koma nkhani yakwa Nsundwe yandinyasa nsaname mpaka Roadblock?

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 26 ต.ค. 2024

ความคิดเห็น • 118

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +5

    Amwene vuto ndi chimwendo
    Cox ndamene anayambitsa kuyankhula mawu wobwetetsa nkhondo
    Ndipo mwa chakwera mulibe utsogoleri ndipo ndikape komanso chitsiru cox mtdogoleri wanzeru sayang'anira zopusa

    • @TrizaGeorge-q8w
      @TrizaGeorge-q8w ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndipo nyasi zokha zokha mmm

  • @MercyChipeta-h4d
    @MercyChipeta-h4d 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +8

    Achita bwino kuwonekera dziko linse akuwona ngati ndi ma champion koma akuziyika pamavuto. Anthu ali mbuuuuu!!! Alibe kalikonse pomwe anzawo akumipando akumwa wa mkaka. Chimwendo sapitatu ku prison apite ndi iwowo. Challenge yabwanji iyi? Ooooooh my Malawi is gone beyond ndi Chakwera.

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Aka kachitatu akuphwanya ndikumenya anthu a DPP, a police aliphee kumangoyang'ana ndikumatenga Kaliati opanda mulandu. Thanks tibweza

    • @GeorgeBanda-x6l
      @GeorgeBanda-x6l ชั่วโมงที่ผ่านมา

      ndipodi sindikuziwa kuti bomali likuganiza bwanji

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kodi ku DPP kulibe anyamata azitho odziwa kupambadza ???
    Chifukwa sikoyamba mcp kupanga zopusazi , basi kumangosekelelabe ndizopusa zonwe ??
    Panopa tisamayendele kuti police ilowelele ,
    Because malawi police is very very useless and foolishness .

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Kulakwa kwambiri ukutu eish

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ana a chikangawa awa, koma dziko laphwekadi mweee ndi awa omwe kupangitsa road block zoona????? 💔💔💔

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Komatso,inu abale.anthuwa,akuoneka kuti,sidziyenda,koma boma lomwelo,lozudza zithu zadula cement ndi zinna zotelo koma ndindalama zingati zomwe akupasidwa.aaaaa,boma la chakwela lalephela,kutetedza.izi,atha kuchitila abale Athu ndikunena monenetsa,azatsiya,achakazawo ndi ana.

  • @yusufbakali
    @yusufbakali ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthu ozolowera kukumba mbewa ndi choncho

  • @SueWahna-y8m
    @SueWahna-y8m ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Latha bas dzikoli chisoni changa chili kwa azigogo anga ndi nthu aulumali 😢 nanga chonchi pot ena za chipanizi ndi zovala zawo atakhala avala mwakusaziwa kut kunja kulinji sibas aphedwa sitili safe dzikoli achitetezo adapita ndi chilima😢

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 52 นาทีที่ผ่านมา

    Ine monga wakuno ku nkhata bay mutonga weniwemi.
    Ndingofusa kodi apolice asilikali akuno kumupoto asilikali ndi apolice akumwera mdi kumawa wose akuopa lilongwe ndichifukwa chani anthu apakati akuziva nchochi iyi ndinkhomdo wait and see zimene zichitike mumalawi

  • @LameckBanda-gk6ri
    @LameckBanda-gk6ri 53 นาทีที่ผ่านมา

    Akulemekeza maganizo achikwanje ,achina chisale ndi anamalomba

  • @ChaonekaSande
    @ChaonekaSande 8 นาทีที่ผ่านมา

    Amenewa akufunika apezedwe asatenge ngati dziko ndila mcp we are in democracy

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 4 นาทีที่ผ่านมา

    Chakwela ndi president wa dziko koma vuto mphamvu alibe mphamvu dzili ndi nduna osati iye ayi amachita kuudzidwa chilichose akadakhala ndi mphamvu mbwenu uchisiluwu kulibeko nde pano anthu kupanga chipongwe saopa Pena democracy iyi yabweletsa manyi pa dziko

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz 59 นาทีที่ผ่านมา

    CHIMWENDO BANDA YOMWEYO KUCHEPETSA MA VOTE YA MCP KOMA CHAKWERA SURE ANGATENGE MBUTUMA IYI KUT IPITILIZE KUWONONGA MBIRI KKKKK😂🤣🤣🤣🤣🤣 ZIKHALE NG'OMA,KUKUYU AND MANGANYA AWEEE KUDZANGOVUNDURA MCP

