ไม่สามารถเล่นวิดีโอนี้
ขออภัยในความไม่สะดวก

KWA TENTHA UKU 🙌 HOT CURRENT

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 13 ก.ค. 2024

ความคิดเห็น • 26

  • @user-nj3gn5xq2s
    @user-nj3gn5xq2s หลายเดือนก่อน +2

    Watsala ekha manganya,koma ife tonse akumidzi tatuluka

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 หลายเดือนก่อน +3

    Kumalawi vuto ndi azimayi amavotera anthu andale chifukwa chi zitenjee

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of หลายเดือนก่อน +2

    Ku utm bvuto chiphwilikiti kaya ife akongelesi pheee ndi chakwela wathuyu

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน

      Ana anjoka inu khalani

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn หลายเดือนก่อน +3

    Manganya simunthu wabwino sanali wa UTM

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 หลายเดือนก่อน +1

    Abwana UTM ya Kaliyati ndi UTM ya Chilima imene ija osati ya manganyayo n for yr information manganya akukaimila u MP ku Blantyre ngati independent candidate mukatiuze kuti ndiwa UTM ameneyo,panopo or awiriwa atati aitanitse msonkhano wa UTM manganya ndi Kaliyati komwe kungadzadze anthu ndikwa kaliyatikotu

  • @prestorjk6949
    @prestorjk6949 หลายเดือนก่อน

    How do u expect a rubble removing another rubble?

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s หลายเดือนก่อน

    Please you guyyys we are proud of uu yakhula iii kwambliii osaopaaaahhh

  • @samsamuel9280
    @samsamuel9280 หลายเดือนก่อน

    A usi ngaumbombo sangachoke,ankawaikila kampeni kumphasa achilima.

    • @omardyman8083
      @omardyman8083 หลายเดือนก่อน

      Ndi mzimbabwe amene uja big osamaiwala mazimbabwe si anthu abwino ndi adyera kwambiri

  • @mathewsmakina7845
    @mathewsmakina7845 หลายเดือนก่อน

    Alindi chidodo ndi a president ayini akewo asanamizile a Malawi ayi ngakhale malankhulidwe a president ndi achidodo ndiye aMalawi angachangamuke bwanji asatinamizile Ife ayi

  • @iangondwe6857
    @iangondwe6857 หลายเดือนก่อน

    utm pitani ku dpp akugwilisen ntchito DAD

  • @magamwagomba9721
    @magamwagomba9721 หลายเดือนก่อน

    hahahaha kodi bayala ungamudzudzule? 😂

  • @ishmaelsiffah9900
    @ishmaelsiffah9900 หลายเดือนก่อน

    Zamgwirizano inunso munazimva nokha a SG a mcp akukana kuti palibe mgwirizano uli onse wapakati pa ife ndi UTM come 2025 ndiye mukundiuza kuti panopo tizikhalabe phati phati ndi MCP yo kuipangira compaign akawina ozanyozeka mkumazakhala ife mmalo mokuti tichokeko ife tipange zathu patokha ao tiwasiye akhale ndikuzindikira kwaoko

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r หลายเดือนก่อน

    Khani yakuchikangawa chona chimaziwika ,koma sangatiuze kalikose mapeto ake muzava kt inali ngozi akudikira amalawi ayiware

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi หลายเดือนก่อน

    Kabambe watuluka ku DPP

  • @MikeMwale-bw1xw
    @MikeMwale-bw1xw หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂 A Malaw tikuchedwa aaasa aPule back to sender.

  • @TravelodgeMalawi
    @TravelodgeMalawi หลายเดือนก่อน

    Paja ndiwachipha maso ameneyi,akunama amachedwa ndiiye

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda หลายเดือนก่อน

    Utm kutuka nkhunandi,

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4i หลายเดือนก่อน

    Aliyese wasalila Ku MCP akuziwapo kathu zaifa yachilima akudya mapwevupwevu khosa kunja nkati ng'ona

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn หลายเดือนก่อน +1

    Munthu uyu zawo wa sisyayu ndi wa mcp akukamba za nonsense

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r หลายเดือนก่อน

    Ku mcp kuli athu amakan ,kwambili mot izaluzise mcp ndi mr tayezeka,ndare zopanga us

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน +1

      Zoona anthu amene wa ndi omwe a kuononga ndithu

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu หลายเดือนก่อน

    Leave America what about Biyeni

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn หลายเดือนก่อน

    Zake wasisya ndikanakhala ndi number yake nkanamutukwana

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z หลายเดือนก่อน

    Ma boss inuyo mumatha.ndipo mumatiimilira. We're still waiting for chikangawa ujatu,ndipo maliro achilima anthu tiwalira koposa. Chinthu china or akuyankhula mwano a mcp koma kuchoka kwa utm mmmhhh chabwino palibe