BON KALINDO LERO PA 20 JANUARY WANG'ALURA A POLICE POMUMANGA LAYTON MANGOCHI OPANDA CHIFUKWA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 31 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 137

  • @maxwelljuwaophiri
    @maxwelljuwaophiri 11 วันที่ผ่านมา +9

    Bwana Honorable Kalindo,
    Mumatha and you represent Us.

  • @RaphaelSamson-z4d
    @RaphaelSamson-z4d 11 วันที่ผ่านมา +1

    Big up DC never stop fight for us

  • @Isaac-u3v
    @Isaac-u3v 11 วันที่ผ่านมา +7

    Abale timpange sapot bon kalindo uyu amayankhula zoonad

    • @FrancisNyayi
      @FrancisNyayi 11 วันที่ผ่านมา

      Kungoti Amalawi timadana ndi chilungamo

  • @ABDURASHEEDMATEMBA-b2b
    @ABDURASHEEDMATEMBA-b2b 11 วันที่ผ่านมา

    Boss DC your the best solar of malawi 🇲🇼

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 12 วันที่ผ่านมา +5

    Wina Mr DC azapite azakhulupilile kuti inuyo ndimwana oopsa

  • @CassimCawanga
    @CassimCawanga 11 วันที่ผ่านมา +1

    Boom kalindo u is de best than MBC TV

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 11 วันที่ผ่านมา

    The DC❤❤❤

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 11 วันที่ผ่านมา

    More fire mr Bon Kalindo 🔥 🔥 🔥

  • @Jamaat-m7l
    @Jamaat-m7l 11 วันที่ผ่านมา +1

    Kamandiwaza komati MA kape aku area 30 😂😂😂😂😂 eeeee koma the DC ayi zikomo

  • @MacdonaldMisomali-lt4wu
    @MacdonaldMisomali-lt4wu 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkkk bon kalindo ase

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 12 วันที่ผ่านมา

    If all Malawians were Bon Kalindo,Malawi would be a paradise on earth!Where are
    You my heavenly Father ???

  • @MussWalasi
    @MussWalasi 11 วันที่ผ่านมา

    🙏🙏🙏🙏

  • @MarthaGama-q1o
    @MarthaGama-q1o 11 วันที่ผ่านมา

    Dziko lathu lili ndi atsogoleli wovetsa chisoni mmaganizidwe awo ngati ana koma chonsecho ndi anthu wophunzila bwino thu kaya vuto ndi chiyani kaya, chimanga mmalo moti chipite kwa admarc aliyense adzikagula yekha, ali busy kugawa kwa anthu wowadziwa okha okha ndiye ena mukuwamanawa akagula kuti huuuu! More fire 🔥🔥 Born Lap ndo

  • @ChristopherNakhumwa
    @ChristopherNakhumwa 11 วันที่ผ่านมา

    Chief chief

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 10 วันที่ผ่านมา

    Ulemu wanu mr Dc

  • @RaymondJlawila
    @RaymondJlawila 11 วันที่ผ่านมา +1

    Apiteso ku chiradzulu hospital utsiku magesi sayaka utsiku😂😂😂😂

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 12 วันที่ผ่านมา

    DC ❤❤❤❤

  • @ChisomoMathews-u1u
    @ChisomoMathews-u1u 11 วันที่ผ่านมา

    ❤ Congratulations Mr bon kalindo respect 🙏

  • @GivesonBanda
    @GivesonBanda 11 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂😂😂😂 amwene bon kalindo ndaseka kwambili mwati winawake akufuna kukapepesa manyumba awathu ochita bwino 😂😂😂😂

  • @CharityKangulero
    @CharityKangulero 11 วันที่ผ่านมา

    DC 🎉🎉🎉🎉

  • @BeforeZayekha
    @BeforeZayekha 11 วันที่ผ่านมา

    Good your point

  • @DominiqueChitimbe
    @DominiqueChitimbe 11 วันที่ผ่านมา

    chesaopa the DC akatundu 🔥💪💪🔥

  • @AubreymedsonMbewe
    @AubreymedsonMbewe 11 วันที่ผ่านมา

    Anthu awawa sadzamva ayi kuuzidwa xochita Koma osasintha kachitidwe ka zinthu,KP it up B. Kalindo

