Amumba continue doing a good work , indeed your were chosen to stand before us by God. May God keep on blessing you and give you healthy life. Osafoka, osasintha gear up and osatopa😂
Ineyo ndikugwirizananawo anduna amenewa ndipo pempho langa anthuna musalole anthu ena kukupatsani chinbansi chifukwa nduna zinzanu zizikukondwa nanu chondechonde anduna pitilizani ntchito yabwino we love you so much ♥️ ❤❤❤
Good work, koma kutengela ndi umphawi ku malawi akuyenera kupanga consider Anthu ogwila ntchitoyo kamba koti anthuwo ngakhare kukumana ndi zovuta pa ntchitopo koma amapezabe cholowa after payment.
Komano vitumbiko akugwira nchito kuposa chakwera na ku mcp anayenera kukhara president ndi ameneyu osat mbuzi zinazo zinazo zikungoziwa kutukwana kumanga ndi kuba bas
Amumba continue doing a good work , indeed your were chosen to stand before us by God. May God keep on blessing you and give you healthy life. Osafoka, osasintha gear up and osatopa😂
Dunayi sikulakwitsa koma...anthu tikuzuzika dziko lathu lomwe...Mr Mumba keep it up ❤️ ❤️ ❤️
Ineyo ndikugwirizananawo anduna amenewa ndipo pempho langa anthuna musalole anthu ena kukupatsani chinbansi chifukwa nduna zinzanu zizikukondwa nanu chondechonde anduna pitilizani ntchito yabwino we love you so much ♥️ ❤❤❤
Ziribwino❤❤❤ yekayu borako
Excellent anduna !! A true Malawian citizen !!
Amen.. & Amen !!
I love you Mr nduna good job
Samu ndakunyadilaso chifukwa suyang'ana mbali koma chilungamo like you first
God bless you vitumbiko
He is a good examples of ministers who have nominated all these years
Bwana Mumba your doing a good Job......
Good
To be honest he is doing great job
this guy ili bho.ndipo ndizomwe zikufunika kt anthu obwerawa asamatizunze ife okhala amalawi.
May God enlarge his territory,ziiilii bwinoo kwambiri apitirizeee
We more of these leaders
Chifukwa akupanga zokomela a Malawi one osati a MCP okha ayi anthu omwe akufunika pa Malawi ndi ameneyu Mumba keep it up..
We need strong ministers like him not poor ministers who are hunting the corruption
He is doing a good job. Keep it up honourable Minister.
Vitumbiko wayimba bho kwambiri please continue ❤🎉
This what Malawian's want
Mumba ntchito imene Mulungu anakupatsa ndiimenei Amalawitu tikuzunzika moti ena atenge chitsanzo pa inu mbiri yabwino iposa chuma
Nchito yabwinokwabiri osati ndunazinazi zogonazi zopondereza Malawi kukonda anthu obwera!!
Ameneyo ayamba bwino ndithu apitilize kutero kuli nyasi kuja kuno mulungu amupase mphamvu ndi nzeru vitumbiko Mumba
Well done an continue
Time up mwachedwa nazo mukanayamba 2020 komaso mupite ku migration ndi road traffic tapangani zimenezo
🎉
Aa mmene ndaganizira ine ngati M"MALAWI a president akanapangitsa cabinet meeting awaphunzitse ma ministers ena mmene akuyenera kugwilira ntchito. 85% yanduna atati azigwira ntchito modzipeleka chonchi ayindithu bwezi lDziko lathu lilipena pake. Pomaliza ndingoti Enginer v, Mumba pitirizani ntchito ya bwino, Aliyense amene angabwere kwayinu kufuna kukupatsani chiBANZ MANGENI BASI.
Ambuye anutsogolere asafooke a Malawi tikuzunzika chifukwa cha umphawi
the best minister ever in chakwera administration,tikanakhala ndi nduna ngati izi chakwera could have delivered.
