Tadzimvela tokha a malawi mumutumizileko VN imenei uyu otuwa mmutuyi, sasambayi jessy chabwila cifukwa atafunsidwa amati dpp ndimene anatuma dzifwambazi.ndipo jessy pa u chisilu pa mache mumuze conco kaya ndi hule ukumupangitsa cifukwa naenso akunyengana ndi cimwendo uyu wanyenga mkazi wa dan lu
Shame to the government of 🇲🇼 that's embarrassment to the president, scr how could a government minister do something bad like that to his own people Shame
Mwagwanayo😅😅😅😅😅😅 mulungu akukathani
Kkkkkkkkkkkkk nzosezija munali musanalandile😂😂😂😂😂
Amvekele kt bola tapenza zikwanje😂😂😂😂😂😂😂😂 tizikadulila nkhuni
Kkkkkk mwayendana njomba kkkkk
Muyamike Chileso chakwa DC.anthu ambiri Anabwedza maganizo opita kumademo.muyerekedzeso Ena akubwerawo
Ndiye uchitsiruwoo anyamata ndichiyani makamaka nanunso a issa mukuoneka ngati ndiwachisilamu munatumidwa ndi antenje
😂😂😂😂 mavuto atiphesa ndithu Kaya ndi dyera tifanayo
😂😂😂 chikwanje muzidulira nkhuni kkkk
😂😂😂😂 muli ndi tsoka lalikukulu ... Mulungu akukhululukireni
Ndiye mitengoso inatha ndi kuontcha makala ndiye zikwanjezo muzidulila chani azibambo ena mumanganiza mopelewela ndithu 😂😂😂 achita bwino osakupatsani ma k50000
😂😂😂😂 Ndi pamene mungaziwe opusa inu
😂😂😂😂😂 Muli bho man
Kkkkk Amalawi kufoila mungatenge nyau kuti iyendetse boma ati ulendo wa ku kenani lero ndizimenezotu
MCP nde imeneyo kkkkkk mufuse DAN LUU.mukafuseso Nyau Kkk zinapanga mademo after kunamidzidwa ma 5pin 😂
😂😂😂😂😂 Koma kumeneko zilikotu
Audio yaboza iyi Ngakhale ikukamba zolondola
Kkkkkkk😂😂😂😂 dulilan mitengoyo
Tadzimvela tokha a malawi mumutumizileko VN imenei uyu otuwa mmutuyi, sasambayi jessy chabwila cifukwa atafunsidwa amati dpp ndimene anatuma dzifwambazi.ndipo jessy pa u chisilu pa mache mumuze conco kaya ndi hule ukumupangitsa cifukwa naenso akunyengana ndi cimwendo uyu wanyenga mkazi wa dan lu
Nde uchisiluwo anthu opepela siku lina chikwanjecho chizakuphani anaimba kale billy kaunda mwana wa kwathu ku mphimbi
Creativity
Kodi chili chose fake inu chikwanje simudachione?
Mwaigwira ya jamaaaa kkkkk
Shame to the government of 🇲🇼 that's embarrassment to the president, scr how could a government minister do something bad like that to his own people Shame
😂😂😂😂 chaphindu ndichikwanje
Ngati audio chabwino koma ndi call bwanji winayo sakumveka
Ululan zonse zomwe mukuzidziwa agalu amenewa asamakane
Eyaa muzidulira mitengo mawa adzadulira inuyo mudziyidziwa mcp
Choka wabodza iwe,cha DPP iwe!!!
