FRIDAY SPECIAL ON LIMPOPO FM NDI COMRADE NTANYIWA 28 JUNE 2025

แชร์
ฝัง

ความคิดเห็น • 171

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r 4 วันที่ผ่านมา +8

    May these innocent Souls of Late Right Honorable Dr Saulos Klaus Chilima and other 8 Malawians continue resting in eternal Peace

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 4 วันที่ผ่านมา +5

    Munasowatu comrade,wina athawa state house akuifuna tipemphere kwambili anthu anapha aja azimubwelera onse kuchipinda kwa ndi a kasambara omwe

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 3 วันที่ผ่านมา +4

    I will join that fasting zikutipweteka

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 3 วันที่ผ่านมา +3

    Woza Friday comrade ntanyiwa more fireeeeeee the spirit of Chilima still moving muyaluka anthu azipembezo chifukwa cha dyera shame Mulungu akulangeni nonse anthu opanda chisoni

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 3 วันที่ผ่านมา +2

    Tili Pano mdicholinga cha Yehova sangatisiye tikulira achitapo kathu ndithu amenewa alandire zilonda ndithu mabala osapora ayende maliseche azingobwebweta We love you Ntanyiwa ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i 3 วันที่ผ่านมา +3

    We follow you Mr Ntanyiwa Lero simunayimbe nawo kanyimbo kaja mizimu 9 I were pamutu pake pa chalakwe😂😂😂

  • @JohnChiwaya-ym5me
    @JohnChiwaya-ym5me 3 วันที่ผ่านมา +2

    Honestly speaking, a Mtanyiwa mmatiimilira. Myoyo yaanthu ambili omwe tikulilira justice mitima yathu imakhala nchiyembekezo chifukwa cha inu. Keep the 🔥 burning

  • @RiyemaDomybusiness
    @RiyemaDomybusiness 3 วันที่ผ่านมา +4

    You❤❤❤ have to exactly for tell us poor people true god bless you 💕 end keep it up ❤

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 3 วันที่ผ่านมา +4

    Jesus said clergies sit on Moses seat believe whatever they tell you but don't follow them because they are hypocrites Matthew 23

  • @user-zr7wk4oq2x
    @user-zr7wk4oq2x 4 วันที่ผ่านมา +2

    Buddy Ntanyiwa ‼️
    Ulemu wanu bwana
    Keep doing the needful ♥️🔥

  • @aligrayjeo1071
    @aligrayjeo1071 3 วันที่ผ่านมา +3

    Tiuzeni ifeyo Comrade Ntanyiwa tili pambuyo panu ife tili kuno ku South Africa tithana naye akusaka moyo wanuyu

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 3 วันที่ผ่านมา +2

    Wosadandaula tizikupemphelela brother we love you so much ❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤

  • @LiamTennessee
    @LiamTennessee 4 วันที่ผ่านมา +3

    Mmapemphero anthu tisayiwale kupemphaMulungu kuti apengese misala azibusa ansembe ndi wina aliyense amene wadya ndalama kuti imfa ya aChilima isa wululike

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 3 วันที่ผ่านมา +3

    Nkhani yokoma zedi fasting idziyamba nthawi yanji ndipo izintha nthawi yanji tipatseni program

  • @user-oy2yn2bk1l
    @user-oy2yn2bk1l 3 วันที่ผ่านมา +3

    Ngozi yagalimoto anthu amanyenyeka koma ya ndege ai ndithu kungovula ma jacket bas ati afa bwino. Ai zikomo a MCP

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 3 วันที่ผ่านมา +2

    Am waiting for you my brother came with it more fire i ❤❤❤❤❤❤ it

  • @user-gr2vr6yw8b
    @user-gr2vr6yw8b 3 วันที่ผ่านมา +3

    Msamasowe a comrade timadalira inu pachilungamo

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 3 วันที่ผ่านมา +2

    Zoona brother tiyeini tisale kudya choonadi chidziwike

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 3 วันที่ผ่านมา +2

    Osaiwala Amene tikusala kudya tisale ndinyumba momwe

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em 4 วันที่ผ่านมา +1

    Ntanyiwa we're together from fasting, until something happen, Rip SKC and 8 others

