Born Kalindo Iyiyi sanadikire kuti kuche akuti kuli yemwe wamupereka Kaliati uja wa UTM

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 170

  • @MalawianCamera
    @MalawianCamera  2 วันที่ผ่านมา +16

    Ndimangoti mwagonatu guys 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
    M'makwana inuyo ndi nambala wani😂

    • @MonalisaMwale-c5k
      @MonalisaMwale-c5k 2 วันที่ผ่านมา +3

      Kugona kulibe

    • @patrickmacheso5062
      @patrickmacheso5062 2 วันที่ผ่านมา +2

      @@MalawianCamera Tilipo ndithu,, tulo sitikubwera malingana ndi zomwe akuchita Mr Chikangawa.

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 วันที่ผ่านมา +1

      @@MonalisaMwale-c5k 👌🎉

    • @MalawianCamera
      @MalawianCamera  2 วันที่ผ่านมา +1

      @@patrickmacheso5062 Eeeee zoonadi man zaukape

    • @LaylaPhiriMuhammad
      @LaylaPhiriMuhammad 2 วันที่ผ่านมา +2

      Olo kugonako mkumayambila Pati bro? 😂

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 2 วันที่ผ่านมา +8

    That's the voice of our President Dr Bon Kalindo the DC,,, Tiyeni tiyeni tonse pamodzi tikapange Support Mayi Kaliati,, DPP,, AFORD,, UDF,, UTM plus other parties let's work together.

    • @OdettaLowrence
      @OdettaLowrence 2 วันที่ผ่านมา

      UDF,AFORD ili mu mcp, ngozi

    • @patrickmacheso5062
      @patrickmacheso5062 2 วันที่ผ่านมา

      @@OdettaLowrence Never,, never and never again MCP.

  • @MariarosaMandawala
    @MariarosaMandawala 3 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mabishop Mulungu akugwiritseni ntchito kuombola amalawi. Munathaza kusintha one party system kubwera multiparty system ndinuyo. Musakhale chete, God is with you.
    God bless you ma Bishop athu.

  • @SophieKabango-b7p
    @SophieKabango-b7p 2 วันที่ผ่านมา +3

    The RC Priests, pliz take action, MW needs your quick action to force the govt to stop immediately from leading us

    • @HarrisonMwanga-xy4sc
      @HarrisonMwanga-xy4sc 2 วันที่ผ่านมา

      Nthawi yakwana,yoti mcp iziwe mu ulamulilo wa democracy sikotsewelela,si one panty system.anthu, kofunika atuluke,mwela yonse go koko

  • @MADALITSOMISHEC
    @MADALITSOMISHEC 2 วันที่ผ่านมา +7

    Manganya akufuna Abe chipani apte nacho ku MCP

  • @JogaJoseph
    @JogaJoseph 2 วันที่ผ่านมา +8

    Koma mcp yafikapotu Mpakana kumanga mzimayiii 😢😢 but let GOD to be GOD Eksodo 14vs14 powerful vs Amen😢😢😢

    • @chancychikoko-ns5nl
      @chancychikoko-ns5nl วันที่ผ่านมา

      Mvoto Bakili tv ikutichedwetsa ku Turkey zimai anatenga gun ndi ndikukapha anthu

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 2 วันที่ผ่านมา +5

    Ndipo Anthu tulukani ndithu zisanafike ❤️❤️❤️❤️❤️❤️

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 2 วันที่ผ่านมา

    Akweni don't worry about it, God is great, tili nanu mama 💪💪💪💪

  • @ChristinaMdeza
    @ChristinaMdeza 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kom mavuto kwabas akuganiza bwanji chakwera alipamenepo chifukwa cha mai kaliyati wo leo kumawapanga chipongwe chotelo iye chakwerayo anapha a chilima bwanji?a police akewo osamanga, moses uja anapha watika bwanji osamanga chomangira zimayi ndi chani chani make make inu, anthu oyipa inu? we love you Bon Kalindo❤

