe asapiteko malamulo akapereke ku mpingo wKe kuja anaphako yemwe adamupeza eeee wooipa uyu asogolleri a mcp 3/4 owoneka obadwa mopotoka nkhope komanso ndi mitima yomwe alephera amenewo

  • @RamseyWasi
    @RamseyWasi หลายเดือนก่อน

    😂Kumpanjeeko nkoonkoma kwambili

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v หลายเดือนก่อน

    Chakwera Chikangawa Congress party

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน

    Musamale naye ameneo mumusiye apiteko yekha zake ndi zakumidima kkkk ati galu ameneu kkkkk koma chikangawa eish

  • @BrianJoe-z7u
    @BrianJoe-z7u หลายเดือนก่อน

    Fiti fiti ndithu

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di หลายเดือนก่อน +1

    😂😂 anthu a mcp ndi iyaluka manyazi ndi umunthu alibe Inu pitani mungoima papemphelo lomanga zoipa zakezo ndalamazo agawe ndithu voti ili muntima aziwona 2025 ameneyo

  • @user-yk9ib1bg2b
    @user-yk9ib1bg2b หลายเดือนก่อน

    Abale imvani ichi samalani, mukapusa ndi ma church mutha nonse, Musapiteko please amalawi

  • @AndyGama-m3u
    @AndyGama-m3u หลายเดือนก่อน

    Komatu mulindi time

  • @user-ny5nt9vy9i
    @user-ny5nt9vy9i หลายเดือนก่อน

    Mmmmmmm koma inu

  • @brainsmkumbwa6267
    @brainsmkumbwa6267 หลายเดือนก่อน

    Mumuuze Chakwerayo kuti ndi mbuzi ya ma president yoti sitinakhalepo nayo kumalawi kuno ndiponso siyizapezekaso

  • @user-sk3ld2ss7s
    @user-sk3ld2ss7s หลายเดือนก่อน

    A Malawi ndinu dzitsiru, mumafuna president OTAN i?mumafuna president adzikuseserani m'makomo kapena adzikuvulilani Kodi?

  • @user-qf7ko2dd5g
    @user-qf7ko2dd5g หลายเดือนก่อน

    Ndalama idyani

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 หลายเดือนก่อน

    Aaaa zavuta ku mpanda basi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 หลายเดือนก่อน +1

    Monga ine wa ccap woopa Mulungu mulendo sangandiuze zochita pa khomo panga. Iyeyo ali ndi church lake ndikumene skapange zimenezo. And iyeyo si Mulungu wa ccap Mulungu wa ccap ali kumwamba asatenge ulamuliro waluchipani kwake kapena wakuboma or waku church kwa iye ndikubwera nawo mumupingo wathu ayi mupingo umayendesedwa ndi malamulo a Mulungu. Ndiye a tsogoleri athu a ccap musalole zimenezo opani Mulungu. Osaseka pa khomo aliyese phone asazimise ndindani iye akuyesa amaposa Mulungu wamambwa kodi? Ngati ali ndizifukwa ndi anthu ena asabwere ku mupingo wathu please ziko opani Mulungu wosati olengedwa

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg หลายเดือนก่อน

    Chakwela nd galu ameneyoo kwabasi

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym หลายเดือนก่อน

    Msayiwale kt munthu ochimwa amakhala ndi mantha chifukwa samayenda ndi Yesu... Nde chichakwera ndicha satanic ndipake kukhala ndi mantha.

  • @CaphusJailosi
    @CaphusJailosi หลายเดือนก่อน +1

    Mayi pitani mukagone mwadwala chifine.

  • @Chrisyuzy
    @Chrisyuzy หลายเดือนก่อน

    Kod ndi mulungu ameneyu KAPENA 😢😢

  • @johnmsona8845
    @johnmsona8845 หลายเดือนก่อน

    Apenga misala ameneyo zimu wachilima ndi abale anthu Ena aja wina Anya awo a chitsilu cha president

  • @sheila5812
    @sheila5812 หลายเดือนก่อน

    Inuyo musapite ku church ko mukapatsa anthu chimfine

  • @Hopenandola-zg6kz
    @Hopenandola-zg6kz หลายเดือนก่อน

    Machende ake

  • @user-wg8tp8in1v
    @user-wg8tp8in1v หลายเดือนก่อน

    Vuto inuyo simuli molalika uthenga. Muli mowona matchimo amunthu. Kusowa choyankhula inu. Kwanuko kukabwela alendo wopemphela simulankhula pano mukulengeza pamenepo simukuziwa kut uyu ali ndi udindo wa ukulu. Nanga mumene mungalandilile mwana wa bale wanu ndi abusa akumpingo malandilidwe ake angafanane

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂 wayamba ndiye kukhala ndi udindo waukulu?? Zinachitikapo kt zimenez ngt ndi udindo mku politics konko not kumpingo, mulendo safika mkulamulira eni khomo achuruka nzeru mpingo umaendesedwa ndi malamulo a Mulungu not a politics