  • @ProphetessEzinass-qu4ir
    @ProphetessEzinass-qu4ir 3 วันที่ผ่านมา

    You have my support prayerß job already And God is revange continue to save the people dont sale your grace .God bless u

  • @masterchitabwino898
    @masterchitabwino898 4 วันที่ผ่านมา +2

    People's Power, Don't Take People For Granted

  • @CorencPromise
    @CorencPromise 4 วันที่ผ่านมา +2

    Amene akudana ndiyinu mutu sukuyenda ukubebesa ayise

  • @shuraimuwamama2349
    @shuraimuwamama2349 4 วันที่ผ่านมา +2

    Mvuto kumalawi timangolongolola nthawi nkumatha maiko anzathuwa sangwatero mphamvu zimakhala ndi anthu osati atsogoleri

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 4 วันที่ผ่านมา +1

    " Atampachika pa Mtanda anagawana msalu zake napanga mayere" . Those evil men akudziwa komwe kuli tie,Msapato 😂😂😂😂

  • @YankhoGuza
    @YankhoGuza 4 วันที่ผ่านมา +2

    Dokotalayonso ndopusa amudyesera azinena mawumboni abozawi ayaluka ili ndi dziko awakatha oansi pompano ndithu mulungu wathu ndi wa noyo

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 4 วันที่ผ่านมา +2

    Tipemphelere kuti Chakwera akakhara pampando adziyabwidwa mpaka authawe

  • @user-td6qe4gr6w
    @user-td6qe4gr6w 3 วันที่ผ่านมา +1

    Koma mizimu ya anthu 9 awa mmm itikantha ndithu pangachedwe maka Ambuye tipatseni vumbulutso ndi mzimu wachidziwitso. Its becoming more scarily especially with this issie involving the clergy eish my Mw serious??

  • @MphatsoMwale-it4xd
    @MphatsoMwale-it4xd 3 วันที่ผ่านมา +2

    Athu akuzuzika ku malawi plz tiyeni tisangoonerera

  • @StephanonachipoMakawa
    @StephanonachipoMakawa 3 วันที่ผ่านมา +1

    Kod pa limpopo pano timafuna kudziwa kuti msilikali wa kamudzu balakisi unja zikuti bwanji alimoyo kapena kulibe

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt 3 วันที่ผ่านมา +1

    May God protect you sir!

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 4 วันที่ผ่านมา +1

    Following mwachidwi always......

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 3 วันที่ผ่านมา +1

    Nkhanga izooo!!!!

  • @EllenPhiri-xt8pt
    @EllenPhiri-xt8pt 3 วันที่ผ่านมา +2

    Tiyeni tipempheledi awakantha mulungu awonekela poyela amene anachita chipongwecho ndithu

  • @HajiraMatandika
    @HajiraMatandika 4 วันที่ผ่านมา

    Timakunyadilani Comrade mtanyiwa❤we. Love u

  • @WezzieChimuzi-ek7bk
    @WezzieChimuzi-ek7bk 4 วันที่ผ่านมา

    Takunyadilani Mr Mtanyiwa.... Mulungu wathu ndiwamoyo ndipo ndiwamayankho

  • @SmartJumbe
    @SmartJumbe 4 วันที่ผ่านมา

    This is true radio number one

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 4 วันที่ผ่านมา

    Eish tinakusowa welcome back 🙏

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 3 วันที่ผ่านมา

    God bless you ntanyiwa We're following you

  • @joyahmedjoma4615
    @joyahmedjoma4615 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ndipo live tisara kudya brother allah atiyankha so soon

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6k 4 วันที่ผ่านมา +2

    Kom imfa ya Chilima yosaiwalikatu😭😭 Rest well Legend

    • @mthawisakaunda
      @mthawisakaunda 3 วันที่ผ่านมา

      Ndpo zoopsa 😢

    • @user-td6qe4gr6w
      @user-td6qe4gr6w 3 วันที่ผ่านมา

      Ndipo comrade Ntanyiwa tionjezekepo pa ma prayer petitions po kuti: Mulungu akanthenso onse amene akulandira ndalama ndi cholinga chofuna kubisa chilungamo komanso kuwatseka pakamwa Mulungu wodziwa kubwezera (Psalm 94) atero mdithu.