  • @ChikuCharlie-w5f
    @ChikuCharlie-w5f 2 วันที่ผ่านมา +3

    Born Kalindo the DC mawa ndodo ituluke nthawi yakwana yokha💪💪

  • @manzyhetekele8697
    @manzyhetekele8697 2 วันที่ผ่านมา +1

    The only last man to stand we have the DC u are the best keep it up

  • @MosesBanda-h4x
    @MosesBanda-h4x 2 วันที่ผ่านมา +3

    Catholic Bishops & churches clerges yesetsani kut khalidwe loti tibwerere ku one party state tisabwerere. Yetsetsani posalola kut tisabwerere ku Egypt Kuja kut tizikaphula njerwa zamoto

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 2 วันที่ผ่านมา

    Manganya mbolo yako, umve👊👊👊👊 Mr Kalindo more fireeeeee DC

  • @SahilluYusuf-sk7es
    @SahilluYusuf-sk7es 2 วันที่ผ่านมา +4

    Chikangawa chakwera ndi manganya mayikolo usiiii akufuna ataphedwa agalu amenewa

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ndiye Patricia kaliyatiyo ndindani iyeyo lamulo silimaona khope Andale akuzolowera kwambiri amaona ngati dziko ili ndilamawo.komaso Mary chilima musamupangise Kuti asauke osamukakamiza zandale zanuzo zanuzo

  • @AlinafeMtungama
    @AlinafeMtungama 2 วันที่ผ่านมา

    Bwana ulemu wanu mwandilakhulira chilungamo ngakhale chilungamo ndi mwano ❤

  • @dalitson3558
    @dalitson3558 2 วันที่ผ่านมา +2

    Mayi Kaliati ndi munthu olimba mtima we will vote for her

  • @LaswellSakala-ks6fx
    @LaswellSakala-ks6fx 2 วันที่ผ่านมา +1

    Koma akufuna nkhondo chakwela nd usi please please please tulukani mawa kumenya ndithu osawopa zangolakwika enafe tilikutali zandinyasa kwambiy😢

  • @StanleyMunthali-s1d
    @StanleyMunthali-s1d 2 วันที่ผ่านมา +1

    Amalawi simunati ! Tough time is lying ahead .

  • @MartinLungu-z1h
    @MartinLungu-z1h 2 วันที่ผ่านมา

    Akalindo Pena chilungamo ndikuona ngati chikusowa Pena ndindale izi muphana zinazi zotumidwa izi politic iyiiii

  • @Johnybegood260
    @Johnybegood260 2 วันที่ผ่านมา +1

    Trust is a luxury you cant aford betrayal is something you cant ignore

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 วันที่ผ่านมา

    Akuyambitsa zonsezi ndi manganya
    Malawi kuyambika mademo from no where

  • @RaphaelKatimba
    @RaphaelKatimba 2 วันที่ผ่านมา +2

    Manganya achotsedwe ku UTM chifukwa ndi kazitape munthu oipa kwambili ndipo ndi mfiti. Kamunthu kaja kangofupika koma ndi oipa kwambili. ndikupempheni a Malawi 🇲🇼 ma demonstration aja ayambike lero. osadikilanso ndipo ineyo ndikanakhala mfiti ndikanamulodza Manganya ndi Chakwela. Koma osadandaula anthu amenewa atsala ndi nthawi yochepa kuti afe. Ndipo anthu amenewa adzafa ngati nkhuku za chitopa. let's wait and see and God he watching everything. God is God. and God is not Chakwela and Manganya. and let's pray all Malawians for madam Patricia Kaliyati.

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 2 วันที่ผ่านมา +2

    Aaaaaaaa Bon aaaaa ndi 1 amaona patari yooooh mumakwana mumatiimilira ndithu ulemu wanu 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @andreambewe1851
    @andreambewe1851 2 วันที่ผ่านมา +3

    Respect the DC

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi anyapapi inu mukumukakamiza mayi Chilima kundale chifukwa chiyani mukufuna mudzamubele`compasation yake eti. Zipani zakumabanjazi zikukakamiza mayi Chilima kuzolowera kusiyirana ma udindo achimwene apapansotu akukonzekera kusiyira ana awo chipanichi akukakamira akudikira kuti ana akwane zaka 35.
    Tikanena za Kaliati ngati pali umboni okwanira kuti waphwanya malamulo adziko amangidwe chifukwa munthu ukakhala wandale sindiye kuti ali pamwamba pa lamulo ayi.

