PRESIDENT LAZAROUS CHAKWERA WAFIKA KU BLANTYRE - MOLARO YOKHAYO SIZINAONEKETU MAKOSANA

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 15 ม.ค. 2025

ความคิดเห็น • 86

  • @JackMvura
    @JackMvura วันที่ผ่านมา +1

    Chipani chafuko chakwera bomaa ndilomweli ndipo sitikusintha Kodi mukumva bwanji kumeneko chakwera mukumunenayo alipa chiongolerotu mulimba ma Kadett ya shuta BP kumangochi

  • @WysonChilonga
    @WysonChilonga 2 วันที่ผ่านมา +4

    anthu aku Kasiya awa😢,kuchita kwatenga pa lorry,dzanja lalemba pakhoma basi😢

  • @ValerieSteward-m8i
    @ValerieSteward-m8i 2 วันที่ผ่านมา +5

    Mudyeleni mfitiyo , palibe azamuvotele, anthu kuchota kubwela nawo from Lilongwe

  • @gizzykondwani865
    @gizzykondwani865 2 วันที่ผ่านมา +5

    Zazii nawoso azimayi aku malawi kutengeka ndi zopusa aaaaaahh😅😅😅😅

    • @ChangeLive-w7t
      @ChangeLive-w7t วันที่ผ่านมา

      @@gizzykondwani865 mawu volume

  • @BurunoMbewu
    @BurunoMbewu วันที่ผ่านมา +1

    Vot amalawi ndilimenelo masapota Muthu wot akukuzuzan ay kalikonse mukawona 🙌

  • @JuliusChipinde-l9c
    @JuliusChipinde-l9c วันที่ผ่านมา +2

    Anthu aku Lilongwe awa ndipo agona pa Namiwawa primary school

  • @WilsonFelix-j9n
    @WilsonFelix-j9n 2 วันที่ผ่านมา +5

    Anthu abwera mmalore awa

  • @ThomasShuga-z5p
    @ThomasShuga-z5p วันที่ผ่านมา +2

    Mutachoka apo muzikagonera chitedze akakaka inu mumvekere boma ndilomweli zaziii 😔

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 2 วันที่ผ่านมา +2

    Zaziii anthu akusowa zochita kma anthuwa siaku bt awachita kuwabwelesa awawa aaaa

  • @FatimaKhan-i5p
    @FatimaKhan-i5p วันที่ผ่านมา

    Asilikali onsewo Koopa kugendedwa😅😅😅

  • @JOHNOlesmasCosmas
    @JOHNOlesmasCosmas วันที่ผ่านมา

    Anthu achita kubwera nawo kuchokera ku Lilongwe ku BT sangapange zopeperazo

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm วันที่ผ่านมา +2

    BT ndi ya peter iyi vote ndi mumtima chakwera sangawineso akagwere

    • @FranksonKennethChipande
      @FranksonKennethChipande วันที่ผ่านมา

      Zoonadi voti ili mumntima.Politics is about numbers Let's wait the days are fast tafika kale February apa

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx วันที่ผ่านมา +3

    Anthu aku Blantyre ndi aja munawaona kwa Adad aja awa ngobwera nkhope zachilendo zokhazokha😂😂😂😂😂😂

    • @JackMvura
      @JackMvura วันที่ผ่านมา

      @@IshmaelNesta-rb8dx fiti simavomera kuti ndapha ndine ndiomweo siomweo end of time they are Malawians waiting to give vote for Dr chakwera usi ndi chakwera sitikusintha

  • @DeversonMasamba
    @DeversonMasamba วันที่ผ่านมา

    Zoona anthu mukugulisa voti chifukwa cha 100000

  • @Malawian-q5f
    @Malawian-q5f วันที่ผ่านมา

    Kusawukitsa dziko cholinga adzikulambira, zikutha izi pa 16 September. Mcp ya chimwebdo simuzayiwonanso

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ndiye ndaletu zimenezizi 2025 wuno wotsutsawe ukhumudwaso tikuwonera boma sitikusitha

  • @StanleyChamasowa
    @StanleyChamasowa วันที่ผ่านมา +1

    Nchenjeleseni obwabwanayo

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw 2 วันที่ผ่านมา +1

    MTV tsiku Lina muzangoika Ka background song ko basi; ulemu wanu mtv

    • @amtvmw
      @amtvmw  2 วันที่ผ่านมา

      Am Tv boss not MTv 🤗

    • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
      @ChiyembekezoPhiri-sv8nw 2 วันที่ผ่านมา