    • @user-td6qe4gr6w
      @user-td6qe4gr6w 3 วันที่ผ่านมา

      Za mapemphero ndi kusala zakudya. comrade fotokozani bwino bwino nthawi yomasulira fasting imeneyi chifukwa mwangoti 5 days Mon-Fri

  • @RoseChiphiri-ts8jx
    @RoseChiphiri-ts8jx 4 วันที่ผ่านมา

    My everything radio ❤ watching from Israel 😂

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 3 วันที่ผ่านมา

    My fellow Malawians the problem we are currently facing is that we cannot differentiate between the righteous and the hypocrites in churches, mosques,politics,and in all human gatherings

  • @mensuremegrem8330
    @mensuremegrem8330 4 วันที่ผ่านมา +2

    Awalanga ndipo asala pang'ono

  • @GiftManuel-er7yh
    @GiftManuel-er7yh 4 วันที่ผ่านมา +1

    Salute bigy limpopo

  • @GiftPhiri-tt7nn
    @GiftPhiri-tt7nn 3 วันที่ผ่านมา +1

    Nanga lamba wa trauzer ndege ndiyomwe inamasulasoooooo

  • @user-xx4mt8ox8e
    @user-xx4mt8ox8e 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ine ndayamba kale kutsala
    Moti kunyumbaku sindikudya

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 3 วันที่ผ่านมา +2

    After Kenya Malawi get ready

  • @AGNESSNYIRENDA-h1z
    @AGNESSNYIRENDA-h1z 3 วันที่ผ่านมา

    Following you

  • @TressLuka
    @TressLuka 3 วันที่ผ่านมา

    Iwe Mtanyiwa ndikatundu kwambiri. Limpopo ndiyokha radio ya ife 🇲🇼 oxindikira😢😢😢😅

  • @MAFUNSOMOLESI
    @MAFUNSOMOLESI 4 วันที่ผ่านมา

    I love you Mr comrade go ahead

  • @user-tg3bl5ey9v
    @user-tg3bl5ey9v 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mangochi boys tanola kare zida apa tikungodikila pa 10 ndipo munverako

  • @robenallie6985
    @robenallie6985 4 วันที่ผ่านมา

    Number one radio

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe 3 วันที่ผ่านมา

    We proud of guys God bless you

  • @WezzieChimuzi-ek7bk
    @WezzieChimuzi-ek7bk 4 วันที่ผ่านมา +2

    Kodi Ndege ikagwa kumakhalanso kuona nkhope??

    • @user-un6qv6sj3h
      @user-un6qv6sj3h 4 วันที่ผ่านมา +1

      Kkkkkk nanenso kudabwa😊

  • @ZondoChirwa
    @ZondoChirwa 4 วันที่ผ่านมา

    Do your job guy we are proud of you.

  • @SamamaMagone
    @SamamaMagone 3 วันที่ผ่านมา +2

    Lampopo tioseni zoona

  • @mariezorgen7735
    @mariezorgen7735 3 วันที่ผ่านมา +1

    If is rue shame to you Bishops ,,,,bloody money!,!

