Msatisokoneze abale za mndyango zikhale za mndyango za mfumukazi zikhale za mfumu kazi osati mpange mpange mix anthu omwewo kwa mndyangu omwewo kwa mfumukazi
Apapa ndiye mfumukazi ndi mdyangu akuyisokoneza , potenga nkhani ya uko kubweretsa mbali ina . Otherwise izizi ananyoniwo amayenera kuwapeza ku mdyangu komweko osati ku fumukazi
Joshua Agabu as much as I love the link as well but I think somehow it will be confusing as some characters appear on both shows under different names i.e. Sasoka on Mdyangu while Gututu on Mfumukazi. Imagine Nanyoni appearing on Mdyangu and being welcomed by Sasoka how was just hitting on her few weeks ago on Mfumukazi under Gututu.. kikikikiki
Queen wayatsa moto on a mission to settle her bill ya ku chipinda plus kukonza mental health challenge za Cecilia Ananyoni sing'anga. Queen ndi maulendo Mr ShopRite wayang'ana mopherela
Pajatu Nanyoni aka Mfumukazi amapanga za traditional Dr mu tikuferanji, and if you remember a couple of episodes ago in Mdyangu Queen anagwilizana ndi ashokoshoko kuti akapeze sing'anga to help Mrs Shokoshoko...
Kusonyeza kut Msing, anga yemwe akufunikira mwa mdyangu pa misala ya Mayi shokoshoko ndi mfumukaziwa eeti kkkkk ndikuzitsatira bhobhoo ndpo tili limodz ndthu
off course mwapanga cross over from mdzyangu to mfumukadzi bwino apapa koma munayiwala za mercy, kodi munthu modzi azipezeka ku mudzi yomweyenso ku town? but anyway keep it
Nde zitha bwanji apa..... gututu ndi sasoka mesa 🤐🤐🤐🤐
I can't wait 🥰🥰🥰🥰🥰
😂😂😂😂😂😂aaaaa queen kuchoka kwa mdyangu nkuzailowa komanso mfumukazi akufuna kukayilowa kwa mdyangu zili bhoo kwambiri ndithu
Congratulations amalawi you are doing great pick it up moffat from Zambia.
I have liked the blending of Mfumukazi and Mdyangu. Can't wait to see Giling'ande kukawonjezera chipwilikiti.
Queen wafika Kwa Mfumukazi, umaitha iweyo!😂😂😂
Komatu Queen muli plan eishhhh wangolipeka bodza basi.
Kokasaka mankhwala wapezako captal koma ayi zikomo iyi comedy ndi 1
Koma Queen 🤣🤣🤣 mwalowatu chapter china muziwayankhula bwino akuluakulu 😝😝
Good video
Zoonadi ahead, palibe zochedwetsana
Queen pola moto mmmm
Koma giling'ande, yekha, bambo mfumu, mr shoprite, Queen ndiosokoneza 😂
Ili bho
Love you guys, koma kubanja Kwa padela simumatha kukita sikumabeba Maka abambowo
So much love ❤️ 😍 from here 💖 💓 my people ❤️
Msatisokoneze abale za mndyango zikhale za mndyango za mfumukazi zikhale za mfumu kazi osati mpange mpange mix anthu omwewo kwa mndyangu omwewo kwa mfumukazi
Abale inu aah!! Zophatikizazi nde sizili bwino
Ndani wabwelesa queen know 😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂 ukufuna utipalamulise yet
Queen yendera chimodzi😂Mr shoprite mamuna wachikondi kwabasi 😁 next Mfumukadzi wa kwa MDyaku basi🏇💃
Ngongolenso ndi mulandu....mulandu sumaola ndakuona neba...woza Queen🤣🤣🤣🤣🤣
Queen Upole moto
Komadi ngati, sukumudziwa munthuyo, palibenso nkhani pamenepo yoti iIpitirira kulankhulana.
Apapa ndiye mfumukazi ndi mdyangu akuyisokoneza , potenga nkhani ya uko kubweretsa mbali ina . Otherwise izizi ananyoniwo amayenera kuwapeza ku mdyangu komweko osati ku fumukazi
Queen ndakuona welcome❤
I pray kuti mix iyi isasokoneze zinthu,Mfumukazi comedy ndimbali imodzi ya moyo wanga
Tikuzunguzukati mdyangu nmfumukazi
😂😂😂 mwatisokoneza mututu, Mdyaku kenako Mfumukazi,
Koma Queen ulendo uja unali wamilandu eti?😂😂 kukupitaku timva zoti Mercy ndi mwana wa ananyonitu😅😅😅
❤❤❤❤
😂😂😂😂😂Ati malaulo awisi kapena ouma
queen wavuta eeee Moto moto
@ liki-liki ladies muzitipadiraso inside diaries chonde
Moto Queen wadza kikikiikiki Ananyoni kubisa dzina kikikiikiki.