Hahahahaha😂😂😂 ndipo zofelazak ndinu anthu ovetsachison kwambili
Mutengepo phunzilo kufuna kupha anzanu chifukwa cha ndalama mudzasiya ma banja anu chifukwa cha dyera
Za ziiii even your voice betrays you kuti ndiwe cadet 😂😂😂😂
Kkkkkkkk akunama uyu ndimulomwe sinchewa ameneu
😂😂😂😂😂😂 zoonadi
Timalandilatu ndalama game isanayambe ndiye munangoyamba ndalama asanakupaseni ? Umenewo ndiye uchisiluwo anyamata achigawo Cha pakati mukutukwanisa achewa azanu osalakwa chifukwa Cha umbuli wanuwo taziyendani muziwona anyamata momwe atukukila osati za chamba zanuzo anthu azakuphani ndalama usanalandile ndiye achibale azakhale busy kukusongelani ndalama ya box anyamata inu ndi zisiludi
ATI bola apheza chikwanje😢 adzikadulila nkuni
Kumeneko ndiye kuputsa basi 5000 mukagulila chani zinthu Mene zakwelelamu kkkkkkkkkk
Tsiku lina ofunika kuzangonukhapa otumayo pompo chifukwa amakhala Ali ndi ndrama zochuluka kusiyana kugwira ntchito ndikupasidwa 5pin.
Kkkkkkk zidulirani mitengo basi
Yooo ai zikomo
Zitsilu za anthu ndipo ana anu adzavutika kwa mnanu mpakana moyo wawo onse inunso palibe chomwe mudzapamge mpaka kutha kwa moyo wako onse.
Oky thawi yanu ikwana achewa inu iri ndi dziko kapena mpira uwu
Ngati muli anzeru mwaphunzilapo
Kd ndekuti iweyo wachikwanje dziko ukuliva kukoma? Zooon iweyo ukukalepheletse zinthu zothandiza chifukwa cha kandalama kochepa?
Ndimu opepela ganyu ameneyo mukanalandilIlatu
K50,000 yathumba limodzi mukaphele anzanu mulungu akuyendelen mwapadeladela
Uchitsiru kkkk malo mopanga zachitukuko
Uyu si mchewa ndi mlomwe uyu
Achewa timawadziwila mayankhulidwe a chichewa
Kaya angopeka kaya bwanji
Nanga issa ndi mchewa ngati jafari simchewa
Ndiye galu kabwira amalesa chani,akulankhulawo ndi asena,Mai opusa
Kabwila ndi galuwa mzimayi
Chi mzimayi chopanda manyazi chimenechija
Chimandinyasamo bwanji
Zochititsa manyazi zedi?
Mwina simunamvetsese 5000
Pajanso timayitchula kuti 50 bar
...so it means anangochotsera zero m'modzi m'mesa... payment gone wrong patiii...maulendo ongodzukiramo ngt Chiwala-wa...any way.😅😅
mmmh ine si wa Tambala koma Audio iyi,.Pali bodza apa..!
Mcp? Ndichani tsano? Nkhanza zija simunasiyedi mpaka Lero? Chipani chamwazi ichi, mcp or ikupangitsa msonkhano pa sitting room yanga ine kuchipinda singatulukeko
Zaugalu mot muzisaka fuel mukupasa zogawenga tionesana 2025
Ineyo ndinanena kuti anyamatawo akuwalipira koma azaulura okha kamba kamalipiro
Ulendo wina mudzafa
Ana anga akuonongeka chfukwa chakusadziwa tingolapa basi
Bozaiwe kufuna kuononga zina la mcp achewa inu
Zaziiii😢
wena adzafela zayen
Kkkkkk muziona
Zausilu basi nose ndinu wopusa wokutumanoyo ndi Inu nomwe
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Anena zambili ameneyo
Abale 50 pin ndalama zimenezo mpakana kulolela kuononga moyo kunjaku satana alipo
Mudzafela zayeni
Kodi winayo samayankhula??ukungomvekapo wekha bwaa???
komadi
Lupanga!
akuchitani bwino agalu inu athu osasamba zitsilu
MCP chipani chochinda akazi aweni anthu anyele
Bola mwadya ka 5pin
Anyamata opusa inu
Mbuzi inu
Zisiluinu
Kkkk
Anthu opusa inu, zitsilu zachabe chabe inu
Kkkkkkk
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Mabodza
😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮😮🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔
Mcp 😢
Aaaaaaaah
This is fake if the call was recorded the other side could also be audible.
True fake call
Am not MCP but this fake
Worry not broh end tym