  • @JohnSanudi-p9f
    @JohnSanudi-p9f 4 วันที่ผ่านมา

    Timakunyadiran antanyiwa❤

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 4 วันที่ผ่านมา

    Mudasowatu boss 💪💪🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 3 วันที่ผ่านมา +1

    Lipopo FM good

  • @nyanguoipa6996
    @nyanguoipa6996 4 วันที่ผ่านมา

    Limpopo fm number one Ulemu wanu big

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 4 วันที่ผ่านมา +1

    Komatu MCP ifa ya chilima mupedza mayo soka mudzimatsa anthu ndalama cholinga wadzelu ndipamene akudxiwa kuti mwapha chilima kuti mupitilile 2025 KKKKK NUTSO ADZIBUTSA MAPHETSA MWANA NDIKUMAPITATSO KOKO PANO ALIYETSE AKUDZIWA KUTI KUKOKOMANA NDI FITI YAFITI CHAKWELA NDE AKAPATSIDWA NDALAMA MAFUMU MABUTSA KAYA ENA AKHALA NDANI KOM ZIWANI NDALAMA YAMAGADZI CHAKWELA 2025 CHAKE PALIBE

  • @NastonVickta
    @NastonVickta 3 วันที่ผ่านมา +1

    Limpopo fm koma iwe wabweraso

  • @Y0hanelLyson
    @Y0hanelLyson 4 วันที่ผ่านมา

    You are one mtanyiwaa

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 3 วันที่ผ่านมา

    Am not fear, am a citizen of Malawi, Malawi is my home country as am home soil i have right of freedom of expression , right to life, so no one can't threat me if am doing right thing, working professionally, same applying to nonsense president Chakwera if you know you're doing right things to Malawians, why most citizens of Malawi were not happy with you? Beware Chakwera, the blood of Chilima and others is on your head you never have a peace in life.

  • @sylviachisama3829
    @sylviachisama3829 3 วันที่ผ่านมา +2

    Sabasaba uja bwanji?

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 3 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂😂Apengedi misala amenewa iyaaa

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 4 วันที่ผ่านมา +1

    chakwera ndi chigawenga ma chende abambo ake ndithu mfiti satana

  • @NelsonMarley-r8l
    @NelsonMarley-r8l 4 วันที่ผ่านมา

    Umaitha iweyo umatuimvetsa kukoma. More fire 16:57

  • @user-oy6dl1pv9e
    @user-oy6dl1pv9e 4 วันที่ผ่านมา

    Following Limpopo
    Fasting baasii titelo ndiithu

  • @IjilanMwalija
    @IjilanMwalija 3 วันที่ผ่านมา +1

    Nanga y we didn't see Ring or helicopter took it 😅😅😅😅😅

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551 3 วันที่ผ่านมา +2

    Mwati a mpingo so konko dollar?????????

  • @OmarMkwela
    @OmarMkwela 4 วันที่ผ่านมา

    Haaa kodi mmabishop omwe akudyya thupi la anthu amene adwalira pangozi ya ndege ku chikangawa ayibo koma ndi my dangerous

  • @reginakamaliza8414
    @reginakamaliza8414 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mulungu wathu sangatisiye tikulila chonchi zanyanya

  • @OsmanBande
    @OsmanBande 4 วันที่ผ่านมา

    Nkanga zaona🎉

  • @crosbyphiri1745
    @crosbyphiri1745 4 วันที่ผ่านมา

    Good prayer points.😢😢

  • @JosephChiyuni-xc9nd
    @JosephChiyuni-xc9nd 4 วันที่ผ่านมา

    Mumatiimirira Mr ulemu wanu

  • @user-hu4gu7op7n
    @user-hu4gu7op7n 4 วันที่ผ่านมา

    Ife amalawi mantha nde ndiosayamba koma tikufatu tilimaso nde lets go guys timange malawi wathu

  • @AyandaJanga-fe7wp
    @AyandaJanga-fe7wp 3 วันที่ผ่านมา

    We are ready brother and we are together

  • @SurprisedAlbatross-up6wb
    @SurprisedAlbatross-up6wb 4 วันที่ผ่านมา

    Mumatipatsa khawatu comradeee

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 3 วันที่ผ่านมา

    Mr Mtanyiwa kunja kwacha chilungamo chimveke timadalira inu mwadzuka bwanji kumenekoooooooooo

