Dr, please come to the north. When you will be in the north please try to travel from Rumphi through Nthalire to Chitipa boma. The long awaited road since the British came to rule us. We are still waiting for that road to be have bitumen. I need UTM govt..inflation to be at one digit. Bravo UTM.
Mama Kaliat akweni am Happy to see you ,Mai owugwira mtima opanda nsanje ozichepetsa ,Ambuye azikudalitsani mamay❤
❤❤❤❤❤❤ Thump up Akweni for still clinging to UTM
Very much Happy to see Mai Kaliati again,,, Mai wathu, Mai wapfuko. Mulungu akudalitseni Mai wathu. UTM forever
Love this woman l tell you a woman who knows what is right at the right time we honor you mama God bless you
Dr, please come to the north. When you will be in the north please try to travel from Rumphi through Nthalire to Chitipa boma. The long awaited road since the British came to rule us. We are still waiting for that road to be have bitumen. I need UTM govt..inflation to be at one digit. Bravo UTM.
Akweni i love you ❤ happy to see you with Dk
Zonyaditsa kwambiri kuona Kaliati akugwirana chanza ndi DK, kuli ine kuno kubva tseketseke.
Salima woyeeeee😂😂😂
utm chipani cha athu ozindikila 🔥🔥🔥kaya azawina kaya azaluza km i will vote for Kabambe
Kuganiza kwa bwino, inenso DK my vote
Indee iwe Dr Kabambe my vote ❤❤❤❤
Mai kaliyati more fire
Now I can see solidarity in UTM fire mabomba
My Vote ❤
Ine ndanva kukoma mumtima powawona mayi kariyati uremu wanu mayi
Akatundu mai kaliyati❤
Dr. Kabambe tsogoleri wodzichepetsa wosavala ma glass mmaso
Viva kaliyati viva❤❤
Mai kaliati may the Lord be your guide
Akweni inu ndi one
Mama God bless you
Please go north, Chitipa_ chinunkha ,ifumbo, ichinga,misuku, nthalire, ipenza, kameme, chisenga, nthalire
Muwineeeee, musawineeeee DK my vote
Ndale Za kwanthu kumalawi kunyozana si zonse chakwela abale Zina muziwauzako chilungamo anthuwa Kuti ndalama simabwela kungokhala all kulima kuli mteza chinangwa sizimalilila fertilizer munthu ukhoza kulima kugulitsa nteza uja ndugula chimanga chinangwa ndi simaso inuyo pamene mwayimapo mupanga company sichina mwayimapo mufuna ndalama zotchulukilapo auzeni anthuwa kulibe ndalama Za milacle azikalimbikila uko katundu kulikose wakwela all mupite kuziko lina osati chifukwa cha president auzeni ayike Pasi ng'omazo akalime mteza kukamwa kokuwila pamenepo alinako Koma kulima nde ayi
Welcome mumie we love you so much❤❤❤❤
Will definitely DK for presidency
God bres mai kaliyati opanda sanje.tiyeninayo mcp igwe basi
Ineso ndimamukonda zimai uyu chifukwa amanena chilungamo thawi zambili
Ine ndili konko
Viva. Mayi. Kaliyati Mayi. Odzichepetsa , mulungu azikutsogolelani. Ndi kukutetezani
Akweni mumatha ndipo Mau anu ndi amphavu
Nokha simungawine aiiiiiiiii
Akweni chonde Musa bwelere mumbuyo liphulani ziko pamoto ili chonde pamozi ndi a adada ka bambe Ndine Michael kalikokha zhakata msimuko
Apule a u t m akuoneka odzikonda akungokamba zakulirangwe pa ma president onse wabwno anar bakiri basi
DK MY VOTE
Mayi❤❤
ndipo kaliat ndizimayi wodzichepesa kwambili guys osati usi ndimbuzi yamuthu kwambili
Ndamva kukoma lero, poona Mai kaliat
Muziona
Camera man tajambula bwino.
Doctor Patricia kaliati boma
My vote UTm skc Dk
DK machine
Mai uyu ndipangolin pachipani kukula uku takunyadilani
Vincent kachijere boma ndilomweri osati mbwerera zinaz, kabambe yomweyo
A mcp khamu lija ndilit osamangoti khamu anthu awili🤣
Masanje awa
Koma kaliati mmmmm uyu anapanga kkkkkkkk
Kodi kulilangwe ndimbali yiti kumalawi abale 😮😮
Blantyre Nseu wa Zalewa
@amtvmw ok🙏🙏
@@MaryNyirenda-nq3mh my village 🏡
Utm akanasewera game iyi mwa smart posakulilana mitima ndi Judas guys akanatenga position n revenge zakuchikangawa
Blantyre north
Bwana ine pano ndagula kale machine koma koti ndkatenge fertilizer sindkukuzwaiii😢 tiyeni tisiye ndale malawi apite kusogolo
Zabwino kwambili
Mumati mutani, chipongwe chakupwetekani. You will need DPP for you to survive.
Achakwera bodza ngati mkazi English for nothing
Please go north, Chitipa_ chinunkha ,ifumbo, ichinga,misuku, nthalire, ipenza, kameme, chisenga, nthalire