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 2 วันที่ผ่านมา +2

    Anthu atuluka!!!! Ganyu wa lero ali pa lingazi😂😂😂😂😂😂

  • @ramseymavuto3546
    @ramseymavuto3546 2 วันที่ผ่านมา +2

    Tulo silingabwere kweni Ali pa cement. Mpakana kuche. Akweni must be free

  • @JaneBanda-ht4ve
    @JaneBanda-ht4ve 2 วันที่ผ่านมา +2

    A police ali ndi umboni ogwilika, Patricia Kaliati ndi anzake anakonza chiwembu choti aphe president wa dziko, ndipo pali VN imene Patricia akulankhulamo zoophya. Azinzake a Patricia atamva kuti wamangidwa iwo athawa. Nkhani ili lero tisathe mau tiyeni timve zomwe Kaliati wamangidwila

    • @JudithKatungwe
      @JudithKatungwe 2 วันที่ผ่านมา

      Mulungu alipo ndipo salora

    • @mustafamakwinja2428
      @mustafamakwinja2428 2 วันที่ผ่านมา

      Choka iwe this is propaganda

    • @InnocentMakungwa
      @InnocentMakungwa 2 วันที่ผ่านมา

      Osaperekera umboni zaathu anafa kuchikangaw 9 osalakwa aja bwanj? Imfa ya pilot ija imandipweteka kwambiri,lero ukupangira umboni zoputsa?

    • @CharityMhone-uk9ym
      @CharityMhone-uk9ym 2 วันที่ผ่านมา

      Bwanji osatulutsa VN yo kt aMalawi akhulupilire kt amafunad kupha chikangawa...

    • @JaneBanda-ht4ve
      @JaneBanda-ht4ve 2 วันที่ผ่านมา

      @@CharityMhone-uk9ym pompano mumva, sizobisatu izi

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 2 วันที่ผ่านมา

    Ambuye mulowelele mu nyengo imenei kt patricia atuluke ndife olira azimai anzake chachtika ndi chian?

  • @marthaphiri3600
    @marthaphiri3600 2 วันที่ผ่านมา +4

    You can't even guess to say who is behind this. A father her daughter is involved in a road accident and is in hospital, who can be the first person to run to the hospital to see her? Imwee, manganya alikuti?

  • @SahilluYusuf-sk7es
    @SahilluYusuf-sk7es 2 วันที่ผ่านมา +1

    Michael usi ndiwakupha ,ndiyemwe anapeleke chilima kut aphedwe leromso ndi izi afuna out aphe kaliat kmano sizitheka ndthuuu

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 2 วันที่ผ่านมา +1

    Koma iwe chakwela uliko hmmmm manganya iwe usi ai zikomo MULUNGU AKUWONA ZOSEZI M'MALAWI.......