😅😅😅😅😅😅 wow guys what a combination 😍
This is really nice. Apapa payaka moto koopsa
Thanks
A Nanyon ndkuwamfuna kkkk
Queen yendelan chimodz 😂😂😂😂😂
Tikudikila kwa dyangukoo ananyon kut akawathile madzi amoto 😂😂😂😂
Kma queen iwe ayi ndithu koyang'ana wamakhwala kukakafusako ngongolele ya ku bala 2021 ithik nonse akusakileni makhwala😂😂😂😊
Queen ndi 1 aise😂
Kkkkkkk koma zokutheka ndithu mfumu nkadzi ntchito mukugwira maka maka maliro ndi nkadzi wake moto kuti buuuu
Koma Queen ati blantyre yonse amamudziwa kkkkkkkkkk wasokoneza compound ya mdyangu asokonezanso Ku mfumukazi umakwana iweyo
Nice guys
Here
I love the cross over between Mdyangu and Mfumukazi, could this mean Ananyoni aka Mfumukazi will be m,aking an appearance in Mdyangu? This is genius.
Joshua Agabu as much as I love the link as well but I think somehow it will be confusing as some characters appear on both shows under different names i.e. Sasoka on Mdyangu while Gututu on Mfumukazi.
Imagine Nanyoni appearing on Mdyangu and being welcomed by Sasoka how was just hitting on her few weeks ago on Mfumukazi under Gututu.. kikikikiki
Ineso ndasangalala nazo🤣🤣🤣
Apa ndiye fumukazi comedy mwaisokoneza basi
Tiziti tikuonera fumukazi kapena mdyangu?
Padela💥
Kkkk ukakwana
Pandela amenyo kkkkkk
🎉
kusetsa ndi m'mawa basi
Queen ndi namfuneya sanasiyane kkkkkkk
Koma Queen uthesa banja kkkkkk
😂😂😂😂😂😂 koma queen 😂😂
Queen wabwera kuzasokonezaso kuno😂😂😂😂😂
Queen more fire 🔥🔥🔥
Kkkkkkkkk Koma Qeen suzatheka iwee 😂😂😂😂😂
Madala opanda ulemu ndinu😂
Koma Queen... eeeeee balibeso kkkkkk
Queen kkkkkkkk wabwera
Queen ngongole yaku Bar 2021 yavumbuluka lero kkkkk
Koma musatitsokonezere sewerol, mfumu kazi isayambe kuodera ma criant aku Mdyangu. Ife taithawa yadyangu coz mulelemba amationongera nthawi. Mlelemba mangolongolola zopanda phindu.
Queen wabwera ngt coming
Kma qeen upole moto
Queen wayatsa moto on a mission to settle her bill ya ku chipinda plus kukonza mental health challenge za Cecilia Ananyoni sing'anga. Queen ndi maulendo Mr ShopRite wayang'ana mopherela
queen sazatheka hahahaha
Queen atipha 💥🇲🇼 💗💗💗
Mli bho ndipo pitilizana kutiphunzisa ma guys inu
Queen sopano
Malawulo awisi owuma kkkkkk
Queen wabwera ndimoto😂😂😂😂
Queen you so sweet but you are destroyer 😂😂😂
Welcome queen
Kkkkk
Dyangu mix kodi
ATI ndithupi lako losalala😂
koma banja lija amai akuti Iyise kkkkk
Queen wabwela ndi Moto Ku mudzi wa kwawo
iiii queen wabwela mwachi coming
I love the way you've blended the two Mdyangu and Mfumukazi
Queen ngongole ya 2021 december kkkkkkkk🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Koma queen 2021 😂😂😂😂😂
Zilibwno km mukumatalikitsa zkutopetsa pamodz pomwepo mpaka 10 mns?
Queen umayitha ❤
mwaitenga kwa dyangu
Pajatu Nanyoni aka Mfumukazi amapanga za traditional Dr mu tikuferanji, and if you remember a couple of episodes ago in Mdyangu Queen anagwilizana ndi ashokoshoko kuti akapeze sing'anga to help Mrs Shokoshoko...
@@joshuaagabu3032 eeetu koma ili boh kwabas
Queen wafika ngati coming 😂😂😂😂
Abale ndalakwa 😂😂😂😂😂😂😂😂
Kusonyeza kut Msing, anga yemwe akufunikira mwa mdyangu pa misala ya Mayi shokoshoko ndi mfumukaziwa eeti kkkkk ndikuzitsatira bhobhoo ndpo tili limodz ndthu
off course mwapanga cross over from mdzyangu to mfumukadzi bwino apapa koma munayiwala za mercy, kodi munthu modzi azipezeka ku mudzi yomweyenso ku town? but anyway keep it
Mdyandu plus mfumukazi kkkkkk
Mwalakwitsa kupanga mix coz kuli mercy en bambo a ju
In mfumukazi she's not mercy she's namoyo
Queen mwabwela ngati coming ❤
Mr ShopRite 😂😂😂😂
😂😂koma queen
😂😂
Koma
Kwini
Ma guys muli bho
Kwavuta basi😂
Rong jane kk
queen koma ndye ndiokongola eeeee uli pa banja?
Mfumukazi now kujoina mdyangu series
mixing mdyangu and mfumukazi hahahahaha
Zaphatikizidwaso zinthu zija🙉🙉 mwati tiphulapo zazeru apa? Nde izikhala one hour tu osati 30 minutes yomwe ija kubelana uku