  • @user-yh3ys3qn6p
    @user-yh3ys3qn6p 4 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂😂😂 km u umakwana Mr mtayiwa 😊😊😊😊😊

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek 3 วันที่ผ่านมา +1

    Ife kuno ku Capetown tili nanu PA 10 pano
    Chakwera atupe mutu

  • @user-gb2sl1jt4s
    @user-gb2sl1jt4s 3 วันที่ผ่านมา

    Bwana mulungu akutetrdzan.ndithu

  • @HarryNtanga
    @HarryNtanga 4 วันที่ผ่านมา

    Osaopa, osafooka mpaka zofuna zathu zikwanilisidwe kumanga malawi 🇲🇼 wathu

  • @AmosBandula-up4yb
    @AmosBandula-up4yb 4 วันที่ผ่านมา

    Number 1 mumatiimilila

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 3 วันที่ผ่านมา

    Mabishop Misa yoseija mwalandila ndrama

  • @AyandaJanga-fe7wp
    @AyandaJanga-fe7wp 3 วันที่ผ่านมา +1

    Amen

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 วันที่ผ่านมา

    Ayambe ku pita ma activists wonse apite cause Kupanga support zopusazo

  • @jacksonkamoto6959
    @jacksonkamoto6959 3 วันที่ผ่านมา

    Zibonga zituluka pa 10 tiri chete kayeee...

  • @GrivinSauka
    @GrivinSauka 4 วันที่ผ่านมา +2

    You have nothing to tell Malawians apart from your empty vendetta. Kulibe izoooooooo. Forget about all those idiots you are mentioning. Failed politicians.

  • @user-td6qe4gr6w
    @user-td6qe4gr6w 3 วันที่ผ่านมา

    Ndipo kungoti dziko lathu transparency ma nkhani ngati izi imasowa. If we are to calculate imfa ya ngoziyi yapangitsa dziko to spend billions of kwacha right away from ndege which beyond repair, all those officers who were involved in to transfer dead bodies to where the Zambian plane collected and flew to LLs. All those press briefing, private mortuary charges, coffins/caskets, all those vehicles to Church, area 12, parliament, BNS and finally to Nsipe. Honestly guys even the venue ku Nsipe and other related processes.

  • @JamesMadina-uv6xe
    @JamesMadina-uv6xe 4 วันที่ผ่านมา +1

    Naye bakili muluxi waying'alula tu ku

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 3 วันที่ผ่านมา

    A Malawi tikugulitsa ufulu ndi ndalama imagine to the extent yoti mpaka mipingo nkumakalandira ndalama Kamba ka imfa ya munthu this is very shameful!!!!!!

  • @user-td6qe4gr6w
    @user-td6qe4gr6w 3 วันที่ผ่านมา

    Komanso kwa omwe akulandira ndalamazi chonde tiziganizile kuti imfa yi ikanatichitikira ife tingamamve bwanji kumva kuti ena akupezerapo cholowa?

  • @Jamesmwale-iz4ri
    @Jamesmwale-iz4ri 4 วันที่ผ่านมา

    Ine ndikumakutsatilan zedi

  • @user-td6qe4gr6w
    @user-td6qe4gr6w 3 วันที่ผ่านมา

    Additionally the Germany clue, trabsport, hotel charges, daily operstions etc, yet we have trillions of unpaid debt, are we serious? Chenicheni a malawi fe tikufuna chani ngati dziko makamaka atsogoleri? Mulungu tipatseni mavumbulutso otherwise we are moving backward more faster than the opposite direction.

  • @ElasonAimon
    @ElasonAimon 3 วันที่ผ่านมา +1

    Mulungu atithandizedi pazimenezi

  • @Jamesmwale-iz4ri
    @Jamesmwale-iz4ri 3 วันที่ผ่านมา +1

    Tikumva