Peter Muthalika wati 2025 awina ndipo Boma lake lizakomera liyense. Wayakhula lero.

แชร์
ฝัง
  • เผยแพร่เมื่อ 23 ส.ค. 2024

ความคิดเห็น • 26

  • @MfipaKapwera
    @MfipaKapwera หลายเดือนก่อน +5

    May God bless you, so that you can save Malawi from the mouth of thugs.

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3e หลายเดือนก่อน +4

    May Allah protect this man

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete หลายเดือนก่อน +2

    Please muzasiseko cement ndi malata nyumba yanga chiimileni mu 2021

  • @user-ek1um1ie3e
    @user-ek1um1ie3e หลายเดือนก่อน +3

    Apm my vote

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d หลายเดือนก่อน +3

    Ndipo boma lokomeladi aliyese osati lakupha kuba ndi kuononga la satana chakwela muthu oti kukamuchela kumangoganiza za upandu basi ndipo mulungu achilange komwe chiliko mawa chisazuke

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc หลายเดือนก่อน +2

    Akadzawina azachonse, American embassy,ngati sazatelo,azachonsedwatso.amalawi,tilibe two koloko.ichi,chilipochi,chichoka,2025,ngati sitichichotsa,ndi ma demo

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 หลายเดือนก่อน +3

    Mwina fertilizer uja mkufikanso pa 21 pin paja osati 100 thousand 1 bag, olo atafika pa 35 bolabe

    • @chadreckchibwithala1493
      @chadreckchibwithala1493 หลายเดือนก่อน +1

      agogo msanamize anthu aaa lokomera zigewenga za chilomwe aaa mwakalamba echi mcp simungayi2ine inu mwachepa kwambiri

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 หลายเดือนก่อน

      Alimi ife fertilizer ndi otchipa urea ndi 85000 koma tikugulitsa two bags ya chimanga kugula thumba ali pa 21000 timagulitsa matumba 7 kt tigule thumba limodzi alimi sitikudandaula fodya amagula no sale lero 600000 bale limodzi tikuva kukoma chakwara 2030 wooooooo

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 หลายเดือนก่อน +3

    Dinner ija imenei?
    Mukawagwira asilikali a ku ruandawo mungoapha tione kuti mbuyawo anena kuti chani.

  • @JohnMwafongo
    @JohnMwafongo หลายเดือนก่อน

    Winayo akut ooh yes zaziiii

  • @ElizabethMajiga
    @ElizabethMajiga หลายเดือนก่อน

    Ana achakwela mulibwanji pano mukumva nyunyutu apa😂😂😂😂😂

  • @NDIZOTHEKABANDA
    @NDIZOTHEKABANDA หลายเดือนก่อน

    Mmmmmmm Inu znakukanikan kale mukunamapochan apa tyen uko isaaah!!!!!

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg หลายเดือนก่อน

    Boma iloooo

  • @kennethmatamanda9057
    @kennethmatamanda9057 หลายเดือนก่อน

    Boma lake la ntholotu nanga lomweli ndikuliziwali,zanu zinapita bs koma ngati boma la nthyolo mukuza kukawina bs

  • @PricillaKanyangama
    @PricillaKanyangama หลายเดือนก่อน

    Boma ilooo

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 หลายเดือนก่อน

    Tsanko lija adzasiya kod kubera alimi fodya adzasia njanje akozayi sadzaletsaso kod auction Canberra 42billion abweza kod malawi leaf 🌿 adzayipatsa ndalama zogulira fodya anayiberayi kod? Ma no sales anja anali ku auction mufuna abwereso kod dpp ndi alimi ndiye ayi sitiyifuna or kuva dzina

  • @kingsleyhopematchaya5184
    @kingsleyhopematchaya5184 หลายเดือนก่อน

    Zachipani amakapangira kunyumba kwamuthu mugofuna kumumalizira tindalana tinatsala apm ana adad mmagalimotomu mudzayabeso aaaa zosatheka mulungu salora kt mudzabeso zinakukwanani zomwexija manyazi mulibe? Athu atsakho lodutsa mlingo misewu mumakoza ku mmwera kokha agalu

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki หลายเดือนก่อน

    Same what's up group! Unless you change otherwise malawi will remain a farm of politicians.

  • @FazilaJames
    @FazilaJames หลายเดือนก่อน

    A dad liomboleni dziko lanthu moto

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 หลายเดือนก่อน +1

    Nonsense

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o หลายเดือนก่อน +1

    Zaziii ukhutukumve uja mwasiya😮😮

  • @ganizanitembo1492
    @ganizanitembo1492 หลายเดือนก่อน +1

    I think you should rest sir why African leaders you have been tried and rejected don't take advantage of the people please

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 หลายเดือนก่อน

    inu agogo msanamize anyh1

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o หลายเดือนก่อน

    Sindikunva

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza หลายเดือนก่อน

    Lakula ndi dyela nukalowa boma muzayambilanso zanu zija aaaa