Am following this thoughtful moving comedy's all times And cousin from Lusaka Zambia was very interested to keep on watching mfumukazi comedy.please May the good Lord Jesus give you knowledge and strength.give as more.
I like that Duncan guy. The costume and the acting are on point! Flora and team this is a great episode full of lessons. Akazi pena amatha kukodwa chifukwa cha tizinthu ting'onong'ono - the case ya jumbo. Mayi munadya za enitu. Mulipira ndithu kkkkk. Koma Farai ali kwaanii?? Great work! Keep up the great work!!
Yaaa zimenezo ndi zoonadi azitumiki a mulungu wo ndiye asamangotchulidwa palipose inde ose ndi atumiki koma specially Muhammad yo ndiye sitimafuna kumuseweletsa
Kkkk kulumidwa ndi njuchi za kumanda ndi madalitso....pasakapezeke wokathawa
Kkkkkkkk akuti wina Yesu(mtendere wa Mulungu akhale naye) amuyendere wina Muhammad (SAW) amuyendere 😂😂😂😂😂😂😂😂
Am following this thoughtful moving comedy's all times And cousin from Lusaka Zambia was very interested to keep on watching mfumukazi comedy.please May the good Lord Jesus give you knowledge and strength.give as more.
😂😂😂 Malo amodzi koma losakola, big up guys Inuyo mumatha
Koma honestly I enjoy this comedy😂😂...osanama,,mmatha guys...Actors and actresses, all are just on point, superb!
Lululuuuuuu nagama ndi zimenedzo azimuna awiri iwe wekha tiyeni naoni tiri ku mustund kuonelera mitala yankadzi m'modzi adzimuna awiri buuuuu ❤❤❤❤❤
Thanks all for watching..kindly share and invite others to subscribe to our Channel...much❤
😂😂😂😂 nde mwati njuchi kutiluma ndi madalitso😅😅 owooh kwavutatu 😂 ayi yesu palibe oooh koma lero ndaseka😂
Koma mayi nagama ndinutu okongoooooooooooo{la
Koma shorp rite ndiye mukuchoka ndalama zikungogawidwa.❤❤❤❤
Bola Ife tizidya😂😂😂😂km padela ine ndimakukondani ndibanja lanu nonse😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma mumatha gyz 😂😂😂😂😂 mwapangisa sikulanga kukhala lokoma😂😂😂
😂😂😂chipewa cha mwana wachibayo
kkkkkk Kodi gututu limeneli likhaletu lamanyi la makhoza pa Jozi 😂😂😂😂😂😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣kwamfumu kwavuta yooooo
Nagama ndiwe chiphazuwa or ineso ndimakufila nditulusa nyimbo titled nagama flora
angling,ande umatha kwambili ndithu 😂😂😂😂😂😂
Awesome 😂😂😂 keep up the good work guys , i salute you.
Amfumukazi khani yakanika kugamula sikumeneko kkkkkkkm
Kkkkkk apadela eti yesu amuyendele😂😅😅
iyi nde mwaitchakula nsaname
Mwamveka gaez shop write mukudabwisatu mukuafuna anagama bwanji😂😂😂😂😂😂
Good
Koma milandu ya pa drama inu 🤣🤣🤣🤣🤣🙌🙌🙌🙌🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Kkkk koma aduna mmm ayi, Mayi nagama akuti kozani kolala kkkk
Ku bwalo la mfumu koma kugemulana kwakeko😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Akuti Kodi inu,ine ndi mkazi mnzanu 🤣🤣🤣🤣 in ching'axy voice 😂
Ndipo ndaseka nalo koopsa funso limenelo kkkkkk
😂😂😂😂jumbo ikalowa ya lowa lv to lv❤
Mfumukazi sakufuna mbeta mmudzi make
Aaa😂😂😂😂 koma ya ana achibayo ya ndiwaza
I can't stop laughing. Kodi naye Kalanka Ali chapatipati. mpaka mmimba kuwawa ndikuseka.