  • @VanGregoryKwekwesa-vr2fc
    @VanGregoryKwekwesa-vr2fc 11 วันที่ผ่านมา

    Our 2 an' half Man, The most Dangerous

  • @PiassDayit
    @PiassDayit 11 วันที่ผ่านมา +2

    komatu lero M'mene zilirimu Mmalawi Muno palibe akupanga mademu Koma likangolowa M'boma la Dpp muzingot pang'ono pang'ono mademu

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 11 วันที่ผ่านมา +1

      Ndiconco kumene cifukwa dpp ndi ya democrancy ndichifukwa anthu akuifuna kuti ibwelele kuti adzipanga dzomwe akufuna 💙💙💙💙💙

  • @MariaDandazaraJSDmoio2024e
    @MariaDandazaraJSDmoio2024e 12 วันที่ผ่านมา

    Fire the Dc kuyakhula kosaopa auzeni aziwe chimene akupanga ndizauchitsilu ndiye ine ndilipamodzi ndizimene mwayakhula lero God bless you

  • @PatrickMungomo
    @PatrickMungomo 11 วันที่ผ่านมา

  • @Baaggah
    @Baaggah 11 วันที่ผ่านมา

    The best bon kalindo

  • @KossimasiMaluwa
    @KossimasiMaluwa 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkk osat akupita kukapepha ameneyo 😂😂😂😂😂

  • @HestingsChikapa-g2e
    @HestingsChikapa-g2e 11 วันที่ผ่านมา +1

    Dziko silamunthu modzi km ndi lamalawi dziwani kt kunja kumada ndipo kumacha lamulo la dziko ukalitengela manja mwako ndi chimodzimodzi kumwa asidi samalani pakamwapo malawi ndiokwiya kwambiri zonse za padziko tinazipeza ndipo zotsala tidzasila ena ndibwino tingoyang'ana kumwamba chomwe atipatse yehova mulungu chikhala chomwecho cz tikapezerana zifukwa pano tingazuzike kutsogoloku komaso mwina kuzizitsa ana athu kapena abale athu kumene tiyeni tikhale anthu odzichepetsa ndi omvetsetsa masiku athakale awa zikomo

  • @GribetaBongis
    @GribetaBongis 10 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkk kma bon iwe anakonza

  • @yusufuemmanuelmacsuid
    @yusufuemmanuelmacsuid 11 วันที่ผ่านมา

    Boon kalindoooo😂

  • @Aden-m8d
    @Aden-m8d 12 วันที่ผ่านมา

    First viewer

  • @emmanuelmaomba5163
    @emmanuelmaomba5163 11 วันที่ผ่านมา +1

    VP nde ali busy kugawa ufa tima 2 kgs 😂😂😂😂😂😂😂🙌🏻🙌🏻🙌🏻🙌🏻🙌🏻

    • @fannyzimba149
      @fannyzimba149 11 วันที่ผ่านมา

      Kkkkk ali busy kuphikilira mphala ana mhuuuu kumalawi tiziona

  • @RosangelMoyenda
    @RosangelMoyenda 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk munthu yemwe sanaimepo pawindo la video show sangamuuze bon chochita 😂😂😂😂

  • @GivesonBanda
    @GivesonBanda 11 วันที่ผ่านมา +1

    Thawi ya kamuzu athu amachita zoipa mbiliyoyipayi imamuyipisa kamuzu zithuzina kamuzu samaziwa ndizomwe zikuchitkaso lelo ku mcp komweko athu akuwononga mbili zomwe zimugwese chakwela ndipo agwa ndithu omvesa chisoni

  • @PreciousMmera
    @PreciousMmera 11 วันที่ผ่านมา +1

    Mumatiimilira boss

  • @thesouthfacemusic896
    @thesouthfacemusic896 11 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂 koma ndaseka chimodzimodzi Muthu kutunga madzi musinje kukanthira munyanja.
    Muthu was mzeru wake kumatenga ndalama kumakapeleka Ku Amelikano 😂😂😂😂 izizi ndizashupiti zokhazokha ndinthu

