Wayakhula mosaopa ndipo Chilungamo chimawawa Achakwera mukuva bwaaa??

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 38

  • @jomochirwa
    @jomochirwa หลายเดือนก่อน +10

    Mukutililitsatu imfa za anthu amenewa esh kunena zoona mcp imafunika ibanidwe isadzayimileso chisankho chilichonse mdziko muno esh .

    • @cynthiandekhakatundu6890
      @cynthiandekhakatundu6890 หลายเดือนก่อน

      Ndikanakhala wa lamulo ine ndikanatero ndithu .... Abale / abwenzi / alongo afa imfa yowawa

    • @user-no2mx4go8p
      @user-no2mx4go8p หลายเดือนก่อน

      Chilungamo cheni cheni

    • @SolomonNjolomole
      @SolomonNjolomole หลายเดือนก่อน

      Achakwera akakhala akumatinji mkati mwa mtima zoopsya kwambiri kuyipa mtima.

  • @lyiemax
    @lyiemax หลายเดือนก่อน +3

    Talking wisely ndipo osaopa, osafooka, forward ever and backward never 🔥🔥🔥🔥

  • @KennedyKanyama-ce8lb
    @KennedyKanyama-ce8lb หลายเดือนก่อน +3

    Kuyankhula kwamzeru uku. Ndakunyadilani braz. Ineo ndinasunga mau a skc osaopa. Osafoooka, osatopa. Ndipo ngati kuli kufa tifera mbendera imeneyi.

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน +2

    😢😢😢Eish mulungu alowelerepo

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td 26 วันที่ผ่านมา

    Iwe usatengele mwayi pa IFA yanzako Siya zibwana udzapanga manyazi Mwana iwe

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 หลายเดือนก่อน

    MCP ikumva kuwawa kuposa.mmene inamvera kuwawa DPP nthawi ya milandu yama vote ija😂😂😂

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 หลายเดือนก่อน +1

    Chakwela anyanayo game yakulila dzedi sopano dzipani dzotsuya tawonjezelapo UTM atakomana ndi NYENKWEEEE KU MCP MALINDILIDWA KOMA MUKODZEKELA KUKOMANA NDIMATSAUTSO ASATI MATSEWELA muthalika mukamunyodza popanda otuma a police kuti akayankhepo molandu KOMA FITI MUNAYIKA PAPANDOYI NDE KODZEKELA KUMANDIDWANO MCP NDI ACHIPANI CHIMODZI NDE ULAMULILO OMWE AMAUDZIWA IWO UMENEWO

  • @MaryJefry
    @MaryJefry หลายเดือนก่อน +1

    Achakwera zanu zada basi

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246 หลายเดือนก่อน

    This generation achakwera mukumva kuwawatu eish . Mwachita bwino kuyankhula mosanyengerelayi

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw หลายเดือนก่อน

    Koma mukubwera bwino tikulirabe amalawi

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 หลายเดือนก่อน

    Anasewera game yoduka

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga หลายเดือนก่อน

    Kuseweretsa malirotu uku.chibwana chenicheni.Generation yotembereredwa iyi

    • @louisbonongwe8537
      @louisbonongwe8537 หลายเดือนก่อน

      And the sad part is that iweso uli mu generation yotembeleledwayo.u ar such a beautiful and humble idiot.u have no sense.

