CHILEMBWE DAY YA YANJANITSA ADANI PA NDALE - MCP, DPP, UTM, UDF x PDP. CHIMWENDO BANDA WATOKOTA IZI

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 15 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 126

  • @ZivanaiGwatura
    @ZivanaiGwatura 20 ชั่วโมงที่ผ่านมา +1

    Admarc yalandidwa muulamulilo wanu

  • @YusufMaulidi-b2c
    @YusufMaulidi-b2c วันที่ผ่านมา +3

    Achimwendo simunabwere pa msonkhano wa ndale

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq วันที่ผ่านมา +2

    Kodi mwabwela kuzapanga ndale osati kukumbukila chilembwe

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chimwendo umandinyasa kwambiri, ndiwe bulutu

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc วันที่ผ่านมา +1

    Kulowesa ndale galu iwe Your days are numbered.....✍️

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 วันที่ผ่านมา +1

    Chimwendo Banda Mbuzi, uwu si mnsonkhano wandale u chitsiru umenewu

  • @FayinesiKondwani
    @FayinesiKondwani 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Komatu chimwendo Ali ndi voice yonyasa angokhala Ngati Akuyimba kwayaa😅😅😅😅😅

  • @GeraldMkandawire-u2v
    @GeraldMkandawire-u2v วันที่ผ่านมา +2

    Nyengo zinasithadi anthu amangomangidwa osalakwa

  • @AubreyMukhwapa-k1t
    @AubreyMukhwapa-k1t 9 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Waiwala kunena Kuti 5 yrs Ina ikubwerayo azidzabwera ngat former president chifukwa watsala ndi miyez 7

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly วันที่ผ่านมา +1

    Uyuyo ndiamenedi akumuononga chikangawa

  • @TamaniKumposha
    @TamaniKumposha วันที่ผ่านมา +1

    Chimwendo usapange zandsle kumeneko panga za chilembwe basi basi wanva Muthu uyipa iwe

  • @MjombaMoosa
    @MjombaMoosa วันที่ผ่านมา +1

    Kodi za ndale kapena chilembwe day iwe chimeendo ndiye katundu ochipayo ali kuti koma mutu wako umatogwira

  • @JuweriaMussa
    @JuweriaMussa วันที่ผ่านมา +1

    Mulandeni mike ameneyo sikumusonkhano wandale kumeneko ndikumarilo chonde asatinyase chonde mulandeni atumbukafe mumatikonda ? Mesa mumatisankha

  • @StandwellNjoka
    @StandwellNjoka วันที่ผ่านมา

    Zikwanje mwasunga ku dambwe mwatsekula ku area 10 zija ndikulumikizitsa umodzi wambwiyako?

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu วันที่ผ่านมา +1

    Chimwendo garu ndi mbuya wakoyo athu oyipa mtima inu kumupha chilima zoona simaluonelani kukondwa athu inu

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga วันที่ผ่านมา

    bulutu weniweni,akuyesa msonkhano wa Chikangawa eti, forsake 😢

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Kodi inali Chilembwe day or inali kampeni abale?

  • @NiccoGama
    @NiccoGama วันที่ผ่านมา +1

    Apakire bas tatopa alowe ena tione dzina

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 วันที่ผ่านมา +1

    Chimwendo woyeee😂😂😂😂

  • @MalickMkweche
    @MalickMkweche วันที่ผ่านมา +1

    Azimayi kudedeluka iiiiii

  • @Ausward-Jasket
    @Ausward-Jasket 12 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Ma cadet mwatani kodi?

  • @Simionluhanga
    @Simionluhanga วันที่ผ่านมา +1

    Mwautenga ngat msonkhano wa ndale achimwendo

  • @YassenYasin-v6o
    @YassenYasin-v6o วันที่ผ่านมา +1

    Chimwendo galu kobazi ukulalika kuchipani kapena kuchilembe mukuchoka popano boma ndipo muzamangidwa noze😂😂😂😂😂

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl วันที่ผ่านมา

    Achimwendo muzichita manyazi iyi ndi chilembwe day osati popangila ndale

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Andale ndinu anthu okaikitsa , ndinu amodzi agalu inu

  • @MissyThobve
    @MissyThobve วันที่ผ่านมา

    Eish nkhani yama degree moti mukambe za chilembwe mmmm

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Mukatero mukuti mukuwapenta amalawi mwauponda, kwanu kwathaaa

