We don't want failed leaders like chakwela. a person without mercy and I have never seen a leader as cruel as chakwela and we made a mistake to put a beast in the chair we are suffering a lot from us
Ma soldier amakwera ndege koma Lero kulibe akukwera ma TATA ndi kasinja😢 chakwera full of sheet kwabas analolera kupha ndikuononga Chuma cha a silikali za ugalu
Chikangawa manyadzi bwanji apule kwanutu kumeneko mwalephera kuyendedza dziko la Malawi 🇲🇼 bas mr president vomelezani bwana bwelera ku chipiku bas kkkkkkkk Apm is coming soon to be president of this country we love Malawi 🇲🇼 guys 🇲🇼 👦 ❤️ 💙 😀 👏 🇲🇼
Mr president Chakwera pls ndikukupepheni kuti tayesani kusitha ngati umaonera misokhano inayi ngati unali kulilongwewu wa dpp move zimene athu akudandaula my beg is do something before it's too late Mr prezident
Ndikuona kuchedwa kuti 2025 ifike ndikavote APM is my vote 🎉🎉🎉🎉🥳🥳🥳🥳♥️♥️♥️♥️
National Director wa amayi walankhula facts
APM my vote from Lilongwe
Apm my vote 🗳
History is the best teacher
My tears r flowing like flooded river the suffering iz too much
Good speech mama❤
Another Gerrizedaaa Jeff uyuuu
Apm my vote
From Mozambique 🇲🇿 apm my vote ❤❤❤
Akuti Dpp inali yoipa koma MCP ndiyoipa times 3😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Apa madzi achita katotondo Lilongwe yayankhula ndipo anthu akwiyadi MCP no more matsiku awo atha azikozekera ulendo okayambilaso
Jealous down this is DPP woyee
Wina akukwiya sinanga anazolowela kudya matewera
Malawians lets just put everything into the hands of the Lord for abetter leader
The Almighty God is with us..let's pray hard for his intervention..we will conquer
I love Mama mumativesa kukoma dpp my vote ❤
Amayi awa angakusekulitse mmimba 😂😂😂😂
Nice mama kulakhula kwabwno moyo waduru kwambiri
Life is hard to be honest,zinthu zikuvuta Anthu oti Ali paganyu what more munthu oti sagwira ndi ganyu yomwe,lord have mercy upon us
Very true broh mulungu atithandize
I'm washing form south Africa roodipoort my vote dpp❤🎉
From mozambique🇲🇿 APM my vote
Mzimai aliyense akuoneka okongola akavala makaka a DPP
Trumph wa kumalawi ndi peter mutalika 😂😂😂😂😂😂🙏🙏🙏🙏🙏
Ndizoonadi koma Trump wakuno ndi APM 🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤
From Moçambique 🇲🇿 apm my vote ❤❤❤
We don't want failed leaders like chakwela. a person without mercy and I have never seen a leader as cruel as chakwela and we made a mistake to put a beast in the chair we are suffering a lot from us
APM my vote
History is the best teacher you mase know kamajekete😂😂
Apm my vote ❤
Exactly mama
We have no food in Malawi 😢
Anthu atopa Chakwera step down
Times ndi 1
Kkkkkkkkkk achakwera zikuvutani zikuwonesa anthu ataya hope kwanuko
Pachisena zikafika apa timati MCP (apichimwana apinyera)
Kkkkkkk
Kuyankhula movekabwino uku👏👏👏
my vote 🔥🔥🔥
ichi ndiye chapani chathu nangati DJ gona paja waituluka MCP ine ndi ndani kt ndisaituluke😂😂
Eh ndipo muwuvuniditu salary k50 rent k30 yotsala k20 ah zithudi zavuta
Kkkkkkk Brian akut nkhwimbi
Apm my,,,,,,,🤩🔥🔥
Koma mayi uyu anakonza😂😂 akut hadadi hoyeeeee❤
Nibodza ilo ❤❤❤❤❤❤❤ MCP my vote
Auzeni anebayo mcp yanya bass akukuyu mulipo chimwendo kamanjekete 😂😂😂😂😂😂 apm my vote
DPP woyee
Take it or leave it
DPP my vote from USA
Nthawi ya kamuzu 1 dollar 1 kwacha, pano zukanika bwanji
Pampando Pali mbuzi ndi agalu okhaokha Maka Mchewayu ndi uuuuuh kudontha kokhakokha
Akuti potchula wanna dzina m'dziwona😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Chakwera
😂😂😂😂😂😂😂. Ayi inuyo ndi number one mumatha
Ma soldier amakwera ndege koma Lero kulibe akukwera ma TATA ndi kasinja😢 chakwera full of sheet kwabas analolera kupha ndikuononga Chuma cha a silikali za ugalu
Wow abwerere bas
Banja la amuthalika ndi lodalitsidwa apm ku state house keep it up
Wa MCP APAPA NDI MFITI UFRESH PAKANA 600 TIZABWERA KOMA MOCHEDWA DZUWA LANYANYA KUMALAWIKO TUZABWERA BOMA LIKASITHIDWA😢
God bless my apm
Apm my vote anemu mwanza
Cathe ndi Brian muzabweleko ku nsanje muzamve mafala😅
APM woyeeeee!!!
