ขนาดวิดีโอ: 1280 X 720853 X 480640 X 360
แสดงแผงควบคุมโปรแกรมเล่น
เล่นอัตโนมัติ
เล่นใหม่
Brian Banda and Cathy Maulidi is the best combination......a Times mukanatumiza anthuwa
It was best convention ever
Hahahahaha ayi amvetsetseni amkakalilira kwaokha ka mchifukwa chake adatuluka
Brian Banda Mpakana Verse?😂
Koma pemene magetsi adazimapaja mudaonapobwanji chidazimitsamagetsi ndichiyani?
Ndipo ine sindikuchiona chomwe asakuvomereza fundo za kabambe zinali zogwira mtima ndimene nyengo yathu momwe tikuyendera
Awesome ❤
Komanso kabambe amatiuza fundo zogwira mtima no matter what sitikana voter chifukwa choti muchipani mwakhalisamp ai koma fundo
Kicks of a dying horse! Anandibera! Kkkkk
Usi ndi mfiti wadyela wokopha galu mbuzi kakakha
Manganya amatamba nkufupika kwake kuja
Zomwe zachitika Ku utm ,ndizomwe akumanenazo a MCP chaka chikuzachi ,koma pokut adalila maschin obera mm mwina azapulumuka
Zoona, ndimasomphenya a momwe zikhalire next yr
Iweyo nde wanena zoona kuti usi chipani cha UTM anthu sanankonde avomeleze kuti iyeyo sakufunika ku UTM
😂😂
❤
Koma kuona kwaine usi chilima samamukonda, ndipo zoti kumwalila kwa chilima athu akamati usi anali ngati rezara kutenga zauku kupita nazo uko, usi ndioipa akufuna kuphaa chipani cha utm
Inu mumatha kwambili
NPK? Koma anyamata inu mmmmm
Brian Banda and Cathy Maulidi is the best combination......a Times mukanatumiza anthuwa
It was best convention ever
Hahahahaha ayi amvetsetseni amkakalilira kwaokha ka mchifukwa chake adatuluka
Brian Banda
Mpakana Verse?😂