@@EstherChilopeJesus Christ Never died???? Who told you that? Please withdraw this statement. If He never died then how did he redeem us from our sins? Remember Jesus is "the Lamb of God which takes away the sins of the world". When you are highly attracted to a prophet, always remember "It is written: ‘Man shall not live on bread alone, but on EVERY WORD THAT COMES FROM THR MOUTH OF GOD." Matthew 4:4
Even Jesus himself was rejected by his own people , today this man is in Malawi but you will here his own people disowning him. For me I don't judge but I believe in miracles. Amene akuti uyu ndiwasananiki apite ndichowonacho akamumasule m'busa waku Zomba yu Chifukwa ngati CHITETE ali onama inuyo ndiye kuti ndinu achowonadi pitani mukamupemphelere akamasulidwe iyeyo
God is angry with us people for doubting him because we’re too proud. It’s good that Jesus is not physically in this generation chifukwa akadakhala mu mbadwo wathu uno, these people would have reached an extent of crucifying him 20 times 🙌. That’s why everything that we will be seeing in the coming years will be well deserved
Achakwera tapita kwa chitete akukuchoseni ziwanda zachuluka 😂😂😂
Koma chonde anthu amulungu samalani ano ndimasku omaliza chilichose chomwe chinalembedwa baibulo chizachitika palibe chomwe chizasale
Mulungu wanthu ndi wabwino ndipo salemphela Kuti munthu akachilisidwa chitengela chimphulupiliro chamunthu amen akufuna kuchilisidwa
Maw amati tisaweluze
Kungopangana uko ndikumawanamiza anthu. Musamale mulungu akukuonani bashop
Mmmmm kuyakhula kwanji uku
@@JoãoChirwa-n3lzoona
Jesus Christ never died.He is still alive ntchito zake zikugwirabe kudzera kwa mtumiki wake Prophet Servant Chitete.May you live long my prophet.Amen
Ndpo zoonad izi apasan ndlm kumbali
@@EstherChilopeJesus Christ Never died???? Who told you that? Please withdraw this statement. If He never died then how did he redeem us from our sins? Remember Jesus is "the Lamb of God which takes away the sins of the world". When you are highly attracted to a prophet, always remember "It is written: ‘Man shall not live on bread alone, but on EVERY WORD THAT COMES FROM THR MOUTH OF GOD." Matthew 4:4
Amanama awa ine sindikhulupirira izi
Mukhale ndikusakhulupilira kwanuko ngakhale yesu Christiu anthu ena samamukhulupilira
Dzikoli mmm
Tikiyamikani Mulungu chifkwa chachisomo chanu potipasa mtumiki wanu Mulandire Ulemu ndi Matamando Zikhale kwa Inu AMENI
Zabodz bwanj osapit mzipatalam momwe mul Anthu omwe akuvutikzak ndizak kudwal ndiy muziwanamiz Anthu yap
Powerful
Powerful ine ndi umboni..
It’s very true the man is anointed
Abale tingolimbikila kupemphela yesu ali pafupi kubwela ,zamatsiku osiliza iziiiiiiiiii
When God speaks the wise listen
Amen
Za Ziii Pali chani pamenepo mulungu mwayesa alamuanu
Even Jesus himself was rejected by his own people , today this man is in Malawi but you will here his own people disowning him.
For me I don't judge but I believe in miracles. Amene akuti uyu ndiwasananiki apite ndichowonacho akamumasule m'busa waku Zomba yu Chifukwa ngati CHITETE ali onama inuyo ndiye kuti ndinu achowonadi pitani mukamupemphelere akamasulidwe iyeyo
God is angry with us people for doubting him because we’re too proud. It’s good that Jesus is not physically in this generation chifukwa akadakhala mu mbadwo wathu uno, these people would have reached an extent of crucifying him 20 times 🙌. That’s why everything that we will be seeing in the coming years will be well deserved
Akanakhala nazo mzeru akanasamalira matsiliziro awo
Deuteronomy 32:29
Aaaa zasatanic izi
Anthu abodza awa ma prophet onyenga Asatana Eni Eni owoneka ndi maso
Pamaso pa Mulungu palibe kunamatu kkkkk😅😅
Hmmm anthu ambirinu kumwamba zimudzalowa ndi mayankhulidwe anu
Mayankhulidwe Ake ati?
@@MMK-p3ymuzaona nokha
Please chonde amalawi osankhulupilira izi zimankhara ziwanda za kumidima
Ukunena chilungamo
Mtumiki wamulungu uyu
Zaboza izi 😂😂😂😂😂😂
Bwanji asakupephelera mvura ku Malawi ko asamakunamizeni bwanj asamapita ku Chipatala komwe kuli odwala zenizeni samalani
Kkkkkkkk boza boza anthu awa asataniki kkkkkkkkkkkk athu aboza awa aziwanda bass
TB Joshua waku malawi
Apite kuchipatala kumeneko akawapeza odwala zenizeni akawachilitse amenewo osati abodzawa
Eti eti. l
Khulupilorani Mlungu inu , mphanvu akuzitenga kuti? Pempherani , Mlungu amasintha nyrngo
Ndipo inuu
Nthawi zija za ulosi ukukwanirisidwa ndithu.
Bola ngati zili zachilungamo chifukwa masiku ano kukuchitika zambiri
Koma achawera atapita ukuku he can be delivered and know the truth
Azimayi kutengeka
Omwe Ali kumeneko ndi azimai okhaokha komanso nawe
Nanunso kupusa bwanji. Ali ku church wo ndi azimayi okhaokha kapena you’re just another sexist trash?
Koma bwanji apite kuku hospital yose yamalawi athu apeze bwino
Koma ena amapanga ma drama
Wekha kukhal chkhulupiliro kugwada nyumba mwako mzimathek Mulungu ndioyankha
Ndipo kwambiri. Osati kumapita kwa prophet ndi mafunso opusa Ngati "should I date her, should I marry her?" Iweee aaa😂
Nde mwapanga malondatu
I wonder why all the testimony givers are from outside Malawi..
I wonder why all of them are able to speak english
Pitani kaye mukaone nokha,,
Hie mama
Prophet chitete nditumikidi wa mulungu
Komano ndizoona kuti akupempherere umafunika kupereka Kaye ndalama???
Mukhale ndi mzimu wachiziwinso
Munawerenga Pati Pati mu Bible?
Zamphamvu
Bushiri 2😂😂😂😂
Fake
Rubbish 😂😂
Amen