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 11 วันที่ผ่านมา

    Apapa boni kalindo akapanga kukumangani ndekut inu ndi mcp mukuziwana

  • @AngolaChinga
    @AngolaChinga 11 วันที่ผ่านมา

    Auzen the DC we are together

  • @LIMBANIALISON
    @LIMBANIALISON 11 วันที่ผ่านมา

    ❤❤❤

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 11 วันที่ผ่านมา

    No fear the DC

  • @GigssyStima-l2c
    @GigssyStima-l2c 11 วันที่ผ่านมา

    The DC

  • @BeforeZayekha
    @BeforeZayekha 11 วันที่ผ่านมา

    Mbuzi ya chabe chabe chakwera😂😂😂😂😂

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f 11 วันที่ผ่านมา

    THE DC😂😂😂😂😂

  • @LimzeySande-b9n
    @LimzeySande-b9n 11 วันที่ผ่านมา

    Makwana big 😂

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 11 วันที่ผ่านมา

    Big kalindo pitilizani kutimenyela nkhondo osaukafe ..No more mcp 2025

  • @SarahChizenga
    @SarahChizenga 11 วันที่ผ่านมา

    Koma mpaka kukapepesa 😂😂😂 koma kumalawi kwakomatu

  • @KondwaniChaponga
    @KondwaniChaponga 11 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂 mpaka makape

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo 12 วันที่ผ่านมา

    Our own pangolin

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x 11 วันที่ผ่านมา

    Kayambe masero ako aja

  • @JorMan-x8e
    @JorMan-x8e 8 วันที่ผ่านมา

    Ukali

  • @VickMuluwera
    @VickMuluwera 11 วันที่ผ่านมา

    Apm analosera kt 5years yamakape Mcp awa nyekweeee tiziwa bwino lelo hehedeee mai kokhwa ine

  • @PatrickBlair-u7m
    @PatrickBlair-u7m 11 วันที่ผ่านมา

    Bon kalindo machende ake

  • @ChristinaStambuli-q3e
    @ChristinaStambuli-q3e 11 วันที่ผ่านมา

    Boma la Mcp likupenga misala tikuona ndi Maso..liri stranded bomali it has nothing to deliver.what it does is kumanga anthu on political grounds

  • @ManuelKanyangala
    @ManuelKanyangala 12 วันที่ผ่านมา

    Koma ichichi chitivuta ndi2 hahahah 😂😂😂😂😂

  • @WestonOzuwell
    @WestonOzuwell 11 วันที่ผ่านมา

    Ndiye mbuzi zina nkumati boma ndlomweli mwina chilipo amakupasani kumbali

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 11 วันที่ผ่านมา

    The DC president of poor people 🔥🔥🔥🔥

  • @HenkitolbeukesBeukes
    @HenkitolbeukesBeukes 11 วันที่ผ่านมา

    Yaaa bwana bon kalindo osafowoka nd mbuz za mcp ndi galu wawo chakwela

  • @ellenrahman9959
    @ellenrahman9959 11 วันที่ผ่านมา

    😢😢😢

  • @ChifundoNkhoma-x7p
    @ChifundoNkhoma-x7p 12 วันที่ผ่านมา +3

    Fire kalindo🔥🔥🔥📢 adad pamalo pawo 2025

  • @HassanMillion
    @HassanMillion 12 วันที่ผ่านมา

    Pangolin wa boma uyu kkkkkk 😂😂😂

  • @AliceJere-k9v
    @AliceJere-k9v 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkk

  • @RoemeldaleePrince-k5r
    @RoemeldaleePrince-k5r 11 วันที่ผ่านมา

    Ndimakape ausilu bazooka iyendepo bwana kalindo commander ndikhara ine tingotenga boma president kalindo zatikwana kwambili

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 11 วันที่ผ่านมา

    Nthawi ndiye yatha yatha auzeni komatu inu a opposition ku uzidwa zofunika ndiye muku uzidwa

  • @EusébioLucianoGaiondo
    @EusébioLucianoGaiondo 11 วันที่ผ่านมา

    Dc

  • @ChrispineMuzungu-l8h
    @ChrispineMuzungu-l8h 11 วันที่ผ่านมา

    Zomvesa chison kwambr 😢😢

  • @MaganizoEvance
    @MaganizoEvance 11 วันที่ผ่านมา +3

    The Dc mwana oopsa kwambili🎉🎉

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 12 วันที่ผ่านมา

    Chitsiru cha president akukapepesa chani kufuna kuba misonkho yathu

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 11 วันที่ผ่านมา

    Koditu olo mutabvula maliseche kumayankhula anthu awa alibe zomvera anakhalira zomvera zawo . Kkkkkkkkkk ndi mgaiwa wasowawu mwina kundendeko kulimsima eti