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w หลายเดือนก่อน

    Mwayankhula bwino koma mwachimwanso potukwana kuti galu ameneyi

  • @DoreenBanda-hg7oe
    @DoreenBanda-hg7oe หลายเดือนก่อน

    Chenjerani akhristu ndi mneneri onyengayo

  • @MerryWayson
    @MerryWayson หลายเดือนก่อน

    Musalole a C.C.A.P zausataniki zaozo asakutaiseni yesu

  • @EliasJimmy-fv1wk
    @EliasJimmy-fv1wk หลายเดือนก่อน +1

    Mukuzawapembeza iwowo

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b หลายเดือนก่อน

    Aaaaaaaa nde zichani zimenezi? Zinayamba zachitika liti, nde zodabwitsa tu akufuna adzagawe ndlama paja ali nazo zogawatu koma chonsecho mankhwala mzipatala mulibe shame

  • @monicagondwe228
    @monicagondwe228 หลายเดือนก่อน

    Komatu mutipatsira chimfine.....,😢

  • @SamsonKatundu
    @SamsonKatundu หลายเดือนก่อน

    Iyeyo ndikandani kodi??

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw หลายเดือนก่อน

    Musamale ampingo akulimbana ndaazibusa poison ameneyo samalani mufa

  • @DevisonHala
    @DevisonHala หลายเดือนก่อน

    Osamulola osamunyengerera akuphani satana chikangawa

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b หลายเดือนก่อน

    Hmmm this man called chakwela

  • @BlessMnyenyembe
    @BlessMnyenyembe หลายเดือนก่อน

    Ngati ndi zoona ndye kuti sizapingo ayi

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira หลายเดือนก่อน

    Muziona inu a chalichi sinanga chalichicho ndi chake

  • @user-nb8wg3fh4u
    @user-nb8wg3fh4u หลายเดือนก่อน

    Musapiteko

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole หลายเดือนก่อน

    Kd iwowa afika pomadzimva ngati mulungu?ngati akuluakulu avomereze zimenezo onse muwaukire coz sizoona ayi asamalikatu achakwera eti za ubusa zija adazitaya chi khristu anavula akulamulidwa ndi winauja.

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy หลายเดือนก่อน

    Adzapempereko yekha ameneyo

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi หลายเดือนก่อน

    Ok chikangawa titsalandila ndalamaso

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr หลายเดือนก่อน

    Ufiti ,,afuna chani

  • @ThomasStephan-tg6ng
    @ThomasStephan-tg6ng หลายเดือนก่อน

    Akuphelani komweko musamulole ndiopusa akufuna akuphelani mukanizeni akayangane kwina kopemphera

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน

    Wamisala Chakwela

  • @user-ew8er1jk3w
    @user-ew8er1jk3w หลายเดือนก่อน

    Mmmm koma muli busy ndimabodza a Malawi, kodi mkamapeka nkhani zanuzo mumapedzapo chani?? Ine ndimapemphera pompano izozo kulibe, ukudwala mnthu komano busy kunama iiiiiii.

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂 iwe unajomba ku church uli ndi udindo wanji umafuna akuyimbire foni kt udziwe ngt ndiwe secretary

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน

      Iweyo nde wabodza musatinamize nkhani yi olo limpmpo yanenso kumapemphera kuti mwana Wa njoka iwe kagwere

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j หลายเดือนก่อน

    Mafoni tinagula na machen amak galu

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms หลายเดือนก่อน

    Asiyeni ma members a church abwere even atachedwa don't stress about that criminal chatsika

  • @BlessMnyenyembe
    @BlessMnyenyembe หลายเดือนก่อน

    Kaya yibwele ya ku ntcheu basi

  • @user-pt8wb4vw6r
    @user-pt8wb4vw6r หลายเดือนก่อน

    Zimamina osamina bwanji iwe ngati zakunyasa ungokhala basi ndwe chisilu galu ndiwe ndipo ulibe yesu

    • @sheila5812
      @sheila5812 หลายเดือนก่อน

      😂😂😂

    • @Zelinakhisswell
      @Zelinakhisswell หลายเดือนก่อน

      😂😂😂😂. Eeee yabayatu akuulurani ndipo simunati mupenga zenizeni

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน

      Chitsiru ndi iweyo mwana Wa njoka 😂😂😂😂😂

  • @LottiAffati
    @LottiAffati หลายเดือนก่อน

    komatu guys ziwanda za uyuyu za chikhamu zija zikuchepera, coz chamudimbayi nde wapengeratu apapa

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu หลายเดือนก่อน

    Ku chalichi kwake bwanji osapita kodi iyeyu ndi Mulungu? Wafikapotu Chakwela koma uziwe kuti Mulungu amatsisa mafumu ku mipando ndikakawasiya ku tchire mkumakadya udzu ngati chinyama ask mfumu Nebuchadnezzar

  • @CaphusJailosi
    @CaphusJailosi หลายเดือนก่อน

    Wadwalamuti wa na mtongo eti

  • @PatrickMaluwaphiri
    @PatrickMaluwaphiri หลายเดือนก่อน

    That day will not day for worship God, better to pray at your home.

  • @Enock-c9l
    @Enock-c9l หลายเดือนก่อน

    This is not a leader