Nzeru zikubwela chifukwa tikupita ku chisankho
Uyu akutha
❤❤❤❤❤
Minister MUMBA apitilire ku onetsetsa anthu ogwira ntchito peze zofuna zao
He is fit. May God comfort him
Congratulations to him😊
Angokhala president wa malawi basi
Iyi...ndiye..nduna ..tikufuna
Akuchita bwino kwambiri ,dziko ndi lathu anthu obwera asamatizunze pamene tikuwapangira ndalama ma company mwawo
Good work, koma kutengela ndi umphawi ku malawi akuyenera kupanga consider Anthu ogwila ntchitoyo kamba koti anthuwo ngakhare kukumana ndi zovuta pa ntchitopo koma amapezabe cholowa after payment.
Izi nde zofunikazo
Uyu ndiye Malawi akufunika
nduna koma vitu
Tiyeseko achinyamata maunduna awa mwina zingasintheko
Nduna iyi ikugwira ntchito yotamandika🎉🎉
Vitumbiko mumba my favorite,,,akugwiradi ntchito yake not zinazi
Congratulations mumba
Anthu ife timadana ND usogolery umene suguira chito yake mokwanila mosangalasa Anthu amene ukuwasogolera,paVitumbiko zikutheka.
Akuchita bwino
Vuto lalikulu unduna amasankha nkhalamba yoti sangayendele company yayikulu mwina zimango nthela ku office basi
Akugwira ntchito bwino kwambili pasapezeke bora asalandile chi Baz
Eyaah nkhani njakuti ntchito yomwe akugwilayo anthu tikuyiona pamene acina chimwendo ndi nduna zi zake palibe cipanga iwo nde chifukwa cake
Ndikufuna DDP izakutenge paundunawo umaziwa kungwila ntchito tinakakhala ngati ameneyu zikoli bwezi likuyenda bwino koma muona ena opondeleza amupasa ndalama kuti asiye kuchita zabwinozi.
Komano vitumbiko akugwira nchito kuposa chakwera na ku mcp anayenera kukhara president ndi ameneyu osat mbuzi zinazo zinazo zikungoziwa kutukwana kumanga ndi kuba bas
Ukutima kugwila ntchito
Nyela ndi chibwadwidwe uyu alimbo apitilize kunyendela
Bodza iwenso nduna zanji zomwe zikumuda vitumbiko tchula dzina ka
❤🎉
Uyu ndi munthu woti chakwera adakamusankha kale bwenzi zinthu Zina zili bwino
Vitumbiko wabwera bhooo hvy
Uyuyu amene kusatila Sulaiman tikuyamikila athu otelewo papa chakwer Ana yitha posakha mbumba Kukhala nduna
Great Job a minister God bless you a Malawi azunzika nthawi yaitali
Muthu km amene ndamene angasithe zi2 zopusa zomwe zimachitika ma company
Ipatse moto
2025 akanayimila ameneyu
Nduna iyi ikudziwa chomwe ikuchitazi osati kimagokhala kunyuma ndikumadya ndalama za mphawi
Awawa akufunika kukhale a president unduna wawachepera
Vitumbiko ndi olemera kale,envelop yo azaikamo zingati zomupanga convince?
Uyu akugwila ntchito koma Bola asasiyile pomwepaa
Ndye matindi anduna kapena ai
Vitu ndi mbambande
Mumba pa pick
Or wangamutinkha mwana wakhwithu,wagwire waka ntchito yake
Zofunika
Munthu amene amadana ndichilungamo which means kut iyey ndiwanyengo
Engineer
Kumbali ya kawalazi yokha sanalakwitse 100%
Vitu. moto buuu wandikumbutsa nthawi ya Kamuzu Banda.
President Vitumbiko Mumba
Mulungu ndp aziwadalitsa abwana awawa
😊😊
😂😂😂😂
Pazokhazi wandiwaza mumba
idiot's only will think his bad but anthu akwathu apindula so spot think like idiot's
A mcp onse akanakhala kuti amagwila ntchito bwino chonchi zikana beba koma osati kungokhuta nyemba kamangeni chisale wamwa thobwa ayi kamangeni gangata what is that stupid
Munthu woyipa
Ndani?
Ndani oyipayo
@Bonisiwentamo olembayo
Lnduna izitelo a are aaaah avitumbiko Mulungu awadalise