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon 2 วันที่ผ่านมา +2

    Lero sitigona pokhapokha atimasulire ndipo iwe manganya panyero pako sungawine

  • @maggienyirendah2507
    @maggienyirendah2507 2 วันที่ผ่านมา

    Please tingwilane manja tonse a Malawi ndi ena onse tiyeni tiyeni

  • @mwayiwawontawanga3969
    @mwayiwawontawanga3969 2 วันที่ผ่านมา

    Ulemu wanu Mr bon kalindo the DC

  • @DanielChipasula
    @DanielChipasula 2 วันที่ผ่านมา +1

    PALIBE ZA ONE PARTY STATE. MALANKHULIDWE ATHU OGOLANKHULAPO NANGA WOSABADWA KWA MUNTHU WA MZIMU... TISIYE. PALIBE KUMANGIDWA MUNTHU WOSACHIMWA . UCHIMWA KWA INEYO , INUYO SIMUNGANDILANDITSE . OSAPANGA MIRANDU POPANDA MIRANDU. NGATI SITIKUDZIWA IFEYO TISAVUTIKE NDI ZINTHU A MZIPANI IZOZO. ZONYOZANANZI NDICHO VHIFUKWA CHAKE TIMAGONYOZANA MOSANGANIZIRA IZO TIKULANKHULAZI. KUGULITSIDWA KWA MALAWI WINA YEKHA SANGALIGULITSE. KULIMBIKIRA POPANDA MTUNDA .. UMADZINYUMWA... AZAKO ATAKUSIYA MMALELE. TIYENI TIBVETSERE MWA CHIDWI IZO ACHIMWA A MAI ..KWENI KALIYATI. INUNSO MUNGAGWE MOMO.. Ati vhifukwa cha Democrancy... Ai Ai ... Need to be responsible citizens of Malawi Nation 🇲🇼💺🎓

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 2 วันที่ผ่านมา

    Manganya wapereka kaliati, machende aku usi

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 2 วันที่ผ่านมา +1

    Wasangalala tsopano iweyo Michael usi chitsiru cha munthu garu iweyo Michael usi munthu wakupha iweyo

  • @NafeAlie
    @NafeAlie 17 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndipo chakwera iwe ulibe zelu mpaka kufika pompo ndi manganha

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 2 วันที่ผ่านมา

    Iweyo kalindo ndiwe ndani kape weniweni iwe amalawi sitikuona cholakwika Ife sitituluka

  • @MableMmera
    @MableMmera 2 วันที่ผ่านมา

    Let love lead Lord have mercy

  • @AyamiMustafa
    @AyamiMustafa 2 วันที่ผ่านมา +1

    😂😂😂Koma akalindo ine paka ndukanika kugona kimangotseka paka apule chisapato chachithali ngati mulamba ine ndilimbuyo mwanumo vote ya ine dpp batsi ndimava kukoma mukamawuza chilungamo agalu amenewa ndipo ndiye afika ponyatsa kwambili

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv 2 วันที่ผ่านมา

    The DC anakoza ndipo live wokupanga chipogwe ndinasi wako or wodya naye Mbale imodzi km MULUNGU simwana

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 วันที่ผ่านมา

    Born kalindo umanena ngakhale chilima mumamuudza inu amanganya nyini yamanu plus yr boss

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym 2 วันที่ผ่านมา

    Akalindo ndmamva kukoma mzoyankhula zanu koma zomkakamiza mary chilima kt ayendetse chipani izo ayi munthu analuza mwamuna wake chifukwa cha ndale nde mphamvu yopitiliza kupanga ndalezo azitenga kt...izo ayi zitsiyen

  • @BenedictChikaoneka
    @BenedictChikaoneka 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi andale akaswa lamulo asamamangidwe?

  • @DanielGanizani-h8r
    @DanielGanizani-h8r 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi Mary Chilima Ali kuti?anthu ayambila kumuuza kuti abwere atenge chipani kapena akulangizidwa ndi anthu ogulidwa?musafike pokuganizilaniso zosayenela amai,zukani.

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 2 วันที่ผ่านมา

    MCP manyazi mulibe .mwapha chilima panoso mukufunaso kupha kaliati?

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 2 วันที่ผ่านมา

    Kongolesi yayaka moto....ngati mmene inayakira 1991/92 kumalipilitsa card azimai amimba..... nthawi yatha pakilani!

  • @CathrenMuleso
    @CathrenMuleso 2 วันที่ผ่านมา +2

    Ino ndi thawi amalawi tidzuke tsopano

  • @petermajor-mb2rb
    @petermajor-mb2rb 2 วันที่ผ่านมา

    Koma 2025 tikuwachotsa mavoti Ali Mwa anthu akulu amenewa atikwana kwambili

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym 2 วันที่ผ่านมา

    Kamanganya chaka chino ndekakutizunguza mitu anthufe wapha chilima pompano..anthu akadali ndi mafutso osayanhidwa lero akupereka kaliati mmmma ka satana aka😮😮😮

  • @misheckmhango2053
    @misheckmhango2053 2 วันที่ผ่านมา

    Sitikufuna mau anu koma chimene a police anene chimene a mmangira. Tidziwe choonadi chifukwa palibe Ali pa mwambapa pa lamulo.