  • @StandwellNjoka
    @StandwellNjoka วันที่ผ่านมา

    Inu munthu akakumenyerani nkhondo mukapeza ufulu paja mumamuphaso,chipanda chilima,sidiki mia munali ndani inu

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chakwela akuonekelatu kut zopangana izi, amalawi wake up please anthu wa ndioipa

  • @HerlbertKaalis
    @HerlbertKaalis วันที่ผ่านมา

    Iwe nde ukhodzekele Kumangidwa BOMA likudzali bwanji mwalowetsa Ndale Aaaaaaaa zachisoni

  • @musasiyama9423
    @musasiyama9423 14 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    chimwendo ,,,,galu ,mbudzi yamunthu,,,sizandale izi

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 22 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    Chimwendo ndi bulutu wa abulutu onse

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg วันที่ผ่านมา

    Kodi mwavala chikopa chanyama yanji 😂😂😂😂

  • @JamesChikwanje
    @JamesChikwanje วันที่ผ่านมา

    😅😅😅😅 Zalowa ndale

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly วันที่ผ่านมา

    This party must end

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s วันที่ผ่านมา

    Tathokoza kuti moyo wa malemu koma akulephera kuyamika zamoyo wake.

  • @PrincestewartPhiri
    @PrincestewartPhiri วันที่ผ่านมา

    A chimwendo ndikuyamikireni mkuyankhula ngati nduna koma msinthe chabe kuntchula pafupipafupi president, mwayankhula Banda pitilizani

  • @YusufAlidi
    @YusufAlidi วันที่ผ่านมา

    Nanga chilima munamuphelanji

  • @EthelLeman
    @EthelLeman วันที่ผ่านมา

    Kodi Chimwendo uku sikopangira kampenitu nachimimba iwe

  • @lytonmilford2110
    @lytonmilford2110 วันที่ผ่านมา

    Speech iyi ikugwilizana bwanji ndi mwambou kkkk koma abale

  • @hassanmussah7821
    @hassanmussah7821 วันที่ผ่านมา

    For the first time ndagwirizana ndi chimwendo

  • @MUSATAFAIIi-c4j
    @MUSATAFAIIi-c4j วันที่ผ่านมา

    😁😁😁😁😁

  • @MosesSangano-g6j
    @MosesSangano-g6j วันที่ผ่านมา

    Fundoless

  • @Andrewmwamadi
    @Andrewmwamadi วันที่ผ่านมา

    Mcp Muziona 2025

  • @HamiltonSinosi
    @HamiltonSinosi วันที่ผ่านมา

    Wakutumayo kumumenyera campen chikangawa kumeneko??? Tachioneni chimutu

  • @GeraldMkandawire-u2v
    @GeraldMkandawire-u2v วันที่ผ่านมา

    Kodi ndimayesa kuti mutiudza mbiri ya chilebwe abale mm koma ndale

  • @MagieJames
    @MagieJames วันที่ผ่านมา

    Ukuyankhula zandale kapena zokumbukira John chilembwe nawe kusowa zochita uzakomoka mcp ikazaluza

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg วันที่ผ่านมา

    Kodi ndi mwambo oyamikira Chakwera kapena okumbukira John Chilembwe?? No sense Chimwendo Bandaa.

  • @Eliza-h6o
    @Eliza-h6o วันที่ผ่านมา

    Ngalu wamuthu ukuyakhula zandale bwanji chakwela kukamwa ngata amudula milomo

  • @ChimzyWesley
    @ChimzyWesley วันที่ผ่านมา

    Kodi osamuchosapo bwanji

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n วันที่ผ่านมา

    Lero ukapolo uja akutipanga ndi mmalawi mzathu: Chakwera watitopesa pokweza maphunziro kuti osauka asaphunzire, kubweresa njala, devaluation nthawi ndi nthawi

  • @ChippieSailesi
    @ChippieSailesi วันที่ผ่านมา

    Chimimba ndi uputsa kwambiri chilichonse ndale bas ngati ukunva kukoma iweyo dziko la nyasalande usaone ngati tonsefe mbuzi iwe

  • @MosesSangano-g6j
    @MosesSangano-g6j วันที่ผ่านมา

    Mmm ponyani fundo inu nsindale izi mbuzi pakilani en tikumangani size 😂😂😂😂 ma account Anu aona nyekwee