  • @peterchikwakwa8476
    @peterchikwakwa8476 หลายเดือนก่อน

    Zamphamvuuuuuii❤❤

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif9556 หลายเดือนก่อน

    MTSRIP 🌹 ameeen,tisaope tisatope

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x หลายเดือนก่อน

    Chakwera ali pa uluru koopsa mmmm😂😂😂😂😂😂

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg หลายเดือนก่อน +1

    Chakwela anyaa

  • @HoseKatsekera
    @HoseKatsekera หลายเดือนก่อน +1

    muzeni avetse

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga หลายเดือนก่อน

    Mmmmmm lindani madzi apite .mfulumira ngwanji

  • @MphatsoMhoney-xn2ft
    @MphatsoMhoney-xn2ft หลายเดือนก่อน

    UTM Danger ⚡✨⚡

  • @DaitonBashir-it4ye
    @DaitonBashir-it4ye หลายเดือนก่อน

    Malawi yonse ikulira

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 หลายเดือนก่อน

    Mulungu ayi thandize

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r หลายเดือนก่อน

    Kodi ngozi ikachitika andale opanda mzeru amawona ngati msangulutso makamaka pa ifa ya chilima anthu opusawa akutengerapo compain paja ngozi ya ndege sinachitikepo mmalawi eti ooooh 😅😅😅ndawonaera mbuli ndi zambili anazolowera ngozi ya galimoto basi or mutani ine sindindidzavoteranso DPP or utm because ifa mayilowetsa ndale koma simudzawina 😅😅😅😅 because kuli Mulungu kumwambaku amayika pa mpando yemwe iye wafuna osati yemwe anthu afuna ayi DPP anthu akaphedwa mwayiwala dala lero ndi yolungama 😅😅😅 zaziiiii utm itha Ngati makatani nayoso mudzachita manyazi ndithu malankhula nkhani zopanda umboni mpakana lero palibe minthu akubweretsa umboni woti chilima amaphedwa umbuliwu si wabwino ndithu anchita bwino ambuye kuvomereza kuti chilima atsogole enaftikupita komweko koma bola kufa ndi mbili yolalikila za dzina la yesu osati dzina la ndale 😅😅😅 aaah palibepo mzeru pamenepo moti Ngati chilima anga maganizo mwake mutadzadza za ndale aaah yesu akabwera sakudzuka nawo pa mdzukilo woyamba wa anthu olungama koma mdzukilo wochiwiri ndiwomwe adzawukitsidwe komatu wakumoto kukakolola ndalezo palibe apa adzapite kumanda ndi udindo Umathera pomwepano basi ndiye pempho langa anthu andale asiyeni amafuna zawo ziwayendere bola ali pa mpando DPP Mulungu anayichotsa pali MCP akafuna ayichotsa kapena ayi ndiye vuto ndikuvonereza kuti ndachotsedwa pa mpando wa president ngati mmene achitira APM dziko ili limafunika kuthandizana mzeru Kuti litikuke koma kumalawi amadziwa kusemerana chirombo basi chikondi chinatha kalekale tinabadwa tisakudziwa za ndale,lero ndale tazidziwa zachotsa chikondi ndiyetu kumangopha ma alubino Ngati nkhuku munthu wayiwala lero akuti DPP ndiyo yabwino chifukwa cha ifa ya chilima 😅😅😅 wafa ameneuja kwake kunatha basi ndawona ngozi za ndege zikuchitika koma osapsa ina inagwa anthu osnse anali momwemo anafa okwana 693 ndiye mukanene chilima wapambana chiyani ndi ngozi imeneija ndithu awaa umbuli uli thooooo mudzapita kumanda ndi mabodza inuwo ndithu work up time is almost finished Jesus Christ is coming soon get ready before we die I love you All ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️🥰🥰🤗🤗🤗

    • @jonasbanda5605
      @jonasbanda5605 หลายเดือนก่อน

      Koma muli zochita angawerenge chonsecho ndani ku malawi kuno 😅😅😅

    • @user-bd5kw8oq1r
      @user-bd5kw8oq1r หลายเดือนก่อน

      @@jonasbanda5605 kkkkkkkk 😊❣️ werengani abwana mwasswera koma

    • @JamesNgwaya-vz1ox
      @JamesNgwaya-vz1ox หลายเดือนก่อน

      Mbolo yosadulayo adaa

    • @user-bd5kw8oq1r
      @user-bd5kw8oq1r หลายเดือนก่อน

      @@JamesNgwaya-vz1ox wanena wekha mnene ulili mbuli iwe

    • @user-bd5kw8oq1r
      @user-bd5kw8oq1r หลายเดือนก่อน

      @@JamesNgwaya-vz1ox ndathokoza powerenga zaphindu mpakana kudananazo zilibwino kudana ndi chilungomo koma bodza 🥰🥰🥰🥰🥰🤗🤗

  • @andrewchiusiwa3487
    @andrewchiusiwa3487 หลายเดือนก่อน

    Siine wa MCP koma, having a channel choti mukuonetseraso mbali yomwe muli makes your channel so boring. I regret subscribing to your channel, ndikutulukani. Why can't you just be neutral and allow your followers to choose their sides politically?

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน

      @@andrewchiusiwa3487 msonkhanowo ndi Wa anthu a UTM asakudziwa ndani kodi???

    • @kennedychinguwo1640
      @kennedychinguwo1640 หลายเดือนก่อน

      Unsubscribe baba,you are not forced@andrewchiusiwa

    • @andrewchiusiwa3487
      @andrewchiusiwa3487 หลายเดือนก่อน

      @@user-qp8kh2hj9o Everyone knows it, nde palibepo chifukwa chomuwoyeza chakwera on a title of this post. That's just being childish and immature. If you want the channel to grow, learn to be professional. Phunzirani kwa anzanu a BBC, CNN, or even your local channels back there in Malawi...

    • @andrewchiusiwa3487
      @andrewchiusiwa3487 หลายเดือนก่อน

      @@kennedychinguwo1640 Well, I've just done that. I'm fast realizing I subscribed to a kids channel.. even the followers looks more of kids themselves

    • @kennedychinguwo1640
      @kennedychinguwo1640 หลายเดือนก่อน

      @@andrewchiusiwa3487 🤣🤣🤣🤣🤣

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba หลายเดือนก่อน

    Maliro kupangira campaign
    Kuyaluka.