Lilongwe wooyeee chinsapo woyee azimai muuzeni chakwerayo kuti amvetsetse,iwe chakwera tula pansi utsgoleli walephela, aliyense akulira
Yes zatikwanadi ambiri
Chakwera sakulemekeza national anthem yathu ... Njala .nthenda. Nsanje zonse mza chakwera akanangofa bas
APM akulowa basi olo popanda kuvota...Azingodikira nthawi yomwe yidayikidwa yokakhala ku State
Ndipo inu a MCP ndinu agalu nonse razalo chakwera ndiwe mbuzi
Dpp woyeeee
Chikangawa manyadzi bwanji apule kwanutu kumeneko mwalephera kuyendedza dziko la Malawi 🇲🇼 bas mr president vomelezani bwana bwelera ku chipiku bas kkkkkkkk Apm is coming soon to be president of this country we love Malawi 🇲🇼 guys 🇲🇼 👦 ❤️ 💙 😀 👏 🇲🇼
Wacthing from cape town kkkkk ati kamajekete
Ine anemu Anu ku mwanza kuno koma my home village is phalombe alomwe nophiya
😂😂😂😂 koma Brian akuti ai msatero
Koma anthu atopad nde mwati Chakwera mukamusiya Kuti??????????? Koma azimayi 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Ndipo 2025 eeeee ndikuona kutalika kma aaaa masiku akuthera kuchitseko APM my vote 16 September 💙💙💙💙💙 2025 bomaaaaaaaa
Boma ilo!!!!! 🔥 🔥
DPP boma lokomela aliyense,ku MCP kulibeko president kuli vacant
Mr president Chakwera pls ndikukupepheni kuti tayesani kusitha ngati umaonera misokhano inayi ngati unali kulilongwewu wa dpp move zimene athu akudandaula my beg is do something before it's too late Mr prezident
😂😂😂😂😂 akut kamajekete😂😂😂
Through BMTV 😂😂😂😂😂😂😂
Anthu zakwana zochitikaza MCP
Low model Brian, APM my vote
Live in SA
APM all the way
Komatu Bryan mafuso amenewa ndiotani kodi kkkkkkkk
Wow
Mamah mumakhala ❤❤❤APM
Koma zoti kuli smartmatic mukuziziwa😮
Proffessor mabig boys MCp small boys kkkkkk😂😂😂 koma kwatelera
replacement ya gelezeda jefule uyu kkkkkk
Naye Banda amapeleka direction Ali ndi mkhwizi
Guys let's try utm awa analephela pls pls pls
Ati azibambo akuzelezeka pano koma azimayi amaonaso eti 😂😂😂😂😂
Koma ada avala t-shirt ya white ndi future minister
Ali mfundo heave
MCP ibwelere Ku dabwe
Dpp woyee 📌
Watching 4rom Namibia Walvis Bay Adad woyeee Trump waife
Tikupanga za Adadi. Mtima ukuwawa kwambili.
Ma shaver mpaka 800 kwacha,,, Inu boma ili litipha ndi mavuzi..
🚶🚶🚶
Masten munayenera kuwathandiza anthuwo kuwapatsa chimanga or chakudya china monga mmene wanenera reverend Kawinga..... Osati ndadya nawo mango ine kumwera madzi mpaka panado yet mukuziwa kut mukadyaaa zolongosoka kwanuu
Akuyankhula sinzika zaku Lilongwe ndiogulitsa nthochi ndimapeyala akumwera awa.
Pasana pako
Apm l❤ u always
Mcp yaludza,koma azayenda kupanga kampeni?mwinatu kwa sundwe😂😂😂😂😂😂. Galatians oputsa oyamba ndi zabwino kumalidzila zoipa.malawi,asithe basi
Mkulankhula kwaanthu ena munkati kwa M'gona anthu ambiri ndi alomwe, kodi ukunso kuli alomwe,,, gulu limeneri😂😂😂😂
Azimai alusatu awa😂😂
Koma amati chosadziwa anaimbila mfiti mmanja ndipo.taimbiladi osati masewela wadzudza miyoyo ya wanthu ambiri pamalawi kudyesa wanthu ziteze yoooh
Paulendoooo paulendoooo ayeeer paulendo akuti adad khomzekani Boma ndilanunao ili
#Dpp my vote die hard weniweni🤜🤛