      @amtvmw kkkkkk ok Am Tv komanso voice yako it's a nice one

  • @LotiBanda-uo5vy
    @LotiBanda-uo5vy วันที่ผ่านมา

    Cadet amayesa ngati Blantyre ndiya DPP yokha wauponda

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 2 วันที่ผ่านมา +1

    Zazi masanje enieni popanda chilima komanso Mia mcp singapange kanthu

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc 2 วันที่ผ่านมา +1

    Mudyeren ameneyo

  • @GetuChingamba
    @GetuChingamba วันที่ผ่านมา

    Boma loongola mafupa ndikuphilitsa zithupsa sitikulifunanso

  • @CharlieChirwa
    @CharlieChirwa 2 วันที่ผ่านมา

    Akudzaona conivo anthuo

  • @IdaMalango
    @IdaMalango วันที่ผ่านมา

    Makape awa

  • @MolesBrown
    @MolesBrown วันที่ผ่านมา

    Makadeti muphulikatu zisinati muwone nantindi wa anthu amene anali kumulanje ndi vp wa mcp mukhaula muwona pangani ndale zopusa zotukwanazo anzanu ali pagalaundi ife sitipanganawo zopusazo

  • @romielectronics
    @romielectronics 2 วันที่ผ่านมา

    Anthu 21 million sitingapange zofanana

  • @Mwaimvange
    @Mwaimvange วันที่ผ่านมา

    anthu awa si aku Blantyre ai

  • @patrickmandalawe745
    @patrickmandalawe745 2 วันที่ผ่านมา +1

    Artificial morale

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs 2 วันที่ผ่านมา +1

    Kkkkkk watutakuti athuwa

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 2 วันที่ผ่านมา

    Aaah inu anthuwa si a mu BT acita kubwera nawo kuchokela ku LL enawo ndi ogudwa, enawo angobwela kuti adziciwone cisilu cimene cayika malawi pamavuto.Musapusisike mcp yagwa kale💙💙💙💙💙💙boma

  • @MuhaSaibu
    @MuhaSaibu 2 วันที่ผ่านมา

    Dyelen ameneyo

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 2 วันที่ผ่านมา

    Ndiye kuti mukamapita kwa munthalika ndinu ampawi eti pepani ife si ampawi

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 วันที่ผ่านมา

    Kod mukuona kut anthu onse dziko muno ndia DPP😅😅😅😅 mudya ndithu

  • @JamesRoben-dy7bx
    @JamesRoben-dy7bx 2 วันที่ผ่านมา

    Ndiye athu ameneo bas atha kuwinisa mcp zoon

  • @PatrickKapendo
    @PatrickKapendo วันที่ผ่านมา

    Osusa opanda mkalidwe ngakhale mutukwane Chakweratu azwina mukuyesa kuti tizingolemelesa anthu azipani Peter anali pampando omwewu akulila akuziwa zokoma zomwe zimapezeka m'menemu ndiye sizithekha ngati wasauka apite akagulise Lisale Estate yili kwa TA Nyambi ija yomwe angula ndi ndalama yotibela ife Amalawi amngolemba aganyu kowopa kuti alembe a ntchito akuleba ofesi aziwa inali ndalama yanthu asowa yochita nawo galu Peter lero minda yamakolo athu akuchita kutilimisa ganyu kuti tilandile munda pamene kale ndimwiniwake anagulisayo ndimaklo angwirizana za kasinthasinda llero wagula Peter tikulimisa munda kuti tilandile ine sindingavotere dpp ndapenga chani

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov วันที่ผ่านมา

    Palibe chinthu chondinyatsa ngat kukhala sapota wa dale ndimakonda mpila basi zinazo umavutika nazo kuzuzidwa ngat ukusapota jehova

  • @StephanoIssah
    @StephanoIssah 2 วันที่ผ่านมา

    Chipan chaximayi ochosa mimba what about chakwera

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 2 วันที่ผ่านมา

    Koma umphawi si zinthu, ka 2000 kakugwira ntchito.

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 วันที่ผ่านมา

    Akapusa mtafunireni

  • @clairemyegha4315
    @clairemyegha4315 2 วันที่ผ่านมา +1

    Ma lorry yayendapo apa musadandaule

    • @amtvmw
      @amtvmw  2 วันที่ผ่านมา

      😂😂

  • @JohnChiwaya-ym5me
    @JohnChiwaya-ym5me วันที่ผ่านมา

    Anthuwotu ngochokera mmaboma ena

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 2 วันที่ผ่านมา

    Chakwera mboleyake

  • @daudicassim
    @daudicassim 5 ชั่วโมงที่ผ่านมา

    achakwera...mukufunika..kuti..mupite..kuchipatara..akakuyeseni
    Mutuwanu...sukugwiranjito

  • @LinlyMathewe
    @LinlyMathewe 2 วันที่ผ่านมา

    Musayiwaletu anthu Ali ndi njala abgothamangura zilizonse 😂😂😂😂😂😂😂

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 2 วันที่ผ่านมา

    Garu iwe crocodile ndi team yako yonse nonse ndi mbuzi zawathu zasatanic chikangawa

