Joab Frank Chakhaza well done you deserve to be awarded to be Dr This is one of the best and inspiring cruese 5 two years ago but like is happening now ma cruese 5 awa ndi amene timafuna opasa chidwiwa ❤
Long life in advance professor Dr Charles Patrick Dzamalala for a work that you have done may God bless you 🙏 Pempho langa ndi loti mukhale professor wa amphawi lolani chilungamo mene chilili coz ndi mulungu amene wakusankhani kuti mufikile anthu onse 👏
So a story is a told about my late dad's encounter with Dr Dzamalala (my father was a clinician at Queen Elizabeth Central Hospital for 15 years)So Dr Dzamalala invited him one day to observe one of his procedures,he literally ran away,went straight home to mom's and hysterically explained his ordeal !!!😂😂😂
What a HERO! Just finished reading a book called Unnatural Causes written by a pathologist in the UK. You learn a lot about the human body. Definitely someone has to do the job. You deserve a medal
Great guy, glad to have been trained by him. his histopathology lectures were awesome, a very kind man
super hero, very humble and professional we need such kind of people in this country
Joab Frank Chakhaza well done you deserve to be awarded to be Dr This is one of the best and inspiring cruese 5 two years ago but like is happening now ma cruese 5 awa ndi amene timafuna opasa chidwiwa ❤
Long life in advance professor Dr Charles Patrick Dzamalala for a work that you have done may God bless you 🙏 Pempho langa ndi loti mukhale professor wa amphawi lolani chilungamo mene chilili coz ndi mulungu amene wakusankhani kuti mufikile anthu onse 👏
Joab you deserve an award. Thank you for the well detailed interview
So a story is a told about my late dad's encounter with Dr Dzamalala (my father was a clinician at Queen Elizabeth Central Hospital for 15 years)So Dr Dzamalala invited him one day to observe one of his procedures,he literally ran away,went straight home to mom's and hysterically explained his ordeal !!!😂😂😂
Big dzamalara doesn't go to pub
It’s very rare to see such stuff. It’s timadzionera pa fbi files basi. Thanks Joab for this wonderful cruise 5
One of the programs I enjoy. I learn alot. Big up Joab
This is very interesting! Keep it up Zodiak cruise 5 team
Nice one.. we need people like you here in Malawi
So ndya 2yrs ago n am here now in 2024 watching it n am loving it 🔥
Currently in America studying forensic pathology, but yoooo it’s not easy😤😤😤😤😤
come back when you finish
Ok
This is wonderful and inspiring. Timangodzionera pa fbi files basi. Thanks Joab for this wonderful cruise 5
He is a star, I remember working with him at Likuni Mortuary ,some guys was shot by police from mchesi
What a HERO! Just finished reading a book called Unnatural Causes written by a pathologist in the UK. You learn a lot about the human body. Definitely someone has to do the job. You deserve a medal
Let me check it out.
Its a calling, this man was gifted to do this.
Nuff respect Dr & Ochakhaza munadza inuyo ✊✊🇲🇼🇲🇼💯
Joab , you are a greatest journalist of our time
We need another interesting interview bwana Joab. Please do the needful
This was a fun interview, thought it would be grim, like he would be dark but he is actually humorous.
A rare gem. One of the most 'expensive' people in Malawi
Somebody must do it ❤️✅🔥Katakweee kwambiri
Thanks Joab, remarkable job
Bravo Joab. Your documentaries never disappoint. Top class!!
This is awesome
Big man. Good lecturer
Koma bwanji osawatenga iwowa ndimadokotala amaiko ena ozungulira kukayeza za imfa yakuchikangawa ija abale. Moti zoona kuikidwa mmanda osafufuzidwa kuti anakhapika ndichani and anafa chifukwa chani mpakana lero anthu ofunikila mumdziko ngati amene aja 😢 mulungu mudzaulule zinsinsi paimfa yosaiwarika ngati imene ija. Shalom Malawi 😢😢
Zimenezotu anapanga kale, chomwe chinasala ndi chakuti apeze chomwe chinapangisa ngozi bansi
Dolo kambirimbiri uyuyu
Zimakhalako ndithuuu
Hhhhhmmm
Anapanga kale zimenezo.report izatuluka km silelo
So interesting
Joab is so good at his job.
