Nanga bwanji Patricia kaliat ndi nkhala kale mu utm koma waluza?? Anthu sakuona unkhalakale povota koma utsogoleri, muchedwatu inu kabambe akutsogolera
Sam mavitha ndi iwe kape. Newton Kambala mwini wake wa UTM ananena poyela kuti ndi amene wakhala akupanga komapa ndikupempha anthu kuchoka ku DPP kupita ku UTM. Iwe nkosho wako wanva.
Amalawi muchedwa ndizimenezo mukati wa si wa UTM ndiye kuti chani eya waangoyimira UTM basi musiyeni naye ayeseko paja amalawi sitinafike pokhazikika tidakali poyesa mpana mulungu adzatipase pule woyenerera sopano tiyeni tiwayeseke A kabambe wa kuti alindizotani osamangokhalira kusathula anthu sizitithandiza apeter tinawayesa aChakwera tawaona amane timkadikira kumuyesaso anapita chilima pano mulungu watizusira kabambe timuyese plz anali ku reserve bank mwina economy akuyiziwako though mkovuta kuti tikhazikike amalawi zinthu zalowa pansi kwambiri koma ndikulimbikira zikhonza kuzasintha plz awuzeni akabambe ayambe kuyenda anthu awaziwe nthawi ikutha iyi apita akuzungulira tu malawi dzukani
I like your comment ukuganiza booo ndipo dizoonadi tiyesepo ena mwina Kabambe angazathandize Malawi wathu
Zaziii UTM my vote Dr Kabambe 2025 boma ❤❤❤❤❤
Ngat ili plan ndagwilizana nao 😅😅😅
Ngat inali plan ya DPP ndekut ndi plan yabwino kwambiri 😂😂
DK my UTM president ...mukamalinbana ndi DK mudzimbvabe kuwawa
Ndipo Kabambe ndilibe naye chifukwa😊
Good plan
Cholinga cha video imeneyi ndi chani. Ngakhale malemu chilima anachokera ku dpp komweko. Tsono Ngati ili plan ndayikonda as long as mcp ichoke basi.
Awa ndimaboza peter sangasiyile munthu mpando
Iwe sam malvita ndwe chitsilu kwabas panga zako ok
Ngati ili Plan ndekuti ndi plan yabwino......DK 2025 bommmaa
Muuchedwa nazo ....UTM NDICHIPANI PACHOKA........
Kayambeko ndale kuti nawenso uzapangeko😂😂😂😂
Za ziiiiiii palibe chomwe unganene apa.kagwere
DPP ukumaisakatu eeee ishi timadziwa kt ndiwe wa PDP
Poyamba l love this guy content but panopa ndy ayiiii
Apa ndie samu waonetsa kut sometimes ndiwe *Mbuzi* yooneka ngt munthu akutuma et? Wandibbowa... Tikupanga za Dan lu
Ine ndichifukwa amabowa
I thought ndiwe mfana oganiza bho kma ay ndthu ase pple need solutions osat za ndale zo
Nkhani ndiiti apa?palibe chamvekapotu
Unyera mwazi galu iwe
Bro Zina timakusatani Koma izi mwa pala
Muchila ndipo mabodza Anu alibe basis
Nanga bwanji Patricia kaliat ndi nkhala kale mu utm koma waluza?? Anthu sakuona unkhalakale povota koma utsogoleri, muchedwatu inu kabambe akutsogolera
Wa mcp iwe kagwere uko sam
Komatu mmmmm ndale ndizotheka kuti ndi zoona mmmmm eeeee komatu
Aaaa inu malemu chilima anachokera kuti ndiye Kopitar ku ddp ko vuto ndi chani, inu
Zaziii mzamulira na na DPP YANUYO
Nankhumwa was the root of those squabbles, mavuto onse anali ku DPP Nankhumwa ndiye amayambitsa
It seems, Pali a ndale ena akukutuma kuti uziyankhula zotsutsa a ndale ena amene anthu akuwafuna.
Iweyo naretawe nde wampungwepugwe
Chikakangawa ufikatu povomeleza Kuti not even Smartimatic or MEC Chair will help to save your face 😂😂😂😂
Ndiye zilibwino kwambiri kabambe yemweyo
Dop my vote
Nawe usatinyase musiye alamulire wasowa mfundo eti akutama nyapapi iwe
Mavitayu wandikwana mboliyamake ndithu uyu ndi chitsiru kwabasi ndiye ngati zirichoncho iweyo chakukhudza ndichani inetu sindikuona vutotu apa
Dpp ilibe fundo kwawo kutukwana basi agalu inu munapanga chani muli mmboma mavutonso okhaokha basi olo mulowenso paline chamzelu mutapange mubamonso ndrama
Koma man Inu anakodza m,manama yooh
Wangokhuta mbatata uko basi utinamizepo pano
Ukukamba zakabamba ukusita zambuzi yakoyo ndiwe chisiru chamunthu wachepa muziona tika vota
A utm anapoila
Mukati Siwa UTM ,adasankhidwa ku convention ya chipani chiti?
Kayatu kkkk
MCP ya chaniso nanu
Ndiinu achitsulu zipangani post mzamzelu ngt amzanu
DK 2025 bommmaaa
Zaziiii
Km iweyo naweso kayambe ndale azako azakambekoso zaiwe
Pali ka sence kenakake mkatimu.
Zazii kusavomereza kukwezedwa kwa ena
Mcp my vot
Osewo sangatenge boma ...
Chokani apo ndiwe chindele
Mcp my vote
Munawamva ndani umboni muli nawo?
Samu chitsilu kwabasi
Kagwere uko iwe zaziiiii bas
Panyopako iwe
Wasowa chokamba galu iwe....mukamupeza kt munthu opanda zifukwa ku Malawi... zimenezo ndy ndalezo..
Iwe ndwonama wamva
❤🎉
Wazipeza kut??
Zoona
Sam mavitha ndi iwe kape. Newton Kambala mwini wake wa UTM ananena poyela kuti ndi amene wakhala akupanga komapa ndikupempha anthu kuchoka ku DPP kupita ku UTM. Iwe nkosho wako wanva.
Sam Malvitha you are NOT qualified journalist/influencer. Can you improve the way you gather your information before presenting it to the public.
Mcp my vote
Mcp my vote