  • @JoaquimElidioChiwisse
    @JoaquimElidioChiwisse 11 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂Bon Iweyo AYI udzangosowa basi

  • @EliasMagwaya
    @EliasMagwaya 10 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @MercyNkhoma-b6h
    @MercyNkhoma-b6h 12 วันที่ผ่านมา

    Kuyankhula kotere kunayamba nthawi ya Chakwera ndi Chilima ndiye panopa zisawabowe. Mbewu iyi anabzala okha.

  • @VickMuluwera
    @VickMuluwera 11 วันที่ผ่านมา

    Tiwauzeso kt eya boma ndilomweli we called Malawi komatigositha mtsongoleli basi

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela 11 วันที่ผ่านมา

    kkkkkk koma bon kalindo

  • @choralmusicchannel
    @choralmusicchannel 10 วันที่ผ่านมา

    Wina uyu kuno mmangeniso !!!

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 12 วันที่ผ่านมา

    Kodi iweyo akukusiya chifukwa chanid kwenikwen😅

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f 11 วันที่ผ่านมา

    Kuno ku Blantyre madzi lero one week madzi sakutuluka,eeeeeee chipanda mvula yomwe ikubwerayi kaya ndipo kaya

  • @Nkhomahevison
    @Nkhomahevison 11 วันที่ผ่านมา

    Auze bon umakwanatu

  • @SelianaGwande
    @SelianaGwande 11 วันที่ผ่านมา

    Iiiiiiiii awawa awa eishhhhh

  • @VickMuluwera
    @VickMuluwera 11 วันที่ผ่านมา

    Dc tiyenawo mpaka moto kt buuuu

  • @aubreyvisuals2416
    @aubreyvisuals2416 11 วันที่ผ่านมา

    wina azafa naye uyu, nditokuuzani kk

  • @AnorldKamponda
    @AnorldKamponda 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk Koma Winiko iiiiiii.

  • @TonexNasibu
    @TonexNasibu 12 วันที่ผ่านมา

    Chikangawa waluza bas okupha uja kkkkk

  • @IanMumba-k6n
    @IanMumba-k6n 11 วันที่ผ่านมา

    live

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 11 วันที่ผ่านมา

    Zikomo ndi lokondera Mangochi mwamusiye yekha no sapoti

  • @FebbyPhiri-n7j
    @FebbyPhiri-n7j 11 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @KennedyBanda-p9x
    @KennedyBanda-p9x 11 วันที่ผ่านมา

    Ukuti kamuromwe Kati kambewa

  • @WilsonFelix-j9n
    @WilsonFelix-j9n 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkk chalakwe

  • @Openjkick
    @Openjkick 11 วันที่ผ่านมา

    th-cam.com/video/o0g35X9MOE0/w-d-xo.htmlfeature=shared

  • @Hezronenkonde
    @Hezronenkonde 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkkk

  • @Andy20247
    @Andy20247 11 วันที่ผ่านมา

    Umakwana biggy

  • @Isaac-u3v
    @Isaac-u3v 11 วันที่ผ่านมา

    Bon kalindo ndikatundu bas

  • @AlickDickison
    @AlickDickison 11 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkk koma abale

  • @KondwaniLubaini
    @KondwaniLubaini 11 วันที่ผ่านมา

    Zoona makape enieni

  • @Isaac-u3v
    @Isaac-u3v 11 วันที่ผ่านมา

    chakwera wangokula mutu km,mzeru alibe boma lamukanika ndinyani ameneyo

  • @Aden-m8d
    @Aden-m8d 12 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkkkkkkkk

  • @GraceKANYOZA-e3v
    @GraceKANYOZA-e3v 12 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @PanganeniRafaelo
    @PanganeniRafaelo 12 วันที่ผ่านมา

    Mumakwana inuyo mesa

  • @RafickBwanali-r3q
    @RafickBwanali-r3q 11 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