Masapota a MCP inu muzafela eni. Osavala za MCP anthu Ali ndi nkhwiyo. Taoneran

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 58

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 11 วันที่ผ่านมา

    More 🔥🔥 bro tikuvutika ndiye wina kuvala MCP chiti

  • @Okalekale
    @Okalekale หลายเดือนก่อน +5

    Zikafika panenepo ndi nkhondo basi,tithamangepo mwina aMalawi nkuchangamukako,chifine chachuluka kwambiri,umbuli.

    • @IssacMateyo
      @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

      Owo kusonyeza kuti amalawi ndi mbuli iweyo ndiye Muthu kape iweyo

  • @user-ui4ux5kc8d
    @user-ui4ux5kc8d หลายเดือนก่อน +1

    Ntibuleni ndi msalunso yovala imeneyo

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน +4

    😂😂😂 chikangawa party ❤❤

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

    Mwayamba zimenezo amalawi kufuna Kumaoanga zimenezo mufela zayeni ake gayezi kkkk

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733 หลายเดือนก่อน +1

    Mpondeni ameneyo

  • @bobykhan3583
    @bobykhan3583 หลายเดือนก่อน

    The funny part ndiyot ndiochewat omenew😂😂😂Mcp is busy saying achewa love the party nonsense😂😂

  • @user-jl6sq3ph1b
    @user-jl6sq3ph1b หลายเดือนก่อน +1

    Kumene tikawona ma sapota a mcp tiziwapanga choncho basi aluta kothinuwa sitikuopaso panopa nafeso tipanga za kenya 🇰🇪 kapena hamas kuionesa nyekhwe Israel 🇮🇱 nafeso tiziinonesa nyekhe mcp osawopa osafowoka ziko ndi lathu ili 😂😂😂😂

  • @StevenMsuku-w4j
    @StevenMsuku-w4j หลายเดือนก่อน +2

    😂😂😂😂 tambala uja kuno akusenda kuno

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo หลายเดือนก่อน

    Thawi yakwana kuti achinyamata agwilitsidwe tchito basi kkkkkk

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td หลายเดือนก่อน

    Mwamupezela ameneyo adzaphwetsa mimba yonyasayo anyamata upitilize udziwanso ndale zaukape wenanso ndiumbuli wandale kumavomeleza ndiye nkhanza a DPP mukupangila odzavota muwina zopusa basi pezelani yemweyo mukunya mukapitiliza tiyenazoni

    • @AkayikosyagaMarsha
      @AkayikosyagaMarsha หลายเดือนก่อน

      Kulibwinokukhala mbuli kusiyana NDI kumpha anthu osalakwa

    • @AkayikosyagaMarsha
      @AkayikosyagaMarsha หลายเดือนก่อน

      Iwe ndimakuziwa bwino bwino Maso Anga Ali paiwe .we are waiting for you bra

  • @oburybindula-nf7ek
    @oburybindula-nf7ek หลายเดือนก่อน

    Kkkkkk big up brother anyere ameneo akungotisaukida iya

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp หลายเดือนก่อน

    Zakalekale izi

  • @marcuswalker2613
    @marcuswalker2613 หลายเดือนก่อน

    I hate mcp with a passion but this is so wrong
    This guy was supposed to be arrested and punished accordingly😢 this is inhumane and DDP was/is supposed to apologize and disassociate itself from this type of behavior that has no place in any democratic dispensation

    • @AkayikosyagaMarsha
      @AkayikosyagaMarsha หลายเดือนก่อน

      Before mumange Kaye Kukuyu amene anamupha witika

    • @Okalekale
      @Okalekale หลายเดือนก่อน

      @@marcuswalker2613 I used to like the DPP of Bingu,this brother of his has divided the nation,his politicking is dirty,look at cadets.vote rigging etc.DPPs leader encourages this type of behaviour,he's simply a very bad and dangerous politician who if left unchecked will plunge the country into civil war.

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m หลายเดือนก่อน

    ameneyotu mwampanga bwino ndithu chifukwa anthu okonda yemusipi ameneyo ali ngat anthu owononga dzikoli dzikoli akuononga ndiawa amcp

    • @Okalekale
      @Okalekale หลายเดือนก่อน

      @@user-hx6ly3cl8m Chitsiru iwe MCP yalowa liti m'boma lophatikizanali?.MCP 1994 inalisiya dziko likuyenda bwino,chuma chikuyenda bwino.Dziko linaonongedwa ndi UDF,PP ndi DPP ya dad wanu ombwambwanayo,Bingu yekha ndi amene anali machine.Kumalankhula zeni.Unabadwa liti iwe?,ukudziwa chuma cha Malawi m'mene chimayendela nthawi ya MCP mbavazi zisanabwere iwe?.

