imfa ya munthu olungama pamaso pa Yehova pamakhara chimwemwe zilibwino indeed waxy mzimu wa Yehova ukuyankhura iye wangokhara chotengera chake may His soul rest in internal peace 😭😭😭
Ndikukumbuka mu ulaliki wina wake bishop kapenga ananena kuti ngati situation ndiyoti sungayisithe no matter what, osalira just say zikomo ambuye. Pachifukwa ichi nane ndikuti zili bwino ndi mzimu wawo for God has relieved him from all his pains🙏
Munthu akamwalira kulira kumatanthauza kusowa chiyembekezo pamene mau ake a Mulengi amati tisalire pakuti mu zonse tidziti zilibwino nde mukati speech yolakwika nde kuti chani. Lolani akulimbika mtima akhale akulimbika mtima pakuti ndi mawu ndipo mwa mawu tidzachuta mwa mawu. Say Amen/Ameen
I personally support waxy. All is well indeed. It reminded me of my late mum. She said all is well and the future is so bright. Kwa okhulupirirafe zilibwino ndithu. Chauta salakwitsa. The lapture is here and Go's is taking his righteous ones. Go well bishop .
He got broken... He wrote a status he was comforted that he should be strong since the father is in a better place Now he is strong anthu muyakhulisaso Mumtima akuliratu munthuyu
He has to say so,, there is no way kut azikhala akudandaula yet zinthunzo zachitika kale komaso sangathe kuzibweza pat. Mmalo moti azingodandaula wasankha kusangalala that's a good choice or adakayankhula zodandaula zidakasintha chan? Umenewo nde umunawo mesa,
Koma ndiye Kuli mixed bag of comments,... Waxy this Waxy that,... aMalawi musiyeni mwana, walimba mtima ndi chiyembekezo kuti bambo ake ali malo abwino opumula ndi Yesu wawo ndipo palibe chodandaula,... Ndiye mukuti chani anthu "abwino" komanso osunga "chikhalidwe" chachiMalawi inu?? Pena ngati ndinene kuti dikirani abambo anu akazamwalira muzayankhule speech yanu yabwinoyo,....koma poti imfa si yabwinonso. So whatever, Rest well Bishop Kapenga. We knew as man of God and we're sure to God your soul has returned. Rest Bishop rest🕊️🕊️
Of course am satisfied with the speech it seems unakonzeka ngati ukupita ku show.i remember you wrote kuti tiyeni mawa tikakumane pa Robins Park ndikaimba nyimbo in other way its not fitting
Mmmm waxy Kay Kuno ndi kumalawi ndye yaaa kumbali Ina it's ok kuti zilibwino koma another side this speech is useless to me when you grow up that's when you will realize that l made silly speech RIP Mr kapenga
Komatu for sure now irealize rhst crying during someone's daeth is for us poor imagine what is this speech 😭😭😭😭😭💔💔end with sure Anyway rest well pastor kapenga
imfa ya munthu olungama pamaso pa Yehova pamakhara chimwemwe zilibwino indeed
waxy mzimu wa Yehova ukuyankhura iye wangokhara chotengera chake
may His soul rest in internal peace 😭😭😭
Ndikukumbuka mu ulaliki wina wake bishop kapenga ananena kuti ngati situation ndiyoti sungayisithe no matter what, osalira just say zikomo ambuye.
Pachifukwa ichi nane ndikuti zili bwino ndi mzimu wawo for God has relieved him from all his pains🙏
Munthu akamwalira kulira kumatanthauza kusowa chiyembekezo pamene mau ake a Mulengi amati tisalire pakuti mu zonse tidziti zilibwino nde mukati speech yolakwika nde kuti chani. Lolani akulimbika mtima akhale akulimbika mtima pakuti ndi mawu ndipo mwa mawu tidzachuta mwa mawu. Say Amen/Ameen
Ifa ya wamuthu olungama kumwamba kuli chimwemwe mwAna wazelu kwabassi ndiwochepa agazindikile mawu wayakhula mwanayu Kwa amene amakhululupila mulungu wava tathsuzo lake amen
Ndipo imfa ya munthu oyera mtima imakhala yokoma chifukwa amakhala akudziwa za komwe akupita
I personally support waxy. All is well indeed. It reminded me of my late mum. She said all is well and the future is so bright. Kwa okhulupirirafe zilibwino ndithu. Chauta salakwitsa. The lapture is here and Go's is taking his righteous ones. Go well bishop .
Beautiful speech for a believer. Celebrating a life well lived.