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Anthuwatu nzotunidwa ndipo apolisi anali atadziwa kale koma sangachite kanthu

  • @AshanAlexx
    @AshanAlexx 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ayi tawona kumene apite nazo ngati iwowo Alibe azitsongoleli, atipeza mbali yakuno

  • @chemandotamwale
    @chemandotamwale 37 นาทีที่ผ่านมา

    Amalawi tidziwe Kuti iyiyi ndinkhondo ngati mtsogoleli samadzudzula zimenezi mukumbukile ku libia nkhondo inayamba bwanji? inayambilat musika kumayambana okhaokha Adani analowelelelapo apa sizikusiyana tikumayambana tokhatokha Mapeto ake ndinkhondo

  • @EthelKubalasa
    @EthelKubalasa ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Apolisi awamange anthu amene anali pa nsundwe kutseka nsewu. Boma lichitepo kathu izi sizoona, anthuwa siapolisi mwanji akupanga roadblock pansewu.

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 43 นาทีที่ผ่านมา

    Iweyonso ndiwe chitsiru mesa umamukalipila ngati makwana munthi una nde apa ukuchita kuwanyengelera naweso ndi wa mcp galu owe chitsiru nyani galu

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi mmesa chakwera anaronjeza ntchito onemirion za achinyamata ntchito zija ndizomwezoka moti panopa achinyamata ambiri akupeza zochita mboma rimeneri kkkkkkkkk

  • @BerthiaMkwera
    @BerthiaMkwera 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ndiye ntanyiwa akalankhula mukuti ndi propaganda, look now.

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    And why Malawi ndi watonse ❤Malawi 🇲🇼

  • @SaidiMussa-kd7lh
    @SaidiMussa-kd7lh ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ango pita ndi thilakki ukokolora osewo ndiye kuti chakwera azipanga msokhano koko basi ngati zikhare chocho azindikire iwo mawa zizakhala bwanji

  • @GeofreyRhonard
    @GeofreyRhonard 8 นาทีที่ผ่านมา

    Anthu opanda umunthu awa mukugona nd njar mulipo wakupangiran chan lazalo wanuo anthu aleke kudutsa chifukwa cha zitsiru inuo nd nthaw ya campanie kaa ino

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo4099 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Where is the police in this kodi Apolice whom do you serve Malawians or politicians

  • @StanleyMkandawire-d5k
    @StanleyMkandawire-d5k ชั่วโมงที่ผ่านมา

    aMCP akutenga dzikoli ngati ndilawo chauta wakuona chakwera unalidwe pastor ?

  • @edsonwolemba3011
    @edsonwolemba3011 18 นาทีที่ผ่านมา

    DPP must stop talking nosence.coz niamene akupanga inciet violence awa akungobweza zomwe ma cadet amapanga kummwela

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe ชั่วโมงที่ผ่านมา

    fundo zachikwanje zimenezo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @mathewssimbi3052
    @mathewssimbi3052 11 นาทีที่ผ่านมา

    Koma where is our Malawi Defence Force

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tione mmene MCP ipangike pano pankhaniyi anenando kuti ndi adpp onwe?? nanga roadblock iyo ngati ya mzimbabwr bwanji pali mbendeta a ng'ona party??

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 43 นาทีที่ผ่านมา

    Ineyo guys i dont understand kt ili ndi dziko kapena ka village chabe

  • @SamwaJohn
    @SamwaJohn 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Eeeee kma xibwino chichi

  • @NdazionaWadi
    @NdazionaWadi ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kujaila kwambiri

  • @EmanuelMwanza-ko7tm
    @EmanuelMwanza-ko7tm 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Vuto ndi umbuli ndale sapanga chonchi

  • @JohnKabila-v7q
    @JohnKabila-v7q 29 นาทีที่ผ่านมา

    Wakamba chilungaamo ndiwe onganiza kampeni amaponda palipose azikudalisani

  • @GeorgeLysoni
    @GeorgeLysoni ชั่วโมงที่ผ่านมา

    apolis mukungo Yang,anila zimenezi kodipakati apainu apolis ndi anyamata amenewa oyenela kuteka nseundindan

  • @FracksonMadani
    @FracksonMadani ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pamenepo sipachitika mulandu wa felony koma?😅

  • @KondwaniBanda-ul8sj
    @KondwaniBanda-ul8sj 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Aaaa ndale zakumalawi zausatana mulibemo umulungu zipani zangosaduka zipembedzo zochitilako zoipa