  • @EuniceSomanje
    @EuniceSomanje หลายเดือนก่อน

    Kkkkkkk asazavalesodi kape ameneyo😂😂😂😂

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y หลายเดือนก่อน +1

    Kkkķkk MCP you mast go

  • @coastersRob
    @coastersRob หลายเดือนก่อน +1

    Jomo uyu kkkkk

  • @Vanheizchitseko
    @Vanheizchitseko หลายเดือนก่อน

    Watching keenly😅

  • @FrankSimfukwe-w1s
    @FrankSimfukwe-w1s หลายเดือนก่อน

    Ukanampatsako makofi awili atatu ku dzimakutu zakezo zitseguke nkuvadi kuti chisazavaleso

  • @IssahAluba
    @IssahAluba หลายเดือนก่อน

    kuona wa MCP kuwotcha Moto bas

  • @user-zt7hy5lh4r
    @user-zt7hy5lh4r หลายเดือนก่อน

    Koma chikangawa party abale 😂😂😂

  • @MaggieMuhone-r7m
    @MaggieMuhone-r7m หลายเดือนก่อน

    Kkkkk

  • @andrewjchalunda
    @andrewjchalunda หลายเดือนก่อน

    This one he needs compensation from the party

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs หลายเดือนก่อน

    Kulakwa aiyese alindiufulu

  • @OsmanPatrick
    @OsmanPatrick หลายเดือนก่อน

    Anthu amafika potopa Robert chiwamba

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 หลายเดือนก่อน

    Izi zinachitikadi kale koma zochitikenso kambirimbiri.

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂 Malawi wafikapo

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b หลายเดือนก่อน

    😂😂😂❤❤

  • @Standwell78
    @Standwell78 หลายเดือนก่อน

    😂😂 km gyz mlidi serious

  • @richardmasina5454
    @richardmasina5454 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 หลายเดือนก่อน

    Kkkk km yomweyo chikangawa

  • @Okalekale
    @Okalekale หลายเดือนก่อน

    Democracy akuyidziwa kuti ndi chani ameneyi?,kapena anangoyifuna samadziwa kuti amafuna chani?,mbuli ngati izi ndizimene zili adani adziko.Kodi mesa democracy ndiye kuti anthu anafuna zipani zambiri (multi paty) kuti anthu azisankha okha?.Ngati iyeyi amakonda chipani china ndindani amene anamukakamiza?.Mbuli zinazi,akuti ma phanza?

    • @faithkafuliza-gf9or
      @faithkafuliza-gf9or หลายเดือนก่อน

      Kkkkkk

    • @user-jl6sq3ph1b
      @user-jl6sq3ph1b หลายเดือนก่อน

      Iwe ku Lilongwe kumene amawamenya azipani zinako iwe wa chamba eti usamayakhule zakozo apa wamva iwe zizikoma galu kuluma ng'ombe kma ng'ombe ibwezela ndie democracy kwanuko 😂😂😂😂 tizibwezela ka

    • @Okalekale
      @Okalekale หลายเดือนก่อน

      @@user-jl6sq3ph1b mbuli itinso iyi?.Musachititse anthu anzeru zawo aku m'mwera manyazi komanso
      uzilankhula mosamala chifukwa sitikudziwana,wanva?.
      Ma savage,useless people in our beloved country you're .You're starting civil war and you gonna be first casualty.

    • @Okalekale
      @Okalekale หลายเดือนก่อน

      @@user-jl6sq3ph1b kkkk,with fools like you I don't argue

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน

    Matama koma akugona ndi njala mumakomo mwaomo

  • @JamesOsman-cz9cw
    @JamesOsman-cz9cw หลายเดือนก่อน +1

    Kkkkkkk

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp หลายเดือนก่อน

    Kkkkk mcp yata 😂😂

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred6539 หลายเดือนก่อน

    Osanyengelelayi

  • @Yoxym
    @Yoxym หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂😂😂😅😅😅

  • @brightphiris.c3387
    @brightphiris.c3387 หลายเดือนก่อน

    Kuti kumeneku?

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz หลายเดือนก่อน

    Kkkkk

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂😂

  • @AnnastasiaChakwiya
    @AnnastasiaChakwiya หลายเดือนก่อน

    Kkkkk

  • @MemoryKamanga-jv4jh
    @MemoryKamanga-jv4jh หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂

  • @yusufbreak905
    @yusufbreak905 หลายเดือนก่อน

    Kkkkk

  • @IreenMughogho-z6f
    @IreenMughogho-z6f หลายเดือนก่อน

    😂😂😂😂