  • @RitaPhiri-nm6hp
    @RitaPhiri-nm6hp วันที่ผ่านมา

    Kkkk olo Eni akewo apule akudabwanazo kuti iwe ukuwonjeza

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 วันที่ผ่านมา

    Ndipo chilembwe kodi amavala makala a mcp? Siku ili ndi la John chirembwe ndipo ndi siku la a Malawi ose sisiku la chipani cha mcp nose mavala mcp mwe azerereza ukongwa simukusiyanisa musonkhano wa chipani ndi musonkhano wa amalawi

  • @ValerieSteward-m8i
    @ValerieSteward-m8i วันที่ผ่านมา

    Mbava iyi imandinyansa bwanji

  • @LukiyaAlick
    @LukiyaAlick วันที่ผ่านมา

    iwe ngalu chakwera ngalu nyani

  • @LuwizaChika
    @LuwizaChika วันที่ผ่านมา

    Kod ndisokhano wandale zovesa chison kwambili 😢😢

  • @ThomasPatrick-n3n
    @ThomasPatrick-n3n วันที่ผ่านมา

    Chimwendo mutuwo wangokula ulibe nzeru kumalo amapephelo ukupitisako ndale chitsilu

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira วันที่ผ่านมา

    Chibwendo ndi amene akulamulila chakwela

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo วันที่ผ่านมา

    Iya opusa uyu atiuze amene anamuuza kuti ndege yazaza

  • @WillyYasin
    @WillyYasin วันที่ผ่านมา

    Mwayamba ndale akulu tikudikila chaka chamawa ndenge sidzadza ndi anthu eight

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂Agalu awa alibe dzelu

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs วันที่ผ่านมา

    Chimwendo nachimimba iwe usatenge mwambowo ngat wa ndale usamutame mnzakoyo Kuti adzakhalanso akubwera kumeneko Zaka Zina 5 ndiwe ozitukumula, ndiwe kape kwambiri ndipo umandibowa

  • @RestarUmi
    @RestarUmi วันที่ผ่านมา

    Kod amenei chisilu et

  • @StandwellNjoka
    @StandwellNjoka วันที่ผ่านมา

    Mbwerera waonjezatu uyu

  • @ElizabethDinala
    @ElizabethDinala วันที่ผ่านมา

    Chende lako ndi zomwe wayakhula iwezo wamva.....akumvutikanso kubereka ndi amako

  • @DavieWinisi
    @DavieWinisi วันที่ผ่านมา

    Iwe chimwendo usaipise mpingo wa pim ukuona ngt uli ku ndale ND chakwela wakoyo agalu Inu

  • @Haka-tb8ih
    @Haka-tb8ih วันที่ผ่านมา

    Wakuuza ndani kt 5 years ikubwerayi mudzapitanso

  • @WilsonNedi-s6t
    @WilsonNedi-s6t วันที่ผ่านมา

    Inu zandale muziwona ndimalo ake

  • @RajiChapollah
    @RajiChapollah วันที่ผ่านมา

    Ali pandale uyu

  • @GrecianSeveli
    @GrecianSeveli วันที่ผ่านมา

    Achimwendo yomweyo 2025 mcp ndi boma kale

  • @Stretor
    @Stretor วันที่ผ่านมา

    Koma ine Chimwendo amandinyasa kwambili Malawi akutenga ngati banja lake akututumuka kwambili azitengera ngat za MCP eish kwinaku nditukwana koma nkhani ndiyoti MCP september pack and go ndinu zitsilu kwambili

  • @RoseKamwaza-v7e
    @RoseKamwaza-v7e วันที่ผ่านมา

    Iwe ndi mbuzi 5yrs yake ITI yomwe mupitilizeyo nthawi yakutherani vomerezani

  • @WillyYasin
    @WillyYasin วันที่ผ่านมา

    Nanga chilima munapha bwanji mwayamba ndale apapa

  • @ChuzyBoy-u1c
    @ChuzyBoy-u1c วันที่ผ่านมา

    Uyuso ndiye wandinyasa ndi kachisilu kachikangawa nkhope ngati galu

    • @ElizabethDinala
      @ElizabethDinala วันที่ผ่านมา

      Khope gati galu bwino or mlomowo gati nyani

  • @MissyThobve
    @MissyThobve วันที่ผ่านมา

    Njanji ilikwani koma abale

  • @WilsonNedi-s6t
    @WilsonNedi-s6t วันที่ผ่านมา

    Ngati mukuona bwino ampingowo sizikuwasangalasa

  • @AlexanderBaluti
    @AlexanderBaluti วันที่ผ่านมา

    Ndale ndale amalawi kunyada ndi misonkho yathu..shame...