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 2 วันที่ผ่านมา +1

    Za ziii mmalo mokafuna chakudya cha ana
    Anu bizy kukapanga sungar wa wina aaa za ukape

  • @fanwelljusitin6087
    @fanwelljusitin6087 2 วันที่ผ่านมา

    Manganya machede ake mbudzi yamuthu sangakhale president wa utm galu wachabe iwe

  • @EyasuDegu-ou7jo
    @EyasuDegu-ou7jo 2 วันที่ผ่านมา +3

    Iwe amene akunyoza mr DC kanyere

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 2 วันที่ผ่านมา

    Ubwinoo wake munkatiuza tivotere MCP, ndipo tinaivotera ndipo tiivoteranso.

  • @LeonardJere-r5y
    @LeonardJere-r5y 2 วันที่ผ่านมา

    Mcp ndichipani choyipa kwambiri zowona mukumanga akweni amene anakumenyerani kampeni kuti milomo yanuyo iziwoneka ngati aswiswiri anthu inu mutimpha tose mumalawi muno

  • @ChristopherKabanga
    @ChristopherKabanga 2 วันที่ผ่านมา

    ukati tiyeni ku 18 tikatani mbuli yachabe chabe lwe unali muselo ndani adamema anthu kuti tiyeni tiyambe kutukwana ngat mwana

  • @sarahmphande6108
    @sarahmphande6108 2 วันที่ผ่านมา

    Enemy within ndi ka Manganya nkhavumbwa ukongwa

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 วันที่ผ่านมา

    MCP ndi ufiti weniweni. Cholinga cha MCP ndikufufuta UTM chifukwa UTM ili my genZ koma MCP ili mu gen D=death.

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 2 วันที่ผ่านมา

    UMAKWANA KALINDO MWANA OOSYA KWAMBILI

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu 2 วันที่ผ่านมา

    Mai chilima pls tamvan muliko

  • @FelixGambiza-fp7tn
    @FelixGambiza-fp7tn 2 วันที่ผ่านมา

    Phuma lo. Vote at tufuna change ndimeneyo osalila tikhaula sitinati

  • @BrandinaMphuka
    @BrandinaMphuka 2 วันที่ผ่านมา

    The DC mwana oopysa kwambiri kkkkk makwana

  • @ShalonwaGasper
    @ShalonwaGasper 2 วันที่ผ่านมา +2

    Manganya tsanachenjere bwino

  • @AmosiChauluka
    @AmosiChauluka 2 วันที่ผ่านมา +2

    Tigonabwanji atimangira mayathu?😂😂

  • @GreyMwanyimbo
    @GreyMwanyimbo 2 วันที่ผ่านมา

    Odya chitedze pitani ku lingadzi ife tupita kokasaka ufa

  • @MACKDBandah
    @MACKDBandah 2 วันที่ผ่านมา +1

    Boma ili eeeee latikwana mawa tili komweko MCP muva manyi agalu inu

  • @SahilluYusuf-sk7es
    @SahilluYusuf-sk7es 2 วันที่ผ่านมา +2

    Uyuyu sakufunikira ku UTM achoke Michael usi sitikumufuna ku UTM

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 2 วันที่ผ่านมา

    Kodi bas Tabwereradi Ku one party???

  • @RobertChikawonda
    @RobertChikawonda 2 วันที่ผ่านมา

    Kkkk mulungu wake uti a DC adakuuzaniyo kkkk

  • @shakilasaid705
    @shakilasaid705 2 วันที่ผ่านมา

    Nthawi ndi kachitsilu lets wait

  • @TaniaMphalumo
    @TaniaMphalumo 2 วันที่ผ่านมา

    Komaso iye nayeso mayi chilima osamva mose muja sangazukeko zona

  • @NdemboBrothersAdam
    @NdemboBrothersAdam 2 วันที่ผ่านมา

    DC ndodo ija ikufunika sopano musachedwe

  • @BlessingWa-Mataya
    @BlessingWa-Mataya 2 วันที่ผ่านมา

    Zuwonesa kuti Maganya is an enemy from within.