Atatenge yapachibwalo Kaya ndan Kaya tiona 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
nyimbo ikhale Mlando by Makhadzi
Ndalama zikugawidwa uku Mr ShopRite 😅
Eeee Kom week ino ai zkom❤
Mulandu tikuukana alandira jumbo ndi mk1000 kkkkkkkkk😂😂😂
Kkkkk kumala mkokoma sure
Koma padera , nkazi sangayambile pa guardian 😂😂😂😂😂😂😂😂
Gututu ndi gemason ndanamuna
Eeeee koma lero ndaseka. Ndinu machine guys😂😂😂😂
Mfumu kazi ulibe mfundo iwowo abweresa majumbo mk 1000 asanalole bwanji kkkk apadera akuti winayo yesu amuyendere winayo Muhammad amuyendere inuyoso amfumu kazi yesu akuyendeleni kkkk
Vere good
Gututu ndi one and friend wake Ajamiso 😅😅😅
Mwamunatu sadyeleka kkkk
Osapereka yodula😂😂
Kkkkk koma sasoka mpaka kulowa mu Bible kkkk
Km moyo kale umakoma love to love kiss to kiss 😂😂😂😂 nagama pa mitala
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Guys pitirizani ndithu kutisangalatsa
Chipewa chamwana wodwala chibayo😂😂😂😂
😂😂😂 koma fututu ayi taa kkkkkkkk
Nice movie
😂😂😂😂 Koma yaaaa
Following ndichidwi
Lero pa bwalo panali masewera 🎉😂😂
😂😂
❤❤❤ this nice movie
Kkkkkk km fundo ya Jamison😅😅
Nawoo a mfumu nkhani ili yonse weshiout
Ndipo inu..!
Iyitu ndimaona ngati chisintha...
😂😂😂😂
Kom iyi yachedwa
Apepe
❤❤❤❤❤ nkhani zake kkkkkk
Ili bwinotu iyi
❤❤❤❤❤❤
Kodi namoyo bwanji watodwala sukuveka mautu
Moto unandi 🔥🔥
Chippewa cha ana achibayo😅😅😅😅😅
Inuso mpakana phone ? Anthu kumakuyimbirani 😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂😂
❤❤❤❤❤❤❤❤❤😂😂😂😂😂😂kkkkkk amalilo kkkkk😮😮
Mfumukazi gamulo lalepeleka kkkkk
Saliyuti kwa mfumu kazi😅😅
This series is very impressive❤ 😅😂
😂😂😂😂 mayo
Eeh Ayo ine
Koma sasoka ni chimphanya 🤣🤣🤣🤣
Mabodza 😂❤
Thanks pondivera pemphero langa loti tapasowa pa bwalo thanks so much guys
Mercy kudekhatu or mawu
Km yaa
Kkkkk
I LOVE THIS CREW ❤❤❤❤😂😂😂😂😂YOUR VERY OWN FOLLOWER FROM ZAMBIA 🇿🇲
Timakunyadirani
❤❤❤😊
😂😂😂😂 adyelana katundu 😂😂
Ching'axy Muhammad amuyendele
Chapabwalo mpaka kupeleka katatu
Kkkk
very outstanding action, love it.
Pabwalo panakoma lero 😂😂😂😂😂
Jameson and gututu mumathaa 🔥🔥
I like that Duncan guy. The costume and the acting are on point! Flora and team this is a great episode full of lessons. Akazi pena amatha kukodwa chifukwa cha tizinthu ting'onong'ono - the case ya jumbo. Mayi munadya za enitu. Mulipira ndithu kkkkk. Koma Farai ali kwaanii?? Great work! Keep up the great work!!
koma athu inuyo mumakwana
Sinakulumeniko njuchi inu
Kkkkkkkkk
Koma ndaseka kokumva kukoma size
Malilo kkkkkkkkkklk
Koma guys
PA bwalo la mfumu ndinapasowa thank you guys
Comedy yalelo yinali yapabwali 😂😂pokha basi
Kachingat in padera voice😂😂😂
Takulandilani
Koma gututu
Zilibwino, koma please stop mentioned Allah messengers pa zinthu zopanda pake. Pangani za comedy basi
Yaaa zimenezo ndi zoonadi azitumiki a mulungu wo ndiye asamangotchulidwa palipose inde ose ndi atumiki koma specially Muhammad yo ndiye sitimafuna kumuseweletsa
😂😂😂😂