  • @ShyreenMajiga
    @ShyreenMajiga วันที่ผ่านมา

    Iwe sindale iyi pangani chomwe mwapitira

  • @euwarttawakali4320
    @euwarttawakali4320 วันที่ผ่านมา

    Msokhano wa chipani eti??

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august วันที่ผ่านมา

    Kodi azimayi atatuwa sakuchita manyazi pamene akukuwa kuchikamwa kwaoko pamene sinsonkhano wadare azimai opusa kwambiri mmmmhu my question is inuyo a leg leg muli ndi ma digress angati chifukwa mukuoneka kuti yanu ndi ya from 4tu

  • @jackalview7491
    @jackalview7491 วันที่ผ่านมา

    Kodi black box yilikuti iwe chimwendo

  • @ZANLUSQUARE
    @ZANLUSQUARE วันที่ผ่านมา

    Chimwendo patumbo pamango

  • @WilsonNedi-s6t
    @WilsonNedi-s6t วันที่ผ่านมา

    Koma ulaliki uja anaumva bwino? Sakwanisa kuwasokoneza anthu

  • @YusufJafali
    @YusufJafali วันที่ผ่านมา

    Hahaha azimayi atatu analipidwa mwina kkkkkk

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc วันที่ผ่านมา

    Sanayanjane munthu suyanja ndi wamisala ndiye kut iweso ngwamisala

  • @ElizabethMajiga
    @ElizabethMajiga วันที่ผ่านมา

    Zimenezi mumafuna azikutamani ndani?Kodi mumaziwa kuti winawake anafa kuti ife tinkhale pa ufulu?shame on your chimwendo

  • @Stretor
    @Stretor วันที่ผ่านมา

    😪😪😪😪😪 When I see this man ine mtima wanga umawawa kwambili eish who told you kut ndege yadzadza? chitsilu kwambili ichi ndipo akutenga ngat Malawi ndi yake.....
    Chakwera kukamwa ngati somba ya chambo

    • @LinlyMathewe
      @LinlyMathewe วันที่ผ่านมา

      Inenso mtima umandiwawa kwambiri hmm😢

  • @Bernarddavide-e1o
    @Bernarddavide-e1o วันที่ผ่านมา

    It's not sonkhano wandale

  • @BlessingsNamilonje
    @BlessingsNamilonje วันที่ผ่านมา

    Mamuna onyenga mbalume🥱

  • @MartinAbraham-v5w
    @MartinAbraham-v5w วันที่ผ่านมา

    Mutu waking sumagwila iwe Chakwela ndi chipani chako Abusawo alalika zaiwe galu

  • @LydiaMushala
    @LydiaMushala วันที่ผ่านมา

    Komatu ma handshake renewable bwino nawo umakangofikira kukomoka kunyumba khayaaa😂

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly วันที่ผ่านมา

    Kod chimwendoyi amakhala pasogolo why

  • @WilsonNedi-s6t
    @WilsonNedi-s6t วันที่ผ่านมา

    Akweni kusekelera kuyiwala kuti anagona muchitokosi chifukwa cha anthu omwewa

    • @InnocentMtafya-c6b
      @InnocentMtafya-c6b วันที่ผ่านมา

      Inu andale asamakudwalitseni, mukupusa nazotu pa media apa, andale ndinuyotu apapo ...

  • @GustinoKamanga
    @GustinoKamanga วันที่ผ่านมา

    Chimwendo mulungu adzakulanga mochititsa chison kwambiri

  • @RichmanBanana
    @RichmanBanana วันที่ผ่านมา

    Koma zandale ndi Mapemphero tidzisiyanitsa

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i วันที่ผ่านมา

    Matama ndi bodza Chimwendo

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 วันที่ผ่านมา

    Chimwendo kuputsa sikuzakuthela pamenepo ndiye ukuti chani

  • @MUSATAFAIIi-c4j
    @MUSATAFAIIi-c4j วันที่ผ่านมา

    koma kuyankhula kosameza malovuku amathawa chani