  • @RamsonKomwa
    @RamsonKomwa 2 วันที่ผ่านมา

    Eni Blantyre anangoima nkumaonelera kwinaku akutonza

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 วันที่ผ่านมา

    Muzalila mayo mayo come September boma ndilomweri

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 2 วันที่ผ่านมา

    Malole mukuwanenawo sitinawawone bwanji pakameza pano zimene mukupangazo ndimabodza opusa mukudzinamiza nokha zilingati munthu wakhu malolewo ayendamwamba Kodi chinantingi chawanthu chonsecho ndimalole angati munthalika wakupengetsani eti

    • @MayaMilanzie
      @MayaMilanzie วันที่ผ่านมา

      Ndipo ineso ndikudabwa coz pakameza roundabout ndinali pompo sindinawonepo rolly yochokera ku lilongwe angosowa zokamba anthuwa

  • @GloriaKamwendo-w2h
    @GloriaKamwendo-w2h 2 วันที่ผ่านมา

    Nde mwati alandira ma 5 handede

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w 2 วันที่ผ่านมา

    Mukutenga.antyu.kudesa.kupita.nao.kubarataya.sanyau.basi

  • @OwenMunde-d8i
    @OwenMunde-d8i 2 วันที่ผ่านมา

    Tika votela dpp bs athuwa akungofuna atsimikize kut ndameneyu akushoka uja 2025

  • @PreciousSteven-e5s
    @PreciousSteven-e5s 2 วันที่ผ่านมา

    Anthuwotu akufuna ndalama zogula gaba yachimanga sikuti mkumukonda chakwerayo anthu target yawo akufuna apeze kandalama basi ndiye ma aim awo sikukonda chipanicho

  • @HamitonFrank
    @HamitonFrank 2 วันที่ผ่านมา

    Ngati kumangochi

  • @clairemyegha4315
    @clairemyegha4315 2 วันที่ผ่านมา

    Azimai paja amatengeka ndi salu ndi K500

  • @SekanawoReuben
    @SekanawoReuben 2 วันที่ผ่านมา

    Paja amawanyamula kudeza musaiwale

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 2 วันที่ผ่านมา

    Anthu ena ngopusa boma ndi lomweli anthu mugona ndi njala mxieeeee

  • @Khadija-q9r
    @Khadija-q9r 2 วันที่ผ่านมา

    Koma anthu akabwela piter kumulandila 😂

  • @HamitonFrank
    @HamitonFrank 2 วันที่ผ่านมา

    Anthu wochita kubwera

  • @LucksonChipofya
    @LucksonChipofya 2 วันที่ผ่านมา

    Onyamulidwa muma lole amenewo ndi ma mp a mcp

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 2 วันที่ผ่านมา

    Chisankho chichitike mwa chilungamo tizaone ngati mcp ingapambane

  • @MakheyiChabwera
    @MakheyiChabwera 2 วันที่ผ่านมา

    Zazi

  • @MercyNkhoma-b6h
    @MercyNkhoma-b6h 2 วันที่ผ่านมา

    Koma ndalama anakonza 😂😂

  • @PatriciaChikondi
    @PatriciaChikondi วันที่ผ่านมา

    😂😂😂😂

  • @AliyuhUsumanah
    @AliyuhUsumanah 2 วันที่ผ่านมา

    Chakwera mbuz ya munthu

  • @LimbikaniChirwa
    @LimbikaniChirwa 2 วันที่ผ่านมา

    Ndinachita bwino kusakhala mchewa ,omangosatira zilizose

  • @PeterKainga-e3h
    @PeterKainga-e3h 2 วันที่ผ่านมา

    Koma olo ndalama Zo mpaka kuvinira zimenezi

  • @AwetuAmidu-u2j
    @AwetuAmidu-u2j 2 วันที่ผ่านมา

    Sakuwina chakwela mukunamizaana

    • @FranksonKennethChipande
      @FranksonKennethChipande วันที่ผ่านมา

      Nkhani ili pa ground koma munalembesa???? Tikaonana mu ballot ndipo a MEC anakasintha tsiku September kwatalika

  • @TimothyvascoVasco-j6d
    @TimothyvascoVasco-j6d 2 วันที่ผ่านมา

    Zabodza

  • @LimbikaniChirwa
    @LimbikaniChirwa 2 วันที่ผ่านมา

    Ndinachita bwino kukakhala mchewa

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w 2 วันที่ผ่านมา

    Kkkkkk

  • @LovemoreChiwaza
    @LovemoreChiwaza วันที่ผ่านมา

    akatha aname kut kwadzanza

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 2 วันที่ผ่านมา

    Aaaa anthu amenewo akungofuna kumuona nkhope chikangawa koma sazakuvotera

    • @ChristopherManase-s1f
      @ChristopherManase-s1f 2 วันที่ผ่านมา

      Mukhumudwa inu pa 16 September

    • @GetuChingamba
      @GetuChingamba วันที่ผ่านมา

      Chikangawa party ikagwere ukooo ,,ndipo anthu omati boma ndilomweliwo mmakwawomo si umphawi wakenso