He got broken... He wrote a status he was comforted that he should be strong since the father is in a better place
Now he is strong anthu muyakhulisaso
Mumtima akuliratu munthuyu
Ulemu wanu a waxy kay 🎉🎉🎉🎉🎉
Zilibwino may God be with him
Chomwe walakwitsa Waxy Kay ndi chani anthu inu? Kapena simudziwa mau simudawelenge?
Koma mwana wakondwelatu 😂😂😂
Zotindipamalilo wayiwala yoh mphamvu ziko likulowa bola
He has to say so,, there is no way kut azikhala akudandaula yet zinthunzo zachitika kale komaso sangathe kuzibweza pat. Mmalo moti azingodandaula wasankha kusangalala that's a good choice or adakayankhula zodandaula zidakasintha chan? Umenewo nde umunawo mesa,
Waxy akunena zoona, mau a munthu okhulupilira ndi oti zilibwino. Abale amzanga munthu akamwalira sinthawi yoti ife tizilira ndi nthawi yosangalala chifukwa chani ndikuyankhula choncho, chisanzo munthu akamagwira ntchito kaya ndi pa company kaya m'boma amayembekezera kuti mwezi ukatha akuyenera kukalandira salary, ndiye funso nali, ndindani amene amapita kokalandira salary akulira tipeza kuti palibe wina aliyense amakhala osangalara kuti lero tikadyera nyama, ndi chimozimozi inu ndi ine mulungu anatisankha ndikutisiya pano pa dziko lampasi cholinga chimene anatisiila pa dziko la pansi ndi chani tizimugwadira nthawi ndi nthawi, ndiye tamugwadira mulungu, mwini wake emweyo yemwe timamutumikira uja watiitana tamwalira ndicholinga choti akatipase malipiro pa ntchito yomwe iye anatipasa takhala tikumugwilira tidakali ndi moyo abale amzanga sinthawi yomalira imene ija ayi ndinthawi yotchulusa kupempha kwa mulungu kumupemphelera m'bale wathu kuti ngati anali ochita ntchito zabwino mulungu amuonjezere zabwino zochuluka pa ntchito yomwe iye anali kugwira adakali ndi moyo komanso ngati anali ochita ntchito pena zoipa mulungu asachulukise kuyang'ana zoipa zake Ameen
Speech iyi ndiyofunika azungu koma ife tiziti mwatilawula😢
Mauabwino kwamunthu olungama❤❤
Indeed zili bwino aliyese azafa komano kuluza munthu sichithu chophweka nde kumankhala makolo ako
My grandma said when someone passed away within two days ,,,,,,, umawona ngat zocheza koma dikila pathe masiku nde akut zilibwino ??? Pamenepa😢
Zoonadi.....Zili bwino mwa Yesu khristu.....
zili bwino..,>all is well waxy
I'm very sorry 😢Your highness young king. If you want to talk ' I'm here at any time
Zibwíno 🙏🏾
Mauabwino kwamunthu olungama❤❤
0:11
Osamamuchemerera mfanayu ndikape chisiru paumunthu speech umatulusa malingana ndimaro ache awa anali bambo ake osati ngt kanali kushow koziwonesera kt kaya akazi akafire zachamba
Zoonad man am gree with you
Ndipo ndikape
Today's children at their parents funeral leaves alot of questions really
Mmhu nanu
Mwana ulimba mtima
RIP Pastor 😭 Anthu awa amkavana
Mwana wamuna azikhara olimba mtima choncho waxy mbiri yako yabwno umakhara bwno ndi bambo ako ambuye akuze malire amoyo wako ndi abale ako😢
Sizilibwino ndizolilitsa kwambili 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Yesu analira pa maliro a Lazaro
Powerful
Chitsiru chamwana ,nde chojowera-jowera ndichani .ngati zili bwino osangoyankhula bwino bwino kupereka ulemu kwa anthu ena bwanji.kufuna kutchuka ndi uchitsiru udzazindikira bwino patsogolo
Koma ndiye Kuli mixed bag of comments,... Waxy this Waxy that,... aMalawi musiyeni mwana, walimba mtima ndi chiyembekezo kuti bambo ake ali malo abwino opumula ndi Yesu wawo ndipo palibe chodandaula,... Ndiye mukuti chani anthu "abwino" komanso osunga "chikhalidwe" chachiMalawi inu??
Pena ngati ndinene kuti dikirani abambo anu akazamwalira muzayankhule speech yanu yabwinoyo,....koma poti imfa si yabwinonso. So whatever,
Rest well Bishop Kapenga. We knew as man of God and we're sure to God your soul has returned. Rest Bishop rest🕊️🕊️
❤❤❤❤❤❤
Muthu akamwarila, timarila pa nthawi imeneyoyo, ndee waxy kay sanalakwitse moti speech yake ili bho ndithu.