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndichimwendo Banda ameneyo ndipo kamachende ameneyu

  • @wellington-w2e
    @wellington-w2e ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthu agwirisiwa ntchitowo ndikusamba kumene sadziwa umbuli ndi kachilombo ndithu

  • @FloraBanda-w7t
    @FloraBanda-w7t 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +2

    Kwa nsundwe sikumalawi😂

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy นาทีที่ผ่านมา

    One million jobs uja NDI imeneyi ..ija chikangawa adalonjeza kkk

  • @LuckyBenson-p9s
    @LuckyBenson-p9s 49 นาทีที่ผ่านมา

    Paja a. Dpp amayenda ndi zikwanje mmagalimoto musamve kuwawa

  • @YamikanBanda-z7z
    @YamikanBanda-z7z ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Tifunilanji umboni wina apa?kma a mcp apapa angakane?

  • @JamesIsaac-zi4kb
    @JamesIsaac-zi4kb ชั่วโมงที่ผ่านมา

    First class fool

  • @JoshTech-h4r
    @JoshTech-h4r 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Ineyo ndi mchewa km too minute inayake achewa ndi ofoila aah

  • @AyasiWhite-l6s
    @AyasiWhite-l6s 7 นาทีที่ผ่านมา

    Achisale please tiyeni tiyambe kubwezela anthu akupha chilimawa ationjexa

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma ndiye mwafikapotu, mpaka roadblock anthu wamba?

  • @petertengani
    @petertengani 25 นาทีที่ผ่านมา

    Ndisamukira ku Karonga.
    🤦🏽‍♂️🤦🏽‍♂️🇲🇼.

    • @AyasiWhite-l6s
      @AyasiWhite-l6s 5 นาทีที่ผ่านมา

      Ku kalongako ndi dxiko lanji kkkk

  • @AminJumah-s9t
    @AminJumah-s9t ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Anthu ake osasamba ooneka kuti sakudya mokwanira zitsiru zanthu

  • @AlexMakawa-j9f
    @AlexMakawa-j9f 22 นาทีที่ผ่านมา

    Anthuyake akupanga zimeneziwa osasambaso ndiyawo

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Pano or ndi nyau zomwe zatasatu ku lilongwe kuno zigawenga zikubisalira mu dzina la nyawu.

  • @IslamMapepa
    @IslamMapepa ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mwaiwona mbindelayo ndiya mcp nde sangamangidwe chifukwa zikuchitikazi ndizaboma lolamula

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Chakwera simunthu WA bwino ndi galu

  • @RobertMalanda
    @RobertMalanda ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi a police ndi arm alikuti ?Kodi awa amyamatawa afikanso poika RoadBlock

  • @MwakapimbaMkandi-s4u
    @MwakapimbaMkandi-s4u 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma boma lipangepo khatu pa anthu amenewo akwa nsundwe , bima likakhala chete iwoo achigao chonse cha pakati aziganizile okha chifukwa iwo Alipakati kuli ku mpoto ndi ku mwera

  • @TracyBanda-i2g
    @TracyBanda-i2g 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Achimwendo banda NDA chisiru mburu ya minister opusa kwambiri

  • @saidiwilliam9832
    @saidiwilliam9832 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ana amaskin awa

  • @AyasiWhite-l6s
    @AyasiWhite-l6s 10 นาทีที่ผ่านมา +1

    Anthu akenso osasamba ali mbuuuu ngt ngawu

  • @JustinMatola
    @JustinMatola 36 นาทีที่ผ่านมา

    Nawoso a MCP adziwona kumwela kuno ndi nkhondo mwayi yambayi

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma chakwera ngati sadzudzula nduna zake ndekuti akudziwapo kanthu

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 22 นาทีที่ผ่านมา

    Chakwera mburi ndithu no more mcp ever

  • @AdamKay-q1l
    @AdamKay-q1l 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Where's police akungoyan'ganila wosachitapo kanthu pmf???