  • @razaqrealkay203
    @razaqrealkay203 2 วันที่ผ่านมา +1

    Boma ilili nde ndi paMtumbo pa bomatu

  • @RajabShahida
    @RajabShahida 2 วันที่ผ่านมา

    Sitinagone kaliati amatiyimilira ku UTM

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 2 วันที่ผ่านมา

    UDF Ndi Manganya asapite kumeneko
    Manganya NDI MCP zatikwana

  • @DanielGeorge-l4h
    @DanielGeorge-l4h 2 วันที่ผ่านมา

    Tikapuma kumanda ngati kuli kopuma

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 2 วันที่ผ่านมา +1

    Manganya simunthu

  • @Georgemsangala
    @Georgemsangala 2 วันที่ผ่านมา

    Mavuto amenewa tikakhale bzy ku police chosecho azathuwo loko Ali police za kudya ndi mbweeee pomwe ife loko tili kunja koma kuchita kusowa ya bonya za ziiii

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge 2 วันที่ผ่านมา

    Tauzeni akafune mafuta uko ndi za imfa ya chilima ilipati

  • @Esa-u3t
    @Esa-u3t 2 วันที่ผ่านมา

    Mr, DC ❤❤❤❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 2 วันที่ผ่านมา +2

    Go to any country anthu akapalamula amazengedwa mlandu basi. Kkkkkk amene atuluke kupita Ku police alibe zochita

    • @razaqrealkay203
      @razaqrealkay203 2 วันที่ผ่านมา

      Inunso nyopanu palibe chomwe mukudziwa tadzingotuwani kwanuko mboli yanu

    • @ShamilahSaizi
      @ShamilahSaizi 2 วันที่ผ่านมา

      Umangoziwilatu kut ndi chikangawa uyu

    • @ruthmalunga2250
      @ruthmalunga2250 2 วันที่ผ่านมา

      Ukudyatu iweyo ife tipita ,Tampa ndi mcp

  • @EmmanuelWhite-h7e
    @EmmanuelWhite-h7e 2 วันที่ผ่านมา

    Enemy from within ithyoke ithyoke pano ndipa home

  • @mlimolubanda6348
    @mlimolubanda6348 2 วันที่ผ่านมา

    Komatu mcp yalakwisa apa

  • @GladysndilimbiraBonongwe-g6c
    @GladysndilimbiraBonongwe-g6c 2 วันที่ผ่านมา

    Manganya ndi yudasi

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 2 วันที่ผ่านมา

    I respect u the dc

  • @Esa-u3t
    @Esa-u3t 2 วันที่ผ่านมา

    Mr, usi Simunthu🚨🚨🚨🚨🚨

  • @NEBRA-lm7ji
    @NEBRA-lm7ji 2 วันที่ผ่านมา

    Kuli ziiii manganya or kuonekela

  • @kelvinfaki7837
    @kelvinfaki7837 2 วันที่ผ่านมา

    Tonse tili maso tifike pano timvele limodzi za DC

  • @AliceChipeta-pc3nb
    @AliceChipeta-pc3nb 2 วันที่ผ่านมา

    The DC munanenadi ndakumbukila

  • @ChifundoNkhoma-k5t
    @ChifundoNkhoma-k5t 2 วันที่ผ่านมา

    Vuto ndife a Malawi serious

  • @rabeccaphiri1333
    @rabeccaphiri1333 2 วันที่ผ่านมา

    Bon Kalindo bodza sutopa nalo mmmmm

  • @MauriceChilombe
    @MauriceChilombe 2 วันที่ผ่านมา

    Kma anthu DC timakonda

  • @JohnMogha-js9oj
    @JohnMogha-js9oj 2 วันที่ผ่านมา

    Chikangawa ituluka, sinathe

  • @emilynthite6545
    @emilynthite6545 2 วันที่ผ่านมา

    Apanga upo ndi manganya osati wina ayi

  • @MatanjeBanent
    @MatanjeBanent 2 วันที่ผ่านมา

    Tikumana mawa Koko mcp mwaonjeza