RIP Munthu wakulu Kapenga we shall miss u
May His Soul Rest in Peace 😢
Kaya mwanayu sanasute koma
Ndalama unadya zacosoma zja nyimbo zake ndizit unaimba?????😩😩😩😩
zabodzazo zosamvekazo Mulunguyo anamuuzira kuti? pamaliro sitchukira. tisamaseweretse dzina la Mulungu. kulowetsa chibwana pamaliro a mtumiki wamulungu.
Some of the tribes in Zim they celebrate when they lose someone zili bwino akapumule ali ndi Yesu wao
😢 what a man up
Km ine kaya ndi chimodzichi km speech yi sinandivekere mwaumunthu
Mau abwino kwa munthu olungam
Zowonadi ziribwino kwaiwo kwantha kwatsara kwaife
Ife ndi a Malawi, izi nzachizungu ndipo naaa ine sindingayankhule chonchi ali oti ndi bambo anga.
Azibambo nthawi zambili amakhala olimba mtim and uyuso panja mean oyamba ayenela kukhala strong komas tiyamike kut bambo ake amwalila waxy atatembenuka mtima komas kwaimayife zovuta kom kwa mamun ngt uyu akudziwa chomwe akuchita komas mwa okhulipilila izi zosavuta ngt munawon live yadzulo mayi ake okhala akaz awo anayimba nyimbo xa phamvuso coz ndi anthu okhulupilila and akudziwa kut akuyakhula mulungu wawo
Sitinazolowele spech ngati izi kuno kwathu
Wakhutu la uximu wanva
Kwa munthu oti amaziwa za kumwamba mwana wayakhura zomwe Mulungu amatilimbikisa pamavuto or pa Mtender tiziti zili bwno
Ku show kapena maliro
Of course am satisfied with the speech it seems unakonzeka ngati ukupita
ku show.i remember you wrote kuti tiyeni mawa tikakumane pa Robins Park ndikaimba nyimbo in other way its not fitting
Wavala mzimuwamji mwanau
Emen
Rip bishop kapenga 😢
A malawi uziwa kurangiza mwana warakwa chani kod simuziwa kuti muthu akafa sibwino kurira mokweza ndemumatu iyi azirira
Owooo chabwino
ubusa uli mwa iwe bra
Eeeeee waxy umatha kuyankhura
Strange
Guys mwanai watani kodi
Paribe muthu amasangalala pa ifa ai .
Uyu wandikaikisa chabwino R.I.P pastor kapenga
Chakaikitsa pamenepo ndichani?? Akuyenera kutero kumene chifukwaso zili mmalemba Mulungu ananena kuti kwaikika kwamunthu kufa,,chamoyo chilichonse chikuyembekeza imfa Ambuye alemekezeke chifukwa wakwanilitsa mau ake,,osati zanuzo apa
Rlp pastel
Iyi ndi lmfa osapanga zibwana kawonesa picture yanji kwa azukulu amipingo pamwambo wamaliro kakuti sharp wachani zachamba
💔🕊
Muzidyatu bwino ganjayo
Rest well Bishop Kapenga
Waxy ndi nfana olimba mwana wamamuna adzitelo
There is nothing wrong jst that we as malawians have poor and shallow minds
Dadas
Waxy akanakhala ngati chija chinthubidwa cha chilima chija akanag'alura
😂😂😂😂
Eish guys 😂😂😂😂😂
Zilibwino
Rest in peace bishop kapenga
Mzimu wawo ukautse mumtendere ngati anachita bwino kudziko lapansi pakuti ntchito zako munthu zimasagana nawe
Kuyankhula kotani uku, mwana wachibwana
😭
Young man where hv u taken the energy to make this non African speech on a day like this?
I think this man waxy mutu wako sumakoka,ngati chili chamba mmmm.are sure bambo ako apita you can say this nonsense sure?
This is not a fitting speech for the day your father passed away 😪😪
Be serious man, waxy mwaonetsa maturity, zili bwino
Sonotu anthu odziwa mawu zimaaiyana ndi osadziwa mau zili bwino basi ambuye walora
Mmmm waxy Kay Kuno ndi kumalawi ndye yaaa kumbali Ina it's ok kuti zilibwino koma another side this speech is useless to me when you grow up that's when you will realize that l made silly speech RIP Mr kapenga
Sorry rnp
Bro thought he killed
Komatu for sure now irealize rhst crying during someone's daeth is for us poor imagine what is this speech 😭😭😭😭😭💔💔end with sure
Anyway rest well pastor kapenga