  • @hassanfaizadaffer2421
    @hassanfaizadaffer2421 24 นาทีที่ผ่านมา

    Ndikamava kut anyamata akwasu dwe ndmaona ngati osamba kodi nd zasasamba chonchi zosowa zochita

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Dziko ili lilimmanja mwa gule wamkulu 😢😢😢

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Let the police do their job or else zivuta izi

  • @Gemcape
    @Gemcape 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kummwera asabwelekonso kudzapanga misonkhano yawo amakanjawa

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli นาทีที่ผ่านมา

    Zonyasa muziko zimenezo kulibe police kumeneko aaaa

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ndibwera komweko ndizakuvinireni jando ndi pulesidenti wanuyo

  • @Gemcape
    @Gemcape 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Izi ndizotumidwa ndi chinkhumba kmnso kamajekete km masiku akupita tidzawona pokolola popeza siife ana ai

  • @JamesMachunga
    @JamesMachunga ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Police ya Malawi ndi MCP chikangawa party

  • @MAYGOSPELALBUMSChawawa
    @MAYGOSPELALBUMSChawawa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Where is MDF please how can you allow this happen in the country where there is Police and Army sham on you MDF staff you're weak.

    • @GreyMtungama
      @GreyMtungama ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Ndiya MCP palibe chomwe angapange

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick ชั่วโมงที่ผ่านมา

      ​@@GreyMtungamaNdipo brother eeeeee MCP guys mmmm

  • @DominicYohane
    @DominicYohane 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma guys MW watani kod? Eeeeh

  • @jamesbanda-l2w
    @jamesbanda-l2w ชั่วโมงที่ผ่านมา

    izi zakunyasani munakondwa ndimau amzimai kuphalombe kuja

  • @ShillaShamil-v2y
    @ShillaShamil-v2y 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Zitsiru za anthu pali owopnso alibe nkathu komwe agalu

  • @SamwaJohn
    @SamwaJohn 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kusowa khalidwe

  • @AdamKay-q1l
    @AdamKay-q1l 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Shipani ndi cha manyi cha MCP zikapitilila nafeso tisatila maganizo awo

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 ชั่วโมงที่ผ่านมา

      dpp inayambitsa zoyipa kumati ku phalombe chimwendo asafikeko kugenda chakwera

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick ชั่วโมงที่ผ่านมา

      Big MCP ndiyazitsiru zokhazokha zimasapota zawo zitsiru atsogoleri zitsiru zokhazokha Koma tibweza wait n c

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Sopano ma foreigners aziwona chisawawa chotere

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    May God punish poverty

  • @ChaonekaSande
    @ChaonekaSande 8 นาทีที่ผ่านมา

    And more over ma video alipo apezedwe ndithu

  • @ClementMunyolowa
    @ClementMunyolowa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Koma shame mbiri ndiya Chikangawa

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Gayz mudzifufuza kaye musana falitse anthu ake atatuwo aaaa bodza ili musakokomeze chifukwa ndiwe wadpp

  • @BrandinaMphuka
    @BrandinaMphuka ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kkkkkk koma abale nsudwe boyz

  • @johnntilah4735
    @johnntilah4735 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Choncho akamangidwa azinena kuti boma ili ndiloipa.

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Umbuli ndi msanje

  • @SaidiMilaji-dk8sr
    @SaidiMilaji-dk8sr 31 นาทีที่ผ่านมา

    Boma lokomela tonse lija ndili meneli? Zoopsatu

  • @HajieMusitafa
    @HajieMusitafa 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Idzi ndinyasi komaso manyi ene

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komaso chakwerayo akudziwa po kathu

  • @AyasiWhite-l6s
    @AyasiWhite-l6s 12 นาทีที่ผ่านมา

    Achewa inu moyo opusa tu umenenewo mwaona ngt dxiko ndilanu

  • @James-v8v8d
    @James-v8v8d 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Akuononga chipani amenewo musawa sekelele

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    This is too much, kujayilatu uku.

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    kuno ku south africa ufuku umakhala mmanja mwa anthu koma saphwanyilana magalimoto kamba ka zipani olo dera ayi ayi kona ma demo ndiye amapangidwadi but stupid mcp young people kusaphunzira basi anyani

  • @leveltrapper4322
    @leveltrapper4322 2 นาทีที่ผ่านมา

    Ths is unexceptional acts

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 20 นาทีที่ผ่านมา

    Osangowa womba mbanji

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 12 นาทีที่ผ่านมา

    Ichi ndie chibwana chenicheni

  • @tebogomaake9375
    @tebogomaake9375 36 นาทีที่ผ่านมา

    Aku jejemera kkkk DPP boma

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mapeto ake dziko ligawanika

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Nanenso zandinyasa

  • @MarkoJele-s4m
    @MarkoJele-s4m 2 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    akhoza inu mudagenda chakwela

  • @DouglasDazuKamwendo
    @DouglasDazuKamwendo 31 นาทีที่ผ่านมา

    Lidzakwana la 40 bro osadanda