Zoona boma lanzeru lingamasangalale kutumiza anthu kunja kuti azikalimila mayiko ayeni chonsecho kuno Minda bwee koma tikukanika kuti tiyilime,nde pamenepo muziti pali nzeru?.azikachita kuzipopa kuti boma la Israel 🇮🇱 latiyamikila popanga machawi zoona zimenezo. Lets be serious sometimes as a country, ndetizi nde maso mphenya a malawi 🇲🇼 2063 shameless government ever.
Boma ili palibe po chamzeru chimene akupanga, akumkuyu amakonda kunama, and boma ili wonse ndi wonama wokha wokha komanso kumkuno kumalawi kuli nthaka yabwino madzi wosayambitsa zaulimi konkuno kuti achinyamata wa adzipeza ntchito konkuno, mukutukula dziko la adzanu lochita bwino kale nde pamenepo dziko la Malawi lingapite patsogolo?
Gwilizano uwu apanga nawo changu kwambri kuposa mbuyomu 😂😂😂gwilizano womupha chilima apanga nawo changu kwambri boma la chakwera atimaliza tonse ndithu 😅
Some nationals are living Israel today because of the situation in Israel and yet our government are busy sending people to Israel what is that
Amalawi .maka maka achnyamata ndiife anthu ogona kwambiri zoona tikulorera boma loputsali kumatiputsitsa kuti bwnji boma ngati lokonda anthu ake lipange create ntchito ngati zimenezo konkuno kumalawi eish kom guys
😂 akunama awa akufuna kutawitsa athu choliga asa vote 😂😂😂😂
Zoona boma lanzeru lingamasangalale kutumiza anthu kunja kuti azikalimila mayiko ayeni chonsecho kuno Minda bwee koma tikukanika kuti tiyilime,nde pamenepo muziti pali nzeru?.azikachita kuzipopa kuti boma la Israel 🇮🇱 latiyamikila popanga machawi zoona zimenezo.
Lets be serious sometimes as a country, ndetizi nde maso mphenya a malawi 🇲🇼 2063 shameless government ever.
😂😂 ma politician wa ndi ma mafia tsogolo palibe
Zovesa chisoni kwambiri 😢
I don't believe in this ka magalas.i
Ku malawi kulibe athu oganiza bhoo
Zonsezo ndi zauchitsiru.dziko lingamatumize anthu kukalima Ku lsraeli?ukoko a Malawi akadzaphedwako mwaunyinji ndipamene padzakhale fullstop.a Malawi ndifenso zitsiru.
Amalawi umphawi ndi wathu ,ku Israeli kuli nkhondo mkutuma Anthu ku nkhondo Kodi Amalawi sitisamala za moyo wanthu
mamafiya aboma muzasiyaliti kunama
Akufuna achepese chiwelengelo Cha mavote chifukwa akudziwa kuti achinyamata ndi a utm
Koma amalawi sazatheka chosecho amat ndalama amasunga ndi agent kupusa basi kulima kowawaku ndalama osayiona 😂😂😂
They cann't use Malawi slot because slots are governed by passport...hence that ask don't arise Wonder Msiska
Boma ili palibe po chamzeru chimene akupanga, akumkuyu amakonda kunama, and boma ili wonse ndi wonama wokha wokha komanso kumkuno kumalawi kuli nthaka yabwino madzi wosayambitsa zaulimi konkuno kuti achinyamata wa adzipeza ntchito konkuno, mukutukula dziko la adzanu lochita bwino kale nde pamenepo dziko la Malawi lingapite patsogolo?
Mpaka ma demo nkhani yaku isilayel guys kumakhala serious 😅
Chimene akufuna achakera ndiowazungulira mchakuti tipite ku Israel iwowo agulitse dziko akatipeza pambuyo😂😂😂😂
Ng'ambi ndiwe mbuzi yamuthu..ukayamikire kunkuyu.boma lake litiro
Km
Galu kwabasi