This is 31 August, 2024. I believe anthu tili ndi mafunso ambiri, kodi Joab simungapangenso program iyi ndi Abwanawa?
Very good joab
I can't work in this field🙌🏽
Indeed he is in the light positive that's why amagwira tchito moona mtima
Zandikanika ndalekeza pa embam🥺🙌
Wonderful
Great man
Great job frank taziwa nawo
Joab adzasandukadi uyu kkkkkk, keep it up teaching the nation
Joab please Connect me to Dr dzamalala I want to ask him some few questions.... Please naneso am puzzled about my uncle's death...
ajoab mmmm nkulu iwe wacheza ndi anthu good job ineso tsiku lina ndikuchita intervew cfk naweso uli ndi luso kumafuso
Wow, we need more like u pa malawi pano
Ayi zikomo 🙌🙌
Ndadziwa nawo
Very interesting
Bravo
Ndi Nkhani yanji idavuta pamkana pa court?
My role model
Great Joab
Abwana Dzamalala
Ngakhale ndayiwonera patatha 2 years ino 2024 ndanjoya kwambiri. Joab pitiliza ntchito yapamwamba pofukula zinthu zoti sitizidziwa ayi. Moti mpaka mafupa chonchi ngati azinyama koma ali anthu? Ngati ndi dziko linatu eee
Koma Joab assssssiii . Unagwiranso green mamba wa moyo
Genius
Ulemu wanu
Genius uyu
Joab watchena kwabasi.
Mmm ngolimba mtima
GREAT
Akanakalowa nawo ku Dissection room 😂😂 aone zosaona osat mafupa ok 😅...it's scary here for the faint hearted
Mmmmmmm koma u doctor sizinthu
Aah mwatani kodi😂
Joab 🎉
Nyama koma amadya big wa??
Ndakaika mmhu
@@aishachisale4267 ayankhatu kuti amadya, even day imene ang'amba mtembo
Amakondanso mang'ina kwambiri
Kkk..uyu olo nyama amadya koma uyu?
Katswiri👏👏👏👏👏
Ndiyetu akafukule thupi la chilima azatiuze zoona zake
Vuto aboma omwewa akunchingilira
Anapanga kale autopsy inu
Joab: Have you broken someone's heart
CPD: Thats my Job...I cut hearts... 😂😂
Wow
Ndaphunzirapo
Kuyankhula kokhako kuchita kumveka kut muli mzeru ndithu.
👍👍👍👍👍
Inu ndiwakulu
Watching this in 2024
👏
👏👏👏👏
Joab mpaka kugwira eeeehh
Munthu wa mzeru kwambili uyu
Who is 2024?😂
Eee koma iyiyi ulemu wanu Achakhaza
Tnkamgomva za akuluwa eeeh ndi shashatu
Tikanaonerakotu akupanga zawozo
Have you ever cried over someone? Awawa nagalire😂 😂
Yatha tili ndizambir zofuna kumva
rad
❤
Anthu ndye mumafukulira andthu
Munthu wankulu kobasi…machine🫡
Katswiri
Eeeeeh maguy
Amatha uyu Joab... Koma kodi ku ZBS anachoka
Ali ku Zbs komko¹ man
Ntchito iyiyi ungadanedi ndi anthu
Eeeh Koma zithu izi zofunika kuzama
Uyu mkatundu mmmm😮
Joab mmatimilila
Eeeh 💔😂🙌
Koma hummer yake shaaaa
Yaaa athu ndi olimba mtima kkkkk
Kkkkkkkk km Joab,,,,ufiti!!!!!
😂😂😂😂😂eish joab umaseka nde mwangokumanatu
Ose nga phwete
Kuseka nkokoma
Eeeee ndinu Munthu wamkulu ndithu
My question can be ; do you eat meat 🍖
Good question
That was asked kkk
Mmmmmmmm😂😂😂
😂😂😂😂
Wonderful